2 Chronicles 14 (BOGWICC)
1 Tsono Abiya anamwalira ndipo anayikidwa mʼmanda mu mzinda wa Davide. Asa mwana wake anakhala mfumu mʼmalo mwake ndipo pa masiku ake, dziko linakhala pa mtendere kwa zaka khumi. 2 Asa anachita zabwino ndi zolungama pamaso pa Yehova Mulungu wake. 3 Iye anachotsa maguwa achilendo ndi malo opembedzerapo mafano, anaphwanya zipilala za miyala yachipembedzo ndi kugwetsa mafano a Asera. 4 Asa analamula Yuda kuti afunefune Yehova Mulungu wa makolo awo ndi kumvera malamulo ndi zolamulira zake. 5 Iye anachotsa malo opembedzera mafano ndi maguwa ofukizira lubani mu mzinda uliwonse wa mu Yuda, ndipo mu ufumu wake munali mtendere pa nthawi ya ulamuliro wake. 6 Asa anamanga mizinda yonse yotetezedwa ya Yuda pakuti dziko linali pa mtendere. Panalibe amene anachita naye nkhondo mʼzaka zimenezo, pakuti Yehova anamupatsa mpumulo. 7 Iye anati kwa Yuda “Tiyeni timange mizinda iyi ndipo timange makoma ndi nsanja, zitseko ndi zotchinga. Dzikoli likanali lathu chifukwa tafuna Yehova Mulungu wathu; tinamufuna Iye ndipo watipatsa mpumulo mbali zonse.” Kotero iwo anamanga ndi kukhala pa ulemerero. 8 Asa anali ndi ankhondo 300,000 ochokera ku Yuda, okhala ndi zishango zikuluzikulu ndi mikondo, ndiponso ankhondo 280,000 ochokera ku Benjamini, okhala ndi zishango ndi mauta. Onsewa anali ankhondo amphamvu ndi olimba mtima. 9 Zera wa ku Kusi anapita kukamenyana nawo ali ndi gulu lalikulu kwambiri la asilikali ndi magaleta 300 ndipo anafika mpaka ku Maresa. 10 Asa anapita kukakumana naye ndipo anakhala pa mizere yawo ya nkhondo mʼchigwa cha Zefata pafupi ndi Maresa. 11 Kenaka Asa anafuwulira Yehova Mulungu wake ndipo anati “Yehova palibe wina wofanana nanu kuti angathandize anthu opanda mphamvu pakati pa amphamvu. Tithandizeni Inu Yehova Mulungu wathu pakuti ife timadalira Inu ndipo mʼdzina lanu ife tabwera kudzalimbana ndi gulu la ankhondo lalikulu kwambiri ngati ili. Inu Yehova ndinu Mulungu wathu, musalole kuti munthu akupambaneni.” 12 Yehova anakantha Akusi pamaso pa Asa ndi Ayuda. Akusi anathawa, 13 ndipo Asa ndi ankhondo ake anawathamangitsa mpaka ku Gerari. Gulu lonse lalikulu lija la Akusi linaphedwa. Sanapezeke mmodzi wamoyo pakati pawo. Iwo anakanthidwa pamaso pa Yehova ndi asilikali ake. Anthu a ku Yuda anatenga katundu wambiri olanda ku nkhondo. 14 Iwo anawononga midzi yonse yozungulira Gerari pakuti mantha aakulu wochokera kwa Yehova anagwera anthuwo. Analanda katundu wa midzi yonse, popeza kunali katundu wambiri kumeneko. 15 Anakathiranso nkhondo misasa ya anthu oweta ziweto ndipo anatenga nkhosa zambiri, mbuzi ndi ngamira. Atatero anabwerera ku Yerusalemu.
In Other Versions
2 Chronicles 14 in the ANGEFD
2 Chronicles 14 in the ANTPNG2D
2 Chronicles 14 in the AS21
2 Chronicles 14 in the BAGH
2 Chronicles 14 in the BBPNG
2 Chronicles 14 in the BBT1E
2 Chronicles 14 in the BDS
2 Chronicles 14 in the BEV
2 Chronicles 14 in the BHAD
2 Chronicles 14 in the BIB
2 Chronicles 14 in the BLPT
2 Chronicles 14 in the BNT
2 Chronicles 14 in the BNTABOOT
2 Chronicles 14 in the BNTLV
2 Chronicles 14 in the BOATCB
2 Chronicles 14 in the BOATCB2
2 Chronicles 14 in the BOBCV
2 Chronicles 14 in the BOCNT
2 Chronicles 14 in the BOECS
2 Chronicles 14 in the BOHCB
2 Chronicles 14 in the BOHCV
2 Chronicles 14 in the BOHLNT
2 Chronicles 14 in the BOHNTLTAL
2 Chronicles 14 in the BOICB
2 Chronicles 14 in the BOILNTAP
2 Chronicles 14 in the BOITCV
2 Chronicles 14 in the BOKCV
2 Chronicles 14 in the BOKCV2
2 Chronicles 14 in the BOKHWOG
2 Chronicles 14 in the BOKSSV
2 Chronicles 14 in the BOLCB
2 Chronicles 14 in the BOLCB2
2 Chronicles 14 in the BOMCV
2 Chronicles 14 in the BONAV
