Jeremiah 9 (BOGWICC)

1 Aa, ndikanakonda kuti mutu wanga ukanakhala chitsime cha madzi,ndi maso anga ngati kasupe wa misozi!Ndikanalira usana ndi usikukulirira anthu anga amene aphedwa. 2 Ndani adzandipatsa maloogona mʼchipululukuti ndiwasiye anthu angandi kuwachokera kupita kutali;pakuti onse ndi achigololo,ndiponso gulu la anthu onyenga. 3 “Amapinda lilime lawo ngati uta.Mʼdzikomo mwadzazandi mabodza okhaokhaosati zoonadi.Amapitirirabe kuchita zoyipa;ndipo sandidziwa Ine.”Akutero Yehova. 4 “Aliyense achenjere ndi abwenzi ake;asadalire ngakhale abale ake.Aliyense amafuna kumudyera mʼbale wake masuku pa mutu.Choncho aliyense amachitira bwenzi lake ugogodi. 5 Aliyense amamunamiza mʼbale wakendipo palibe amene amayankhula choonadi.Anapazoloweza pakamwa pawo kunena zabodza;amalimbika kuchita machimo. 6 Iwe wakhalira mʼchinyengondipo ukukana kundidziwa Ine,”akutero Yehova. 7 Nʼchifukwa chake Yehova Wamphamvuzonse akuti,“Taonani, Ine ndidzawasungunula ngati chitsulo ndi kuwayesa.Kodi ndingachite nawonsobwanji chifukwa cha machimo awo? 8 Lilime lawo lili ngati muvi wakuthwa;limayankhula zachinyengo.Aliyense ndi pakamwa pake amayankhula mawu achikondi kwa mnansi wake,koma mu mtima mwake amakonzekera zomuchita chiwembu. 9 Kodi ndilekerenji kuwalanga chifukwa cha zimenezi?akutero Yehova.‘Kodi ndisawulipsiremtundu wotere wa anthu?’ ” 10 Ndidzakhetsa misozi ndi kulira kwamphamvu chifukwa cha mapirindipo ndidzadandaula chifukwa cha msipu wa ku chipululu.Malo onsewo awonongeka ndipo palibe amene amapitako,ndipo sikumveka kulira kwa ngʼombe.Mbalame zamlengalenga zathawandipo nyama zakuthengo zachokako. 11 Ndipo Yehova anati, “Ndidzasandutsa Yerusalemu kukhala bwinja,malo okhalamo ankhandwe;ndipo ndidzawononga mizinda ya Yudakotero kuti palibe munthu amene adzakhalemo.” 12 Ine ndinati, “Kodi munthu wanzeru ndani woti nʼkumvetsa zimenezi? Kodi ndani amene Yehova anayankhula naye zimenezi kuti akafotokozere ena? Nʼchifukwa chiyani dziko lawonongeka ndi kusanduka chipululu, mʼmene anthu sadutsamo?” 13 Yehova anati, “Nʼchifukwa chakuti anthuwa analeka kutsata malamulo anga amene ndinawapatsa; sanandimvere kapena kuwasamala. 14 Mʼmalo mwake, anatsatira zolakwa za mʼmitima yawo; anapembedza Abaala ngati momwe makolo awo anawaphunzitsira.” 15 Tsono chimene Ine Yehova Wamphamvuzonse, Mulungu wa Israeli ndidzachite ndi anthu amenewa ndi ichi: “Ndidzawadyetsa chakudya cha ziphe ndi kuwamwetsa madzi a ndulu. 16 Ndidzawabalalitsa pakati pa mitundu ya anthu imene iwowo kapena makolo awo sanayidziwe, ndipo ndidzawalondola ndi ankhondo mpaka nditawawononga.” 17 Yehova Wamphamvuzonse akuti,“Tsopano ganizirani! Muyitane akazi olira mwachisoni kuti abwere;itanani akazi odziwa kulira bwino.” 18 Anthu akuti, “Abwere mofulumirakuti adzatilirempaka mʼmaso mwathu mutatuluka misozindi kuti msidze zathu zinyowe ndi madzi. 19 Kulira mwachisoni kukumveka kuchokera mu Ziyoni akuti,‘Aa! Ife tawonongeka!Tachita manyazi kwambiri!Tiyenera kuchoka mʼdziko lathuchifukwa atipirikitsa mʼnyumba zathu.’ ” 20 Tsono inu amayi, imvani mawu a Yehova;tcherani makutu anu kuti mumve mawu a Yehova.Phunzitsani ana anu aakazi kulira mwachisoni;aliyense aphunzitse mnzake nyimbo ya maliro. 21 Imfa yatifikira kudzera mʼmazenera athundipo yalowa mʼnyumba zathu zotetezedwa;yapha ana athu mʼmisewu,ndi achinyamata athu mʼmabwalo. 22 Yehova anandiwuza kuti ndinene izi kuti,“ ‘Mitembo ya anthuidzakhala ili lambalamba ngati ndowe mʼminda,ngati mapesi mʼmbuyo mwa wokolola,popanda munthu woyitola.’ ” 23 Yehova akuti,“Munthu wanzeru asanyadire nzeru zake,kapena munthu wamphamvu kunyadira nyonga zake,kapena munthu wolemera kunyadira chuma chake, 24 koma ngati munthu akufuna kunyadira, anyadire chinthu ichi:kuti iye amamvetsa za Ine ndipo amandidziwa,kuti ndine Yehova, amene ndimakonda chifundo,chilungamo ndiponso ungwiro pa dziko lapansi.Zimenezi ndizo ndimakondwera nazo,”akutero Yehova. 25 “Nthawi ikubwera,” akutero Yehova, “pamene ndidzalanga onse amene anachita mdulidwe koma mu mtima sasamala nʼkomwe. 26 Ndidzalanga anthu a ku Igupto, Yuda, Edomu, Amoni, Mowabu, ndiponso onse amene amakhala kutali ku chipululu. Mitundu ina yonseyi ndi yosachita mdulidwe, ngakhalenso Aisraeli nawonso sanachite mdulidwe wa mu mtima.”

