Isaiah 41 (BOGWICC)

1 “Khalani chete pamaso panga, inu mayiko a mʼmbali mwa nyanja!Alekeni ayandikire ndi kuyankhula;tiyeni tikhale pamodzikuti atiweruze. 2 “Ndani anadzutsa wochokera kummawauja amene ananka napambana kulikonse kumene ankapita?Iye amapereka anthu a mitundu ina mʼmanja mwakendipo ndi lupanga lake anagonjetsandi kusandutsa mafumu kukhala ngati fumbinawamwaza ngati mankhusu ndi uta wake. 3 Amawalondola namayenda mosavutika,mʼnjira imene mapazi ake sanayendemo kale. 4 Ndani anachita zimenezi ndi kuzitsiriza,si uja amene anayambitsa mitundu ya anthu?Ine Yehova, ndine chiyambindipo potsiriza pake ndidzakhalapo.” 5 Mayiko amʼmbali mwa nyanja aona zimenezi ndipo akuopa;anthu a ku mathero a dziko lapansi akunjenjemera.Akuyandikira pafupi, akubwera; 6 aliyense akuthandiza mnzakendipo akuwuza mʼbale wake kuti, “Limba mtima!” 7 Mʼmisiri wa matabwa amalimbikitsa mʼmisiri wa golide,ndipo iye amene amasalaza fano ndi nyundoamalimbikitsa amene amalisanja pa chipala.Ponena za kuwotcherera iye amati, “Zili bwino.”Iye amalikhomerera fanolo ndi misomali kuti lisagwe. 8 “Koma Iwe Israeli mtumiki wanga,Yakobo amene ndakusankha,Ndiwe chidzukulu cha Abrahamu bwenzi langa. 9 Ndinakutengani kuchokera ku mapeto a dziko lapansi,ndinakuyitanani kuchokera ku mbali za kutali za dziko lapansi.Ine ndinati, ‘Iwe ndiwe mtumiki wanga;’Ndinakusankha ndipo sindinakutaye. 10 Tsono usaope, pakuti Ine ndili nawe;usataye mtima chifukwa Ine ndine Mulungu wako.Ndidzakupatsa mphamvu ndipo ndidzakuthandiza,ndidzakutchinjiriza ndi dzanja langa lamanja logonjetsa. 11 “Onse amene akupsera mtimaadzachita manyazi ndithu ndi kunyazitsidwa;onse amene akukangana nawesadzakhalanso kanthu, adzawonongeka. 12 Udzafunafuna adani ako,koma sadzapezeka.Iwo amene akuchita nawe nkhondosadzakhalanso kanthu. 13 Pakuti Ine Yehova, ndine Mulungu wako,amene ndikukugwira dzanja lako lamanjandipo ndikuti, usaope;ndidzakuthandiza. 14 Usachite mantha, iwe Yakobo wofowoka ngati nyongolotsi,iwe wochepa mphamvu Israeli,chifukwa Ine ndidzakuthandiza,”akutero Yehova Mpulumutsi wako, Woyerayo wa Israeli. 15 “Taona, ndidzakusandutsa ngati chipangizo chopunthira tiriguchatsopano, chakunthwa ndi cha mano ambiri.Udzanyenya mapiri ndi kuwaphwanyaphwanya,ndipo zitunda adzazisandutsa ngati mankhusu. 