Micah 5 (BOGWICC)

1 Iwe mzinda wa anthu ankhondo, sonkhanitsa anthu ako ankhondo,pakuti anthu atizungulira kuti alimbane nafe.Adzakantha ndi ndodo pa chibwanocha wolamulira wa Israeli. 2 “Koma iwe Betelehemu Efurata,ngakhale uli wonyozeka pakati pa mafuko a Yuda,mwa iwe mudzatulukamunthu amene adzalamulira Israeli,amene chiyambi chake nʼchakalekale,nʼchamasiku amakedzana.” 3 Nʼchifukwa chake Israeli adzasiyidwampaka pa nthawi imene mayi amene ali woyembekezera adzachire.Ndipo abale ake onse otsalira adzabwererakudzakhala pamodzi ndi Aisraeli. 4 Iye adzalimbika, ndipo adzaweta nkhosa zakemwa mphamvu ya Yehova,mu ulemerero wa dzina la Yehova Mulungu wake.Ndipo iwo adzakhala mu mtendere,pakuti ukulu wake udzakhala ponseponse pa dziko lapansi. 5 Ndipo Iye adzakhala mtendere wawo.Asiriya akadzalowa mʼdziko lathundi kuyamba kuthira nkhondo malo athu otetezedwa,tidzawadzutsira abusa asanu ndi awiri,ngakhalenso atsogoleri asanu ndi atatu. 6 Iwo adzagonjetsa dziko la Asiriya ndi lupanga,dziko la Nimurodi adzalilamulira mwankhondo.Adzatipulumutsa kwa Asiriyaakadzafika mʼmalire a mʼdziko lathukudzatithira nkhondo. 7 Otsalira a Yakobo adzakhalapakati pa mitundu yambiri ya anthungati mame ochokera kwa Yehova,ngati mvumbi pa udzu,omwe sulamulidwa ndi munthukapena kudikira lamulo la anthu. 8 Otsala a Yakobo adzakhala pakati pa mitundu ya anthu,mʼgulu la anthu a mitundu yambiri,ngati mkango pakati pa nyama za mʼnkhalango.Ngati mwana wa mkango pakati pa gulu la nkhosa,amene pozidutsa amazidya ndi kuzikhadzula,ndipo palibe angathe kuzilanditsa. 9 Mudzagonjetsa adani anu,ndipo adani anu onse adzawonongeka. 10 Yehova akuti,“Tsiku limenelo ndidzawononga akavalo anu onsendi kuphwasula magaleta anu. 11 Ndidzawononga mizinda ya mʼdziko mwanundi kugwetsa malinga anu onse. 12 Ndidzawononga ufiti wanundipo sikudzakhalanso anthu owombeza mawula. 13 Ndidzawononga mafano anu osemapamodzi ndi miyala yanu yopatulika imene ili pakati panu;simudzagwadiranso zinthu zopangandi manja anu. 14 Ndidzazula mitengo ya mafano a Asera imene ili pakati panu,ndipo ndidzawononga mizinda yanu. 15 Ndidzayilanga mwaukali ndi mokwiyamitundu imene sinandimvere Ine.”

