Proverbs 5 (BOGWICC)

1 Mwana wanga, mvetsera bwino za nzeru zimene ndikukuwuzazi,tchera khutu ku mawu odziwitsa bwino zinthu ndikukupatsa, 2 kuti uthe kuchita zinthu mochenjera ndi mwanzerundiponso kuti utetezedwe ku mayankhulidwe a mkazi wachilendo. 3 Pakuti mkazi wachigololo ali ndi mawu okoma ngati uchi.Zoyankhula zake ndi zosalala ngati mafuta, 4 koma kotsirizira kwake ngowawa ngati ndulu;ngakuthwa ngati lupanga lakuthwa konsekonse. 5 Mapazi ake amatsikira ku imfa;akamayenda ndiye kuti akupita ku manda. 6 Iye saganizirapo za njira ya moyo;njira zake ndi zokhotakhota koma iye sadziwa izi. 7 Tsopano ana inu, mundimvere;musawasiye mawu anga. 8 Uziyenda kutali ndi mkazi wotereyo,usayandikire khomo la nyumba yake, 9 kuopa kuti ungadzalanditse ulemerero wako kwa anthu ena;ndi zaka zako kwa anthu ankhanza, 10 kapenanso alendo angadyerere chuma chakondi phindu la ntchito yako kulemeretsa anthu ena. 11 Potsiriza pa moyo wako udzabuwula,thupi lako lonse litatheratu. 12 Ndipo udzati, “Mayo ine, ndinkadana ndi kusunga mwambo!Mtima wanga unkanyoza chidzudzulo! 13 Sindinamvere aphunzitsi angakapena alangizi anga. 14 Ine ndatsala pangʼono kuti ndiwonongekepakati pa msonkhano wonse.” 15 Imwa madzi a mʼchitsime chakochako,madzi abwino ochokera mʼchitsime chako. 16 Kodi akasupe ako azingosefukira mʼmisewu?Kodi mitsinje yako izingoyendayenda mʼzipata za mzinda? 17 Mitsinjeyo ikhale ya iwe wekha,osati uyigawireko alendo. 18 Yehova adalitse kasupe wako,ndipo usangalale ndi mkazi wa unyamata wako. 19 Iye uja ali ngati mbalale yayikazi yokongola ndiponso ngati gwape wa maonekedwe abwino.Ukhutitsidwe ndi mawere ake nthawi zonse,ndipo utengeke ndi chikondi chake nthawi zonse. 20 Mwana wanga, nʼchifukwa chiyani ukukopeka ndi mkazi wachigololo?Bwanji ukukumbatira mkazi wachilendo? 21 Pakuti mayendedwe onse a munthu Yehova amawaona,ndipo Iye amapenyetsetsa njira zake zonse. 22 Ntchito zoyipa za munthu woyipa zimamukola yekha;zingwe za tchimo lake zimamumanga yekha. 23 Iye adzafa chifukwa chosowa mwambo,adzasocheretsedwa chifukwa cha uchitsiru wake waukulu.

