Jeremiah 43 (BOGWICC)

1 Yeremiya atatsiriza kuwawuza anthuwo mawu onse a Yehova Mulungu wawo, amene Yehova anamutuma kuti akawawuze, 2 Azariya mwana wa Hosayia ndi Yohanani mwana wa Kareya pamodzi ndi anthu onse odzikuza anawuza Yeremiya kuti, “Ukunama iwe! Yehova Mulungu wathu sanakutume kuti unene kuti, ‘Musapite ku Igupto kukakhala kumeneko.’ 3 Koma ndi Baruki mwana wa Neriya amene akukulimbikitsa kuti utiletse zopita ku Igupto ndi kuti mʼmalo mwake tidzipereke mʼmanja mwa Ababuloni, kuti iwo atiphe kapena kutitenga ukapolo ku Babuloni.” 4 Motero Yohanani mwana wa Kareya ndi atsogoleri onse a ankhondo pamodzi ndi anthu onse sanamvere lamulo la Yehova loti akhale mʼdziko la Yuda. 5 Mʼmalo mwake, Yohanani mwana wa Kareya ndi atsogoleri onse a ankhondo anatenga anthu onse otsala a ku Yuda amene anabwera kudzakhala mʼdziko la Yuda kuchokera ku mayiko onse kumene anabalakirako. 6 Mʼgulu la anthu otengedwalo munali amuna onse, akazi ndi ana, ana aakazi a mfumu, ndiponso anthu amene Nebuzaradani mtsogoleri wa asilikali olonda mfumu anawasiya kwa Gedaliya mwana wa Ahikamu, mdzukulu wa Safani pamodzinso ndi mneneri Yeremiya ndi Baruki mwana wa Neriya. 7 Kotero anthuwo analowa mʼdziko la Igupto chifukwa anakana kumvera Yehova, nakafika ku Tapanesi. 8 Ndipo Yehova anayankhula ndi Yeremiya ku Tapanesi kuti, 9 “Tenga miyala inayi yayikulu ndipo uyikwirire mʼdothi pa chiwundo cha polowera ku nyumba yaufumu ya Farao ku Tapanesi. Uchite zimenezi Ayuda onse akuona. 10 Ndipo uwawuze kuti, ‘Yehova Wamphamvuzonse, Mulungu wa Israeli akuti: Ndidzayitana mtumiki wanga Nebukadinezara mfumu ya ku Babuloni, ndipo adzakhazika mpando wake waufumu pa miyala imene ndayikwirira apayi. Iye adzafunyulula tenti yake yaufumu pa miyala imeneyi. 11 Iye adzabwera kudzathira nkhondo Igupto. Iwo oyenera kufa ndi mliri adzafa ndi mliri, iwo oyenera kutengedwa ukapolo adzatengedwa ukapolo, ndipo iwo oyenera kufa ndi lupanga adzafa ndi lupanga. 12 Adzayatsa moto mʼnyumba zopembedzera milungu ya Igupto. Adzayeretsa dziko la Igupto monga momwe mʼbusa amayeretsera chovala chake pochotsamo nsabwe. Pambuyo pake adzachoka mʼdziko la Igupto mwa mtendere. 13 Ku Iguptoko adzagwetsa zipilala zachipembedzo za ku nyumba yopembedzera mulungu wa dzuwa. Adzatentha ndi moto nyumba za milungu ya ku Igupto.’ ”

