Galatians 1 (BOGWICC)

1 Paulo mtumwi, osati wosankhidwa ndi anthu kapena kutumidwa ndi munthu ayi, koma Yesu Khristu, ndi Mulungu Atate amene anamuukitsa Yesuyo kwa akufa, 2 pamodzi ndi abale onse amene ali nane,Kulembera mipingo ya ku Galatiya: 3 Chisomo ndi mtendere zochokera kwa Mulungu Atate athu ndi Ambuye Yesu Khristu zikhale nanu. 4 Yesuyo anadzipereka yekha chifukwa cha machimo athu kuti atipulumutse ku njira za moyo woyipa uno, molingana ndi chifuniro cha Mulungu ndi Atate athu. 5 Ulemerero ukhale kwa Mulunguyo mpaka muyaya. Ameni. 6 Ine ndikudabwa kuti mukusiya mwamsangamsanga chotere Mulungu amene anakuyitanani mwachisomo cha Khristu ndipo mwatembenuka ndi kutsatira uthenga wina wosiyana, 7 umene si Uthenga Wabwino konse. Pali anthu ena amene akukusokonezani komanso akufuna kupotoza Uthenga Wabwino wa Khristu. 8 Ngakhale ife kapena mngelo wochokera kumwamba, akalalikira Uthenga Wabwino wosiyana ndi umene tinakulalikirani uja, iyeyo akhale wotembereredwa! 9 Monga tanena kale, tsopano ndikubwereza kunenanso kuti, “Ngati wina aliyense akulalikirani Uthenga Wabwino wosiyana ndi umene munawulandira, iyeyo akhale wotembereredwa.” 10 Kodi tsopano ndikufuna kukopa anthu kuti andivomereze, kapena Mulungu? Kapena ndikufuna kukondweretsa anthu? Ngati ine ndikanakhala kuti ndikufunabe kukondweretsa anthu, sindikanakhala mtumiki wa Khristu. 11 Abale, ine ndikufuna kuti mudziwe, kuti Uthenga Wabwino umene ndinalalikira si ochokera kwa munthu ayi. 12 Ine sindinawulandire kuchokera kwa munthu aliyense, kapena kuphunzitsidwa; koma ndinawulandira mwa vumbulutso lochokera kwa Khristu. 13 Pakuti inu munamva za moyo wanga wakale mʼChiyuda, mmene ndinkazunzira mpingo wa Mulungu koopsa ndi kuyesetsa kuwuwononga. 14 Ine ndinkapambana Ayuda ambiri a msinkhu wanga pochita za Chiyuda, ndipo ndinali wachangu koposa pa miyambo ya makolo athu. 15 Koma Mulungu, amene anandipatula ine ndisanabadwe, ndi kundiyitana mwachisomo chake, atakondweretsedwa 16 kuvumbulutsa Mwana wake mwa ine, kuti ndikalalikire Khristuyo pakati pa anthu a mitundu ina, ine sindinapemphe nzeru kwa munthu aliyense. 17 Ine sindinapite ku Yerusalemu kukaonana ndi amene anali atumwi ine ndisanakhale mtumwi. Mʼmalo mwake nthawi yomweyo ndinapita ku Arabiya ndi kubwereranso ku Damasiko. 18 Pambuyo pake, patatha zaka zitatu, ndinapita ku Yerusalemu kukaonana ndi Petro ndikukhala naye masiku khumi ndi asanu. 19 Ine sindinaonane ndi atumwi enawo koma Yakobo yekha, mʼbale wa Ambuye. 20 Ine ndikutsimikizira inu pamaso pa Mulungu kuti zimene ndikukulemberani si zonama ayi. 21 Pambuyo pake ndinapita ku Siriya ndi ku Kilikiya. 22 Koma sindimadziwika ndi nkhope ku mipingo ya ku Yudeya imene ili mwa Khristu. 23 Iwo anangomva mbiri yokha yakuti, “Munthu amene poyamba anatizunza ife, tsopano akulalikira chikhulupiriro chimene iyeyo nthawi ina anafuna kuchiwononga.” 24 Ndipo iwo anayamika Mulungu chifukwa cha ine.

