Psalms 71 (BOGWICC)

1 Mwa Inu Yehova ine ndathawiramo;musalole kuti ndichititsidwe manyazi. 2 Mundilanditse ndi kundipulumutsa mwa chilungamo chanu,mutchere khutu lanu ndi kundipulumutsa. 3 Mukhale thanthwe langa lothawirapo,kumene ine nditha kupita nthawi zonse;lamulani kuti ndipulumuke,pakuti Inu ndinu thanthwe langa ndi linga langa. 4 Landitseni Inu Mulungu wanga, kuchoka mʼdzanja la oyipa,kuchoka mʼdzanja la oyipa ndi anthu ankhanza. 5 Pakuti Inu mwakhala chiyembekezo changa, Inu Ambuye Wamphamvuzonse,chilimbikitso changa kuyambira ndili mwana. 6 Kuyambira pamene ndinabadwa, ndakhala ndikudalira Inu;Inu munanditulutsa mʼmimba mwa amayi anga,ndipo ndidzakupembedzani nthawi zonse. 7 Ine ndakhala chinthu chodabwitsa kwa anthu ambirikoma Inu ndinu wonditchinjiriza wamphamvu. 8 Pakamwa panga padzaza ndi matamando anu,kulengeza ulemerero wanu tsiku lonse. 9 Musanditaye pamene ndakalamba;musandisiye pamene mphamvu zanga zatha. 10 Pakuti adani anga ayankhula motsutsana nane;iwo amene amadikira kuti andiphe amapangana pamodzi. 11 Iwo amati, “Mulungu wamusiya;mutsatireni ndi kumugwira,pakuti palibe amene adzamupulumutse.” 12 Musakhale kutali ndi ine Inu Mulungu,bwerani msanga, Inu Mulungu wanga; thandizeni. 13 Ondineneza anga awonongeke mwa manyazi,iwo amene akufuna kundipwetekaavale chitonzo ndi manyazi. 14 Koma ine ndidzakhala ndi chiyembekezo mwa Inu nthawi zonse,ndidzakutamandani mowirikizawirikiza. 15 Pakamwa panga padzafotokoza za chilungamo chanu,za chipulumutso chanu tsiku lonse,ngakhale sindikudziwa muyeso wake. 16 Ndidzabwera ndi kulengeza za machitidwe amphamvu zanu Inu Ambuye Wamphamvuzonse.Ndidzalengeza chilungamo chanu, chanu chokha. 17 Kuyambira ubwana wanga, Inu Mulungu mwakhala mukundiphunzitsa,ndipo mpaka lero ine ndikulengeza za ntchito zanu zodabwitsa 18 Ngakhale pamene ndakalamba ndipo imvi zili mbuumusanditaye Inu Mulungu,mpaka nditalengeza mphamvu zanukwa mibado yonse yakutsogolo. 19 Mphamvu zanu ndi kulungama kwanu zimafika mpaka kumwambamwamba.Ndani wofanana nanu Inu Mulungu,amene mwachita zazikulu? 20 Ngakhale mwandionetsa mavutoambiri owawa,mudzabwezeretsanso moyo wanga;kuchokera kunsi kwa dziko lapansi,mudzandiukitsanso. 21 Inu mudzachulukitsa ulemu wangandi kunditonthozanso. 22 Ndidzakutamandani ndi zezechifukwa cha kukhulupirika kwanu Mulungu,ndidzayimba matamando kwa Inu ndi pangwe,Inu Woyera wa Israeli. 23 Milomo yanga idzafuwula ndi chimwemwepamene ndidzayimba matamando kwa Inuamene mwandiwombola. 24 Lilime langa lidzafotokoza za ntchito zanu zachilungamotsiku lonse,pakuti iwo amene amafuna kundipwetekaachititsidwa manyazi ndi kusokonezedwa.