In Other Versions

Proverbs 5 in the ANGEFD

Proverbs 5 in the ANTPNG2D

Proverbs 5 in the AS21

Proverbs 5 in the BAGH

Proverbs 5 in the BBPNG

Proverbs 5 in the BBT1E

Proverbs 5 in the BDS

Proverbs 5 in the BEV

Proverbs 5 in the BHAD

Proverbs 5 in the BIB

Proverbs 5 in the BLPT

Proverbs 5 in the BNT

Proverbs 5 in the BNTABOOT

Proverbs 5 in the BNTLV

Proverbs 5 in the BOATCB

Proverbs 5 in the BOATCB2

Proverbs 5 in the BOBCV

Proverbs 5 in the BOCNT

Proverbs 5 in the BOECS

Proverbs 5 in the BOHCB

Proverbs 5 in the BOHCV

Proverbs 5 in the BOHLNT

Proverbs 5 in the BOHNTLTAL

Proverbs 5 in the BOICB

Proverbs 5 in the BOILNTAP

Proverbs 5 in the BOITCV

Proverbs 5 in the BOKCV

Proverbs 5 in the BOKCV2

Proverbs 5 in the BOKHWOG

Proverbs 5 in the BOKSSV

Proverbs 5 in the BOLCB

Proverbs 5 in the BOLCB2

Proverbs 5 in the BOMCV

Proverbs 5 in the BONAV

Proverbs 5 in the BONCB

Proverbs 5 in the BONLT

Proverbs 5 in the BONUT2

Proverbs 5 in the BOPLNT

Proverbs 5 in the BOSCB

Proverbs 5 in the BOSNC

Proverbs 5 in the BOTLNT

Proverbs 5 in the BOVCB

Proverbs 5 in the BOYCB

Proverbs 5 in the BPBB

Proverbs 5 in the BPH

Proverbs 5 in the BSB

Proverbs 5 in the CCB

Proverbs 5 in the CUV

Proverbs 5 in the CUVS

Proverbs 5 in the DBT

Proverbs 5 in the DGDNT

Proverbs 5 in the DHNT

Proverbs 5 in the DNT

Proverbs 5 in the ELBE

Proverbs 5 in the EMTV

Proverbs 5 in the ESV

Proverbs 5 in the FBV

Proverbs 5 in the FEB

Proverbs 5 in the GGMNT

Proverbs 5 in the GNT

Proverbs 5 in the HARY

Proverbs 5 in the HNT

Proverbs 5 in the IRVA

Proverbs 5 in the IRVB

Proverbs 5 in the IRVG

Proverbs 5 in the IRVH

Proverbs 5 in the IRVK

Proverbs 5 in the IRVM

Proverbs 5 in the IRVM2

Proverbs 5 in the IRVO

Proverbs 5 in the IRVP

Proverbs 5 in the IRVT

Proverbs 5 in the IRVT2

Proverbs 5 in the IRVU

Proverbs 5 in the ISVN

Proverbs 5 in the JSNT

Proverbs 5 in the KAPI

Proverbs 5 in the KBT1ETNIK

Proverbs 5 in the KBV

Proverbs 5 in the KJV

Proverbs 5 in the KNFD

Proverbs 5 in the LBA

Proverbs 5 in the LBLA

Proverbs 5 in the LNT

Proverbs 5 in the LSV

Proverbs 5 in the MAAL

Proverbs 5 in the MBV

Proverbs 5 in the MBV2

Proverbs 5 in the MHNT

Proverbs 5 in the MKNFD

Proverbs 5 in the MNG

Proverbs 5 in the MNT

Proverbs 5 in the MNT2

Proverbs 5 in the MRS1T

Proverbs 5 in the NAA

Proverbs 5 in the NASB

Proverbs 5 in the NBLA

Proverbs 5 in the NBS

Proverbs 5 in the NBVTP

Proverbs 5 in the NET2

Proverbs 5 in the NIV11

Proverbs 5 in the NNT

Proverbs 5 in the NNT2

Proverbs 5 in the NNT3

Proverbs 5 in the PDDPT

Proverbs 5 in the PFNT

Proverbs 5 in the RMNT

Proverbs 5 in the SBIAS

Proverbs 5 in the SBIBS

Proverbs 5 in the SBIBS2

Proverbs 5 in the SBICS

Proverbs 5 in the SBIDS

Proverbs 5 in the SBIGS

Proverbs 5 in the SBIHS

Proverbs 5 in the SBIIS

Proverbs 5 in the SBIIS2

Proverbs 5 in the SBIIS3

Proverbs 5 in the SBIKS

Proverbs 5 in the SBIKS2

Proverbs 5 in the SBIMS

Proverbs 5 in the SBIOS

Proverbs 5 in the SBIPS

Proverbs 5 in the SBISS

Proverbs 5 in the SBITS

Proverbs 5 in the SBITS2

Proverbs 5 in the SBITS3

Proverbs 5 in the SBITS4

Proverbs 5 in the SBIUS

Proverbs 5 in the SBIVS

Proverbs 5 in the SBT

Proverbs 5 in the SBT1E

Proverbs 5 in the SCHL

Proverbs 5 in the SNT

Proverbs 5 in the SUSU

Proverbs 5 in the SUSU2

Proverbs 5 in the SYNO

Proverbs 5 in the TBIAOTANT

Proverbs 5 in the TBT1E

Proverbs 5 in the TBT1E2

Proverbs 5 in the TFTIP

Proverbs 5 in the TFTU

Proverbs 5 in the TGNTATF3T

Proverbs 5 in the THAI

Proverbs 5 in the TNFD

Proverbs 5 in the TNT

Proverbs 5 in the TNTIK

Proverbs 5 in the TNTIL

Proverbs 5 in the TNTIN

Proverbs 5 in the TNTIP

Proverbs 5 in the TNTIZ

Proverbs 5 in the TOMA

Proverbs 5 in the TTENT

Proverbs 5 in the UBG

Proverbs 5 in the UGV

Proverbs 5 in the UGV2

Proverbs 5 in the UGV3

Proverbs 5 in the VBL

Proverbs 5 in the VDCC

Proverbs 5 in the YALU

Proverbs 5 in the YAPE

Proverbs 5 in the YBVTP

Proverbs 5 in the ZBP