In Other Versions

Jeremiah 9 in the ANGEFD

Jeremiah 9 in the ANTPNG2D

Jeremiah 9 in the AS21

Jeremiah 9 in the BAGH

Jeremiah 9 in the BBPNG

Jeremiah 9 in the BBT1E

Jeremiah 9 in the BDS

Jeremiah 9 in the BEV

Jeremiah 9 in the BHAD

Jeremiah 9 in the BIB

Jeremiah 9 in the BLPT

Jeremiah 9 in the BNT

Jeremiah 9 in the BNTABOOT

Jeremiah 9 in the BNTLV

Jeremiah 9 in the BOATCB

Jeremiah 9 in the BOATCB2

Jeremiah 9 in the BOBCV

Jeremiah 9 in the BOCNT

Jeremiah 9 in the BOECS

Jeremiah 9 in the BOHCB

Jeremiah 9 in the BOHCV

Jeremiah 9 in the BOHLNT

Jeremiah 9 in the BOHNTLTAL

Jeremiah 9 in the BOICB

Jeremiah 9 in the BOILNTAP

Jeremiah 9 in the BOITCV

Jeremiah 9 in the BOKCV

Jeremiah 9 in the BOKCV2

Jeremiah 9 in the BOKHWOG

Jeremiah 9 in the BOKSSV

Jeremiah 9 in the BOLCB

Jeremiah 9 in the BOLCB2

Jeremiah 9 in the BOMCV

Jeremiah 9 in the BONAV

Jeremiah 9 in the BONCB

Jeremiah 9 in the BONLT

Jeremiah 9 in the BONUT2

Jeremiah 9 in the BOPLNT

Jeremiah 9 in the BOSCB

Jeremiah 9 in the BOSNC

Jeremiah 9 in the BOTLNT

Jeremiah 9 in the BOVCB

Jeremiah 9 in the BOYCB

Jeremiah 9 in the BPBB

Jeremiah 9 in the BPH

Jeremiah 9 in the BSB

Jeremiah 9 in the CCB

Jeremiah 9 in the CUV

Jeremiah 9 in the CUVS

Jeremiah 9 in the DBT

Jeremiah 9 in the DGDNT

Jeremiah 9 in the DHNT

Jeremiah 9 in the DNT

Jeremiah 9 in the ELBE

Jeremiah 9 in the EMTV

Jeremiah 9 in the ESV

Jeremiah 9 in the FBV

Jeremiah 9 in the FEB

Jeremiah 9 in the GGMNT

Jeremiah 9 in the GNT

Jeremiah 9 in the HARY

Jeremiah 9 in the HNT

Jeremiah 9 in the IRVA

Jeremiah 9 in the IRVB

Jeremiah 9 in the IRVG

Jeremiah 9 in the IRVH

Jeremiah 9 in the IRVK

Jeremiah 9 in the IRVM

Jeremiah 9 in the IRVM2

Jeremiah 9 in the IRVO

Jeremiah 9 in the IRVP

Jeremiah 9 in the IRVT

Jeremiah 9 in the IRVT2

Jeremiah 9 in the IRVU

Jeremiah 9 in the ISVN

Jeremiah 9 in the JSNT

Jeremiah 9 in the KAPI

Jeremiah 9 in the KBT1ETNIK

Jeremiah 9 in the KBV

Jeremiah 9 in the KJV