16 Udzawapeta ndipo adzawuluka ndi mphepo komansoadzamwazika ndi kamvuluvulu.Koma iwe udzakondwera chifukwa Ine ndine Mulungu wako,ndipo udzanyadira chifukwa cha Ine Woyerayo wa Israeli: 17 “Pamene amphawi ndi osauka akufunafuna madzi,koma sakuwapeza;ndipo kummero kwawo kwawuma ndi ludzu.Ine Yehova ndidzayankha pemphero lawo;Ine, Mulungu wa Israeli, sindidzawasiya. 18 Ndidzayendetsa mitsinje mʼmalo owuma,ndi akasupe adzatumphuka mu zigwa.Ndidzasandutsa chipululu kukhala dziwe la madzindipo dziko lowuma kukhala akasupe a madzi. 19 Mʼchipululu ndidzameretsamkungudza, kasiya mchisu ndi mtengo wa Olivi.Mʼdziko lowuma ndidzaza mitengoya payini, ya mkuyu ndi ya mlombwa, 20 kuti anthu aone ndi kudziwa;inde, alingalire ndi kumvetsa,kuti Yehova ndiye wachita zimenezi;kuti Woyera wa Israeli ndiye anakonza zimenezi. 21 “Yehova akuwuza milungu ina kuti, ‘Fotokozani mlandu wanu.’Mfumu ya Yakobo ikuti, ‘Perekani umboni wanu.’ 22 Bwerani ndi milungu yanu kuti idzatiwuzezomwe zidzachitike mʼtsogolo.Tifotokozereni zinthu zamakedzanatiziganizirendi kudziwa zotsatira zake.Kapena tiwuzeni zimene zidzachitike mʼtsogolo, 23 tiwuzeni kuti kutsogolo kuli zotani,ndipo ife tidziwa kuti ndinu milungu.Chitani chinthu chabwino kapena choyipa,ndipo mutidabwitsa ndi kutichititsa mantha. 24 Koma inu sindinu kanthundipo zochita zanu nʼzopandapake;amene amapembedza inu ali ngati chinthu chokanidwa chifukwa ndi choyipa. 25 “Ndinawutsa munthu wina kumpoto ndipo anabwera,munthu wochokera kummawa amene ndinamuyitana.Amapondaponda olamulira ngati matope,ngati ndi wowumba mbiya amene akuponda dongo. 26 Ndani anawululiratu zimenezi poyamba pomwe, kuti ife tidziwe,kapena kutiwuziratu zisanachitike kuti ife tinene kuti, ‘Analondola?’Palibe amene ananena,palibe analengeza zimenezi,palibe anamva mawu anu. 27 Ine ndinali woyamba kumuwuza Ziyoni kuti, ‘Taona, si awa akubwera apawa!’Ndinatumiza mthenga wa nkhani yabwino ku Yerusalemu. 28 Koma ndikayangʼana palibe ndi mmodzi yemwe,palibe ndi mmodzi yemwe pakati pawo wotha kupereka uphungu,palibe woti ayankhe pamene ine ndawafunsa. 29 Taonani, milungu yonseyi ndi yachinyengo!Zochita zawo si kanthu konse;mafano awo ali ngati mphepo yachabechabe.