In Other Versions

Micah 5 in the ANGEFD

Micah 5 in the ANTPNG2D

Micah 5 in the AS21

Micah 5 in the BAGH

Micah 5 in the BBPNG

Micah 5 in the BBT1E

Micah 5 in the BDS

Micah 5 in the BEV

Micah 5 in the BHAD

Micah 5 in the BIB

Micah 5 in the BLPT

Micah 5 in the BNT

Micah 5 in the BNTABOOT

Micah 5 in the BNTLV

Micah 5 in the BOATCB

Micah 5 in the BOATCB2

Micah 5 in the BOBCV

Micah 5 in the BOCNT

Micah 5 in the BOECS

Micah 5 in the BOHCB

Micah 5 in the BOHCV

Micah 5 in the BOHLNT

Micah 5 in the BOHNTLTAL

Micah 5 in the BOICB

Micah 5 in the BOILNTAP

Micah 5 in the BOITCV

Micah 5 in the BOKCV

Micah 5 in the BOKCV2

Micah 5 in the BOKHWOG

Micah 5 in the BOKSSV

Micah 5 in the BOLCB

Micah 5 in the BOLCB2

Micah 5 in the BOMCV

Micah 5 in the BONAV

Micah 5 in the BONCB

Micah 5 in the BONLT

Micah 5 in the BONUT2

Micah 5 in the BOPLNT

Micah 5 in the BOSCB

Micah 5 in the BOSNC

Micah 5 in the BOTLNT

Micah 5 in the BOVCB

Micah 5 in the BOYCB

Micah 5 in the BPBB

Micah 5 in the BPH

Micah 5 in the BSB

Micah 5 in the CCB

Micah 5 in the CUV

Micah 5 in the CUVS

Micah 5 in the DBT

Micah 5 in the DGDNT

Micah 5 in the DHNT

Micah 5 in the DNT

Micah 5 in the ELBE

Micah 5 in the EMTV

Micah 5 in the ESV

Micah 5 in the FBV

Micah 5 in the FEB

Micah 5 in the GGMNT

Micah 5 in the GNT

Micah 5 in the HARY

Micah 5 in the HNT

Micah 5 in the IRVA

Micah 5 in the IRVB

Micah 5 in the IRVG

Micah 5 in the IRVH

Micah 5 in the IRVK

Micah 5 in the IRVM

Micah 5 in the IRVM2

Micah 5 in the IRVO

Micah 5 in the IRVP

Micah 5 in the IRVT

Micah 5 in the IRVT2

Micah 5 in the IRVU

Micah 5 in the ISVN

Micah 5 in the JSNT

Micah 5 in the KAPI

Micah 5 in the KBT1ETNIK

Micah 5 in the KBV

Micah 5 in the KJV

Micah 5 in the KNFD

Micah 5 in the LBA

Micah 5 in the LBLA

Micah 5 in the LNT

Micah 5 in the LSV

Micah 5 in the MAAL

Micah 5 in the MBV

Micah 5 in the MBV2

Micah 5 in the MHNT

Micah 5 in the MKNFD

Micah 5 in the MNG

Micah 5 in the MNT

Micah 5 in the MNT2

Micah 5 in the MRS1T

Micah 5 in the NAA

Micah 5 in the NASB

Micah 5 in the NBLA

Micah 5 in the NBS

Micah 5 in the NBVTP

Micah 5 in the NET2

Micah 5 in the NIV11

Micah 5 in the NNT

Micah 5 in the NNT2

Micah 5 in the NNT3

Micah 5 in the PDDPT

Micah 5 in the PFNT

Micah 5 in the RMNT

Micah 5 in the SBIAS

Micah 5 in the SBIBS

Micah 5 in the SBIBS2

Micah 5 in the SBICS

Micah 5 in the SBIDS

Micah 5 in the SBIGS

Micah 5 in the SBIHS

Micah 5 in the SBIIS

Micah 5 in the SBIIS2

Micah 5 in the SBIIS3

Micah 5 in the SBIKS

Micah 5 in the SBIKS2

Micah 5 in the SBIMS

Micah 5 in the SBIOS

Micah 5 in the SBIPS

Micah 5 in the SBISS

Micah 5 in the SBITS

Micah 5 in the SBITS2

Micah 5 in the SBITS3

Micah 5 in the SBITS4

Micah 5 in the SBIUS

Micah 5 in the SBIVS

Micah 5 in the SBT

Micah 5 in the SBT1E

Micah 5 in the SCHL

Micah 5 in the SNT

Micah 5 in the SUSU

Micah 5 in the SUSU2

Micah 5 in the SYNO

Micah 5 in the TBIAOTANT

Micah 5 in the TBT1E

Micah 5 in the TBT1E2

Micah 5 in the TFTIP

Micah 5 in the TFTU

Micah 5 in the TGNTATF3T

Micah 5 in the THAI

Micah 5 in the TNFD

Micah 5 in the TNT

Micah 5 in the TNTIK

Micah 5 in the TNTIL

Micah 5 in the TNTIN

Micah 5 in the TNTIP

Micah 5 in the TNTIZ

Micah 5 in the TOMA

Micah 5 in the TTENT

Micah 5 in the UBG

Micah 5 in the UGV

Micah 5 in the UGV2

Micah 5 in the UGV3

Micah 5 in the VBL

Micah 5 in the VDCC

Micah 5 in the YALU

Micah 5 in the YAPE

Micah 5 in the YBVTP

Micah 5 in the ZBP