Ezekiel 31 (BOGWICC)
1 Pa tsiku loyamba la mwezi wachitatu, chaka cha khumi ndi chimodzi, Yehova anandiyankhula kuti: 2 “Iwe mwana wa munthu, unene kwa Farao mfumu ya Igupto ndi gulu lake lankhondo. Awawuze kuti,“ ‘Kodi mu ukulu wanu ndani angafanane ndi inu? 3 Taonani, ndidzakufanizirani ndi mtengo wa mkungudza wa ku Lebanoni,wa nthambi zokongola zochititsa mthunzi mʼnkhalango.Unali wautali,msonga zake zooneka pamwamba pa nkhalango. 4 Madzi ndiwo ankawukulitsa mkungudzawo,akasupe ozama ankawutalikitsa.Mitsinje yake inkayendamozungulira malo amene unaliwondipo ngalande zake zinkafikaku mitengo yonse ya mʼmunda. 5 Choncho unatalika kwambirikupambana mitengo yonse ya mʼmunda.Nthambi zake zinachulukandi kutalika kwambiri,chifukwa inkalandira madzi ambiri. 6 Mbalame zonse zamlengalengazinkamanga zisa zake mʼnthambi za mtengowo.Nyama zakuthengo zonsezinkaswanirana mʼmunsi mwa nthambi zake.Mitundu yotchuka ya anthuinkakhala mu mthunzi wake. 7 Unali wokongola kwambiri,wa nthambi zake zotambalala,chifukwa mizu yake inazama pansikumene kunali madzi ochuluka. 8 Mʼmunda wa Mulungu munalibemkungudza wofanana nawo,kapena mitengo ya payiniya nthambi zofanafana ndi nthambi zake.Munalibenso mtengo wa mkuyunthambi zofanafana ndi zake.Mʼmunda wa Mulungu munalibe mtengo wina uliwonsewofanana ndi iwo kukongola kwake. 9 Ine ndinawupanga wokongolawa nthambi zochuluka.Mitengo yonse ya mu Edeni, mʼmunda waMulungu inawuchitira nsanje. 10 “ ‘Nʼchifukwa chake Ine Ambuye Yehova ndikuti: Chifukwa kuti mtengowo unatalika kwambiri, unatulutsa songa zake mpaka ku thambo, ndipo unadzikweza chifukwa cha msinkhu wake, 11 ndinawupereka mʼdzanja la mfumu ya mitundu ya anthu kuti awulange molingana ndi kuyipa kwake. 12 Anthu ankhanza kwambiri amitundu ya anthu achilendo adzawudula ndi kuwusiya. Nthambi zake zidzagwera pa mapiri ndi mu zigwa zonse. Nthambi zake zidzathyokera mʼmitsinje ya mʼdzikomo. Motero mitundu yonse ya anthu a dziko lapansi amene ankasangalala mu mthunzi wake idzawusiya. 13 Mbalame zonse zamlengalenga zidzakhala pa mtengo wakugwawo, ndipo nyama zakuthengo zonse zidzakhala pa nthambi zake. 14 Zidzakutero kuti pasakhalenso mitengo inanso ya mʼmbali mwa madzi yotalika kwambiri, imene idzatalike kwambiri ndi songa zake kufika mpaka ku mitambo. Komanso kuti pasadzakhalenso mitengo yolandira bwino madzi, imene idzatalika motero. Paja yonseyo kutha kwake ndi kufa, kupita ku dziko lapansi kukhala ndi anthu akufa amene analowa mʼmanda kale. 15 “ ‘Ine Ambuye Yehova ndikuti: Pa nthawi imene mkungudzawo unatsikira ku manda, ndinawuza nyanja kuti iwulire maliro pakuwuphimba. Ndinawumitsa mitsinje ndipo madzi ambiri anaphwa. Ndinabweretsa mdima pa Lebanoni chifukwa cha mtengowo ndipo mitengo yonse ya mʼdzikomo inawuma. 