Proverbs 13 (BOGWICC)

1 Mwana wanzeru amamvera malangizo a abambo ake,koma mwana wonyoza samamvetsera chidzudzulo. 2 Munthu amapeza zinthu zabwino chifukwa cha mawu ake,koma anthu osakhulupirika amalakalaka zachiwawa basi. 3 Iye amene amagwira pakamwa pake amateteza moyo wake,koma amene amayankhula zopanda pake adzawonongeka. 4 Munthu waulesi amakhumbira zinthu koma sapeza kanthu,koma munthu wakhama adzalemera. 5 Munthu wolungama amadana ndi zabodza,koma zochita za munthu woyipa zimanyansa ndiponso zimachititsa manyazi. 6 Chilungamo chimateteza munthu wangwiro,koma tchimo limagwetsa munthu wochimwa. 7 Wina amadziyesa kuti ndi wolemera chonsecho alibe kanthu kalikonse;munthu wina amaoneka ngati wosauka chonsecho ali ndi chuma chambiri. 8 Chuma cha munthu wolemera chitha kuwombola moyo wake,koma munthu wosauka amamva chidzudzulo. 9 Nyale ya munthu wolungama ndi yokondweretsa,koma nyale ya munthu woyipa imazimitsidwa. 10 Chipongwe chosamalabadirako za anthu ena chimadzetsa mikangano,koma womva malangizo a anzawo ndiwo ali ndi nzeru. 11 Chuma chochipeza mofulumira chidzatha pangʼonopangʼonokoma chuma chosonkhanitsidwa pangʼonopangʼono chidzachulukirachulukira. 12 Chinthu chochiyembekezera chikalephereka chimalefula mtima,koma chinthu chochilakalaka chikachitikadi chimakhala ngati mtengo wamoyo. 13 Amene amanyoza malangizo adzawonongeka,koma amene amasamala lamulo amalandira mphotho. 14 Malangizo a munthu wanzeru ali ngati kasupe wamoyo;amathandiza munthu kuti asakondwe mu msampha wa imfa. 15 Munthu wa nzeru zabwino amapeza kuyanja pakati pa anthu,koma munthu wosakhulupirika adzawonongeka. 16 Munthu wochenjera amachita zinthu mwanzeru,koma chitsiru chimaonetsa poyera uchitsiru wake. 17 Wamthenga woyipa amagwetsa anthu mʼmavuto,koma nthumwi yodalirika imabweretsa mtendere. 18 Wokana mwambo adzasauka ndi kunyozedwa,koma wosamala chidzudzulo adzalemekezedwa. 19 Chinthu chochilakalaka chikachitika chimasangalatsa mtima,koma zitsiru zimadana ndi kuleka zoyipa. 20 Woyenda ndi anthu anzeru nayenso adzakhala wanzeru;koma woyenda ndi zitsiru adzapwetekeka. 21 Choyipa chitsata mwini,koma wochita zolungama adzalandira mphotho yabwino. 22 Munthu wabwino amasiyira zidzukulu zake cholowa,koma chuma cha munthu wochimwa amachilandira ndi olungama. 23 Tsala la munthu wosauka limalola chakudya chambiri,koma anthu opanda chilungamo amachilanda. 24 Amene sakwapula mwana wake, ndiye kuti amamuda,koma wokonda mwana wake sazengereza kumulanga. 25 Munthu wolungama amakhala ndi zakudya zoti adye nʼkukhuta,koma mʼmimba mwa munthu woyipa mumakhala pululu ndi njala.

