Jeremiah 46 (BOGWICC)

1 Yehova anamupatsa Yeremiya uthenga wonena za anthu a mitundu ina. 2 Kunena za Igupto: Yehova ananena za gulu lankhondo la Farao Neko mfumu ya ku Igupto limene Nebukadinezara mfumu ya ku Babuloni analigonjetsa ku Karikemesi ku mtsinje wa Yufurate mʼchaka cha chinayi cha Yehoyakimu mwana wa Yosiya mfumu ya Yuda, 3 anati, “Konzani zishango zanu ndi malihawo,ndipo yambanipo kupita ku nkhondo! 4 Mangani akavalo,ndipo kwerani inu okwerapo!Khalani pa mzeremutavala zipewa!Nolani mikondo yanu,valani malaya anu ankhondo! 5 Yeremiya anati: Kodi ndikuona chiyani?Achita manthaakubwerera,ankhondo awo agonjetsedwa.Akuthawa mofulumirapoosayangʼananso mʼmbuyo,ndipo agwidwa ndi mantha ponseponse,”akutero Yehova. 6 Waliwiro sangathe kuthawangakhale wankhondo wamphamvu sangathe kupulumuka.Akunka napunthwa ndi kugwakumpoto kwa mtsinje wa Yufurate. 7 “Kodi ndani amene akukwera ngati Nailo,ngati mtsinje wa madzi amkokomo? 8 Igupto akusefukira ngati Nailo,ngati mitsinje ya madzi amkokomo.Iye akunena kuti, ‘Ndidzadzuka ndi kuphimba dziko lapansi;ndidzawononga mizinda ndi anthu ake.’ 9 Tiyeni, inu akavalo!Thamangani inu magaleta!Tulukani, inu ankhondo,ankhondo a ku Kusi ndi Puti amene mumanyamula zishango,ankhondo a ku Ludi amene mumaponya uta. 10 Koma tsikulo ndi la Ambuye Yehova Wamphamvuzonse;tsiku lolipsira, lolipsira adani ake.Lupanga lake lidzawononga ndi kukhuta magazi,lidzaledzera ndi magazi.Pakuti Yehova, Yehova Wamphamvuzonse, adzapereka adani ake ngati nsembemʼdziko la kumpoto mʼmbali mwa mtsinje wa Yufurate. 11 “Pita ku Giliyadi ukatenge mankhwalaiwe namwali Igupto.Wayesayesa mankhwala ambiri koma osachira;palibe mankhwala okuchiritsa. 12 Anthu a mitundu ina amva za manyazi ako;kulira kwako kwadzaza dziko lapansi.Ankhondo akunka nagwetsanagwetsana,onse awiri agwa pansi limodzi.” 13 Uthenga umene Yehova anapatsa mneneri Yeremiya wonena za kubwera kwa Nebukadinezara mfumu ya ku Babuloni kudzathira nkhondo Igupto ndi uwu: 14 “Mulengeze ku Igupto. Mulengeze ku Migidoli.Mulengezenso ku Mefisi ndi ku Tapanesi.Muwawuze anthu akumeneko kuti, ‘Imani pamalo panu ndi kukhala okonzeka kudziteteza,chifukwa lupanga lidzawononga zonse zimene muli nazo.’ 15 Chifukwa chiyani mulungu wanu wamphamvu uja Apisi wathawa?Iye sakanatha kulimba chifukwa Yehova anamugwetsa. 