Psalms 35 (BOGWICC)
undefined Salimo la Davide. 1 Inu Yehova, mulimbane nawo amene akulimbana nane;mumenyane nawo amene akumenyana nane. 2 Tengani chishango ndi lihawo;dzukani ndipo bwerani mundithandize. 3 Tengani mkondo ndi nthungo,kulimbana ndi iwo amene akundithamangitsa.Uzani moyo wanga kuti,“Ine ndine chipulumutso chako.” 4 Iwo amene akufunafuna moyo wangaanyozedwe ndi kuchita manyazi;iwo amene akukonza kuti moyo wanga uwonongekeabwerere mʼmbuyo mochititsa mantha. 5 Akhale ngati mankhusu owuluka ndi mphepopamene mngelo wa Yehova akuwapirikitsa. 6 Njira yawo ikhale ya mdima ndi yotererapamene mngelo wa Yehova akuwathamangitsa. 7 Popeza ananditchera ukonde popanda chifukwandipo popanda chifukwa andikumbira dzenje, 8 chiwonongeko chiwapeza modzidzimutsaukonde umene iwo abisa uwakole,agwere mʼdzenje kuti awonongedwe. 9 Pamenepo moyo wanga udzakondwera mwa Yehovandi kusangalala ndi chipulumutso chake. 10 Thupi langa lidzafuwula mokondwera,“Ndani angafanane nanu Yehova?Mumalanditsa osauka kwa amene ali ndi mphamvu zambiri,osauka ndi osowa kwa iwo amene amawalanda.” 11 Mboni zopanda chisoni zinayimirira,zinandifunsa zinthu zimene sindikuzidziwa. 12 Iwo anandibwezera zoyipa pa zabwinondipo anasiya moyo wanga pa chisoni. 13 Koma pamene iwo ankadwala, ine ndinavala chigudulindi kudzichepetsa ndekha posala zakudya.Pamene mapemphero anga anabwerera kwa ine osayankhidwa, 14 ndinayendayenda ndi kulira maliro,kumulira ngati bwenzi langa kapena mʼbale wanga.Ndinaweramitsa mutu wanga mosweka mtimakukhala ngati ndikulira amayi anga. 15 Koma pamene ndinaphunthwa, iwo anasonkhana mosangalala;ondithira nkhondo anasonkhana kutsutsana nane, ineyo osadziwa.Iwo sanasiye kundiyankhulira mawu onyoza. 16 Monga anthu osapembedza, iwo anandinyoza mwachipongwe;anandikukutira mano awo. 17 Ambuye, mpaka liti mudzakhala mukungoyangʼana?Landitsani moyo wanga ku chiwonongeko chawo,moyo wanga wopambana ku mikango. 18 Ndidzakuyamikani mu msonkhano waukulu;pakati pa gulu lalikulu la anthu ndidzakutamandani. 19 Musalole adani anga onyengaakondwere chifukwa cha masautso anga;musalole kuti amene amadana nane popanda chifukwaandiyangʼane chamʼmbali mondinyoza. 20 Iwowo sayankhula mwamtendere,koma amaganizira zonamiziraiwo amene amakhala mwabata mʼdziko. 21 Iwo amandiseka mofuwula ndipo amati, “Haa! Haa!Ndipo ndi maso athuwa ife taziona.” 22 Yehova mwaona zimenezi; musakhale chete.Ambuye musakhale kutali ndi ine. 23 Dzukani, ndipo nyamukani kunditeteza!Mulimbane nawo chifukwa cha ine, Mulungu wanga ndi Ambuye anga. 24 Onetsani kusalakwa kwanga mwa chilungamo chanu, Inu Yehova Mulungu wanga.Musalole kuti akondwere chifukwa cha mavuto anga. 25 Musalole kuti aganize kuti, “Amati atani, zachitika monga momwe timafunira!”Kapena kunena kuti, “Tamutha ameneyu basi.” 26 Onse amene amakondwera ndi masautso angaachite manyazi ndi kusokonezeka.Onse amene amadzikweza kufuna kundipambana,avekedwe manyazi ndi mnyozo ngati zovala. 27 Koma amene amakondwera chifukwa chakuti ndine wosalakwa,afuwule mwachimwemwe ndi chisangalalo.Nthawi zonse azinena kuti, “Yehova akwezeke,Iye amene amakondwera ndi kupeza bwino kwa mtumiki wake.” 28 Pakamwa panga padzayankhula za chilungamo chanundi za matamando anu tsiku lonse.
