Jeremiah 28 (BOGWICC)
1 Chaka chomwecho mwezi wachisanu wa chaka chachinayi, poyambirira pa ulamuliro wa Zedekiya mfumu ya Yuda, mneneri Hananiya mwana wa Azuri, amene amachokera ku Gibiyoni, anandiwuza ine mʼNyumba ya Yehova pamaso pa ansembe ndi anthu onse kuti, 2 “Yehova Wamphamvuzonse, Mulungu wa Israeli, akuti, ‘Ndidzathyola goli la mfumu ya ku Babuloni. 3 Pasanathe zaka ziwiri ndidzabweretsa pa malo ano ziwiya zonse za ku Nyumba ya Yehova zimene Nebukadinezara mfumu ya ku Babuloni anazichotsa pa malo pano ndi kupita nazo ku Babuloni. 4 Ndidzabweretsanso pa malo pano Yekoniya mwana wa Yehoyakimu mfumu ya Yuda pamodzi ndi akapolo ena onse ochokera ku Yuda amene anapita ku Babuloni,’ akutero Yehova, ‘chifukwa ndidzathyola goli la mfumu ya ku Babuloni.’ ” 5 Pamenepo mneneri Yeremiya anayankha mneneri Hananiya pamaso pa ansembe ndi anthu onse amene anasonkhana mʼNyumba ya Yehova. 6 Anati, “Ameni! Yehova achitedi zomwezo! Yehova akwaniritse mawu amene waloserawo. Iye abweretsenso pa malo pano ziwiya za mʼNyumba ya Yehova ndi akapolo onse kuchokera ku Babuloni. 7 Komabe, tamvera zimene nditi ndikuwuze iweyo pamodzi ndi anthu onse: 8 Kunali aneneri kalelo, ine ndi iwe tisanabadwe. Iwowa analosera za nkhondo, mavuto ndi mliri kuti zidzagwera mayiko ambiri ndi maufumu amphamvu. 9 Koma mneneri amene amalosera zamtendere adzadziwika kuti ndi woona ndi kuti watumidwa ndi Yehova ngati zimene wanenera zachitikadi.” 10 Pamenepo mneneri Hananiya anachotsa goli mʼkhosi mwa mneneri Yeremiya nalithyola, 11 ndipo anawuza anthu onse kuti, “Yehova akuti, ‘Umu ndi mmene ndidzathyolere goli la Nebukadinezara mfumu ya ku Babuloni mʼkhosi mwa anthu a mitundu yonse pasanathe zaka ziwiri.’ ” Zitatero, mneneri Yeremiya anachoka. 12 Patapita nthawi pangʼono, mneneri Hananiya atathyola goli mʼkhosi mwa mneneri Yeremiya, Yehova anawuza Yeremiya kuti, 13 “Pita, kawuze mneneri Hananiya kuti, ‘Yehova akuti: Iwe wathyola goli lamtengo, mʼmalo mwake Ine ndidzayika goli lachitsulo. 14 Yehova Wamphamvuzonse, Mulungu wa Israeli akuti: Ndidzayika goli lachitsulo mʼkhosi mwa anthu a mitundu yonseyi kuti atumikire Nebukadinezara mfumu ya ku Babuloni, ndipo iwo adzamutumikiradi. Ndipo ndamupatsanso ulamuliro ngakhale pa nyama zakuthengo.’ ” 15 Ndipo mneneri Yeremiya anawuza mneneri Hananiya kuti, “Tamvera, Hananiya! Iweyo Yehova sanakutume, koma iwe wanyenga anthuwa kuti akhulupirire zabodza. 16 Nʼchifukwa chake Yehova akuti, ‘Ndatsala pangʼono kukuchotsa pa dziko lapansi. Iwe ufa chaka chino chisanathe, chifukwa wakhala ukulalikira zowukira Yehova.’ ” 17 Mʼmwezi wachisanu ndi chiwiri wa chaka chomwecho, mneneri Hananiya anamwaliradi.
