Micah 4 (BOGWICC)

1 Mʼmasiku otsiriza,phiri la Nyumba ya Yehova adzalikhazikitsakukhala lalitali kuposa mapiri ena onse.Lidzaonekera pamwamba pa mapiri ena onse,ndipo anthu amitundu yonse adzathamangira kumeneko. 2 Mayiko ambiri adzabwera ndikunena kuti,“Tiyeni, tikwere ku phiri la Yehova,ku nyumba ya Mulungu wa Yakobo.Iye adzatiphunzitsa njira zake,ndipo tidzayenda mʼnjira zakezo.”Malangizo adzachokera ku Ziyoni,mawu a Yehova adzachokera ku Yerusalemu. 3 Iye adzaweruza pakati pa anthu amitundu yambirindipo adzathetsa kusamvana pakati pa anthu amphamvu akutali ndi apafupi omwe.Anthuwo adzasandutsa malupanga awo kukhala makasundiponso mikondo yawo kukhala zomwetera.Mtundu wina sudzatenganso lupanga kumenyana ndi mtundu wina,kapena kuphunziranso za nkhondo. 4 Munthu aliyense adzakhala pansi pa tsinde pa mtengo wake wa mpesandi pa tsinde pa mtengo wake wamkuyu,ndipo palibe amene adzawachititse mantha,pakuti Yehova Wamphamvuzonse wayankhula. 5 Mitundu yonse ya anthuitha kutsatira milungu yawo;ife tidzayenda mʼnjira za YehovaMulungu wathu mpaka muyaya. 6 “Tsiku limenelo, Yehova akuti,“ndidzasonkhanitsa olumala;ndidzasonkhanitsa pamodzi anthu ochotsedwandiponso amene ndinawalanga. 7 Anthu olumalawo ndidzawasandutsa anthu anga otsala.Anthu amene ndinawachotsa ndidzawasandutsa mtundu wamphamvu.Yehova adzawalamulira mʼPhiri la Yehovakuyambira tsiku limenelo mpaka muyaya. 8 Kunena za iwe, nsanja ya ziweto zanga,iwe linga la mwana wamkazi wa Ziyoni,ulamuliro wako wakale udzabwezeretsedwa kwa iwe;ufumu udzabwera pa mwana wamkazi wa Yerusalemu.” 9 Chifukwa chiyani tsopano ukulira mofuwula,kodi ulibe mfumu?Kodi phungu wako wawonongedwa,kotero kuti ululu wako uli ngati wa mayi amene akubereka? 10 Gubuduka ndi ululu, iwe mwana wamkazi wa Ziyoni,ngati mayi pa nthawi yake yobereka,pakuti tsopano muyenera kuchoka mu mzindandi kugona kunja kwa mzindawo.Udzapita ku Babuloni;kumeneko udzapulumutsidwa,kumeneko Yehova adzakuwombolamʼmanja mwa adani ako. 11 Koma tsopano mitundu yambiri ya anthuyasonkhana kulimbana nawe.Iwo akuti, “Tiyeni timudetse,maso athu aone chiwonongeko cha Ziyoni!” 12 Koma iwo sakudziwamaganizo a Yehova;iwo sakuzindikira cholinga chake,Iye amene amawatuta ngati mitolo ya tirigu ku malo opunthira tirigu. 13 “Imirira, puntha, iwe mwana wamkazi wa Ziyoni,pakuti ndidzakupatsa nyanga zachitsulo;ndidzakupatsa ziboda zamkuwandipo udzaphwanya mitundu yambiri ya anthu.” Phindu lawo lolipeza molakwikalo udzalipereka kwa Yehova,chuma chawo kwa Yehova wa dziko lonse lapansi.

