Proverbs 12 (BOGWICC)
1 Munthu amene amakonda mwambo amakonda kudziwa zinthu,koma amene amadana ndi chidzudzulo ndi wopusa. 2 Munthu wabwino amapeza kuyanja pamaso pa Yehova,koma Yehova amatsutsa munthu wochita chinyengo. 3 Munthu sangakhazikike bwino pochita zoyipa,koma maziko a anthu olungama sadzatekeseka. 4 Mkazi wakhalidwe labwino ali ngati chipewa chaufumu kwa mwamuna wake,koma mkazi wochititsa manyazi ali ngati chilonda cha mafinya kwa mwamuna wake. 5 Maganizo a anthu olungama ndi owongoka,koma malangizo a anthu oyipa ndi achinyengo. 6 Mawu a anthu oyipa ndi ophetsa,koma mawu a anthu olungama amapulumutsa. 7 Anthu oyipa amagonjetsedwa ndipo amayiwalika,koma nyumba ya anthu olungama idzakhalabe. 8 Munthu amatamandidwa malinga ndi nzeru zake,koma anthu amitima yokhota amanyozedwa. 9 Nʼkwabwino kukhala munthu wonyozeka koma wodzigwirira ntchito nʼkukhala ndi zonse zofunika,kuposa kukhala wodzikuza koma ulibe ndi chakudya chomwe. 10 Munthu wolungama amasamalira moyo wa ziweto zake,koma chifundo cha munthu woyipa ndi chakhanza. 11 Wolima mʼmunda mwake mwakhama adzakhala ndi chakudya chochuluka,koma wotsata zopanda pake alibe nzeru. 12 Munthu woyipa amalakalaka zofunkha za anthu oyipa,koma mizu ya anthu olungama imabereka zipatso. 13 Munthu woyipa amakodwa mu msampha wa mayankhulidwe ake oyipa;koma munthu wolungama amatuluka mʼmavuto. 14 Munthu amakhala ndi zabwino zambiri chifukwa cha mawu akendipo ntchito zimene munthu agwira ndi manja ake zimamupindulira. 15 Zochita za chitsiru mwini wakeyo amaziona ngati zabwino,koma munthu wanzeru amamvera malangizo. 16 Mkwiyo wa chitsiru umadziwika nthawi yomweyo,koma munthu wanzeru sasamala kunyozedwa. 17 Woyankhula zoona amapereka umboni woona,koma mboni yabodza imafotokoza zonama. 18 Munthu woyankhula mosasamala mawu ake amalasa ngati lupanga,koma mawu a munthu wanzeru amachiritsa. 19 Mawu woona amakhala mpaka muyayakoma mawu abodza sakhalitsa. 20 Mʼmitima ya anthu amene amakonza zoyipa muli chinyengo;koma anthu olimbikitsa za mtendere amakhala ndi chimwemwe. 21 Palibe choyipa chimene chimagwera munthu wolungama,koma munthu woyipa mavuto samuthera. 22 Pakamwa pa bodza pamamunyansa Yehova,koma amakondwera ndi anthu oyankhula zoona. 23 Munthu wochenjera amabisa nzeru zake,koma munthu wopusa amaonetsa uchitsiru wake poyera. 24 Ogwira ntchito mwakhama adzalamulira,koma aulesi adzakhala ngati kapolo. 25 Nkhawa imakhala ngati katundu wolemera mu mtima mwa munthu,koma mawu abwino amamusangalatsa. 26 Munthu wolungama amatsogolera mnansi wake,koma ntchito za anthu oyipa zimawasocheretsa. 27 Munthu waulesi sapeza chimene akufuna,koma munthu wakhama amapeza chuma chamtengo wapatali. 28 Mʼnjira yachilungamo muli moyo;koma njira ya munthu woyipa imafikitsa ku imfa.