2 Chronicles 14 in the BONCB
2 Chronicles 14 in the BONLT
2 Chronicles 14 in the BONUT2
2 Chronicles 14 in the BOPLNT
2 Chronicles 14 in the BOSCB
2 Chronicles 14 in the BOSNC
2 Chronicles 14 in the BOTLNT
2 Chronicles 14 in the BOVCB
2 Chronicles 14 in the BOYCB
2 Chronicles 14 in the BPBB
2 Chronicles 14 in the BPH
2 Chronicles 14 in the BSB
2 Chronicles 14 in the CCB
2 Chronicles 14 in the CUV
2 Chronicles 14 in the CUVS
2 Chronicles 14 in the DBT
2 Chronicles 14 in the DGDNT
2 Chronicles 14 in the DHNT
2 Chronicles 14 in the DNT
2 Chronicles 14 in the ELBE
2 Chronicles 14 in the EMTV
2 Chronicles 14 in the ESV
2 Chronicles 14 in the FBV
2 Chronicles 14 in the FEB
2 Chronicles 14 in the GGMNT
2 Chronicles 14 in the GNT
2 Chronicles 14 in the HARY
2 Chronicles 14 in the HNT
2 Chronicles 14 in the IRVA
2 Chronicles 14 in the IRVB
2 Chronicles 14 in the IRVG
2 Chronicles 14 in the IRVH
2 Chronicles 14 in the IRVK
2 Chronicles 14 in the IRVM
2 Chronicles 14 in the IRVM2
2 Chronicles 14 in the IRVO
2 Chronicles 14 in the IRVP
2 Chronicles 14 in the IRVT
2 Chronicles 14 in the IRVT2
2 Chronicles 14 in the IRVU
2 Chronicles 14 in the ISVN
2 Chronicles 14 in the JSNT
2 Chronicles 14 in the KAPI
2 Chronicles 14 in the KBT1ETNIK
2 Chronicles 14 in the KBV
2 Chronicles 14 in the KJV
2 Chronicles 14 in the KNFD
2 Chronicles 14 in the LBA
2 Chronicles 14 in the LBLA
2 Chronicles 14 in the LNT
2 Chronicles 14 in the LSV
2 Chronicles 14 in the MAAL
2 Chronicles 14 in the MBV
2 Chronicles 14 in the MBV2
2 Chronicles 14 in the MHNT
2 Chronicles 14 in the MKNFD
2 Chronicles 14 in the MNG
2 Chronicles 14 in the MNT
2 Chronicles 14 in the MNT2
2 Chronicles 14 in the MRS1T
2 Chronicles 14 in the NAA
2 Chronicles 14 in the NASB
2 Chronicles 14 in the NBLA
2 Chronicles 14 in the NBS
2 Chronicles 14 in the NBVTP
2 Chronicles 14 in the NET2
2 Chronicles 14 in the NIV11
2 Chronicles 14 in the NNT
2 Chronicles 14 in the NNT2
2 Chronicles 14 in the NNT3
2 Chronicles 14 in the PDDPT
2 Chronicles 14 in the PFNT
2 Chronicles 14 in the RMNT
2 Chronicles 14 in the SBIAS
2 Chronicles 14 in the SBIBS
2 Chronicles 14 in the SBIBS2
2 Chronicles 14 in the SBICS
2 Chronicles 14 in the SBIDS
2 Chronicles 14 in the SBIGS
2 Chronicles 14 in the SBIHS
2 Chronicles 14 in the SBIIS
2 Chronicles 14 in the SBIIS2
2 Chronicles 14 in the SBIIS3
2 Chronicles 14 in the SBIKS
2 Chronicles 14 in the SBIKS2
2 Chronicles 14 in the SBIMS
2 Chronicles 14 in the SBIOS
2 Chronicles 14 in the SBIPS
2 Chronicles 14 in the SBISS
2 Chronicles 14 in the SBITS
2 Chronicles 14 in the SBITS2
2 Chronicles 14 in the SBITS3
2 Chronicles 14 in the SBITS4
2 Chronicles 14 in the SBIUS
2 Chronicles 14 in the SBIVS
2 Chronicles 14 in the SBT
2 Chronicles 14 in the SBT1E
2 Chronicles 14 in the SCHL
2 Chronicles 14 in the SNT
2 Chronicles 14 in the SUSU
2 Chronicles 14 in the SUSU2
2 Chronicles 14 in the SYNO
2 Chronicles 14 in the TBIAOTANT
2 Chronicles 14 in the TBT1E
2 Chronicles 14 in the TBT1E2
2 Chronicles 14 in the TFTIP
2 Chronicles 14 in the TFTU
2 Chronicles 14 in the TGNTATF3T
2 Chronicles 14 in the THAI
2 Chronicles 14 in the TNFD
2 Chronicles 14 in the TNT
2 Chronicles 14 in the TNTIK
2 Chronicles 14 in the TNTIL
2 Chronicles 14 in the TNTIN
2 Chronicles 14 in the TNTIP
2 Chronicles 14 in the TNTIZ
2 Chronicles 14 in the TOMA
2 Chronicles 14 in the TTENT
2 Chronicles 14 in the UBG
2 Chronicles 14 in the UGV
2 Chronicles 14 in the UGV2
2 Chronicles 14 in the UGV3
2 Chronicles 14 in the VBL
2 Chronicles 14 in the VDCC
2 Chronicles 14 in the YALU
2 Chronicles 14 in the YAPE
2 Chronicles 14 in the YBVTP
2 Chronicles 14 in the ZBP