Proverbs 23 (BOGWICC)

1 Ngati ukhala pansi kuti udye pamodzi ndi wolamulira,uyangʼane bwino zimene zili pamaso pako, 2 ngati ndiwe munthu wadyeraudziletse kuti usaonetse dyera lakolo. 3 Usasirire zakudya zake,pakuti zimenezo ndi zakudya zachinyengo. 4 Usadzitopetse wekha ndi kufuna chuma,ukhale ndi nzeru ya kudziretsa. 5 Ukangoti wachipeza chumacho uwona posachedwa kuti palibepo.Chumacho chimachita ngati chamera mapiko mwadzidzidzindi kuwuluka kunka kumwamba ngati chiwombankhanga. 6 Usadye chakudya cha munthu waumbombo,usalakalake zakudya zake zokoma; 7 paja iye ndi munthu amenenthawi zonse amaganizira za mtengo wakengakhale amati kwa iwe, “Idya ndi kumwa,”koma sakondweretsedwa nawe. 8 Udzasanza zimene wadyazondipo mawu ako woyamikira adzapita pachabe. 9 Usayankhule munthu wopusa akumva,pakuti adzanyoza mawu ako anzeru. 10 Usasunthe mwala wa mʼmalire akalekalekapena kulowerera mʼminda ya ana amasiye, 11 paja Mpulumutsi wawo ndi wamphamvu;iye adzawateteza pa milandu yawo kutsutsana nawe. 12 Mtima wako uzikhala pa malangizondipo makutu ako azimvetsera mawu a chidziwitso. 13 Usaleke kumulangiza mwana;ngati umulanga ndi chikwapu sadzafa. 14 Ukamukwapula ndi tsatsaudzapulumutsa moyo wake. 15 Mwana wanga, ngati mtima wako ukhala wanzeru,inenso mtima wanga udzakondwera. 16 Mtima wanga udzakondwerapamene ndidzakumva ukuyankhula zolungama. 17 Mtima wako usachite nsanje ndi anthu ochimwa,koma uziopa Yehova tsiku ndi tsiku. 18 Ndithu za mʼtsogolo zilipondipo chiyembekezo chakocho sichidzalephereka. 19 Tamvera mwana wanga, ndipo ukhale wanzeru,mtima wako uwuyendetse mʼnjira yabwino. 20 Usakhale pakati pa anthu amene amaledzerakapena pakati pa anthu amene amadya nyama mwadyera. 21 Paja anthu oledzera ndi adyera amadzakhala amphawindipo aulesi adzavala sanza. 22 Mvera abambo ako amene anakubala,usanyoze amayi ako pamene akalamba. 23 Gula choonadi ndipo usachigulitse;ugulenso nzeru, mwambo ndiponso kumvetsa zinthu bwino. 24 Abambo a munthu wolungama ali ndi chimwemwe chachikulu;Wobala mwana wanzeru adzakondwera naye. 25 Abambo ndi amayi ako asangalale;amene anakubereka akondwere! 26 Mwana wanga, undikhulupirirendipo maso ako apenyetsetse njira zanga. 27 Paja mkazi wachiwerewere ali ngati dzenje lozama;ndipo mkazi woyendayenda ali ngati chitsime chopapatiza. 28 Amabisala ngati mbala yachifwamba,ndipo amuna amakhala osakhulupirika chifukwa cha iyeyu. 29 Ndani ali ndi tsoka? Ndani ali ndi chisoni?Ndani ali pa mkangano? Ndani ali ndi madandawulo?Ndani ali ndi zipsera zosadziwika uko zachokera? Ndani ali ndi maso ofiira? 30 Ndi amene amakhalitsa pa mowa,amene amapita nalawa vinyo osakanizidwa. 31 Usatengeke mtima ndi kufiira kwa vinyo,pamene akuwira mʼchikhopamene akumweka bwino! 32 Potsiriza pake amaluma ngati njoka,ndipo amajompha ngati mphiri. 33 Maso ako adzaona zinthu zachilendondipo maganizo ndi mawu ako adzakhala osokonekera. 34 Udzakhala ngati munthu amene ali gone pakati pa nyanja,kapena ngati munthu wogona pa msonga ya mlongoti ya ngalawa. 35 Iwe udzanena kuti, “Anandimenya, koma sindinapwetekedwe!Andimenya koma sindinamve kanthu!Kodi ndidzuka nthawi yanji?Ndiye ndifunefunenso vinyo wina.”

