Ezekiel 25 (BOGWICC)
1 Yehova anandiyankhula kuti: 2 “Iwe mwana wa munthu, tembenukira anthu a ku Amoni ndipo unenere mowadzudzula. 3 Awawuze kuti, ‘Inu anthu a ku Amoni, imvani zimene Ambuye Yehova akunena. Iye akuti: Inu munanena mawu onyoza pamene Nyumba yanga yopatulika inkayipitsidwa. Munanyozanso dziko la Israeli pamene linaguga ndiponso anthu a ku Yuda pamene anatengedwa ukapolo. 4 Nʼchifukwa chake Ine ndidzakuperekani mʼmanja mwa anthu akummawa ngati cholowa chawo. Iwo adzamanga misasa yawo ndi kukhoma matenti awo pakati panu. Adzadya zipatso zanu ndi kumwa mkaka wanu. 5 Ndidzasandutsa Raba kuti akhale busa la ngamira ndi mizinda ya Aamoni kuti ikhale makola a nkhosa. Pamenepo inu mudzadziwa kuti Ine ndine Yehova. 6 Zimene ndikunena Ine Ambuye Yehova ndi izi: Inu munawomba mʼmanja ndi kumalumphalumpha. Munkakondwa mu mtima mwanu pamene munkanyoza dziko la Israeli. 7 Nʼchifukwa chake ndidzatambasula dzanja langa kuti ndikulangeni, ndipo ndidzakuperekani kuti mukhale chofunkha cha anthu a mitundu ina. Ndidzakuchotsani pakati pa anthu a mitundu ina ndi kukufafanizani mʼmayiko onse. Ndidzakuwonongani, ndipo inu mudzadziwa kuti Ine ndine Yehova!’ ” 8 “Ambuye Yehova akuti, ‘Anthu a ku Mowabu ndi a ku Seiri ananena kuti anthu a ku Yuda ali ngati mayiko ena onse.’ 9 Nʼchifukwa chake ndidzagumula mbali ina ya Mowabu, kuyambira ku mizinda yake ya kumalire; mizinda yokongola ya Beti-Yesimoti, Baala-Meoni ndi Kiriataimu. 10 Ndidzapereka Amowabu pamodzi ndi Aamoni mʼmanja mwa anthu akummawa kotero kuti Aamoni adzayiwalikiratu pakati pa anthu a mitundu ina. 11 Ndidzawalangadi Amowabuwo. Pamenepo iwo adzadziwa kuti Ine ndine Yehova.” 12 “Ambuye Yehova akuti, ‘Pakuti Edomu analipsira Ayuda, ndiye kuti analakwa kwambiri pochita zimenezi. 13 Nʼchifukwa chake Ine Ambuye Yehova ndikuti: Ndidzatambasula dzanja langa kulanga Edomu ndi kupha anthu ake ndiponso nyama zawo. Ndidzawonongeratu Edomu ndipo adzaphedwa ndi lupanga kuchokera ku Temani mpaka ku Dedani. 14 Ndidzalanga Edomu ndi dzanja la anthu anga Aisraeli. Adzalanga anthu a ku Edomu molingana ndi mkwiyo ndi ukali wanga. Choncho adzaona kulipsira kwanga akutero Ambuye Yehova.’ ” 15 “Ambuye Yehova akuti, ‘Afilisti analanga anthu anga mwankhanza ndi kuwalipsira. 16 Nʼchifukwa chake Ine Ambuye Yehova ndikuti: Ndidzatambasula dzanja langa kukantha Afilistiwo. Ndidzafafaniza Akereti ndi kuwononga iwo amene amakhala mʼmbali mwa nyanja. 17 Ndidzawabwezera chilango choopsa ndipo ndidzawalanga mu mkwiyo wanga. Ndikadzawalipsira ndipo adzadziwa kuti Ine ndine Yehova.’ ”
In Other Versions
Ezekiel 25 in the ANGEFD
Ezekiel 25 in the ANTPNG2D
Ezekiel 25 in the AS21
Ezekiel 25 in the BAGH
Ezekiel 25 in the BBPNG
Ezekiel 25 in the BBT1E
Ezekiel 25 in the BDS
Ezekiel 25 in the BEV
Ezekiel 25 in the BHAD
Ezekiel 25 in the BIB
Ezekiel 25 in the BLPT
Ezekiel 25 in the BNT
Ezekiel 25 in the BNTABOOT
Ezekiel 25 in the BNTLV
Ezekiel 25 in the BOATCB
Ezekiel 25 in the BOATCB2
Ezekiel 25 in the BOBCV
Ezekiel 25 in the BOCNT
Ezekiel 25 in the BOECS
Ezekiel 25 in the BOHCB
Ezekiel 25 in the BOHCV
Ezekiel 25 in the BOHLNT
Ezekiel 25 in the BOHNTLTAL
Ezekiel 25 in the BOICB
Ezekiel 25 in the BOILNTAP
Ezekiel 25 in the BOITCV