In Other Versions

Isaiah 41 in the ANGEFD

Isaiah 41 in the ANTPNG2D

Isaiah 41 in the AS21

Isaiah 41 in the BAGH

Isaiah 41 in the BBPNG

Isaiah 41 in the BBT1E

Isaiah 41 in the BDS

Isaiah 41 in the BEV

Isaiah 41 in the BHAD

Isaiah 41 in the BIB

Isaiah 41 in the BLPT

Isaiah 41 in the BNT

Isaiah 41 in the BNTABOOT

Isaiah 41 in the BNTLV

Isaiah 41 in the BOATCB

Isaiah 41 in the BOATCB2

Isaiah 41 in the BOBCV

Isaiah 41 in the BOCNT

Isaiah 41 in the BOECS

Isaiah 41 in the BOHCB

Isaiah 41 in the BOHCV

Isaiah 41 in the BOHLNT

Isaiah 41 in the BOHNTLTAL

Isaiah 41 in the BOICB

Isaiah 41 in the BOILNTAP

Isaiah 41 in the BOITCV

Isaiah 41 in the BOKCV

Isaiah 41 in the BOKCV2

Isaiah 41 in the BOKHWOG

Isaiah 41 in the BOKSSV

Isaiah 41 in the BOLCB

Isaiah 41 in the BOLCB2

Isaiah 41 in the BOMCV

Isaiah 41 in the BONAV

Isaiah 41 in the BONCB

Isaiah 41 in the BONLT

Isaiah 41 in the BONUT2

Isaiah 41 in the BOPLNT

Isaiah 41 in the BOSCB

Isaiah 41 in the BOSNC

Isaiah 41 in the BOTLNT

Isaiah 41 in the BOVCB

Isaiah 41 in the BOYCB

Isaiah 41 in the BPBB

Isaiah 41 in the BPH

Isaiah 41 in the BSB

Isaiah 41 in the CCB

Isaiah 41 in the CUV

Isaiah 41 in the CUVS

Isaiah 41 in the DBT

Isaiah 41 in the DGDNT

Isaiah 41 in the DHNT

Isaiah 41 in the DNT

Isaiah 41 in the ELBE

Isaiah 41 in the EMTV

Isaiah 41 in the ESV

Isaiah 41 in the FBV

Isaiah 41 in the FEB

Isaiah 41 in the GGMNT

Isaiah 41 in the GNT

Isaiah 41 in the HARY

Isaiah 41 in the HNT

Isaiah 41 in the IRVA

Isaiah 41 in the IRVB

Isaiah 41 in the IRVG

Isaiah 41 in the IRVH

Isaiah 41 in the IRVK

Isaiah 41 in the IRVM

Isaiah 41 in the IRVM2

Isaiah 41 in the IRVO

Isaiah 41 in the IRVP

Isaiah 41 in the IRVT

Isaiah 41 in the IRVT2

Isaiah 41 in the IRVU

Isaiah 41 in the ISVN

Isaiah 41 in the JSNT

Isaiah 41 in the KAPI

Isaiah 41 in the KBT1ETNIK

Isaiah 41 in the KBV

Isaiah 41 in the KJV

Isaiah 41 in the KNFD

Isaiah 41 in the LBA

Isaiah 41 in the LBLA

Isaiah 41 in the LNT

Isaiah 41 in the LSV

Isaiah 41 in the MAAL

Isaiah 41 in the MBV

Isaiah 41 in the MBV2

Isaiah 41 in the MHNT

Isaiah 41 in the MKNFD

Isaiah 41 in the MNG

Isaiah 41 in the MNT

Isaiah 41 in the MNT2

Isaiah 41 in the MRS1T

Isaiah 41 in the NAA

Isaiah 41 in the NASB

Isaiah 41 in the NBLA

Isaiah 41 in the NBS

Isaiah 41 in the NBVTP

Isaiah 41 in the NET2

Isaiah 41 in the NIV11

Isaiah 41 in the NNT

Isaiah 41 in the NNT2

Isaiah 41 in the NNT3

Isaiah 41 in the PDDPT

Isaiah 41 in the PFNT

Isaiah 41 in the RMNT

Isaiah 41 in the SBIAS

Isaiah 41 in the SBIBS

Isaiah 41 in the SBIBS2

Isaiah 41 in the SBICS

Isaiah 41 in the SBIDS

Isaiah 41 in the SBIGS

Isaiah 41 in the SBIHS

Isaiah 41 in the SBIIS

Isaiah 41 in the SBIIS2

Isaiah 41 in the SBIIS3

Isaiah 41 in the SBIKS

Isaiah 41 in the SBIKS2

Isaiah 41 in the SBIMS

Isaiah 41 in the SBIOS

Isaiah 41 in the SBIPS

Isaiah 41 in the SBISS

Isaiah 41 in the SBITS

Isaiah 41 in the SBITS2

Isaiah 41 in the SBITS3

Isaiah 41 in the SBITS4

Isaiah 41 in the SBIUS

Isaiah 41 in the SBIVS

Isaiah 41 in the SBT

Isaiah 41 in the SBT1E

Isaiah 41 in the SCHL

Isaiah 41 in the SNT

Isaiah 41 in the SUSU

Isaiah 41 in the SUSU2

Isaiah 41 in the SYNO

Isaiah 41 in the TBIAOTANT

Isaiah 41 in the TBT1E

Isaiah 41 in the TBT1E2

Isaiah 41 in the TFTIP

Isaiah 41 in the TFTU

Isaiah 41 in the TGNTATF3T

Isaiah 41 in the THAI

Isaiah 41 in the TNFD

Isaiah 41 in the TNT

Isaiah 41 in the TNTIK

Isaiah 41 in the TNTIL

Isaiah 41 in the TNTIN

Isaiah 41 in the TNTIP

Isaiah 41 in the TNTIZ

Isaiah 41 in the TOMA

Isaiah 41 in the TTENT

Isaiah 41 in the UBG

Isaiah 41 in the UGV

Isaiah 41 in the UGV2

Isaiah 41 in the UGV3

Isaiah 41 in the VBL

Isaiah 41 in the VDCC

Isaiah 41 in the YALU

Isaiah 41 in the YAPE

Isaiah 41 in the YBVTP

Isaiah 41 in the ZBP