16 Ankhondo anu apunthwa ndi kugwa.Aliyense akuwuza mnzake kuti,‘Tiyeni tibwerere kwathu,ku dziko kumene tinabadwira,tithawe lupanga la adani athu.’ 17 Kumeneku iwo adzafuwula kuti,‘Farao, mfumu ya ku Igupto mupatseni dzina lakuti,Waphokoso, Wotaya mwayi wake.’ 18 “Pali Ine wamoyo,” ikutero Mfumu,imene dzina lake ndi Yehova Wamphamvuzonse,“wina adzabwera amene ali ngati Tabori phiri lopambana mapiri ena,ngati phiri la Karimeli loti njoo mʼmbali mwa nyanja. 19 Konzani katundu wanu wopita naye ku ukapoloinu anthu a ku Igupto,pakuti Mefisi adzasanduka chipululundipo adzakhala bwinja mopanda wokhalamo. 20 “Igupto ali ngati mwana wangʼombe wokongola,koma chimphanga chikubwerakuchokera kumpoto kudzalimbana naye. 21 Ngakhale ankhondo aganyu amene ali nayeali ngati ana angʼombe onenepa.Nawonso abwerera mʼmbuyo, nathawa pamodzi.Palibe amene wachirimika.Ndithu, tsiku la tsoka lawafikira;ndiyo nthawi yowalanga. 22 Aigupto akuthawa ndi liwu lawo lili ngati la njoka yothawapamene adani abwera ndi zida zawo,abwera ndi nkhwangwangati anthu odula mitengo. 23 Iwo adzadula nkhalango ya Igupto,”akutero Yehova,“ngakhale kuti ndi yowirira.Anthuwo ndi ochuluka kupambana dzombe,moti sangatheke kuwerengeka. 24 Anthu a ku Igupto achita manyaziatengedwa ukapolo ndi anthu a kumpoto.” 25 Yehova Wamphamvuzonse, Mulungu wa Israeli, akunena kuti, “Ndili pafupi kulanga Amoni mulungu wa Tebesi. Ndidzalanganso Farao ndi Igupto pamodzi ndi milungu yake yonse, mafumu ake ndi onse amene amamukhulupirira. 26 Ndidzawapereka kwa amene akufuna kuwapha, ndiye kuti kwa Nebukadinezara mfumu ya ku Babuloni ndi atsogoleri ake ankhondo. Komabe, mʼtsogolomo Igupto adzakhalanso ndi anthu monga kale,” akutero Yehova. 27 “Iwe mtumiki wanga Yakobo, usachite mantha;usataye mtima, iwe Israeli.Ndithu Ine ndidzakupulumutsa kuchokera ku mayiko akutali,ndidzapulumutsanso zidzukulu zako kuchokera ku mayiko kumene anapita nazo ku ukapolo.Yakobo adzabwerera ndipo adzakhala motakasuka ndi pa mtendere,ndipo palibenso wina amene adzamuopsa. 28 Iwe mtumiki wanga Yakobo, usachite mantha,pakuti Ine ndili nawe,” akutero Yehova.“Ndidzawonongeratu mitundu yonse ya anthua ku mayiko kumene ndakupirikitsira,Koma iwe sindidzakuwononga kotheratu.Ndidzakulanga iwe ndithu koma moyenerera;sindidzakulekerera osakulanga.”