In Other Versions

Proverbs 23 in the ANGEFD

Proverbs 23 in the ANTPNG2D

Proverbs 23 in the AS21

Proverbs 23 in the BAGH

Proverbs 23 in the BBPNG

Proverbs 23 in the BBT1E

Proverbs 23 in the BDS

Proverbs 23 in the BEV

Proverbs 23 in the BHAD

Proverbs 23 in the BIB

Proverbs 23 in the BLPT

Proverbs 23 in the BNT

Proverbs 23 in the BNTABOOT

Proverbs 23 in the BNTLV

Proverbs 23 in the BOATCB

Proverbs 23 in the BOATCB2

Proverbs 23 in the BOBCV

Proverbs 23 in the BOCNT

Proverbs 23 in the BOECS

Proverbs 23 in the BOHCB

Proverbs 23 in the BOHCV

Proverbs 23 in the BOHLNT

Proverbs 23 in the BOHNTLTAL

Proverbs 23 in the BOICB

Proverbs 23 in the BOILNTAP

Proverbs 23 in the BOITCV

Proverbs 23 in the BOKCV

Proverbs 23 in the BOKCV2

Proverbs 23 in the BOKHWOG

Proverbs 23 in the BOKSSV

Proverbs 23 in the BOLCB

Proverbs 23 in the BOLCB2

Proverbs 23 in the BOMCV

Proverbs 23 in the BONAV

Proverbs 23 in the BONCB

Proverbs 23 in the BONLT

Proverbs 23 in the BONUT2

Proverbs 23 in the BOPLNT

Proverbs 23 in the BOSCB

Proverbs 23 in the BOSNC

Proverbs 23 in the BOTLNT

Proverbs 23 in the BOVCB

Proverbs 23 in the BOYCB

Proverbs 23 in the BPBB

Proverbs 23 in the BPH

Proverbs 23 in the BSB

Proverbs 23 in the CCB

Proverbs 23 in the CUV

Proverbs 23 in the CUVS

Proverbs 23 in the DBT

Proverbs 23 in the DGDNT

Proverbs 23 in the DHNT

Proverbs 23 in the DNT

Proverbs 23 in the ELBE

Proverbs 23 in the EMTV

Proverbs 23 in the ESV

Proverbs 23 in the FBV

Proverbs 23 in the FEB

Proverbs 23 in the GGMNT

Proverbs 23 in the GNT

Proverbs 23 in the HARY

Proverbs 23 in the HNT

Proverbs 23 in the IRVA

Proverbs 23 in the IRVB

Proverbs 23 in the IRVG

Proverbs 23 in the IRVH

Proverbs 23 in the IRVK

Proverbs 23 in the IRVM

Proverbs 23 in the IRVM2

Proverbs 23 in the IRVO

Proverbs 23 in the IRVP

Proverbs 23 in the IRVT

Proverbs 23 in the IRVT2

Proverbs 23 in the IRVU

Proverbs 23 in the ISVN

Proverbs 23 in the JSNT

Proverbs 23 in the KAPI

Proverbs 23 in the KBT1ETNIK

Proverbs 23 in the KBV

Proverbs 23 in the KJV

Proverbs 23 in the KNFD

Proverbs 23 in the LBA

Proverbs 23 in the LBLA

Proverbs 23 in the LNT

Proverbs 23 in the LSV

Proverbs 23 in the MAAL

Proverbs 23 in the MBV

Proverbs 23 in the MBV2

Proverbs 23 in the MHNT

Proverbs 23 in the MKNFD

Proverbs 23 in the MNG

Proverbs 23 in the MNT

Proverbs 23 in the MNT2

Proverbs 23 in the MRS1T

Proverbs 23 in the NAA

Proverbs 23 in the NASB

Proverbs 23 in the NBLA

Proverbs 23 in the NBS

Proverbs 23 in the NBVTP

Proverbs 23 in the NET2

Proverbs 23 in the NIV11

Proverbs 23 in the NNT

Proverbs 23 in the NNT2

Proverbs 23 in the NNT3

Proverbs 23 in the PDDPT

Proverbs 23 in the PFNT

Proverbs 23 in the RMNT

Proverbs 23 in the SBIAS

Proverbs 23 in the SBIBS

Proverbs 23 in the SBIBS2

Proverbs 23 in the SBICS

Proverbs 23 in the SBIDS

Proverbs 23 in the SBIGS

Proverbs 23 in the SBIHS

Proverbs 23 in the SBIIS

Proverbs 23 in the SBIIS2

Proverbs 23 in the SBIIS3

Proverbs 23 in the SBIKS

Proverbs 23 in the SBIKS2

Proverbs 23 in the SBIMS

Proverbs 23 in the SBIOS

Proverbs 23 in the SBIPS

Proverbs 23 in the SBISS

Proverbs 23 in the SBITS

Proverbs 23 in the SBITS2

Proverbs 23 in the SBITS3

Proverbs 23 in the SBITS4

Proverbs 23 in the SBIUS

Proverbs 23 in the SBIVS

Proverbs 23 in the SBT

Proverbs 23 in the SBT1E

Proverbs 23 in the SCHL

Proverbs 23 in the SNT

Proverbs 23 in the SUSU

Proverbs 23 in the SUSU2

Proverbs 23 in the SYNO

Proverbs 23 in the TBIAOTANT

Proverbs 23 in the TBT1E

Proverbs 23 in the TBT1E2

Proverbs 23 in the TFTIP

Proverbs 23 in the TFTU

Proverbs 23 in the TGNTATF3T

Proverbs 23 in the THAI

Proverbs 23 in the TNFD

Proverbs 23 in the TNT

Proverbs 23 in the TNTIK

Proverbs 23 in the TNTIL

Proverbs 23 in the TNTIN

Proverbs 23 in the TNTIP

Proverbs 23 in the TNTIZ

Proverbs 23 in the TOMA

Proverbs 23 in the TTENT

Proverbs 23 in the UBG

Proverbs 23 in the UGV

Proverbs 23 in the UGV2

Proverbs 23 in the UGV3

Proverbs 23 in the VBL

Proverbs 23 in the VDCC

Proverbs 23 in the YALU

Proverbs 23 in the YAPE

Proverbs 23 in the YBVTP

Proverbs 23 in the ZBP