Isaiah 8 (BOGWICC)
1 Yehova anati kwa ine, “Tenga cholembapo chachikulu ndipo ulembepo malemba odziwika bwino: KUSAKAZA-KWAMSANGA KUFUNKHA-KOFULUMIRA. 2 Ndipo ndidzayitana wansembe Uriya ndi Zekariya mwana wa Yeberekiya kuti akhale mboni zanga zodalirika.” 3 Ndipo ine ndinapita kwa mneneri wamkazi, ndipo anakhala woyembekezera nabala mwana wamwamuna. Ndipo Yehova anati kwa ine, “Umutche dzina lakuti, ‘Kusakaza-Kwamsanga Kufunkha-Kofulumira.’ 4 Mwanayo asanayambe kudziwa kuyitana kuti, ‘Ababa’ kapena ‘Amama’ chuma cha Damasiko ndi zofunkha za Samariya zidzatengedwa ndi mfumu ya ku Asiriya.” 5 Yehova anayankhulanso ndi Ine; 6 “Popeza anthu a dziko ili akanamadzi anga oyenda mwachifatse a ku Siloamu,ndipo akukondwerera Rezinindi mwana wa Remaliya, 7 nʼchifukwa chake Ambuye ali pafupi kubweretsamadzi amkokomo a mtsinje wa Yufurate kudzalimbana nawo;mfumu ya ku Asiriya ndi gulu lake lonse lankhondo.Madziwo adzasefukira mʼngalande zake zonsendi mʼmagombe ake onse. 8 Ndipo adzalowa mwamphamvu mʼdziko la Yuda, adzasefukira,adzapitirira mpaka kumuyesa mʼkhosi.Mapiko ake otambasuka adzaphimba dziko lako lonse,iwe Imanueli!” 9 Chitani phokoso lankhondo, inu mitundu ya anthu, ndipo munjenjemere!Tamverani, inu mayiko onse akutali.Konzekerani nkhondo ndipo munjenjemere!Konzekerani nkhondo ndipo munjenjemere! 10 Konzani kachitidwe kanu kankhondo, koma simudzaphula kanthu,kambiranani zochita, koma zidzalephereka,pakuti Mulungu ali nafe. 11 Yehova anandiyankhula ine mwamphamvu, ndipo anandichenjeza kuti ndisamayende mʼnjira za anthuwa. Iye anati: 12 “Usamanene kuti ndi chiwembu,chilichonse chimene anthuwa amati ndi chiwembuusamaope zimene anthuwa amaziopa,ndipo usamachite nazo mantha. 13 Yehova Wamphamvuzonse ndiye amene uyenera kumuona kuti ndi woyera,ndiye amene uyenera kumuopa,ndiye amene uyenera kuchita naye mantha, 14 ndipo ndiye amene adzakhala malo opatulika;koma kwa anthu a ku Yuda ndi kwa anthu a ku Israeli adzakhalamwala wopunthwitsa,mwala umene umapunthwitsa anthu,thanthwe limene limagwetsa anthu.Ndipo kwa anthu a mu Yerusalemu adzakhala ngati msampha ndi khwekhwe. 15 Anthu ambiri adzapunthwapoadzagwa ndi kuthyokathyoka,adzakodwa ndi kugwidwa.” 16 Manga umboniwundipo umate malamulowa pamaso pa ophunzira anga. 17 Ndidzayembekezera Yehova,amene akubisira nkhope yake nyumba ya Yakobo.Ine ndidzakhulupirira Iyeyo. 18 Onani, ine ndili pano pamodzi ndi ana amene Yehova wandipatsa, ndife zizindikiro ndi zodabwitsa kwa Aisraeli zochokera kwa Yehova Wamphamvuzonse, amene amakhala pa Phiri la Ziyoni. 19 Anthu akakuwuza kuti kafunsire kwa oyankhula ndi mizimu, amene amayankhula monongʼona ndi mongʼungʼudza, kodi anthu sayenera kukafunsira kwa Mulungu wawo? Chifukwa chiyani amafunsira kwa anthu akufa mʼmalo mwa kwa anthu amoyo, 20 kuti akalandireko mawu enieni ndi malangizo? Ngati anthuwo sayankhula monga mwa mawu awa, mwa iwo mulibe kuwala. 21 Anthu adzayendayenda mʼdziko movutika kwambiri ali ndi njala; pamene afowokeratu ndi njala, iwo adzakwiya kwambiri ndipo adzayangʼana kumwamba ndi kutemberera mfumu yawo ndi Mulungu wawo. 22 Ndipo akadzayangʼana pa dziko lapansi adzangoona mavuto okhaokha ndi mdima woopsa ndi wodetsa nkhawa, ndipo adzaponyedwa mu mdima wandiweyani.