16 Mitundu ya anthu inagwedezeka pakumva mkokomo wa kugwa kwake, pamene ndinawutsitsira ku manda pamodzi ndi iwo amene anafa. Pamenepo ku dziko la akufa mitengo yonse ya ku Edeni pamodzi ndi ya ku Lebanoni yosankhidwa bwino inasangalatsidwa chifukwa cha zimenezi. 17 Amene ankakhala mu mthunzi wake, amene ankayanjana nawo, iwonso anapita nawo pamodzi ku manda, kukakhala pamodzi ndi amene anaphedwa ndi lupanga pakati pa mitundu ya anthu. 18 “ ‘Ndi mitengo iti ya mu Edeni imene ingafanane ndi kukongola kwako ndi ulemerero wako? Komabe iwenso, udzatsikira ku dziko la anthu akufa pamodzi ndi mitengo ya mu Edeni. Udzagona pamodzi ndi anthu osachita mdulidwe, anthu amene anaphedwa pa nkhondo.“ ‘Mtengowo ndi Farao ndi gulu lake lankhondo, akutero Ambuye Yehova.’ ”
In Other Versions
Ezekiel 31 in the ANGEFD
Ezekiel 31 in the ANTPNG2D
Ezekiel 31 in the AS21
Ezekiel 31 in the BAGH
Ezekiel 31 in the BBPNG
Ezekiel 31 in the BBT1E
Ezekiel 31 in the BDS
Ezekiel 31 in the BEV
Ezekiel 31 in the BHAD
Ezekiel 31 in the BIB
Ezekiel 31 in the BLPT
Ezekiel 31 in the BNT
Ezekiel 31 in the BNTABOOT
Ezekiel 31 in the BNTLV
Ezekiel 31 in the BOATCB
Ezekiel 31 in the BOATCB2
Ezekiel 31 in the BOBCV
Ezekiel 31 in the BOCNT
Ezekiel 31 in the BOECS
Ezekiel 31 in the BOHCB
Ezekiel 31 in the BOHCV
Ezekiel 31 in the BOHLNT
Ezekiel 31 in the BOHNTLTAL
Ezekiel 31 in the BOICB
Ezekiel 31 in the BOILNTAP
Ezekiel 31 in the BOITCV
Ezekiel 31 in the BOKCV
Ezekiel 31 in the BOKCV2
Ezekiel 31 in the BOKHWOG
Ezekiel 31 in the BOKSSV
Ezekiel 31 in the BOLCB
Ezekiel 31 in the BOLCB2
Ezekiel 31 in the BOMCV
Ezekiel 31 in the BONAV
Ezekiel 31 in the BONCB
Ezekiel 31 in the BONLT
Ezekiel 31 in the BONUT2
Ezekiel 31 in the BOPLNT
Ezekiel 31 in the BOSCB
Ezekiel 31 in the BOSNC
Ezekiel 31 in the BOTLNT
Ezekiel 31 in the BOVCB
Ezekiel 31 in the BOYCB
Ezekiel 31 in the BPBB
Ezekiel 31 in the BPH
Ezekiel 31 in the BSB
Ezekiel 31 in the CCB
Ezekiel 31 in the CUV
Ezekiel 31 in the CUVS
Ezekiel 31 in the DBT
Ezekiel 31 in the DGDNT
Ezekiel 31 in the DHNT
Ezekiel 31 in the DNT
Ezekiel 31 in the ELBE
Ezekiel 31 in the EMTV
Ezekiel 31 in the ESV
Ezekiel 31 in the FBV
