Proverbs 4 (BOGWICC)
1 Ananu, mverani malangizo a abambo anu;tcherani khutu kuti mupeze nzeru zodziwira zinthu. 2 Zimene ndikukuphunzitsani ndi zabwino.Choncho musasiye malangizo anga. 3 Paja ndinalinso mwana mʼnyumba mwa abambo anga;mwana mmodzi yekha wapamtima pa amayi anga. 4 Ndipo abambo anandiphunzitsa ndi mawu akuti,“Ugwiritse mawu anga pa mtima pako,usunge malamulo anga kuti ukhale ndi moyo. 5 Upeze nzeru, upeze nzeru zomvetsa zinthu;usayiwale mawu anga kapena kutayana nawo. 6 Usasiye nzeru ndipo idzakusunga.Uziyikonda ndipo idzakuteteza. 7 Fundo yayikulu pa za nzeru ndi iyi: upeze nzeru.Kaya pali china chilichonse chimene ungapeze, koma upeze nzeru yomvetsa bwino zinthu. 8 Uyilemekeze nzeruyo ndipo idzakukweza;ikumbatire nzeruyo ndipo idzakupatsa ulemu. 9 Idzayika sangamutu yokongola yamaluwa pamutu pako;idzakupatsa chipewa chaufumu chaulemu.” 10 Mwana wanga, umvere ndi kuvomereza zimene ndikunena,ndipo zaka za moyo wako zidzakhala zochuluka. 11 Ndakuphunzitsa njira yake ya nzeru.Ndakutsogolera mʼnjira zolungama. 12 Pamene ukuyenda, mapazi ako sadzawombana;ukamadzathamanga, sudzapunthwa. 13 Ugwiritse zimene ndikukuphunzitsazi osazitaya ayi.Uwasamale bwino pakuti moyo wako wagona pamenepa. 14 Usayende mʼnjira za anthu oyipakapena kuyenda mʼnjira ya anthu ochimwa. 15 Pewa njira zawo, usayende mʼmenemo;uzilambalala nʼkumangopita. 16 Pakuti iwo sagona mpaka atachita zoyipa;tulo salipeza mpaka atapunthwitsa munthu wina. 17 Paja chakudya chawo ndicho kuchita zoyipa basindipo chakumwa chawo ndi chiwawa. 18 Koma njira ya anthu olungama ili ngati kuwala kwa mʼbandakuchakumene kumanka kuwalirawalira mpaka dzuwa litafika pa mutu. 19 Koma njira ya anthu oyipa ili ngati mdima wandiweyani;iwo sadziwa chomwe chimawapunthwitsa. 20 Mwana wanga, mvetsetsa zimene ndikunena;tchera khutu ku mawu anga. 21 Usayiwale malangizo angawa,koma uwasunge mu mtima mwako. 22 Pakuti amapatsa moyo kwa aliyense amene awapezandipo amachiritsa thupi lake lonse. 23 Ndipotu mtima wako uziwuyangʼanira bwino ndithupakuti ndiwo magwero a moyo. 24 Usiyiretu kuyankhula zokhotakhota;ndipo ulekeretu kuyankhula zinthu zonyansa. 25 Maso ako ayangʼane patsogolo;uziyangʼana kutsogolo molunjika. 26 Uzilingalira bwino kumene kupita mapazi akondipo njira zako zonse zidzakhala zosakayikitsa. 27 Usapatukire kumanja kapena kumanzere;usapite kumene kuli zoyipa.
