Jeremiah 1 (BOGWICC)
1 Mawu a Yeremiya mwana wa Hilikiya, mmodzi mwa ansembe a ku Anatoti, mʼdziko la Benjamini. 2 Mawuwa Yehova anayankhula naye mʼchaka cha 13 cha ulamuliro wa Yosiya mwana wa Amoni mfumu ya Yuda. 3 Yehova anayankhulanso naye pa nthawi yonse ya ulamuliro wa Yehoyakimu mwana wa Yosiya mfumu ya Yuda, mpaka mwezi wachisanu wa chaka cha 11 cha ufumu wa Zedekiya mwana wa Yosiya mfumu ya Yuda, pamene anthu a ku Yerusalemu anapita ku ukapolo. 4 Yehova anayankhula nane kuti, 5 “Ndisanakuwumbe mʼmimba mwa amayi ako ndinali nditakudziwa kale,iwe usanabadwe ndinali nditakupatula kale;ndinakuyika kuti ukhale mneneri kwa anthu a mitundu yonse.” 6 Ine ndinati, “Haa! Ambuye Yehova, ine sinditha kuyankhula; popeza ndikanali wamngʼono.” 7 Koma Yehova anandiwuza kuti, “Usanene kuti, ‘Ndikanali wamngʼono’ popeza udzapita kwa munthu aliyense kumene ndidzakutuma ndi kunena chilichonse chimene ndidzakulamulira. 8 Usawaope, pakuti Ine ndili nawe, ndipo ndidzakupulumutsa,” akutero Yehova. 9 Pamenepo Yehova anatambalitsa dzanja lake nakhudza pakamwa panga, nandiwuza kuti, “Taona, tsopano ndayika mawu anga mʼkamwa mwako. 10 Lero ndakusankha kuti ukhale ndi ulamuliro pa mitundu ya anthu ndi pa maufumu awo kuti uzule ndi kugwetsa, uwononge ndi kugumula, kuti uwamange ndi kudzala.” 11 Yehova anandifunsa kuti, “Yeremiya, kodi ukuona chiyani?”Ine ndinayankha kuti, “Ndikuona nthambi ya mtengo wa mtowo.” 12 Yehova anandiwuza kuti, “Waona bwino, chifukwa Ine ndikuonetsetsa kuti mawu angawa akwaniritsidwe.” 13 Yehova anandifunsanso kachiwiri kuti, “Kodi ukuona chiyani?”Ine ndinayankha kuti, “Ndikuona mʼphika wa madzi owira, ndipo wagudukira kuno kummwera.” 14 Yehova anandiwuza kuti, “Mavuto a anthu onse okhala mʼdziko lino adzachokera kumpoto. 15 Ine ndikuyitana anthu onse a ku maufumu a kumpoto,” akutero Yehova.“Mafumu awo adzabwera ndipo aliyense adzakhazika mpando wake waufumupolowera pa zipata za Yerusalemu;iwo adzabwera ndi kuzungulira makoma akendiponso midzi yonse ya dziko la Yuda. 16 Ndidzatulutsa mlandu wanga ndi iwochifukwa cha zoyipa zimene anachita pondisiya Ine.Iwo anakafukiza lubani kwa milungu ina,ndi kupembedza zimene anapanga ndi manja awo. 17 “Koma iwe Yeremiya konzeka! Nyamuka ndipo ukawawuze zonse zimene ndakulamulira. Usachite nawo mantha, kuopa kuti Ine ndingakuchititse mantha iwo akuona. 18 Taona, lero ndakupanga kukhala ngati mzinda wotetezedwa, ngati mzati wachitsulo ndiponso ngati makoma a mkuwa kuti usaopsedwe ndi munthu aliyense wa mʼdzikomo; kaya ndi mafumu a Yuda, akuluakulu ake, ansembe ake, kapena munthu wamba wa mʼdzikomo. 19 Iwo adzalimbana nawe koma sadzakugonjetsa, popeza Ine ndili nawe ndipo ndidzakupulumutsa,” akutero Yehova.
