1 Thessalonians 2 (BOGWICC)

1 Abale, mukudziwa kuti kudzacheza kwathu kwa inu sikunali kosapindulitsa. 2 Monga mukudziwa, ife nʼkuti titazunzika ndi kunyozedwa ku Filipi. Koma mothandizidwa ndi Mulungu wathu, tinalimba mtima mpaka kukulalikirani uthenga wake wabwino ngakhale ambiri ankatsutsana nafe. 3 Pakuti kulalikira kumene tikuchita, sitikuchita ndi maganizo olakwika kapena zolinga zoyipa, kapenanso kufuna kukunamizani. 4 Koma timayankhula monga anthu ovomerezeka ndi Mulungu ndi osungitsidwa Uthenga Wabwino. Ife sitikufuna kukondweretsa anthu koma Mulungu, amene amasanthula mitima yathu. 5 Monga mukudziwa kuti sitinagwiritse ntchito mawu oshashalika kapena mtima wofuna phindu, Mulungu ndiye mboni yathu. 6 Ife sitinafune kutamidwa ndi anthu, kapena ndi inu, kapena wina aliyense mwa inu. 7 Ngati atumwi a Khristu tikanatha kukhala cholemetsa kwa inu, mʼmalo mwake tinali ngati ana aangʼono pakati panu.Monga mmene amayi amasamalira ana awo angʼono, 8 moteronso tinakusamalirani. Chifukwa tinakukondani kwambiri, tinali okondwa kugawana nanu osati Uthenga Wabwino wa Mulungu wokha, komanso miyoyo yathu. 9 Abale, pakuti mukumbukira kugwira ntchito kwathu kwambiri ndi kuvutika; ife tinagwira ntchito usana ndi usiku ndi cholinga chakuti tisakhale cholemetsa, kwa aliyense pamene ife tinkalalikira Uthenga Wabwino wa Mulungu kwa inu. 10 Inu ndinu mboni, ndiponso Mulungu, kuti tinali oyera mtima, olungama ndi wopanda chifukwa pakati panu amene munakhulupirira. 11 Monga mudziwa kuti ife tinkasamala aliyense wa inu monga abambo amasamalira ana ake, 12 kulimbikitsa, kutonthoza ndi kukupemphani kuti mukhale moyo oyenera Mulungu amene anakuyitanani kuti mulowe mu ufumu wake ndi ulemerero. 13 Ndipo ifenso tikuyamika Mulungu kosalekeza chifukwa mutalandira Mawu a Mulungu, amene munawamva kuchokera kwa ife, munawalandira osati ngati mawu a anthu, koma monga momwe alili, Mawu a Mulungu, amene akugwira ntchito mwa inu amene mukhulupirira. 14 Pakuti inu abale, munakhala otsanzira mipingo ya Mulungu ya ku Yudeya, imene ili mwa Khristu Yesu. Munasautsidwa kuchokera kwa anthu a mtundu wanu, zinthu zomwezo zimene mipingo imeneyi inasautsidwa ndi Ayuda, 15 amene anapha Ambuye Yesu ndi aneneri ndipo anatithamangitsanso ife. Iwo sakondweretsa Mulungu ndipo amadana ndi anthu onse 16 ndikutiretsa ife kuti tisayankhule ndi a mitundu ina kuti angapulumuke. Motero iwo amadziwunjikira okha machimo awo. Mkwiyo wa Mulungu wa afikira tsopano. 17 Koma abale, titasiyana kwa nthawi pangʼono (mʼthupi osati mʼmaganizo), tinayesetsa koposa kuti tikuoneni. 18 Pakuti ife tinafuna kubweranso kwa inu, makamaka ine Paulo, ndinayesa kangapo koma Satana anatiletsa. 19 Nanga chiyembekezo chathu, chimwemwe chathu kapena chaufumu chimene ife tidzanyadira pamaso pa Ambuye athu Yesu Khristu pamene abwere ndi chiyani? Kodi si inu? 20 Indedi, inu ndinu ulemerero wathu ndi chimwemwe.