In Other Versions
Jeremiah 28 in the ANGEFD
Jeremiah 28 in the ANTPNG2D
Jeremiah 28 in the AS21
Jeremiah 28 in the BAGH
Jeremiah 28 in the BBPNG
Jeremiah 28 in the BBT1E
Jeremiah 28 in the BDS
Jeremiah 28 in the BEV
Jeremiah 28 in the BHAD
Jeremiah 28 in the BIB
Jeremiah 28 in the BLPT
Jeremiah 28 in the BNT
Jeremiah 28 in the BNTABOOT
Jeremiah 28 in the BNTLV
Jeremiah 28 in the BOATCB
Jeremiah 28 in the BOATCB2
Jeremiah 28 in the BOBCV
Jeremiah 28 in the BOCNT
Jeremiah 28 in the BOECS
Jeremiah 28 in the BOHCB
Jeremiah 28 in the BOHCV
Jeremiah 28 in the BOHLNT
Jeremiah 28 in the BOHNTLTAL
Jeremiah 28 in the BOICB
Jeremiah 28 in the BOILNTAP
Jeremiah 28 in the BOITCV
Jeremiah 28 in the BOKCV
Jeremiah 28 in the BOKCV2
Jeremiah 28 in the BOKHWOG
Jeremiah 28 in the BOKSSV
Jeremiah 28 in the BOLCB
Jeremiah 28 in the BOLCB2
Jeremiah 28 in the BOMCV
Jeremiah 28 in the BONAV
Jeremiah 28 in the BONCB
Jeremiah 28 in the BONLT
Jeremiah 28 in the BONUT2
Jeremiah 28 in the BOPLNT
Jeremiah 28 in the BOSCB
Jeremiah 28 in the BOSNC
Jeremiah 28 in the BOTLNT
Jeremiah 28 in the BOVCB
Jeremiah 28 in the BOYCB
Jeremiah 28 in the BPBB
Jeremiah 28 in the BPH
Jeremiah 28 in the BSB
Jeremiah 28 in the CCB
Jeremiah 28 in the CUV
Jeremiah 28 in the CUVS
Jeremiah 28 in the DBT
Jeremiah 28 in the DGDNT
Jeremiah 28 in the DHNT
Jeremiah 28 in the DNT
Jeremiah 28 in the ELBE
Jeremiah 28 in the EMTV
Jeremiah 28 in the ESV
Jeremiah 28 in the FBV
Jeremiah 28 in the FEB
Jeremiah 28 in the GGMNT
Jeremiah 28 in the GNT
Jeremiah 28 in the HARY
Jeremiah 28 in the HNT
Jeremiah 28 in the IRVA
Jeremiah 28 in the IRVB
Jeremiah 28 in the IRVG
Jeremiah 28 in the IRVH
Jeremiah 28 in the IRVK
Jeremiah 28 in the IRVM
Jeremiah 28 in the IRVM2
Jeremiah 28 in the IRVO
Jeremiah 28 in the IRVP
Jeremiah 28 in the IRVT
Jeremiah 28 in the IRVT2
Jeremiah 28 in the IRVU
Jeremiah 28 in the ISVN
Jeremiah 28 in the JSNT
Jeremiah 28 in the KAPI
Jeremiah 28 in the KBT1ETNIK
Jeremiah 28 in the KBV
Jeremiah 28 in the KJV
Jeremiah 28 in the KNFD
Jeremiah 28 in the LBA
Jeremiah 28 in the LBLA
Jeremiah 28 in the LNT
Jeremiah 28 in the LSV
Jeremiah 28 in the MAAL
Jeremiah 28 in the MBV
Jeremiah 28 in the MBV2
Jeremiah 28 in the MHNT
Jeremiah 28 in the MKNFD
Jeremiah 28 in the MNG
Jeremiah 28 in the MNT
Jeremiah 28 in the MNT2
Jeremiah 28 in the MRS1T
Jeremiah 28 in the NAA
Jeremiah 28 in the NASB
Jeremiah 28 in the NBLA
Jeremiah 28 in the NBS
Jeremiah 28 in the NBVTP
Jeremiah 28 in the NET2
Jeremiah 28 in the NIV11
Jeremiah 28 in the NNT
Jeremiah 28 in the NNT2
Jeremiah 28 in the NNT3
Jeremiah 28 in the PDDPT
Jeremiah 28 in the PFNT
Jeremiah 28 in the RMNT
Jeremiah 28 in the SBIAS
Jeremiah 28 in the SBIBS
Jeremiah 28 in the SBIBS2
Jeremiah 28 in the SBICS
Jeremiah 28 in the SBIDS
Jeremiah 28 in the SBIGS
Jeremiah 28 in the SBIHS
Jeremiah 28 in the SBIIS
Jeremiah 28 in the SBIIS2
Jeremiah 28 in the SBIIS3
Jeremiah 28 in the SBIKS
Jeremiah 28 in the SBIKS2
Jeremiah 28 in the SBIMS
Jeremiah 28 in the SBIOS
Jeremiah 28 in the SBIPS
Jeremiah 28 in the SBISS
Jeremiah 28 in the SBITS
Jeremiah 28 in the SBITS2
Jeremiah 28 in the SBITS3
Jeremiah 28 in the SBITS4
Jeremiah 28 in the SBIUS
Jeremiah 28 in the SBIVS
Jeremiah 28 in the SBT
Jeremiah 28 in the SBT1E
Jeremiah 28 in the SCHL
Jeremiah 28 in the SNT
Jeremiah 28 in the SUSU
Jeremiah 28 in the SUSU2
Jeremiah 28 in the SYNO
Jeremiah 28 in the TBIAOTANT
Jeremiah 28 in the TBT1E
Jeremiah 28 in the TBT1E2
Jeremiah 28 in the TFTIP
Jeremiah 28 in the TFTU
Jeremiah 28 in the TGNTATF3T
Jeremiah 28 in the THAI
Jeremiah 28 in the TNFD
Jeremiah 28 in the TNT
Jeremiah 28 in the TNTIK
Jeremiah 28 in the TNTIL
Jeremiah 28 in the TNTIN
Jeremiah 28 in the TNTIP
Jeremiah 28 in the TNTIZ
Jeremiah 28 in the TOMA
Jeremiah 28 in the TTENT
Jeremiah 28 in the UBG
Jeremiah 28 in the UGV
Jeremiah 28 in the UGV2
Jeremiah 28 in the UGV3
Jeremiah 28 in the VBL
Jeremiah 28 in the VDCC
Jeremiah 28 in the YALU
Jeremiah 28 in the YAPE
Jeremiah 28 in the YBVTP
Jeremiah 28 in the ZBP