In Other Versions
Jeremiah 1 in the ANGEFD
Jeremiah 1 in the ANTPNG2D
Jeremiah 1 in the AS21
Jeremiah 1 in the BAGH
Jeremiah 1 in the BBPNG
Jeremiah 1 in the BBT1E
Jeremiah 1 in the BDS
Jeremiah 1 in the BEV
Jeremiah 1 in the BHAD
Jeremiah 1 in the BIB
Jeremiah 1 in the BLPT
Jeremiah 1 in the BNT
Jeremiah 1 in the BNTABOOT
Jeremiah 1 in the BNTLV
Jeremiah 1 in the BOATCB
Jeremiah 1 in the BOATCB2
Jeremiah 1 in the BOBCV
Jeremiah 1 in the BOCNT
Jeremiah 1 in the BOECS
Jeremiah 1 in the BOHCB
Jeremiah 1 in the BOHCV
Jeremiah 1 in the BOHLNT
Jeremiah 1 in the BOHNTLTAL
Jeremiah 1 in the BOICB
Jeremiah 1 in the BOILNTAP
Jeremiah 1 in the BOITCV
Jeremiah 1 in the BOKCV
Jeremiah 1 in the BOKCV2
Jeremiah 1 in the BOKHWOG
Jeremiah 1 in the BOKSSV
Jeremiah 1 in the BOLCB
Jeremiah 1 in the BOLCB2
Jeremiah 1 in the BOMCV
Jeremiah 1 in the BONAV
Jeremiah 1 in the BONCB
Jeremiah 1 in the BONLT
Jeremiah 1 in the BONUT2
Jeremiah 1 in the BOPLNT
Jeremiah 1 in the BOSCB
Jeremiah 1 in the BOSNC
Jeremiah 1 in the BOTLNT
Jeremiah 1 in the BOVCB
Jeremiah 1 in the BOYCB
Jeremiah 1 in the BPBB
Jeremiah 1 in the BPH
Jeremiah 1 in the BSB
Jeremiah 1 in the CCB
Jeremiah 1 in the CUV
Jeremiah 1 in the CUVS
Jeremiah 1 in the DBT
Jeremiah 1 in the DGDNT
Jeremiah 1 in the DHNT
Jeremiah 1 in the DNT
Jeremiah 1 in the ELBE
Jeremiah 1 in the EMTV
Jeremiah 1 in the ESV
Jeremiah 1 in the FBV
Jeremiah 1 in the FEB
Jeremiah 1 in the GGMNT
Jeremiah 1 in the GNT
Jeremiah 1 in the HARY
Jeremiah 1 in the HNT
Jeremiah 1 in the IRVA
Jeremiah 1 in the IRVB
Jeremiah 1 in the IRVG
Jeremiah 1 in the IRVH
Jeremiah 1 in the IRVK
Jeremiah 1 in the IRVM
Jeremiah 1 in the IRVM2
Jeremiah 1 in the IRVO
Jeremiah 1 in the IRVP
Jeremiah 1 in the IRVT
Jeremiah 1 in the IRVT2
Jeremiah 1 in the IRVU
Jeremiah 1 in the ISVN
Jeremiah 1 in the JSNT
Jeremiah 1 in the KAPI
Jeremiah 1 in the KBT1ETNIK
Jeremiah 1 in the KBV
Jeremiah 1 in the KJV
Jeremiah 1 in the KNFD
Jeremiah 1 in the LBA
Jeremiah 1 in the LBLA
Jeremiah 1 in the LNT
Jeremiah 1 in the LSV
Jeremiah 1 in the MAAL
Jeremiah 1 in the MBV
Jeremiah 1 in the MBV2
Jeremiah 1 in the MHNT
Jeremiah 1 in the MKNFD
Jeremiah 1 in the MNG
Jeremiah 1 in the MNT
Jeremiah 1 in the MNT2
Jeremiah 1 in the MRS1T
Jeremiah 1 in the NAA
Jeremiah 1 in the NASB
Jeremiah 1 in the NBLA
Jeremiah 1 in the NBS
Jeremiah 1 in the NBVTP
Jeremiah 1 in the NET2
Jeremiah 1 in the NIV11
Jeremiah 1 in the NNT
Jeremiah 1 in the NNT2
Jeremiah 1 in the NNT3
Jeremiah 1 in the PDDPT
Jeremiah 1 in the PFNT
Jeremiah 1 in the RMNT
Jeremiah 1 in the SBIAS
Jeremiah 1 in the SBIBS
Jeremiah 1 in the SBIBS2
Jeremiah 1 in the SBICS
Jeremiah 1 in the SBIDS
Jeremiah 1 in the SBIGS
Jeremiah 1 in the SBIHS
Jeremiah 1 in the SBIIS
Jeremiah 1 in the SBIIS2
Jeremiah 1 in the SBIIS3
Jeremiah 1 in the SBIKS
Jeremiah 1 in the SBIKS2
Jeremiah 1 in the SBIMS
Jeremiah 1 in the SBIOS
Jeremiah 1 in the SBIPS
Jeremiah 1 in the SBISS
Jeremiah 1 in the SBITS
Jeremiah 1 in the SBITS2
Jeremiah 1 in the SBITS3
Jeremiah 1 in the SBITS4
Jeremiah 1 in the SBIUS
Jeremiah 1 in the SBIVS
Jeremiah 1 in the SBT
Jeremiah 1 in the SBT1E
Jeremiah 1 in the SCHL
Jeremiah 1 in the SNT
Jeremiah 1 in the SUSU
Jeremiah 1 in the SUSU2
Jeremiah 1 in the SYNO
Jeremiah 1 in the TBIAOTANT
Jeremiah 1 in the TBT1E
Jeremiah 1 in the TBT1E2
Jeremiah 1 in the TFTIP
Jeremiah 1 in the TFTU
Jeremiah 1 in the TGNTATF3T
Jeremiah 1 in the THAI
Jeremiah 1 in the TNFD
Jeremiah 1 in the TNT
Jeremiah 1 in the TNTIK
Jeremiah 1 in the TNTIL
Jeremiah 1 in the TNTIN
Jeremiah 1 in the TNTIP
Jeremiah 1 in the TNTIZ
Jeremiah 1 in the TOMA
Jeremiah 1 in the TTENT
Jeremiah 1 in the UBG
Jeremiah 1 in the UGV
Jeremiah 1 in the UGV2
Jeremiah 1 in the UGV3
Jeremiah 1 in the VBL
Jeremiah 1 in the VDCC
Jeremiah 1 in the YALU
Jeremiah 1 in the YAPE
Jeremiah 1 in the YBVTP
Jeremiah 1 in the ZBP