In Other Versions

Jeremiah 46 in the ANGEFD

Jeremiah 46 in the ANTPNG2D

Jeremiah 46 in the AS21

Jeremiah 46 in the BAGH

Jeremiah 46 in the BBPNG

Jeremiah 46 in the BBT1E

Jeremiah 46 in the BDS

Jeremiah 46 in the BEV

Jeremiah 46 in the BHAD

Jeremiah 46 in the BIB

Jeremiah 46 in the BLPT

Jeremiah 46 in the BNT

Jeremiah 46 in the BNTABOOT

Jeremiah 46 in the BNTLV

Jeremiah 46 in the BOATCB

Jeremiah 46 in the BOATCB2

Jeremiah 46 in the BOBCV

Jeremiah 46 in the BOCNT

Jeremiah 46 in the BOECS

Jeremiah 46 in the BOHCB

Jeremiah 46 in the BOHCV

Jeremiah 46 in the BOHLNT

Jeremiah 46 in the BOHNTLTAL

Jeremiah 46 in the BOICB

Jeremiah 46 in the BOILNTAP

Jeremiah 46 in the BOITCV

Jeremiah 46 in the BOKCV

Jeremiah 46 in the BOKCV2

Jeremiah 46 in the BOKHWOG

Jeremiah 46 in the BOKSSV

Jeremiah 46 in the BOLCB

Jeremiah 46 in the BOLCB2

Jeremiah 46 in the BOMCV

Jeremiah 46 in the BONAV

Jeremiah 46 in the BONCB

Jeremiah 46 in the BONLT

Jeremiah 46 in the BONUT2

Jeremiah 46 in the BOPLNT

Jeremiah 46 in the BOSCB

Jeremiah 46 in the BOSNC

Jeremiah 46 in the BOTLNT

Jeremiah 46 in the BOVCB

Jeremiah 46 in the BOYCB

Jeremiah 46 in the BPBB

Jeremiah 46 in the BPH

Jeremiah 46 in the BSB

Jeremiah 46 in the CCB

Jeremiah 46 in the CUV

Jeremiah 46 in the CUVS

Jeremiah 46 in the DBT

Jeremiah 46 in the DGDNT

Jeremiah 46 in the DHNT

Jeremiah 46 in the DNT

Jeremiah 46 in the ELBE

Jeremiah 46 in the EMTV

Jeremiah 46 in the ESV

Jeremiah 46 in the FBV

Jeremiah 46 in the FEB

Jeremiah 46 in the GGMNT

Jeremiah 46 in the GNT

Jeremiah 46 in the HARY

Jeremiah 46 in the HNT

Jeremiah 46 in the IRVA

Jeremiah 46 in the IRVB

Jeremiah 46 in the IRVG

Jeremiah 46 in the IRVH

Jeremiah 46 in the IRVK

Jeremiah 46 in the IRVM

Jeremiah 46 in the IRVM2

Jeremiah 46 in the IRVO

Jeremiah 46 in the IRVP

Jeremiah 46 in the IRVT

Jeremiah 46 in the IRVT2

Jeremiah 46 in the IRVU

Jeremiah 46 in the ISVN

Jeremiah 46 in the JSNT

Jeremiah 46 in the KAPI

Jeremiah 46 in the KBT1ETNIK

Jeremiah 46 in the KBV

Jeremiah 46 in the KJV

Jeremiah 46 in the KNFD

Jeremiah 46 in the LBA

Jeremiah 46 in the LBLA

Jeremiah 46 in the LNT

Jeremiah 46 in the LSV

Jeremiah 46 in the MAAL

Jeremiah 46 in the MBV

Jeremiah 46 in the MBV2

Jeremiah 46 in the MHNT

Jeremiah 46 in the MKNFD

Jeremiah 46 in the MNG

Jeremiah 46 in the MNT

Jeremiah 46 in the MNT2

Jeremiah 46 in the MRS1T

Jeremiah 46 in the NAA

Jeremiah 46 in the NASB

Jeremiah 46 in the NBLA

Jeremiah 46 in the NBS

Jeremiah 46 in the NBVTP

Jeremiah 46 in the NET2

Jeremiah 46 in the NIV11

Jeremiah 46 in the NNT

Jeremiah 46 in the NNT2

Jeremiah 46 in the NNT3

Jeremiah 46 in the PDDPT

Jeremiah 46 in the PFNT

Jeremiah 46 in the RMNT

Jeremiah 46 in the SBIAS

Jeremiah 46 in the SBIBS

Jeremiah 46 in the SBIBS2

Jeremiah 46 in the SBICS

Jeremiah 46 in the SBIDS

Jeremiah 46 in the SBIGS

Jeremiah 46 in the SBIHS

Jeremiah 46 in the SBIIS

Jeremiah 46 in the SBIIS2

Jeremiah 46 in the SBIIS3

Jeremiah 46 in the SBIKS

Jeremiah 46 in the SBIKS2

Jeremiah 46 in the SBIMS

Jeremiah 46 in the SBIOS

Jeremiah 46 in the SBIPS

Jeremiah 46 in the SBISS

Jeremiah 46 in the SBITS

Jeremiah 46 in the SBITS2

Jeremiah 46 in the SBITS3

Jeremiah 46 in the SBITS4

Jeremiah 46 in the SBIUS

Jeremiah 46 in the SBIVS

Jeremiah 46 in the SBT

Jeremiah 46 in the SBT1E

Jeremiah 46 in the SCHL

Jeremiah 46 in the SNT

Jeremiah 46 in the SUSU

Jeremiah 46 in the SUSU2

Jeremiah 46 in the SYNO

Jeremiah 46 in the TBIAOTANT

Jeremiah 46 in the TBT1E

Jeremiah 46 in the TBT1E2

Jeremiah 46 in the TFTIP

Jeremiah 46 in the TFTU

Jeremiah 46 in the TGNTATF3T

Jeremiah 46 in the THAI

Jeremiah 46 in the TNFD

Jeremiah 46 in the TNT

Jeremiah 46 in the TNTIK

Jeremiah 46 in the TNTIL

Jeremiah 46 in the TNTIN

Jeremiah 46 in the TNTIP

Jeremiah 46 in the TNTIZ

Jeremiah 46 in the TOMA

Jeremiah 46 in the TTENT

Jeremiah 46 in the UBG

Jeremiah 46 in the UGV

Jeremiah 46 in the UGV2

Jeremiah 46 in the UGV3

Jeremiah 46 in the VBL

Jeremiah 46 in the VDCC

Jeremiah 46 in the YALU

Jeremiah 46 in the YAPE

Jeremiah 46 in the YBVTP

Jeremiah 46 in the ZBP