In Other Versions

Micah 4 in the ANGEFD

Micah 4 in the ANTPNG2D

Micah 4 in the AS21

Micah 4 in the BAGH

Micah 4 in the BBPNG

Micah 4 in the BBT1E

Micah 4 in the BDS

Micah 4 in the BEV

Micah 4 in the BHAD

Micah 4 in the BIB

Micah 4 in the BLPT

Micah 4 in the BNT

Micah 4 in the BNTABOOT

Micah 4 in the BNTLV

Micah 4 in the BOATCB

Micah 4 in the BOATCB2

Micah 4 in the BOBCV

Micah 4 in the BOCNT

Micah 4 in the BOECS

Micah 4 in the BOHCB

Micah 4 in the BOHCV

Micah 4 in the BOHLNT

Micah 4 in the BOHNTLTAL

Micah 4 in the BOICB

Micah 4 in the BOILNTAP

Micah 4 in the BOITCV

Micah 4 in the BOKCV

Micah 4 in the BOKCV2

Micah 4 in the BOKHWOG

Micah 4 in the BOKSSV

Micah 4 in the BOLCB

Micah 4 in the BOLCB2

Micah 4 in the BOMCV

Micah 4 in the BONAV

Micah 4 in the BONCB

Micah 4 in the BONLT

Micah 4 in the BONUT2

Micah 4 in the BOPLNT

Micah 4 in the BOSCB

Micah 4 in the BOSNC

Micah 4 in the BOTLNT

Micah 4 in the BOVCB

Micah 4 in the BOYCB

Micah 4 in the BPBB

Micah 4 in the BPH

Micah 4 in the BSB

Micah 4 in the CCB

Micah 4 in the CUV

Micah 4 in the CUVS

Micah 4 in the DBT

Micah 4 in the DGDNT

Micah 4 in the DHNT

Micah 4 in the DNT

Micah 4 in the ELBE

Micah 4 in the EMTV

Micah 4 in the ESV

Micah 4 in the FBV

Micah 4 in the FEB

Micah 4 in the GGMNT

Micah 4 in the GNT

Micah 4 in the HARY

Micah 4 in the HNT

Micah 4 in the IRVA

Micah 4 in the IRVB

Micah 4 in the IRVG

Micah 4 in the IRVH

Micah 4 in the IRVK

Micah 4 in the IRVM

Micah 4 in the IRVM2

Micah 4 in the IRVO

Micah 4 in the IRVP

Micah 4 in the IRVT

Micah 4 in the IRVT2

Micah 4 in the IRVU

Micah 4 in the ISVN

Micah 4 in the JSNT

Micah 4 in the KAPI

Micah 4 in the KBT1ETNIK

Micah 4 in the KBV

Micah 4 in the KJV

Micah 4 in the KNFD

Micah 4 in the LBA

Micah 4 in the LBLA

Micah 4 in the LNT

Micah 4 in the LSV

Micah 4 in the MAAL

Micah 4 in the MBV

Micah 4 in the MBV2

Micah 4 in the MHNT

Micah 4 in the MKNFD

Micah 4 in the MNG

Micah 4 in the MNT

Micah 4 in the MNT2

Micah 4 in the MRS1T

Micah 4 in the NAA

Micah 4 in the NASB

Micah 4 in the NBLA

Micah 4 in the NBS

Micah 4 in the NBVTP

Micah 4 in the NET2

Micah 4 in the NIV11

Micah 4 in the NNT

Micah 4 in the NNT2

Micah 4 in the NNT3

Micah 4 in the PDDPT

Micah 4 in the PFNT

Micah 4 in the RMNT

Micah 4 in the SBIAS

Micah 4 in the SBIBS

Micah 4 in the SBIBS2

Micah 4 in the SBICS

Micah 4 in the SBIDS

Micah 4 in the SBIGS

Micah 4 in the SBIHS

Micah 4 in the SBIIS

Micah 4 in the SBIIS2

Micah 4 in the SBIIS3

Micah 4 in the SBIKS

Micah 4 in the SBIKS2

Micah 4 in the SBIMS

Micah 4 in the SBIOS

Micah 4 in the SBIPS

Micah 4 in the SBISS

Micah 4 in the SBITS

Micah 4 in the SBITS2

Micah 4 in the SBITS3

Micah 4 in the SBITS4

Micah 4 in the SBIUS

Micah 4 in the SBIVS

Micah 4 in the SBT

Micah 4 in the SBT1E

Micah 4 in the SCHL

Micah 4 in the SNT

Micah 4 in the SUSU

Micah 4 in the SUSU2

Micah 4 in the SYNO

Micah 4 in the TBIAOTANT

Micah 4 in the TBT1E

Micah 4 in the TBT1E2

Micah 4 in the TFTIP

Micah 4 in the TFTU

Micah 4 in the TGNTATF3T

Micah 4 in the THAI

Micah 4 in the TNFD

Micah 4 in the TNT

Micah 4 in the TNTIK

Micah 4 in the TNTIL

Micah 4 in the TNTIN

Micah 4 in the TNTIP

Micah 4 in the TNTIZ

Micah 4 in the TOMA

Micah 4 in the TTENT

Micah 4 in the UBG

Micah 4 in the UGV

Micah 4 in the UGV2

Micah 4 in the UGV3

Micah 4 in the VBL

Micah 4 in the VDCC

Micah 4 in the YALU

Micah 4 in the YAPE

Micah 4 in the YBVTP

Micah 4 in the ZBP