In Other Versions

Galatians 1 in the ANGEFD

Galatians 1 in the ANTPNG2D

Galatians 1 in the AS21

Galatians 1 in the BAGH

Galatians 1 in the BBPNG

Galatians 1 in the BBT1E

Galatians 1 in the BDS

Galatians 1 in the BEV

Galatians 1 in the BHAD

Galatians 1 in the BIB

Galatians 1 in the BLPT

Galatians 1 in the BNT

Galatians 1 in the BNTABOOT

Galatians 1 in the BNTLV

Galatians 1 in the BOATCB

Galatians 1 in the BOATCB2

Galatians 1 in the BOBCV

Galatians 1 in the BOCNT

Galatians 1 in the BOECS

Galatians 1 in the BOHCB

Galatians 1 in the BOHCV

Galatians 1 in the BOHLNT

Galatians 1 in the BOHNTLTAL

Galatians 1 in the BOICB

Galatians 1 in the BOILNTAP

Galatians 1 in the BOITCV

Galatians 1 in the BOKCV

Galatians 1 in the BOKCV2

Galatians 1 in the BOKHWOG

Galatians 1 in the BOKSSV

Galatians 1 in the BOLCB

Galatians 1 in the BOLCB2

Galatians 1 in the BOMCV

Galatians 1 in the BONAV

Galatians 1 in the BONCB

Galatians 1 in the BONLT

Galatians 1 in the BONUT2

Galatians 1 in the BOPLNT

Galatians 1 in the BOSCB

Galatians 1 in the BOSNC

Galatians 1 in the BOTLNT

Galatians 1 in the BOVCB

Galatians 1 in the BOYCB

Galatians 1 in the BPBB

Galatians 1 in the BPH

Galatians 1 in the BSB

Galatians 1 in the CCB

Galatians 1 in the CUV

Galatians 1 in the CUVS

Galatians 1 in the DBT

Galatians 1 in the DGDNT

Galatians 1 in the DHNT

Galatians 1 in the DNT

Galatians 1 in the ELBE

Galatians 1 in the EMTV

Galatians 1 in the ESV

Galatians 1 in the FBV

Galatians 1 in the FEB

Galatians 1 in the GGMNT

Galatians 1 in the GNT

Galatians 1 in the HARY

Galatians 1 in the HNT

Galatians 1 in the IRVA

Galatians 1 in the IRVB

Galatians 1 in the IRVG

Galatians 1 in the IRVH

Galatians 1 in the IRVK

Galatians 1 in the IRVM

Galatians 1 in the IRVM2

Galatians 1 in the IRVO

Galatians 1 in the IRVP

Galatians 1 in the IRVT

Galatians 1 in the IRVT2

Galatians 1 in the IRVU

Galatians 1 in the ISVN

Galatians 1 in the JSNT

Galatians 1 in the KAPI

Galatians 1 in the KBT1ETNIK

Galatians 1 in the KBV

Galatians 1 in the KJV

Galatians 1 in the KNFD

Galatians 1 in the LBA

Galatians 1 in the LBLA

Galatians 1 in the LNT

Galatians 1 in the LSV

Galatians 1 in the MAAL

Galatians 1 in the MBV

Galatians 1 in the MBV2

Galatians 1 in the MHNT

Galatians 1 in the MKNFD

Galatians 1 in the MNG

Galatians 1 in the MNT

Galatians 1 in the MNT2

Galatians 1 in the MRS1T

Galatians 1 in the NAA

Galatians 1 in the NASB

Galatians 1 in the NBLA

Galatians 1 in the NBS

Galatians 1 in the NBVTP

Galatians 1 in the NET2

Galatians 1 in the NIV11

Galatians 1 in the NNT

Galatians 1 in the NNT2

Galatians 1 in the NNT3

Galatians 1 in the PDDPT

Galatians 1 in the PFNT

Galatians 1 in the RMNT

Galatians 1 in the SBIAS

Galatians 1 in the SBIBS

Galatians 1 in the SBIBS2

Galatians 1 in the SBICS

Galatians 1 in the SBIDS

Galatians 1 in the SBIGS

Galatians 1 in the SBIHS

Galatians 1 in the SBIIS

Galatians 1 in the SBIIS2

Galatians 1 in the SBIIS3

Galatians 1 in the SBIKS

Galatians 1 in the SBIKS2

Galatians 1 in the SBIMS

Galatians 1 in the SBIOS

Galatians 1 in the SBIPS

Galatians 1 in the SBISS

Galatians 1 in the SBITS

Galatians 1 in the SBITS2

Galatians 1 in the SBITS3

Galatians 1 in the SBITS4

Galatians 1 in the SBIUS

Galatians 1 in the SBIVS

Galatians 1 in the SBT

Galatians 1 in the SBT1E

Galatians 1 in the SCHL

Galatians 1 in the SNT

Galatians 1 in the SUSU

Galatians 1 in the SUSU2

Galatians 1 in the SYNO

Galatians 1 in the TBIAOTANT

Galatians 1 in the TBT1E

Galatians 1 in the TBT1E2

Galatians 1 in the TFTIP

Galatians 1 in the TFTU

Galatians 1 in the TGNTATF3T

Galatians 1 in the THAI

Galatians 1 in the TNFD

Galatians 1 in the TNT

Galatians 1 in the TNTIK

Galatians 1 in the TNTIL

Galatians 1 in the TNTIN

Galatians 1 in the TNTIP

Galatians 1 in the TNTIZ

Galatians 1 in the TOMA

Galatians 1 in the TTENT

Galatians 1 in the UBG

Galatians 1 in the UGV

Galatians 1 in the UGV2

Galatians 1 in the UGV3

Galatians 1 in the VBL

Galatians 1 in the VDCC

Galatians 1 in the YALU

Galatians 1 in the YAPE

Galatians 1 in the YBVTP

Galatians 1 in the ZBP