Ezekiel 31 in the FEB
Ezekiel 31 in the GGMNT
Ezekiel 31 in the GNT
Ezekiel 31 in the HARY
Ezekiel 31 in the HNT
Ezekiel 31 in the IRVA
Ezekiel 31 in the IRVB
Ezekiel 31 in the IRVG
Ezekiel 31 in the IRVH
Ezekiel 31 in the IRVK
Ezekiel 31 in the IRVM
Ezekiel 31 in the IRVM2
Ezekiel 31 in the IRVO
Ezekiel 31 in the IRVP
Ezekiel 31 in the IRVT
Ezekiel 31 in the IRVT2
Ezekiel 31 in the IRVU
Ezekiel 31 in the ISVN
Ezekiel 31 in the JSNT
Ezekiel 31 in the KAPI
Ezekiel 31 in the KBT1ETNIK
Ezekiel 31 in the KBV
Ezekiel 31 in the KJV
Ezekiel 31 in the KNFD
Ezekiel 31 in the LBA
Ezekiel 31 in the LBLA
Ezekiel 31 in the LNT
Ezekiel 31 in the LSV
Ezekiel 31 in the MAAL
Ezekiel 31 in the MBV
Ezekiel 31 in the MBV2
Ezekiel 31 in the MHNT
Ezekiel 31 in the MKNFD
Ezekiel 31 in the MNG
Ezekiel 31 in the MNT
Ezekiel 31 in the MNT2
Ezekiel 31 in the MRS1T
Ezekiel 31 in the NAA
Ezekiel 31 in the NASB
Ezekiel 31 in the NBLA
Ezekiel 31 in the NBS
Ezekiel 31 in the NBVTP
Ezekiel 31 in the NET2
Ezekiel 31 in the NIV11
Ezekiel 31 in the NNT
Ezekiel 31 in the NNT2
Ezekiel 31 in the NNT3
Ezekiel 31 in the PDDPT
Ezekiel 31 in the PFNT
Ezekiel 31 in the RMNT
Ezekiel 31 in the SBIAS
Ezekiel 31 in the SBIBS
Ezekiel 31 in the SBIBS2
Ezekiel 31 in the SBICS
Ezekiel 31 in the SBIDS
Ezekiel 31 in the SBIGS
Ezekiel 31 in the SBIHS
Ezekiel 31 in the SBIIS
Ezekiel 31 in the SBIIS2
Ezekiel 31 in the SBIIS3
Ezekiel 31 in the SBIKS
Ezekiel 31 in the SBIKS2
Ezekiel 31 in the SBIMS
Ezekiel 31 in the SBIOS
Ezekiel 31 in the SBIPS
Ezekiel 31 in the SBISS
Ezekiel 31 in the SBITS
Ezekiel 31 in the SBITS2
Ezekiel 31 in the SBITS3
Ezekiel 31 in the SBITS4
Ezekiel 31 in the SBIUS
Ezekiel 31 in the SBIVS
Ezekiel 31 in the SBT
Ezekiel 31 in the SBT1E
Ezekiel 31 in the SCHL
Ezekiel 31 in the SNT
Ezekiel 31 in the SUSU
Ezekiel 31 in the SUSU2
Ezekiel 31 in the SYNO
Ezekiel 31 in the TBIAOTANT
Ezekiel 31 in the TBT1E
Ezekiel 31 in the TBT1E2
Ezekiel 31 in the TFTIP
Ezekiel 31 in the TFTU
Ezekiel 31 in the TGNTATF3T
Ezekiel 31 in the THAI
Ezekiel 31 in the TNFD
Ezekiel 31 in the TNT
Ezekiel 31 in the TNTIK
Ezekiel 31 in the TNTIL
Ezekiel 31 in the TNTIN
Ezekiel 31 in the TNTIP
Ezekiel 31 in the TNTIZ
Ezekiel 31 in the TOMA
Ezekiel 31 in the TTENT
Ezekiel 31 in the UBG
Ezekiel 31 in the UGV
Ezekiel 31 in the UGV2
Ezekiel 31 in the UGV3
Ezekiel 31 in the VBL
Ezekiel 31 in the VDCC
Ezekiel 31 in the YALU
Ezekiel 31 in the YAPE
Ezekiel 31 in the YBVTP
Ezekiel 31 in the ZBP