In Other Versions

Jeremiah 43 in the ANGEFD

Jeremiah 43 in the ANTPNG2D

Jeremiah 43 in the AS21

Jeremiah 43 in the BAGH

Jeremiah 43 in the BBPNG

Jeremiah 43 in the BBT1E

Jeremiah 43 in the BDS

Jeremiah 43 in the BEV

Jeremiah 43 in the BHAD

Jeremiah 43 in the BIB

Jeremiah 43 in the BLPT

Jeremiah 43 in the BNT

Jeremiah 43 in the BNTABOOT

Jeremiah 43 in the BNTLV

Jeremiah 43 in the BOATCB

Jeremiah 43 in the BOATCB2

Jeremiah 43 in the BOBCV

Jeremiah 43 in the BOCNT

Jeremiah 43 in the BOECS

Jeremiah 43 in the BOHCB

Jeremiah 43 in the BOHCV

Jeremiah 43 in the BOHLNT

Jeremiah 43 in the BOHNTLTAL

Jeremiah 43 in the BOICB

Jeremiah 43 in the BOILNTAP

Jeremiah 43 in the BOITCV

Jeremiah 43 in the BOKCV

Jeremiah 43 in the BOKCV2

Jeremiah 43 in the BOKHWOG

Jeremiah 43 in the BOKSSV

Jeremiah 43 in the BOLCB

Jeremiah 43 in the BOLCB2

Jeremiah 43 in the BOMCV

Jeremiah 43 in the BONAV

Jeremiah 43 in the BONCB

Jeremiah 43 in the BONLT

Jeremiah 43 in the BONUT2

Jeremiah 43 in the BOPLNT

Jeremiah 43 in the BOSCB

Jeremiah 43 in the BOSNC

Jeremiah 43 in the BOTLNT

Jeremiah 43 in the BOVCB

Jeremiah 43 in the BOYCB

Jeremiah 43 in the BPBB

Jeremiah 43 in the BPH

Jeremiah 43 in the BSB

Jeremiah 43 in the CCB

Jeremiah 43 in the CUV

Jeremiah 43 in the CUVS

Jeremiah 43 in the DBT

Jeremiah 43 in the DGDNT

Jeremiah 43 in the DHNT

Jeremiah 43 in the DNT

Jeremiah 43 in the ELBE

Jeremiah 43 in the EMTV

Jeremiah 43 in the ESV

Jeremiah 43 in the FBV

Jeremiah 43 in the FEB

Jeremiah 43 in the GGMNT

Jeremiah 43 in the GNT

Jeremiah 43 in the HARY

Jeremiah 43 in the HNT

Jeremiah 43 in the IRVA

Jeremiah 43 in the IRVB

Jeremiah 43 in the IRVG

Jeremiah 43 in the IRVH

Jeremiah 43 in the IRVK

Jeremiah 43 in the IRVM

Jeremiah 43 in the IRVM2

Jeremiah 43 in the IRVO

Jeremiah 43 in the IRVP

Jeremiah 43 in the IRVT

Jeremiah 43 in the IRVT2

Jeremiah 43 in the IRVU

Jeremiah 43 in the ISVN

Jeremiah 43 in the JSNT

Jeremiah 43 in the KAPI

Jeremiah 43 in the KBT1ETNIK

Jeremiah 43 in the KBV

Jeremiah 43 in the KJV

Jeremiah 43 in the KNFD

Jeremiah 43 in the LBA

Jeremiah 43 in the LBLA

Jeremiah 43 in the LNT

Jeremiah 43 in the LSV

Jeremiah 43 in the MAAL

Jeremiah 43 in the MBV

Jeremiah 43 in the MBV2

Jeremiah 43 in the MHNT

Jeremiah 43 in the MKNFD

Jeremiah 43 in the MNG

Jeremiah 43 in the MNT

Jeremiah 43 in the MNT2

Jeremiah 43 in the MRS1T

Jeremiah 43 in the NAA

Jeremiah 43 in the NASB

Jeremiah 43 in the NBLA

Jeremiah 43 in the NBS

Jeremiah 43 in the NBVTP

Jeremiah 43 in the NET2

Jeremiah 43 in the NIV11

Jeremiah 43 in the NNT

Jeremiah 43 in the NNT2

Jeremiah 43 in the NNT3

Jeremiah 43 in the PDDPT

Jeremiah 43 in the PFNT

Jeremiah 43 in the RMNT

Jeremiah 43 in the SBIAS

Jeremiah 43 in the SBIBS

Jeremiah 43 in the SBIBS2

Jeremiah 43 in the SBICS

Jeremiah 43 in the SBIDS

Jeremiah 43 in the SBIGS

Jeremiah 43 in the SBIHS

Jeremiah 43 in the SBIIS

Jeremiah 43 in the SBIIS2

Jeremiah 43 in the SBIIS3

Jeremiah 43 in the SBIKS

Jeremiah 43 in the SBIKS2

Jeremiah 43 in the SBIMS

Jeremiah 43 in the SBIOS

Jeremiah 43 in the SBIPS

Jeremiah 43 in the SBISS

Jeremiah 43 in the SBITS

Jeremiah 43 in the SBITS2

Jeremiah 43 in the SBITS3

Jeremiah 43 in the SBITS4

Jeremiah 43 in the SBIUS

Jeremiah 43 in the SBIVS

Jeremiah 43 in the SBT

Jeremiah 43 in the SBT1E

Jeremiah 43 in the SCHL

Jeremiah 43 in the SNT

Jeremiah 43 in the SUSU

Jeremiah 43 in the SUSU2

Jeremiah 43 in the SYNO

Jeremiah 43 in the TBIAOTANT

Jeremiah 43 in the TBT1E

Jeremiah 43 in the TBT1E2

Jeremiah 43 in the TFTIP

Jeremiah 43 in the TFTU

Jeremiah 43 in the TGNTATF3T

Jeremiah 43 in the THAI

Jeremiah 43 in the TNFD

Jeremiah 43 in the TNT

Jeremiah 43 in the TNTIK

Jeremiah 43 in the TNTIL

Jeremiah 43 in the TNTIN

Jeremiah 43 in the TNTIP

Jeremiah 43 in the TNTIZ

Jeremiah 43 in the TOMA

Jeremiah 43 in the TTENT

Jeremiah 43 in the UBG

Jeremiah 43 in the UGV

Jeremiah 43 in the UGV2

Jeremiah 43 in the UGV3

Jeremiah 43 in the VBL

Jeremiah 43 in the VDCC

Jeremiah 43 in the YALU

Jeremiah 43 in the YAPE

Jeremiah 43 in the YBVTP

Jeremiah 43 in the ZBP