In Other Versions
Proverbs 4 in the ANGEFD
Proverbs 4 in the ANTPNG2D
Proverbs 4 in the AS21
Proverbs 4 in the BAGH
Proverbs 4 in the BBPNG
Proverbs 4 in the BBT1E
Proverbs 4 in the BDS
Proverbs 4 in the BEV
Proverbs 4 in the BHAD
Proverbs 4 in the BIB
Proverbs 4 in the BLPT
Proverbs 4 in the BNT
Proverbs 4 in the BNTABOOT
Proverbs 4 in the BNTLV
Proverbs 4 in the BOATCB
Proverbs 4 in the BOATCB2
Proverbs 4 in the BOBCV
Proverbs 4 in the BOCNT
Proverbs 4 in the BOECS
Proverbs 4 in the BOHCB
Proverbs 4 in the BOHCV
Proverbs 4 in the BOHLNT
Proverbs 4 in the BOHNTLTAL
Proverbs 4 in the BOICB
Proverbs 4 in the BOILNTAP
Proverbs 4 in the BOITCV
Proverbs 4 in the BOKCV
Proverbs 4 in the BOKCV2
Proverbs 4 in the BOKHWOG
Proverbs 4 in the BOKSSV
Proverbs 4 in the BOLCB
Proverbs 4 in the BOLCB2
Proverbs 4 in the BOMCV
Proverbs 4 in the BONAV
Proverbs 4 in the BONCB
Proverbs 4 in the BONLT
Proverbs 4 in the BONUT2
Proverbs 4 in the BOPLNT
Proverbs 4 in the BOSCB
Proverbs 4 in the BOSNC
Proverbs 4 in the BOTLNT
Proverbs 4 in the BOVCB
Proverbs 4 in the BOYCB
Proverbs 4 in the BPBB
Proverbs 4 in the BPH
Proverbs 4 in the BSB
Proverbs 4 in the CCB
Proverbs 4 in the CUV
Proverbs 4 in the CUVS
Proverbs 4 in the DBT
Proverbs 4 in the DGDNT
Proverbs 4 in the DHNT
Proverbs 4 in the DNT
Proverbs 4 in the ELBE
Proverbs 4 in the EMTV
Proverbs 4 in the ESV
Proverbs 4 in the FBV
Proverbs 4 in the FEB
Proverbs 4 in the GGMNT
Proverbs 4 in the GNT
Proverbs 4 in the HARY
Proverbs 4 in the HNT
Proverbs 4 in the IRVA
Proverbs 4 in the IRVB
Proverbs 4 in the IRVG
Proverbs 4 in the IRVH
Proverbs 4 in the IRVK
Proverbs 4 in the IRVM
Proverbs 4 in the IRVM2
Proverbs 4 in the IRVO
Proverbs 4 in the IRVP
Proverbs 4 in the IRVT
Proverbs 4 in the IRVT2
Proverbs 4 in the IRVU
Proverbs 4 in the ISVN
Proverbs 4 in the JSNT
Proverbs 4 in the KAPI
Proverbs 4 in the KBT1ETNIK
Proverbs 4 in the KBV
Proverbs 4 in the KJV
Proverbs 4 in the KNFD
Proverbs 4 in the LBA
Proverbs 4 in the LBLA
Proverbs 4 in the LNT
Proverbs 4 in the LSV
Proverbs 4 in the MAAL
Proverbs 4 in the MBV
Proverbs 4 in the MBV2
Proverbs 4 in the MHNT
Proverbs 4 in the MKNFD
Proverbs 4 in the MNG
Proverbs 4 in the MNT
Proverbs 4 in the MNT2
Proverbs 4 in the MRS1T
Proverbs 4 in the NAA
Proverbs 4 in the NASB
Proverbs 4 in the NBLA
Proverbs 4 in the NBS
Proverbs 4 in the NBVTP
Proverbs 4 in the NET2
Proverbs 4 in the NIV11
Proverbs 4 in the NNT
Proverbs 4 in the NNT2
Proverbs 4 in the NNT3
Proverbs 4 in the PDDPT
Proverbs 4 in the PFNT
Proverbs 4 in the RMNT
Proverbs 4 in the SBIAS
Proverbs 4 in the SBIBS
Proverbs 4 in the SBIBS2
Proverbs 4 in the SBICS
Proverbs 4 in the SBIDS
Proverbs 4 in the SBIGS
Proverbs 4 in the SBIHS
Proverbs 4 in the SBIIS
Proverbs 4 in the SBIIS2
Proverbs 4 in the SBIIS3
Proverbs 4 in the SBIKS
Proverbs 4 in the SBIKS2
Proverbs 4 in the SBIMS
Proverbs 4 in the SBIOS
Proverbs 4 in the SBIPS
Proverbs 4 in the SBISS
Proverbs 4 in the SBITS
Proverbs 4 in the SBITS2
Proverbs 4 in the SBITS3
Proverbs 4 in the SBITS4
Proverbs 4 in the SBIUS
Proverbs 4 in the SBIVS
Proverbs 4 in the SBT
Proverbs 4 in the SBT1E
Proverbs 4 in the SCHL
Proverbs 4 in the SNT
Proverbs 4 in the SUSU
Proverbs 4 in the SUSU2
Proverbs 4 in the SYNO
Proverbs 4 in the TBIAOTANT
Proverbs 4 in the TBT1E
Proverbs 4 in the TBT1E2
Proverbs 4 in the TFTIP
Proverbs 4 in the TFTU
Proverbs 4 in the TGNTATF3T
Proverbs 4 in the THAI
Proverbs 4 in the TNFD
Proverbs 4 in the TNT
Proverbs 4 in the TNTIK
Proverbs 4 in the TNTIL
Proverbs 4 in the TNTIN
Proverbs 4 in the TNTIP
Proverbs 4 in the TNTIZ
Proverbs 4 in the TOMA
Proverbs 4 in the TTENT
Proverbs 4 in the UBG
Proverbs 4 in the UGV
Proverbs 4 in the UGV2
Proverbs 4 in the UGV3
Proverbs 4 in the VBL
Proverbs 4 in the VDCC
Proverbs 4 in the YALU
Proverbs 4 in the YAPE
Proverbs 4 in the YBVTP
Proverbs 4 in the ZBP