Job 5 (BOGWICC)

1 “Itana ngati ungathe, koma ndani adzakuyankhe?Kodi ndi kwa mngelo uti ungapezeko thandizo? 2 Mkwiyo umapha chitsiru,ndipo njiru imawononga wopusa. 3 Ine ndinaona chitsiru chitamera mizu,koma mwadzidzidzi nyumba yake inatembereredwa. 4 Ana ake alibe ndi chitetezo chomwe;amaponderezedwa mʼbwalo la milandu popanda owateteza. 5 Anthu anjala amamudyera zokolola zake,amamutengera ndi za pa minga pomwe,ndipo anthu akhwinthi amafunkha chuma chake. 6 Pakuti masautso satuluka mʼfumbi,ndipo kuwukira sikuchokera mʼdothi. 7 Komatu munthu amabadwira kuti azunzikemonga momwe mbaliwali zimathethekera mlengalenga. 8 “Koma ndikanakhala ine, ndikanamudandawulira Mulungu;ndikanapereka mlandu wanga kwa Iye. 9 Iye amachita zozizwitsa zimene sizimvetsetseka,zodabwitsa zimene sizingatheke kuwerengedwa. 10 Iye amagwetsa mvula pa dziko lapansi,ndipo amathirira minda ya anthu. 11 Iye amakweza anthu wamba,ndipo iwo amene akulira amawayika pa malo otetezedwa. 12 Iyeyo amalepheretsa chiwembu cha anthu ochenjera,kotero kuti cholinga chawo sichipindula kanthu. 13 Iye amakola anthu ochenjera mu msampha wa kuchenjera kwawo,ndipo zolinga za atambwali amazithetsa msangamsanga. 14 Mdima umawagwera nthawi yamasana;nthawi yamasana amayenda moyambasayambasa monga nthawi ya usiku. 15 Mulungu amapulumutsa amphawi ku lupanga la mʼkamwa mwawo;amawapulumutsa mʼmanja mwa anthu amphamvu. 16 Choncho osauka ali ndi chiyembekezo,ndipo anthu opanda chilungamo amawatseka pakamwa. 17 “Wodala munthu amene Mulungu amamudzudzula;nʼchifukwa chake usanyoze chilango cha Wamphamvuzonse. 18 Pakuti Iye amavulaza koma amamanganso mabalawo;Iye amakantha munthu, komanso manja ake amachiritsa. 19 Pakuti adzakupulumutsa ku masautso nthawi ndi nthawi,mavuto angachuluke bwanji, sadzakukhudza ndi pangʼono pomwe. 20 Pa nthawi ya njala adzakulanditsa ku imfa,ndipo nthawi ya nkhondo adzakupulumutsa ku lupanga. 21 Adzakuteteza kwa anthu osinjirira,ndipo palibe chifukwa chochitira mantha pamene chiwonongeko chafika. 22 Uzidzaseka pa nthawi ya chiwonongeko ndi ya njala,ndipo palibe chifukwa chochitira mantha ndi zirombo za mʼdziko lapansi. 23 Pakuti udzachita pangano ndi miyala ya mʼmunda mwako,ndipo nyama zakuthengo zidzakhala nawe mwamtendere. 24 Udzadziwa kuti nyumba yako ndi malo otetezedwa;udzawerengera katundu wako ndipo sudzapeza kanthu kamene kasowapo. 25 Udzadziwa kuti ana ako adzakhala ambiri,ndipo zidzukulu zako zidzakhala ngati udzu wa mʼdziko lapansi. 26 Udzafika ku manda utakalamba,monga mitolo ya zokolola pa nyengo yake. 27 “Ife tafufuza zimenezi ndipo ndi zoona,choncho uzimvere ndi kuzitsata.”

