2 Corinthians 9 (BOGWICC)

1 Nʼkosafunika kuti ndikulembereni za utumiki othandiza anthu a Mulungu. 2 Popeza ndikudziwa mtima wanu wofuna kuthandiza, ndipo ndakhala ndikuwawuza monyadira a ku Makedoniya za chimenechi. Ndimawawuza kuti inu a ku Akaya munakonzeka kale chaka chatha kuti mupereke. Ndipo changu chanu chapatsa chidwi ambiri mwa iwo kuti nawonso achitepo kanthu. 3 Koma ndikutumiza abalewo kuti kukunyadirani kwathu pa zimenezi kutsimikizike kuti si kwachabe ndi kuti mukhale okonzeka monga ndinanenera. 4 Pakuti nditabwera kumeneko ndi abale ena a ku Makedoniya, ndikukupezani kuti simunakonzeke, tingadzachite manyazi chifukwa chokudalirani. Koma amene angadzachite manyazi kwambiri ndi inuyo. 5 Choncho ndinaganiza kuti nʼkofunika kupempha abale kuti adzakuchezereni ineyo ndisanafike, ndikuti adzatsirize kukonzekera mphatso zomwe munalonjeza kupereka mowolowamanja. Motero mphatsoyo idzakhala yokonzeratu, ndipo idzakhala mphatso yoperekedwa mowolowamanja, osati mokakamizidwa. 6 Takumbukirani mawu awa: Amene adzala pangʼono, adzakololanso pangʼono, ndipo amene adzala zochuluka, adzakololanso zochuluka. 7 Munthu aliyense apereke chimene watsimikiza mu mtima mwake kuti apereka, osati monyinyirika kapena mokakamizidwa, pakuti Mulungu amakonda wopereka mokondwera. 8 Ndipo Mulungu akhoza kukudalitsani kwambiri, kuti inuyo nthawi zonse mukhale ndi zinthu zokukwanirani, ndiponso ndi zina zochuluka kuti muthandize pa ntchito zonse zabwino. 9 Paja analemba kuti,“Wopereka mphatso zake mowolowamanja kwa osauka,chilungamo chake chimanka mpaka muyaya.” 10 Tsono Mulungu amene amapereka mbewu kwa wofesa, ndiponso chakudya kuti adye, adzaperekanso mbewu mʼnkhokwe zanu ndi kuzichulukitsa. Iye adzachulukitsanso zipatso za chilungamo chanu. 11 Adzakulemeretsani pa zonse kuti mukhale owolowamanja pa nthawi zonse. Ndipo kuwolowamanja kwanu kudzera mwa ife, kudzakhala kuthokoza kwa Mulungu. 12 Ntchito imene mukugwirayi siyongothandiza kokha anthu a Mulungu kupeza zosowa, komanso ikuthandiza kuti anthu ambiri ayamike Mulungu. 13 Chifukwa cha ntchito imene mwawatsimikizira nokha, anthu ena onse adzayamika Mulungu chifukwa cha kumvera kwanu kumene kumaonekera pamene mukuvomereza Uthenga Wabwino wa Khristu, ndiponso chifukwa chowagawira mowolowamanja iwowo pamodzi ndi wina aliyense. 14 Ndipo iwowo adzakupemphererani mwachikondi chifukwa cha chisomo choposa chimene Ambuye wakupatsani. 15 Tiyamike Mulungu chifukwa cha mphatso zake zosaneneka!