In Other Versions

Proverbs 13 in the ANGEFD

Proverbs 13 in the ANTPNG2D

Proverbs 13 in the AS21

Proverbs 13 in the BAGH

Proverbs 13 in the BBPNG

Proverbs 13 in the BBT1E

Proverbs 13 in the BDS

Proverbs 13 in the BEV

Proverbs 13 in the BHAD

Proverbs 13 in the BIB

Proverbs 13 in the BLPT

Proverbs 13 in the BNT

Proverbs 13 in the BNTABOOT

Proverbs 13 in the BNTLV

Proverbs 13 in the BOATCB

Proverbs 13 in the BOATCB2

Proverbs 13 in the BOBCV

Proverbs 13 in the BOCNT

Proverbs 13 in the BOECS

Proverbs 13 in the BOHCB

Proverbs 13 in the BOHCV

Proverbs 13 in the BOHLNT

Proverbs 13 in the BOHNTLTAL

Proverbs 13 in the BOICB

Proverbs 13 in the BOILNTAP

Proverbs 13 in the BOITCV

Proverbs 13 in the BOKCV

Proverbs 13 in the BOKCV2

Proverbs 13 in the BOKHWOG

Proverbs 13 in the BOKSSV

Proverbs 13 in the BOLCB

Proverbs 13 in the BOLCB2

Proverbs 13 in the BOMCV

Proverbs 13 in the BONAV

Proverbs 13 in the BONCB

Proverbs 13 in the BONLT

Proverbs 13 in the BONUT2

Proverbs 13 in the BOPLNT

Proverbs 13 in the BOSCB

Proverbs 13 in the BOSNC

Proverbs 13 in the BOTLNT

Proverbs 13 in the BOVCB

Proverbs 13 in the BOYCB

Proverbs 13 in the BPBB

Proverbs 13 in the BPH

Proverbs 13 in the BSB

Proverbs 13 in the CCB

Proverbs 13 in the CUV

Proverbs 13 in the CUVS

Proverbs 13 in the DBT

Proverbs 13 in the DGDNT

Proverbs 13 in the DHNT

Proverbs 13 in the DNT

Proverbs 13 in the ELBE

Proverbs 13 in the EMTV

Proverbs 13 in the ESV

Proverbs 13 in the FBV

Proverbs 13 in the FEB

Proverbs 13 in the GGMNT

Proverbs 13 in the GNT

Proverbs 13 in the HARY

Proverbs 13 in the HNT

Proverbs 13 in the IRVA

Proverbs 13 in the IRVB

Proverbs 13 in the IRVG

Proverbs 13 in the IRVH

Proverbs 13 in the IRVK

Proverbs 13 in the IRVM

Proverbs 13 in the IRVM2

Proverbs 13 in the IRVO

Proverbs 13 in the IRVP

Proverbs 13 in the IRVT

Proverbs 13 in the IRVT2

Proverbs 13 in the IRVU

Proverbs 13 in the ISVN

Proverbs 13 in the JSNT

Proverbs 13 in the KAPI

Proverbs 13 in the KBT1ETNIK

Proverbs 13 in the KBV

Proverbs 13 in the KJV

Proverbs 13 in the KNFD

Proverbs 13 in the LBA

Proverbs 13 in the LBLA

Proverbs 13 in the LNT

Proverbs 13 in the LSV

Proverbs 13 in the MAAL

Proverbs 13 in the MBV

Proverbs 13 in the MBV2

Proverbs 13 in the MHNT

Proverbs 13 in the MKNFD

Proverbs 13 in the MNG

Proverbs 13 in the MNT

Proverbs 13 in the MNT2

Proverbs 13 in the MRS1T

Proverbs 13 in the NAA

Proverbs 13 in the NASB

Proverbs 13 in the NBLA

Proverbs 13 in the NBS

Proverbs 13 in the NBVTP

Proverbs 13 in the NET2

Proverbs 13 in the NIV11

Proverbs 13 in the NNT

Proverbs 13 in the NNT2

Proverbs 13 in the NNT3

Proverbs 13 in the PDDPT

Proverbs 13 in the PFNT

Proverbs 13 in the RMNT

Proverbs 13 in the SBIAS

Proverbs 13 in the SBIBS

Proverbs 13 in the SBIBS2

Proverbs 13 in the SBICS

Proverbs 13 in the SBIDS

Proverbs 13 in the SBIGS

Proverbs 13 in the SBIHS

Proverbs 13 in the SBIIS

Proverbs 13 in the SBIIS2

Proverbs 13 in the SBIIS3

Proverbs 13 in the SBIKS

Proverbs 13 in the SBIKS2

Proverbs 13 in the SBIMS

Proverbs 13 in the SBIOS

Proverbs 13 in the SBIPS

Proverbs 13 in the SBISS

Proverbs 13 in the SBITS

Proverbs 13 in the SBITS2

Proverbs 13 in the SBITS3

Proverbs 13 in the SBITS4

Proverbs 13 in the SBIUS

Proverbs 13 in the SBIVS

Proverbs 13 in the SBT

Proverbs 13 in the SBT1E

Proverbs 13 in the SCHL

Proverbs 13 in the SNT

Proverbs 13 in the SUSU

Proverbs 13 in the SUSU2

Proverbs 13 in the SYNO

Proverbs 13 in the TBIAOTANT

Proverbs 13 in the TBT1E

Proverbs 13 in the TBT1E2

Proverbs 13 in the TFTIP

Proverbs 13 in the TFTU

Proverbs 13 in the TGNTATF3T

Proverbs 13 in the THAI

Proverbs 13 in the TNFD

Proverbs 13 in the TNT

Proverbs 13 in the TNTIK

Proverbs 13 in the TNTIL

Proverbs 13 in the TNTIN

Proverbs 13 in the TNTIP

Proverbs 13 in the TNTIZ

Proverbs 13 in the TOMA

Proverbs 13 in the TTENT

Proverbs 13 in the UBG

Proverbs 13 in the UGV

Proverbs 13 in the UGV2

Proverbs 13 in the UGV3

Proverbs 13 in the VBL

Proverbs 13 in the VDCC

Proverbs 13 in the YALU

Proverbs 13 in the YAPE

Proverbs 13 in the YBVTP

Proverbs 13 in the ZBP