In Other Versions

Job 5 in the ANGEFD

Job 5 in the ANTPNG2D

Job 5 in the AS21

Job 5 in the BAGH

Job 5 in the BBPNG

Job 5 in the BBT1E

Job 5 in the BDS

Job 5 in the BEV

Job 5 in the BHAD

Job 5 in the BIB

Job 5 in the BLPT

Job 5 in the BNT

Job 5 in the BNTABOOT

Job 5 in the BNTLV

Job 5 in the BOATCB

Job 5 in the BOATCB2

Job 5 in the BOBCV

Job 5 in the BOCNT

Job 5 in the BOECS

Job 5 in the BOHCB

Job 5 in the BOHCV

Job 5 in the BOHLNT

Job 5 in the BOHNTLTAL

Job 5 in the BOICB

Job 5 in the BOILNTAP

Job 5 in the BOITCV

Job 5 in the BOKCV

Job 5 in the BOKCV2

Job 5 in the BOKHWOG

Job 5 in the BOKSSV

Job 5 in the BOLCB

Job 5 in the BOLCB2

Job 5 in the BOMCV

Job 5 in the BONAV

Job 5 in the BONCB

Job 5 in the BONLT

Job 5 in the BONUT2

Job 5 in the BOPLNT

Job 5 in the BOSCB

Job 5 in the BOSNC

Job 5 in the BOTLNT

Job 5 in the BOVCB

Job 5 in the BOYCB

Job 5 in the BPBB

Job 5 in the BPH

Job 5 in the BSB

Job 5 in the CCB

Job 5 in the CUV

Job 5 in the CUVS

Job 5 in the DBT

Job 5 in the DGDNT

Job 5 in the DHNT

Job 5 in the DNT

Job 5 in the ELBE

Job 5 in the EMTV

Job 5 in the ESV

Job 5 in the FBV

Job 5 in the FEB

Job 5 in the GGMNT

Job 5 in the GNT

Job 5 in the HARY

Job 5 in the HNT

Job 5 in the IRVA

Job 5 in the IRVB

Job 5 in the IRVG

Job 5 in the IRVH

Job 5 in the IRVK

Job 5 in the IRVM

Job 5 in the IRVM2

Job 5 in the IRVO

Job 5 in the IRVP

Job 5 in the IRVT

Job 5 in the IRVT2

Job 5 in the IRVU

Job 5 in the ISVN

Job 5 in the JSNT

Job 5 in the KAPI

Job 5 in the KBT1ETNIK

Job 5 in the KBV

Job 5 in the KJV

Job 5 in the KNFD

Job 5 in the LBA

Job 5 in the LBLA

Job 5 in the LNT

Job 5 in the LSV

Job 5 in the MAAL

Job 5 in the MBV

Job 5 in the MBV2

Job 5 in the MHNT

Job 5 in the MKNFD

Job 5 in the MNG

Job 5 in the MNT

Job 5 in the MNT2

Job 5 in the MRS1T

Job 5 in the NAA

Job 5 in the NASB

Job 5 in the NBLA

Job 5 in the NBS

Job 5 in the NBVTP

Job 5 in the NET2

Job 5 in the NIV11

Job 5 in the NNT

Job 5 in the NNT2

Job 5 in the NNT3

Job 5 in the PDDPT

Job 5 in the PFNT

Job 5 in the RMNT

Job 5 in the SBIAS

Job 5 in the SBIBS

Job 5 in the SBIBS2

Job 5 in the SBICS

Job 5 in the SBIDS

Job 5 in the SBIGS

Job 5 in the SBIHS

Job 5 in the SBIIS

Job 5 in the SBIIS2

Job 5 in the SBIIS3

Job 5 in the SBIKS

Job 5 in the SBIKS2

Job 5 in the SBIMS

Job 5 in the SBIOS

Job 5 in the SBIPS

Job 5 in the SBISS

Job 5 in the SBITS

Job 5 in the SBITS2

Job 5 in the SBITS3

Job 5 in the SBITS4

Job 5 in the SBIUS

Job 5 in the SBIVS

Job 5 in the SBT

Job 5 in the SBT1E

Job 5 in the SCHL

Job 5 in the SNT

Job 5 in the SUSU

Job 5 in the SUSU2

Job 5 in the SYNO

Job 5 in the TBIAOTANT

Job 5 in the TBT1E

Job 5 in the TBT1E2

Job 5 in the TFTIP

Job 5 in the TFTU

Job 5 in the TGNTATF3T

Job 5 in the THAI

Job 5 in the TNFD

Job 5 in the TNT

Job 5 in the TNTIK

Job 5 in the TNTIL

Job 5 in the TNTIN

Job 5 in the TNTIP

Job 5 in the TNTIZ

Job 5 in the TOMA

Job 5 in the TTENT

Job 5 in the UBG

Job 5 in the UGV

Job 5 in the UGV2

Job 5 in the UGV3

Job 5 in the VBL

Job 5 in the VDCC

Job 5 in the YALU

Job 5 in the YAPE

Job 5 in the YBVTP

Job 5 in the ZBP