Matthew 4 (BOGWICC)

1 Pambuyo pake Yesu anatsogozedwa ndi Mzimu Woyera kupita ku chipululu kukayesedwa ndi mdierekezi. 2 Ndipo atasala kudya masiku makumi anayi usana ndi usiku, anamva njala. 3 Woyesayo anadza kwa Iye nati, “Ngati ndinu mwana wa Mulungu, sandutsani miyala iyi kuti ikhale buledi.” 4 Yesu anayankha kuti, “Zalembedwa, ‘Munthu sadzakhala ndi moyo ndi chakudya chokha, koma ndi mawu aliwonse ochokera mʼkamwa mwa Mulungu.’ ” 5 Pamenepo mdierekezi anapita naye ku mzinda woyera namuyimiritsa pamwamba penipeni pa Nyumba ya Mulungu. 6 Ndipo anati, “Ngati ndinu Mwana wa Mulungu, dziponyeni nokha pansi. Pakuti kwalembedwa:“ ‘Adzalamulira angelo ake za iwe,ndipo adzakunyamula ndi manja awokuti phazi lako lisagunde pa mwala.’ ” 7 Yesu anamuyankha kuti, “Kwalembedwanso: ‘Musamuyese Yehova Mulungu wanu.’ ” 8 Kenaka mdierekezi anamutengera Yesu ku phiri lalitali kwambiri namuonetsa maufumu onse a dziko lapansi ndi ulemerero wawo. 9 Ndipo anati kwa Iye, “Zonsezi ndidzakupatsani ngati mutandiweramira ndi kundipembedza ine.” 10 Yesu anati kwa iye, “Choka Satana! Zalembedwa, ‘Pembedza Yehova Mulungu wako ndi kumutumikira Iye yekha.’ ” 11 Pamenepo mdierekezi anamusiya ndipo angelo anamutumikira Iye. 12 Yesu atamva kuti Yohane anamutsekera mʼndende, anabwerera ku Galileya. 13 Ndipo atachoka ku Nazareti anapita ku Kaperenawo ndi kukhala mʼmbali mwa nyanja, mʼdera la Zebuloni ndi Nafutali; 14 pokwaniritsa zimene zinanenedwa kudzera mwa mneneri Yesaya kuti, 15 “Dziko la Zebuloni ndi dziko la Nafutali,njira ya ku nyanja, kutsidya lija la Yorodani,Galileya wa anthu a mitundu ina, 16 anthu okhala mu mdimaawona kuwala kwakukulu;ndi kwa iwo okhala mʼdziko la mthunzi wa imfakuwunika kwawafikira.” 17 Kuyambira nthawi imeneyo, Yesu anayamba kulalikira nati, “Tembenukani mtima ufumu wakumwamba wayandikira.” 18 Pamene Yesu ankayenda mʼmbali mwa nyanja ya Galileya, anaona abale awiri, Simoni wotchedwa Petro ndi mʼbale wake Andreya akuponya khoka mʼnyanja popeza anali asodzi. 19 Yesu anati, “Bwerani, tsateni Ine ndipo ndidzakusandutsani asodzi a anthu.” 20 Nthawi yomweyo anasiya makoka awo namutsata Iye. 21 Atapita patsogolo, anaona abale ena awiri, Yakobo ndi mʼbale wake Yohane ana a Zebedayo. Iwowa anali mʼbwato ndi abambo awo, Zebedayo, akukonza makoka awo ndipo Yesu anawayitana. 22 Nthawi yomweyo anasiya bwato ndi abambo awo namutsata Iye. 23 Yesu anayendayenda mu Galileya kuphunzitsa mʼmasunagoge awo, nalalikira Uthenga Wabwino wa ufumu ndi kuchiritsa matenda onse pakati pa anthu. 24 Mbiri yake yonse inawanda ku Siriya konse ndipo anthu anabweretsa kwa Iye onse amene anali odwala nthenda zosiyanasiyana, womva maululu aakulu, ogwidwa ndi ziwanda, odwala matenda akugwa ndi olumala ndipo Iye anawachiritsa. 25 Magulu ambiri a anthu anachokera ku Galileya, Dekapoli, Yerusalemu, Yudeya ndi ku madera a kutsidya la mtsinje wa Yorodani namutsata Iye.