In Other Versions

Psalms 71 in the ANGEFD

Psalms 71 in the ANTPNG2D

Psalms 71 in the AS21

Psalms 71 in the BAGH

Psalms 71 in the BBPNG

Psalms 71 in the BBT1E

Psalms 71 in the BDS

Psalms 71 in the BEV

Psalms 71 in the BHAD

Psalms 71 in the BIB

Psalms 71 in the BLPT

Psalms 71 in the BNT

Psalms 71 in the BNTABOOT

Psalms 71 in the BNTLV

Psalms 71 in the BOATCB

Psalms 71 in the BOATCB2

Psalms 71 in the BOBCV

Psalms 71 in the BOCNT

Psalms 71 in the BOECS

Psalms 71 in the BOHCB

Psalms 71 in the BOHCV

Psalms 71 in the BOHLNT

Psalms 71 in the BOHNTLTAL

Psalms 71 in the BOICB

Psalms 71 in the BOILNTAP

Psalms 71 in the BOITCV

Psalms 71 in the BOKCV

Psalms 71 in the BOKCV2

Psalms 71 in the BOKHWOG

Psalms 71 in the BOKSSV

Psalms 71 in the BOLCB

Psalms 71 in the BOLCB2

Psalms 71 in the BOMCV

Psalms 71 in the BONAV

Psalms 71 in the BONCB

Psalms 71 in the BONLT

Psalms 71 in the BONUT2

Psalms 71 in the BOPLNT

Psalms 71 in the BOSCB

Psalms 71 in the BOSNC

Psalms 71 in the BOTLNT

Psalms 71 in the BOVCB

Psalms 71 in the BOYCB

Psalms 71 in the BPBB

Psalms 71 in the BPH

Psalms 71 in the BSB

Psalms 71 in the CCB

Psalms 71 in the CUV

Psalms 71 in the CUVS

Psalms 71 in the DBT

Psalms 71 in the DGDNT

Psalms 71 in the DHNT

Psalms 71 in the DNT

Psalms 71 in the ELBE

Psalms 71 in the EMTV

Psalms 71 in the ESV

Psalms 71 in the FBV

Psalms 71 in the FEB

Psalms 71 in the GGMNT

Psalms 71 in the GNT

Psalms 71 in the HARY

Psalms 71 in the HNT

Psalms 71 in the IRVA

Psalms 71 in the IRVB

Psalms 71 in the IRVG

Psalms 71 in the IRVH

Psalms 71 in the IRVK

Psalms 71 in the IRVM

Psalms 71 in the IRVM2

Psalms 71 in the IRVO

Psalms 71 in the IRVP

Psalms 71 in the IRVT

Psalms 71 in the IRVT2

Psalms 71 in the IRVU

Psalms 71 in the ISVN

Psalms 71 in the JSNT

Psalms 71 in the KAPI

Psalms 71 in the KBT1ETNIK

Psalms 71 in the KBV

Psalms 71 in the KJV

Psalms 71 in the KNFD

Psalms 71 in the LBA

Psalms 71 in the LBLA

Psalms 71 in the LNT

Psalms 71 in the LSV

Psalms 71 in the MAAL

Psalms 71 in the MBV

Psalms 71 in the MBV2

Psalms 71 in the MHNT

Psalms 71 in the MKNFD

Psalms 71 in the MNG

Psalms 71 in the MNT

Psalms 71 in the MNT2

Psalms 71 in the MRS1T

Psalms 71 in the NAA

Psalms 71 in the NASB

Psalms 71 in the NBLA

Psalms 71 in the NBS

Psalms 71 in the NBVTP

Psalms 71 in the NET2

Psalms 71 in the NIV11

Psalms 71 in the NNT

Psalms 71 in the NNT2

Psalms 71 in the NNT3

Psalms 71 in the PDDPT

Psalms 71 in the PFNT

Psalms 71 in the RMNT

Psalms 71 in the SBIAS

Psalms 71 in the SBIBS

Psalms 71 in the SBIBS2

Psalms 71 in the SBICS

Psalms 71 in the SBIDS

Psalms 71 in the SBIGS

Psalms 71 in the SBIHS

Psalms 71 in the SBIIS

Psalms 71 in the SBIIS2

Psalms 71 in the SBIIS3

Psalms 71 in the SBIKS

Psalms 71 in the SBIKS2

Psalms 71 in the SBIMS

Psalms 71 in the SBIOS

Psalms 71 in the SBIPS

Psalms 71 in the SBISS

Psalms 71 in the SBITS

Psalms 71 in the SBITS2

Psalms 71 in the SBITS3

Psalms 71 in the SBITS4

Psalms 71 in the SBIUS

Psalms 71 in the SBIVS

Psalms 71 in the SBT

Psalms 71 in the SBT1E

Psalms 71 in the SCHL

Psalms 71 in the SNT

Psalms 71 in the SUSU

Psalms 71 in the SUSU2

Psalms 71 in the SYNO

Psalms 71 in the TBIAOTANT

Psalms 71 in the TBT1E

Psalms 71 in the TBT1E2

Psalms 71 in the TFTIP

Psalms 71 in the TFTU

Psalms 71 in the TGNTATF3T

Psalms 71 in the THAI

Psalms 71 in the TNFD

Psalms 71 in the TNT

Psalms 71 in the TNTIK

Psalms 71 in the TNTIL

Psalms 71 in the TNTIN

Psalms 71 in the TNTIP

Psalms 71 in the TNTIZ

Psalms 71 in the TOMA

Psalms 71 in the TTENT

Psalms 71 in the UBG

Psalms 71 in the UGV

Psalms 71 in the UGV2

Psalms 71 in the UGV3

Psalms 71 in the VBL

Psalms 71 in the VDCC

Psalms 71 in the YALU

Psalms 71 in the YAPE

Psalms 71 in the YBVTP

Psalms 71 in the ZBP