In Other Versions

1 Thessalonians 2 in the ANGEFD

1 Thessalonians 2 in the ANTPNG2D

1 Thessalonians 2 in the AS21

1 Thessalonians 2 in the BAGH

1 Thessalonians 2 in the BBPNG

1 Thessalonians 2 in the BBT1E

1 Thessalonians 2 in the BDS

1 Thessalonians 2 in the BEV

1 Thessalonians 2 in the BHAD

1 Thessalonians 2 in the BIB

1 Thessalonians 2 in the BLPT

1 Thessalonians 2 in the BNT

1 Thessalonians 2 in the BNTABOOT

1 Thessalonians 2 in the BNTLV

1 Thessalonians 2 in the BOATCB

1 Thessalonians 2 in the BOATCB2

1 Thessalonians 2 in the BOBCV

1 Thessalonians 2 in the BOCNT

1 Thessalonians 2 in the BOECS

1 Thessalonians 2 in the BOHCB

1 Thessalonians 2 in the BOHCV

1 Thessalonians 2 in the BOHLNT

1 Thessalonians 2 in the BOHNTLTAL

1 Thessalonians 2 in the BOICB

1 Thessalonians 2 in the BOILNTAP

1 Thessalonians 2 in the BOITCV

1 Thessalonians 2 in the BOKCV

1 Thessalonians 2 in the BOKCV2

1 Thessalonians 2 in the BOKHWOG

1 Thessalonians 2 in the BOKSSV

1 Thessalonians 2 in the BOLCB

1 Thessalonians 2 in the BOLCB2

1 Thessalonians 2 in the BOMCV

1 Thessalonians 2 in the BONAV

1 Thessalonians 2 in the BONCB

1 Thessalonians 2 in the BONLT

1 Thessalonians 2 in the BONUT2

1 Thessalonians 2 in the BOPLNT

1 Thessalonians 2 in the BOSCB

1 Thessalonians 2 in the BOSNC

1 Thessalonians 2 in the BOTLNT

1 Thessalonians 2 in the BOVCB

1 Thessalonians 2 in the BOYCB

1 Thessalonians 2 in the BPBB

1 Thessalonians 2 in the BPH

1 Thessalonians 2 in the BSB

1 Thessalonians 2 in the CCB

1 Thessalonians 2 in the CUV

1 Thessalonians 2 in the CUVS

1 Thessalonians 2 in the DBT

1 Thessalonians 2 in the DGDNT

1 Thessalonians 2 in the DHNT

1 Thessalonians 2 in the DNT

1 Thessalonians 2 in the ELBE

1 Thessalonians 2 in the EMTV

1 Thessalonians 2 in the ESV

1 Thessalonians 2 in the FBV

1 Thessalonians 2 in the FEB

1 Thessalonians 2 in the GGMNT

1 Thessalonians 2 in the GNT

1 Thessalonians 2 in the HARY

1 Thessalonians 2 in the HNT

1 Thessalonians 2 in the IRVA

1 Thessalonians 2 in the IRVB

1 Thessalonians 2 in the IRVG

1 Thessalonians 2 in the IRVH

1 Thessalonians 2 in the IRVK

1 Thessalonians 2 in the IRVM

1 Thessalonians 2 in the IRVM2

1 Thessalonians 2 in the IRVO

1 Thessalonians 2 in the IRVP

1 Thessalonians 2 in the IRVT

1 Thessalonians 2 in the IRVT2

1 Thessalonians 2 in the IRVU

1 Thessalonians 2 in the ISVN

1 Thessalonians 2 in the JSNT

1 Thessalonians 2 in the KAPI

1 Thessalonians 2 in the KBT1ETNIK

1 Thessalonians 2 in the KBV

1 Thessalonians 2 in the KJV

1 Thessalonians 2 in the KNFD

1 Thessalonians 2 in the LBA

1 Thessalonians 2 in the LBLA

1 Thessalonians 2 in the LNT

1 Thessalonians 2 in the LSV

1 Thessalonians 2 in the MAAL

1 Thessalonians 2 in the MBV

1 Thessalonians 2 in the MBV2

1 Thessalonians 2 in the MHNT

1 Thessalonians 2 in the MKNFD

1 Thessalonians 2 in the MNG

1 Thessalonians 2 in the MNT

1 Thessalonians 2 in the MNT2

1 Thessalonians 2 in the MRS1T

1 Thessalonians 2 in the NAA

1 Thessalonians 2 in the NASB

1 Thessalonians 2 in the NBLA

1 Thessalonians 2 in the NBS

1 Thessalonians 2 in the NBVTP

1 Thessalonians 2 in the NET2

1 Thessalonians 2 in the NIV11

1 Thessalonians 2 in the NNT

1 Thessalonians 2 in the NNT2

1 Thessalonians 2 in the NNT3

1 Thessalonians 2 in the PDDPT

1 Thessalonians 2 in the PFNT

1 Thessalonians 2 in the RMNT

1 Thessalonians 2 in the SBIAS

1 Thessalonians 2 in the SBIBS

1 Thessalonians 2 in the SBIBS2

1 Thessalonians 2 in the SBICS

1 Thessalonians 2 in the SBIDS

1 Thessalonians 2 in the SBIGS

1 Thessalonians 2 in the SBIHS

1 Thessalonians 2 in the SBIIS

1 Thessalonians 2 in the SBIIS2

1 Thessalonians 2 in the SBIIS3

1 Thessalonians 2 in the SBIKS

1 Thessalonians 2 in the SBIKS2

1 Thessalonians 2 in the SBIMS

1 Thessalonians 2 in the SBIOS

1 Thessalonians 2 in the SBIPS

1 Thessalonians 2 in the SBISS

1 Thessalonians 2 in the SBITS

1 Thessalonians 2 in the SBITS2

1 Thessalonians 2 in the SBITS3

1 Thessalonians 2 in the SBITS4

1 Thessalonians 2 in the SBIUS

1 Thessalonians 2 in the SBIVS

1 Thessalonians 2 in the SBT

1 Thessalonians 2 in the SBT1E

1 Thessalonians 2 in the SCHL

1 Thessalonians 2 in the SNT

1 Thessalonians 2 in the SUSU

1 Thessalonians 2 in the SUSU2

1 Thessalonians 2 in the SYNO

1 Thessalonians 2 in the TBIAOTANT

1 Thessalonians 2 in the TBT1E

1 Thessalonians 2 in the TBT1E2

1 Thessalonians 2 in the TFTIP

1 Thessalonians 2 in the TFTU

1 Thessalonians 2 in the TGNTATF3T

1 Thessalonians 2 in the THAI

1 Thessalonians 2 in the TNFD

1 Thessalonians 2 in the TNT

1 Thessalonians 2 in the TNTIK

1 Thessalonians 2 in the TNTIL

1 Thessalonians 2 in the TNTIN

1 Thessalonians 2 in the TNTIP

1 Thessalonians 2 in the TNTIZ

1 Thessalonians 2 in the TOMA

1 Thessalonians 2 in the TTENT

1 Thessalonians 2 in the UBG

1 Thessalonians 2 in the UGV

1 Thessalonians 2 in the UGV2

1 Thessalonians 2 in the UGV3

1 Thessalonians 2 in the VBL

1 Thessalonians 2 in the VDCC

1 Thessalonians 2 in the YALU

1 Thessalonians 2 in the YAPE

1 Thessalonians 2 in the YBVTP

1 Thessalonians 2 in the ZBP