Ezekiel 25 in the BOKCV
Ezekiel 25 in the BOKCV2
Ezekiel 25 in the BOKHWOG
Ezekiel 25 in the BOKSSV
Ezekiel 25 in the BOLCB
Ezekiel 25 in the BOLCB2
Ezekiel 25 in the BOMCV
Ezekiel 25 in the BONAV
Ezekiel 25 in the BONCB
Ezekiel 25 in the BONLT
Ezekiel 25 in the BONUT2
Ezekiel 25 in the BOPLNT
Ezekiel 25 in the BOSCB
Ezekiel 25 in the BOSNC
Ezekiel 25 in the BOTLNT
Ezekiel 25 in the BOVCB
Ezekiel 25 in the BOYCB
Ezekiel 25 in the BPBB
Ezekiel 25 in the BPH
Ezekiel 25 in the BSB
Ezekiel 25 in the CCB
Ezekiel 25 in the CUV
Ezekiel 25 in the CUVS
Ezekiel 25 in the DBT
Ezekiel 25 in the DGDNT
Ezekiel 25 in the DHNT
Ezekiel 25 in the DNT
Ezekiel 25 in the ELBE
Ezekiel 25 in the EMTV
Ezekiel 25 in the ESV
Ezekiel 25 in the FBV
Ezekiel 25 in the FEB
Ezekiel 25 in the GGMNT
Ezekiel 25 in the GNT
Ezekiel 25 in the HARY
Ezekiel 25 in the HNT
Ezekiel 25 in the IRVA
Ezekiel 25 in the IRVB
Ezekiel 25 in the IRVG
Ezekiel 25 in the IRVH
Ezekiel 25 in the IRVK
Ezekiel 25 in the IRVM
Ezekiel 25 in the IRVM2
Ezekiel 25 in the IRVO
Ezekiel 25 in the IRVP
Ezekiel 25 in the IRVT
Ezekiel 25 in the IRVT2
Ezekiel 25 in the IRVU
Ezekiel 25 in the ISVN
Ezekiel 25 in the JSNT
Ezekiel 25 in the KAPI
Ezekiel 25 in the KBT1ETNIK
Ezekiel 25 in the KBV
Ezekiel 25 in the KJV
Ezekiel 25 in the KNFD
Ezekiel 25 in the LBA
Ezekiel 25 in the LBLA
Ezekiel 25 in the LNT
Ezekiel 25 in the LSV
Ezekiel 25 in the MAAL
Ezekiel 25 in the MBV
Ezekiel 25 in the MBV2
Ezekiel 25 in the MHNT
Ezekiel 25 in the MKNFD
Ezekiel 25 in the MNG
Ezekiel 25 in the MNT
Ezekiel 25 in the MNT2
Ezekiel 25 in the MRS1T
Ezekiel 25 in the NAA
Ezekiel 25 in the NASB
Ezekiel 25 in the NBLA
Ezekiel 25 in the NBS
Ezekiel 25 in the NBVTP
Ezekiel 25 in the NET2
Ezekiel 25 in the NIV11
Ezekiel 25 in the NNT
Ezekiel 25 in the NNT2
Ezekiel 25 in the NNT3
Ezekiel 25 in the PDDPT
Ezekiel 25 in the PFNT
Ezekiel 25 in the RMNT
Ezekiel 25 in the SBIAS
Ezekiel 25 in the SBIBS
Ezekiel 25 in the SBIBS2
Ezekiel 25 in the SBICS
Ezekiel 25 in the SBIDS
Ezekiel 25 in the SBIGS
Ezekiel 25 in the SBIHS
Ezekiel 25 in the SBIIS
Ezekiel 25 in the SBIIS2
Ezekiel 25 in the SBIIS3
Ezekiel 25 in the SBIKS
Ezekiel 25 in the SBIKS2
Ezekiel 25 in the SBIMS
Ezekiel 25 in the SBIOS
Ezekiel 25 in the SBIPS
Ezekiel 25 in the SBISS
Ezekiel 25 in the SBITS
Ezekiel 25 in the SBITS2
Ezekiel 25 in the SBITS3
Ezekiel 25 in the SBITS4
Ezekiel 25 in the SBIUS
Ezekiel 25 in the SBIVS
Ezekiel 25 in the SBT
Ezekiel 25 in the SBT1E
Ezekiel 25 in the SCHL
Ezekiel 25 in the SNT
Ezekiel 25 in the SUSU
Ezekiel 25 in the SUSU2
Ezekiel 25 in the SYNO
Ezekiel 25 in the TBIAOTANT
Ezekiel 25 in the TBT1E
Ezekiel 25 in the TBT1E2
Ezekiel 25 in the TFTIP
Ezekiel 25 in the TFTU
Ezekiel 25 in the TGNTATF3T
Ezekiel 25 in the THAI
Ezekiel 25 in the TNFD
Ezekiel 25 in the TNT
Ezekiel 25 in the TNTIK
Ezekiel 25 in the TNTIL
Ezekiel 25 in the TNTIN
Ezekiel 25 in the TNTIP
Ezekiel 25 in the TNTIZ
Ezekiel 25 in the TOMA
Ezekiel 25 in the TTENT
Ezekiel 25 in the UBG
Ezekiel 25 in the UGV
Ezekiel 25 in the UGV2
Ezekiel 25 in the UGV3
Ezekiel 25 in the VBL
Ezekiel 25 in the VDCC
Ezekiel 25 in the YALU
Ezekiel 25 in the YAPE
Ezekiel 25 in the YBVTP
Ezekiel 25 in the ZBP