In Other Versions
Isaiah 8 in the ANGEFD
Isaiah 8 in the ANTPNG2D
Isaiah 8 in the AS21
Isaiah 8 in the BAGH
Isaiah 8 in the BBPNG
Isaiah 8 in the BBT1E
Isaiah 8 in the BDS
Isaiah 8 in the BEV
Isaiah 8 in the BHAD
Isaiah 8 in the BIB
Isaiah 8 in the BLPT
Isaiah 8 in the BNT
Isaiah 8 in the BNTABOOT
Isaiah 8 in the BNTLV
Isaiah 8 in the BOATCB
Isaiah 8 in the BOATCB2
Isaiah 8 in the BOBCV
Isaiah 8 in the BOCNT
Isaiah 8 in the BOECS
Isaiah 8 in the BOHCB
Isaiah 8 in the BOHCV
Isaiah 8 in the BOHLNT
Isaiah 8 in the BOHNTLTAL
Isaiah 8 in the BOICB
Isaiah 8 in the BOILNTAP
Isaiah 8 in the BOITCV
Isaiah 8 in the BOKCV
Isaiah 8 in the BOKCV2
Isaiah 8 in the BOKHWOG
Isaiah 8 in the BOKSSV
Isaiah 8 in the BOLCB
Isaiah 8 in the BOLCB2
Isaiah 8 in the BOMCV
Isaiah 8 in the BONAV
Isaiah 8 in the BONCB
Isaiah 8 in the BONLT
Isaiah 8 in the BONUT2
Isaiah 8 in the BOPLNT
Isaiah 8 in the BOSCB
Isaiah 8 in the BOSNC
Isaiah 8 in the BOTLNT
Isaiah 8 in the BOVCB
Isaiah 8 in the BOYCB
Isaiah 8 in the BPBB
Isaiah 8 in the BPH
Isaiah 8 in the BSB
Isaiah 8 in the CCB
Isaiah 8 in the CUV
Isaiah 8 in the CUVS
Isaiah 8 in the DBT
Isaiah 8 in the DGDNT
Isaiah 8 in the DHNT
Isaiah 8 in the DNT
Isaiah 8 in the ELBE
Isaiah 8 in the EMTV
Isaiah 8 in the ESV
Isaiah 8 in the FBV
Isaiah 8 in the FEB
Isaiah 8 in the GGMNT
Isaiah 8 in the GNT
Isaiah 8 in the HARY
Isaiah 8 in the HNT
Isaiah 8 in the IRVA
Isaiah 8 in the IRVB
Isaiah 8 in the IRVG
Isaiah 8 in the IRVH
Isaiah 8 in the IRVK
Isaiah 8 in the IRVM
Isaiah 8 in the IRVM2
Isaiah 8 in the IRVO
Isaiah 8 in the IRVP
Isaiah 8 in the IRVT
Isaiah 8 in the IRVT2
Isaiah 8 in the IRVU
Isaiah 8 in the ISVN
Isaiah 8 in the JSNT
Isaiah 8 in the KAPI
Isaiah 8 in the KBT1ETNIK
Isaiah 8 in the KBV
Isaiah 8 in the KJV
Isaiah 8 in the KNFD
Isaiah 8 in the LBA
Isaiah 8 in the LBLA
Isaiah 8 in the LNT
Isaiah 8 in the LSV
Isaiah 8 in the MAAL
Isaiah 8 in the MBV
Isaiah 8 in the MBV2
Isaiah 8 in the MHNT
Isaiah 8 in the MKNFD
Isaiah 8 in the MNG
Isaiah 8 in the MNT
Isaiah 8 in the MNT2
Isaiah 8 in the MRS1T
Isaiah 8 in the NAA
Isaiah 8 in the NASB
Isaiah 8 in the NBLA
Isaiah 8 in the NBS
Isaiah 8 in the NBVTP
Isaiah 8 in the NET2
Isaiah 8 in the NIV11
Isaiah 8 in the NNT
Isaiah 8 in the NNT2
Isaiah 8 in the NNT3
Isaiah 8 in the PDDPT
Isaiah 8 in the PFNT
Isaiah 8 in the RMNT
Isaiah 8 in the SBIAS
Isaiah 8 in the SBIBS
Isaiah 8 in the SBIBS2
Isaiah 8 in the SBICS
Isaiah 8 in the SBIDS
Isaiah 8 in the SBIGS
Isaiah 8 in the SBIHS
Isaiah 8 in the SBIIS
Isaiah 8 in the SBIIS2
Isaiah 8 in the SBIIS3
Isaiah 8 in the SBIKS
Isaiah 8 in the SBIKS2
Isaiah 8 in the SBIMS
Isaiah 8 in the SBIOS
Isaiah 8 in the SBIPS
Isaiah 8 in the SBISS
Isaiah 8 in the SBITS
Isaiah 8 in the SBITS2
Isaiah 8 in the SBITS3
Isaiah 8 in the SBITS4
Isaiah 8 in the SBIUS
Isaiah 8 in the SBIVS
Isaiah 8 in the SBT
Isaiah 8 in the SBT1E
Isaiah 8 in the SCHL
Isaiah 8 in the SNT
Isaiah 8 in the SUSU
Isaiah 8 in the SUSU2
Isaiah 8 in the SYNO
Isaiah 8 in the TBIAOTANT
Isaiah 8 in the TBT1E
Isaiah 8 in the TBT1E2
Isaiah 8 in the TFTIP
Isaiah 8 in the TFTU
Isaiah 8 in the TGNTATF3T
Isaiah 8 in the THAI
Isaiah 8 in the TNFD
Isaiah 8 in the TNT
Isaiah 8 in the TNTIK
Isaiah 8 in the TNTIL
Isaiah 8 in the TNTIN
Isaiah 8 in the TNTIP
Isaiah 8 in the TNTIZ
Isaiah 8 in the TOMA
Isaiah 8 in the TTENT
Isaiah 8 in the UBG
Isaiah 8 in the UGV
Isaiah 8 in the UGV2
Isaiah 8 in the UGV3
Isaiah 8 in the VBL
Isaiah 8 in the VDCC
Isaiah 8 in the YALU
Isaiah 8 in the YAPE
Isaiah 8 in the YBVTP
Isaiah 8 in the ZBP