In Other Versions
Proverbs 12 in the ANGEFD
Proverbs 12 in the ANTPNG2D
Proverbs 12 in the AS21
Proverbs 12 in the BAGH
Proverbs 12 in the BBPNG
Proverbs 12 in the BBT1E
Proverbs 12 in the BDS
Proverbs 12 in the BEV
Proverbs 12 in the BHAD
Proverbs 12 in the BIB
Proverbs 12 in the BLPT
Proverbs 12 in the BNT
Proverbs 12 in the BNTABOOT
Proverbs 12 in the BNTLV
Proverbs 12 in the BOATCB
Proverbs 12 in the BOATCB2
Proverbs 12 in the BOBCV
Proverbs 12 in the BOCNT
Proverbs 12 in the BOECS
Proverbs 12 in the BOHCB
Proverbs 12 in the BOHCV
Proverbs 12 in the BOHLNT
Proverbs 12 in the BOHNTLTAL
Proverbs 12 in the BOICB
Proverbs 12 in the BOILNTAP
Proverbs 12 in the BOITCV
Proverbs 12 in the BOKCV
Proverbs 12 in the BOKCV2
Proverbs 12 in the BOKHWOG
Proverbs 12 in the BOKSSV
Proverbs 12 in the BOLCB
Proverbs 12 in the BOLCB2
Proverbs 12 in the BOMCV
Proverbs 12 in the BONAV
Proverbs 12 in the BONCB
Proverbs 12 in the BONLT
Proverbs 12 in the BONUT2
Proverbs 12 in the BOPLNT
Proverbs 12 in the BOSCB
Proverbs 12 in the BOSNC
Proverbs 12 in the BOTLNT
Proverbs 12 in the BOVCB
Proverbs 12 in the BOYCB
Proverbs 12 in the BPBB
Proverbs 12 in the BPH
Proverbs 12 in the BSB
Proverbs 12 in the CCB
Proverbs 12 in the CUV
Proverbs 12 in the CUVS
Proverbs 12 in the DBT
Proverbs 12 in the DGDNT
Proverbs 12 in the DHNT
Proverbs 12 in the DNT
Proverbs 12 in the ELBE
Proverbs 12 in the EMTV
Proverbs 12 in the ESV
Proverbs 12 in the FBV
Proverbs 12 in the FEB
Proverbs 12 in the GGMNT
Proverbs 12 in the GNT
Proverbs 12 in the HARY
Proverbs 12 in the HNT
Proverbs 12 in the IRVA
Proverbs 12 in the IRVB
Proverbs 12 in the IRVG
Proverbs 12 in the IRVH
Proverbs 12 in the IRVK
Proverbs 12 in the IRVM
Proverbs 12 in the IRVM2
Proverbs 12 in the IRVO
Proverbs 12 in the IRVP
Proverbs 12 in the IRVT
Proverbs 12 in the IRVT2
Proverbs 12 in the IRVU
Proverbs 12 in the ISVN
Proverbs 12 in the JSNT
Proverbs 12 in the KAPI
Proverbs 12 in the KBT1ETNIK
Proverbs 12 in the KBV
Proverbs 12 in the KJV
Proverbs 12 in the KNFD
Proverbs 12 in the LBA
Proverbs 12 in the LBLA
Proverbs 12 in the LNT
Proverbs 12 in the LSV
Proverbs 12 in the MAAL
Proverbs 12 in the MBV
Proverbs 12 in the MBV2
Proverbs 12 in the MHNT
Proverbs 12 in the MKNFD
Proverbs 12 in the MNG
Proverbs 12 in the MNT
Proverbs 12 in the MNT2
Proverbs 12 in the MRS1T
Proverbs 12 in the NAA
Proverbs 12 in the NASB
Proverbs 12 in the NBLA
Proverbs 12 in the NBS
Proverbs 12 in the NBVTP
Proverbs 12 in the NET2
Proverbs 12 in the NIV11
Proverbs 12 in the NNT
Proverbs 12 in the NNT2
Proverbs 12 in the NNT3
Proverbs 12 in the PDDPT
Proverbs 12 in the PFNT
Proverbs 12 in the RMNT
Proverbs 12 in the SBIAS
Proverbs 12 in the SBIBS
Proverbs 12 in the SBIBS2
Proverbs 12 in the SBICS
Proverbs 12 in the SBIDS
Proverbs 12 in the SBIGS
Proverbs 12 in the SBIHS
Proverbs 12 in the SBIIS
Proverbs 12 in the SBIIS2
Proverbs 12 in the SBIIS3
Proverbs 12 in the SBIKS
Proverbs 12 in the SBIKS2
Proverbs 12 in the SBIMS
Proverbs 12 in the SBIOS
Proverbs 12 in the SBIPS
Proverbs 12 in the SBISS
Proverbs 12 in the SBITS
Proverbs 12 in the SBITS2
Proverbs 12 in the SBITS3
Proverbs 12 in the SBITS4
Proverbs 12 in the SBIUS
Proverbs 12 in the SBIVS
Proverbs 12 in the SBT
Proverbs 12 in the SBT1E
Proverbs 12 in the SCHL
Proverbs 12 in the SNT
Proverbs 12 in the SUSU
Proverbs 12 in the SUSU2
Proverbs 12 in the SYNO
Proverbs 12 in the TBIAOTANT
Proverbs 12 in the TBT1E
Proverbs 12 in the TBT1E2
Proverbs 12 in the TFTIP
Proverbs 12 in the TFTU
Proverbs 12 in the TGNTATF3T
Proverbs 12 in the THAI
Proverbs 12 in the TNFD
Proverbs 12 in the TNT
Proverbs 12 in the TNTIK
Proverbs 12 in the TNTIL
Proverbs 12 in the TNTIN
Proverbs 12 in the TNTIP
Proverbs 12 in the TNTIZ
Proverbs 12 in the TOMA
Proverbs 12 in the TTENT
Proverbs 12 in the UBG
Proverbs 12 in the UGV
Proverbs 12 in the UGV2
Proverbs 12 in the UGV3
Proverbs 12 in the VBL
Proverbs 12 in the VDCC
Proverbs 12 in the YALU
Proverbs 12 in the YAPE
Proverbs 12 in the YBVTP
Proverbs 12 in the ZBP