In Other Versions
Psalms 35 in the ANGEFD
Psalms 35 in the ANTPNG2D
Psalms 35 in the AS21
Psalms 35 in the BAGH
Psalms 35 in the BBPNG
Psalms 35 in the BBT1E
Psalms 35 in the BDS
Psalms 35 in the BEV
Psalms 35 in the BHAD
Psalms 35 in the BIB
Psalms 35 in the BLPT
Psalms 35 in the BNT
Psalms 35 in the BNTABOOT
Psalms 35 in the BNTLV
Psalms 35 in the BOATCB
Psalms 35 in the BOATCB2
Psalms 35 in the BOBCV
Psalms 35 in the BOCNT
Psalms 35 in the BOECS
Psalms 35 in the BOHCB
Psalms 35 in the BOHCV
Psalms 35 in the BOHLNT
Psalms 35 in the BOHNTLTAL
Psalms 35 in the BOICB
Psalms 35 in the BOILNTAP
Psalms 35 in the BOITCV
Psalms 35 in the BOKCV
Psalms 35 in the BOKCV2
Psalms 35 in the BOKHWOG
Psalms 35 in the BOKSSV
Psalms 35 in the BOLCB
Psalms 35 in the BOLCB2
Psalms 35 in the BOMCV
Psalms 35 in the BONAV
Psalms 35 in the BONCB
Psalms 35 in the BONLT
Psalms 35 in the BONUT2
Psalms 35 in the BOPLNT
Psalms 35 in the BOSCB
Psalms 35 in the BOSNC
Psalms 35 in the BOTLNT
Psalms 35 in the BOVCB
Psalms 35 in the BOYCB
Psalms 35 in the BPBB
Psalms 35 in the BPH
Psalms 35 in the BSB
Psalms 35 in the CCB
Psalms 35 in the CUV
Psalms 35 in the CUVS
Psalms 35 in the DBT
Psalms 35 in the DGDNT
Psalms 35 in the DHNT
Psalms 35 in the DNT
Psalms 35 in the ELBE
Psalms 35 in the EMTV
Psalms 35 in the ESV
Psalms 35 in the FBV
Psalms 35 in the FEB
Psalms 35 in the GGMNT
Psalms 35 in the GNT
Psalms 35 in the HARY
Psalms 35 in the HNT
Psalms 35 in the IRVA
Psalms 35 in the IRVB
Psalms 35 in the IRVG
Psalms 35 in the IRVH
Psalms 35 in the IRVK
Psalms 35 in the IRVM
Psalms 35 in the IRVM2
Psalms 35 in the IRVO
Psalms 35 in the IRVP
Psalms 35 in the IRVT
Psalms 35 in the IRVT2
Psalms 35 in the IRVU
Psalms 35 in the ISVN
Psalms 35 in the JSNT
Psalms 35 in the KAPI
Psalms 35 in the KBT1ETNIK
Psalms 35 in the KBV
Psalms 35 in the KJV
Psalms 35 in the KNFD
Psalms 35 in the LBA
Psalms 35 in the LBLA
Psalms 35 in the LNT
Psalms 35 in the LSV
Psalms 35 in the MAAL
Psalms 35 in the MBV
Psalms 35 in the MBV2
Psalms 35 in the MHNT
Psalms 35 in the MKNFD
Psalms 35 in the MNG
Psalms 35 in the MNT
Psalms 35 in the MNT2
Psalms 35 in the MRS1T
Psalms 35 in the NAA
Psalms 35 in the NASB
Psalms 35 in the NBLA
Psalms 35 in the NBS
Psalms 35 in the NBVTP
Psalms 35 in the NET2
Psalms 35 in the NIV11
Psalms 35 in the NNT
Psalms 35 in the NNT2
Psalms 35 in the NNT3
Psalms 35 in the PDDPT
Psalms 35 in the PFNT
Psalms 35 in the RMNT
Psalms 35 in the SBIAS
Psalms 35 in the SBIBS
Psalms 35 in the SBIBS2
Psalms 35 in the SBICS
Psalms 35 in the SBIDS
Psalms 35 in the SBIGS
Psalms 35 in the SBIHS
Psalms 35 in the SBIIS
Psalms 35 in the SBIIS2
Psalms 35 in the SBIIS3
Psalms 35 in the SBIKS
Psalms 35 in the SBIKS2
Psalms 35 in the SBIMS
Psalms 35 in the SBIOS
Psalms 35 in the SBIPS
Psalms 35 in the SBISS
Psalms 35 in the SBITS
Psalms 35 in the SBITS2
Psalms 35 in the SBITS3
Psalms 35 in the SBITS4
Psalms 35 in the SBIUS
Psalms 35 in the SBIVS
Psalms 35 in the SBT
Psalms 35 in the SBT1E
Psalms 35 in the SCHL
Psalms 35 in the SNT
Psalms 35 in the SUSU
Psalms 35 in the SUSU2
Psalms 35 in the SYNO
Psalms 35 in the TBIAOTANT
Psalms 35 in the TBT1E
Psalms 35 in the TBT1E2
Psalms 35 in the TFTIP
Psalms 35 in the TFTU
Psalms 35 in the TGNTATF3T
Psalms 35 in the THAI
Psalms 35 in the TNFD
Psalms 35 in the TNT
Psalms 35 in the TNTIK
Psalms 35 in the TNTIL
Psalms 35 in the TNTIN
Psalms 35 in the TNTIP
Psalms 35 in the TNTIZ
Psalms 35 in the TOMA
Psalms 35 in the TTENT
Psalms 35 in the UBG
Psalms 35 in the UGV
Psalms 35 in the UGV2
Psalms 35 in the UGV3
Psalms 35 in the VBL
Psalms 35 in the VDCC
Psalms 35 in the YALU
Psalms 35 in the YAPE
Psalms 35 in the YBVTP
Psalms 35 in the ZBP