In Other Versions

2 Corinthians 9 in the ANGEFD

2 Corinthians 9 in the ANTPNG2D

2 Corinthians 9 in the AS21

2 Corinthians 9 in the BAGH

2 Corinthians 9 in the BBPNG

2 Corinthians 9 in the BBT1E

2 Corinthians 9 in the BDS

2 Corinthians 9 in the BEV

2 Corinthians 9 in the BHAD

2 Corinthians 9 in the BIB

2 Corinthians 9 in the BLPT

2 Corinthians 9 in the BNT

2 Corinthians 9 in the BNTABOOT

2 Corinthians 9 in the BNTLV

2 Corinthians 9 in the BOATCB

2 Corinthians 9 in the BOATCB2

2 Corinthians 9 in the BOBCV

2 Corinthians 9 in the BOCNT

2 Corinthians 9 in the BOECS

2 Corinthians 9 in the BOHCB

2 Corinthians 9 in the BOHCV

2 Corinthians 9 in the BOHLNT

2 Corinthians 9 in the BOHNTLTAL

2 Corinthians 9 in the BOICB

2 Corinthians 9 in the BOILNTAP

2 Corinthians 9 in the BOITCV

2 Corinthians 9 in the BOKCV

2 Corinthians 9 in the BOKCV2

2 Corinthians 9 in the BOKHWOG

2 Corinthians 9 in the BOKSSV

2 Corinthians 9 in the BOLCB

2 Corinthians 9 in the BOLCB2

2 Corinthians 9 in the BOMCV

2 Corinthians 9 in the BONAV

2 Corinthians 9 in the BONCB

2 Corinthians 9 in the BONLT

2 Corinthians 9 in the BONUT2

2 Corinthians 9 in the BOPLNT

2 Corinthians 9 in the BOSCB

2 Corinthians 9 in the BOSNC

2 Corinthians 9 in the BOTLNT

2 Corinthians 9 in the BOVCB

2 Corinthians 9 in the BOYCB

2 Corinthians 9 in the BPBB

2 Corinthians 9 in the BPH

2 Corinthians 9 in the BSB

2 Corinthians 9 in the CCB

2 Corinthians 9 in the CUV

2 Corinthians 9 in the CUVS

2 Corinthians 9 in the DBT

2 Corinthians 9 in the DGDNT

2 Corinthians 9 in the DHNT

2 Corinthians 9 in the DNT

2 Corinthians 9 in the ELBE

2 Corinthians 9 in the EMTV

2 Corinthians 9 in the ESV

2 Corinthians 9 in the FBV

2 Corinthians 9 in the FEB

2 Corinthians 9 in the GGMNT

2 Corinthians 9 in the GNT

2 Corinthians 9 in the HARY

2 Corinthians 9 in the HNT

2 Corinthians 9 in the IRVA

2 Corinthians 9 in the IRVB

2 Corinthians 9 in the IRVG

2 Corinthians 9 in the IRVH

2 Corinthians 9 in the IRVK

2 Corinthians 9 in the IRVM

2 Corinthians 9 in the IRVM2

2 Corinthians 9 in the IRVO

2 Corinthians 9 in the IRVP

2 Corinthians 9 in the IRVT

2 Corinthians 9 in the IRVT2

2 Corinthians 9 in the IRVU

2 Corinthians 9 in the ISVN

2 Corinthians 9 in the JSNT

2 Corinthians 9 in the KAPI

2 Corinthians 9 in the KBT1ETNIK

2 Corinthians 9 in the KBV

2 Corinthians 9 in the KJV

2 Corinthians 9 in the KNFD

2 Corinthians 9 in the LBA

2 Corinthians 9 in the LBLA

2 Corinthians 9 in the LNT

2 Corinthians 9 in the LSV

2 Corinthians 9 in the MAAL

2 Corinthians 9 in the MBV

2 Corinthians 9 in the MBV2

2 Corinthians 9 in the MHNT

2 Corinthians 9 in the MKNFD

2 Corinthians 9 in the MNG

2 Corinthians 9 in the MNT

2 Corinthians 9 in the MNT2

2 Corinthians 9 in the MRS1T

2 Corinthians 9 in the NAA

2 Corinthians 9 in the NASB

2 Corinthians 9 in the NBLA

2 Corinthians 9 in the NBS

2 Corinthians 9 in the NBVTP

2 Corinthians 9 in the NET2

2 Corinthians 9 in the NIV11

2 Corinthians 9 in the NNT

2 Corinthians 9 in the NNT2

2 Corinthians 9 in the NNT3

2 Corinthians 9 in the PDDPT

2 Corinthians 9 in the PFNT

2 Corinthians 9 in the RMNT

2 Corinthians 9 in the SBIAS

2 Corinthians 9 in the SBIBS

2 Corinthians 9 in the SBIBS2

2 Corinthians 9 in the SBICS

2 Corinthians 9 in the SBIDS

2 Corinthians 9 in the SBIGS

2 Corinthians 9 in the SBIHS

2 Corinthians 9 in the SBIIS

2 Corinthians 9 in the SBIIS2

2 Corinthians 9 in the SBIIS3

2 Corinthians 9 in the SBIKS

2 Corinthians 9 in the SBIKS2

2 Corinthians 9 in the SBIMS

2 Corinthians 9 in the SBIOS

2 Corinthians 9 in the SBIPS

2 Corinthians 9 in the SBISS

2 Corinthians 9 in the SBITS

2 Corinthians 9 in the SBITS2

2 Corinthians 9 in the SBITS3

2 Corinthians 9 in the SBITS4

2 Corinthians 9 in the SBIUS

2 Corinthians 9 in the SBIVS

2 Corinthians 9 in the SBT

2 Corinthians 9 in the SBT1E

2 Corinthians 9 in the SCHL

2 Corinthians 9 in the SNT

2 Corinthians 9 in the SUSU

2 Corinthians 9 in the SUSU2

2 Corinthians 9 in the SYNO

2 Corinthians 9 in the TBIAOTANT

2 Corinthians 9 in the TBT1E

2 Corinthians 9 in the TBT1E2

2 Corinthians 9 in the TFTIP

2 Corinthians 9 in the TFTU

2 Corinthians 9 in the TGNTATF3T

2 Corinthians 9 in the THAI

2 Corinthians 9 in the TNFD

2 Corinthians 9 in the TNT

2 Corinthians 9 in the TNTIK

2 Corinthians 9 in the TNTIL

2 Corinthians 9 in the TNTIN

2 Corinthians 9 in the TNTIP

2 Corinthians 9 in the TNTIZ

2 Corinthians 9 in the TOMA

2 Corinthians 9 in the TTENT

2 Corinthians 9 in the UBG

2 Corinthians 9 in the UGV

2 Corinthians 9 in the UGV2

2 Corinthians 9 in the UGV3

2 Corinthians 9 in the VBL

2 Corinthians 9 in the VDCC

2 Corinthians 9 in the YALU

2 Corinthians 9 in the YAPE

2 Corinthians 9 in the YBVTP

2 Corinthians 9 in the ZBP