In Other Versions

Matthew 4 in the ANGEFD

Matthew 4 in the ANTPNG2D

Matthew 4 in the AS21

Matthew 4 in the BAGH

Matthew 4 in the BBPNG

Matthew 4 in the BBT1E

Matthew 4 in the BDS

Matthew 4 in the BEV

Matthew 4 in the BHAD

Matthew 4 in the BIB

Matthew 4 in the BLPT

Matthew 4 in the BNT

Matthew 4 in the BNTABOOT

Matthew 4 in the BNTLV

Matthew 4 in the BOATCB

Matthew 4 in the BOATCB2

Matthew 4 in the BOBCV

Matthew 4 in the BOCNT

Matthew 4 in the BOECS

Matthew 4 in the BOHCB

Matthew 4 in the BOHCV

Matthew 4 in the BOHLNT

Matthew 4 in the BOHNTLTAL

Matthew 4 in the BOICB

Matthew 4 in the BOILNTAP

Matthew 4 in the BOITCV

Matthew 4 in the BOKCV

Matthew 4 in the BOKCV2

Matthew 4 in the BOKHWOG

Matthew 4 in the BOKSSV

Matthew 4 in the BOLCB

Matthew 4 in the BOLCB2

Matthew 4 in the BOMCV

Matthew 4 in the BONAV

Matthew 4 in the BONCB

Matthew 4 in the BONLT

Matthew 4 in the BONUT2

Matthew 4 in the BOPLNT

Matthew 4 in the BOSCB

Matthew 4 in the BOSNC

Matthew 4 in the BOTLNT

Matthew 4 in the BOVCB

Matthew 4 in the BOYCB

Matthew 4 in the BPBB

Matthew 4 in the BPH

Matthew 4 in the BSB

Matthew 4 in the CCB

Matthew 4 in the CUV

Matthew 4 in the CUVS

Matthew 4 in the DBT

Matthew 4 in the DGDNT

Matthew 4 in the DHNT

Matthew 4 in the DNT

Matthew 4 in the ELBE

Matthew 4 in the EMTV

Matthew 4 in the ESV

Matthew 4 in the FBV

Matthew 4 in the FEB

Matthew 4 in the GGMNT

Matthew 4 in the GNT

Matthew 4 in the HARY

Matthew 4 in the HNT

Matthew 4 in the IRVA

Matthew 4 in the IRVB

Matthew 4 in the IRVG

Matthew 4 in the IRVH

Matthew 4 in the IRVK

Matthew 4 in the IRVM

Matthew 4 in the IRVM2

Matthew 4 in the IRVO

Matthew 4 in the IRVP

Matthew 4 in the IRVT

Matthew 4 in the IRVT2

Matthew 4 in the IRVU

Matthew 4 in the ISVN

Matthew 4 in the JSNT

Matthew 4 in the KAPI

Matthew 4 in the KBT1ETNIK

Matthew 4 in the KBV

Matthew 4 in the KJV

Matthew 4 in the KNFD

Matthew 4 in the LBA

Matthew 4 in the LBLA

Matthew 4 in the LNT

Matthew 4 in the LSV

Matthew 4 in the MAAL

Matthew 4 in the MBV

Matthew 4 in the MBV2

Matthew 4 in the MHNT

Matthew 4 in the MKNFD

Matthew 4 in the MNG

Matthew 4 in the MNT

Matthew 4 in the MNT2

Matthew 4 in the MRS1T

Matthew 4 in the NAA

Matthew 4 in the NASB

Matthew 4 in the NBLA

Matthew 4 in the NBS

Matthew 4 in the NBVTP

Matthew 4 in the NET2

Matthew 4 in the NIV11

Matthew 4 in the NNT

Matthew 4 in the NNT2

Matthew 4 in the NNT3

Matthew 4 in the PDDPT

Matthew 4 in the PFNT

Matthew 4 in the RMNT

Matthew 4 in the SBIAS

Matthew 4 in the SBIBS

Matthew 4 in the SBIBS2

Matthew 4 in the SBICS

Matthew 4 in the SBIDS

Matthew 4 in the SBIGS

Matthew 4 in the SBIHS

Matthew 4 in the SBIIS

Matthew 4 in the SBIIS2

Matthew 4 in the SBIIS3

Matthew 4 in the SBIKS

Matthew 4 in the SBIKS2

Matthew 4 in the SBIMS

Matthew 4 in the SBIOS

Matthew 4 in the SBIPS

Matthew 4 in the SBISS

Matthew 4 in the SBITS

Matthew 4 in the SBITS2

Matthew 4 in the SBITS3

Matthew 4 in the SBITS4

Matthew 4 in the SBIUS

Matthew 4 in the SBIVS

Matthew 4 in the SBT

Matthew 4 in the SBT1E

Matthew 4 in the SCHL

Matthew 4 in the SNT

Matthew 4 in the SUSU

Matthew 4 in the SUSU2

Matthew 4 in the SYNO

Matthew 4 in the TBIAOTANT

Matthew 4 in the TBT1E

Matthew 4 in the TBT1E2

Matthew 4 in the TFTIP

Matthew 4 in the TFTU

Matthew 4 in the TGNTATF3T

Matthew 4 in the THAI

Matthew 4 in the TNFD

Matthew 4 in the TNT

Matthew 4 in the TNTIK

Matthew 4 in the TNTIL

Matthew 4 in the TNTIN

Matthew 4 in the TNTIP

Matthew 4 in the TNTIZ

Matthew 4 in the TOMA

Matthew 4 in the TTENT

Matthew 4 in the UBG

Matthew 4 in the UGV

Matthew 4 in the UGV2

Matthew 4 in the UGV3

Matthew 4 in the VBL

Matthew 4 in the VDCC

Matthew 4 in the YALU

Matthew 4 in the YAPE

Matthew 4 in the YBVTP

Matthew 4 in the ZBP