Jeremiah 9 in the KNFD

Jeremiah 9 in the LBA

Jeremiah 9 in the LBLA

Jeremiah 9 in the LNT

Jeremiah 9 in the LSV

Jeremiah 9 in the MAAL

Jeremiah 9 in the MBV

Jeremiah 9 in the MBV2

Jeremiah 9 in the MHNT

Jeremiah 9 in the MKNFD

Jeremiah 9 in the MNG

Jeremiah 9 in the MNT

Jeremiah 9 in the MNT2

Jeremiah 9 in the MRS1T

Jeremiah 9 in the NAA

Jeremiah 9 in the NASB

Jeremiah 9 in the NBLA

Jeremiah 9 in the NBS

Jeremiah 9 in the NBVTP

Jeremiah 9 in the NET2

Jeremiah 9 in the NIV11

Jeremiah 9 in the NNT

Jeremiah 9 in the NNT2

Jeremiah 9 in the NNT3

Jeremiah 9 in the PDDPT

Jeremiah 9 in the PFNT

Jeremiah 9 in the RMNT

Jeremiah 9 in the SBIAS

Jeremiah 9 in the SBIBS

Jeremiah 9 in the SBIBS2

Jeremiah 9 in the SBICS

Jeremiah 9 in the SBIDS

Jeremiah 9 in the SBIGS

Jeremiah 9 in the SBIHS

Jeremiah 9 in the SBIIS

Jeremiah 9 in the SBIIS2

Jeremiah 9 in the SBIIS3

Jeremiah 9 in the SBIKS

Jeremiah 9 in the SBIKS2

Jeremiah 9 in the SBIMS

Jeremiah 9 in the SBIOS

Jeremiah 9 in the SBIPS

Jeremiah 9 in the SBISS

Jeremiah 9 in the SBITS

Jeremiah 9 in the SBITS2

Jeremiah 9 in the SBITS3

Jeremiah 9 in the SBITS4

Jeremiah 9 in the SBIUS

Jeremiah 9 in the SBIVS

Jeremiah 9 in the SBT

Jeremiah 9 in the SBT1E

Jeremiah 9 in the SCHL

Jeremiah 9 in the SNT

Jeremiah 9 in the SUSU

Jeremiah 9 in the SUSU2

Jeremiah 9 in the SYNO

Jeremiah 9 in the TBIAOTANT

Jeremiah 9 in the TBT1E

Jeremiah 9 in the TBT1E2

Jeremiah 9 in the TFTIP

Jeremiah 9 in the TFTU

Jeremiah 9 in the TGNTATF3T

Jeremiah 9 in the THAI

Jeremiah 9 in the TNFD

Jeremiah 9 in the TNT

Jeremiah 9 in the TNTIK

Jeremiah 9 in the TNTIL

Jeremiah 9 in the TNTIN

Jeremiah 9 in the TNTIP

Jeremiah 9 in the TNTIZ

Jeremiah 9 in the TOMA

Jeremiah 9 in the TTENT

Jeremiah 9 in the UBG

Jeremiah 9 in the UGV

Jeremiah 9 in the UGV2

Jeremiah 9 in the UGV3

Jeremiah 9 in the VBL

Jeremiah 9 in the VDCC

Jeremiah 9 in the YALU

Jeremiah 9 in the YAPE

Jeremiah 9 in the YBVTP

Jeremiah 9 in the ZBP