Psalms 31 (BOGWICC)
undefined Kwa mtsogoleri wa mayimbidwe. Salimo la Davide. 1 Mwa Inu Yehova, ine ndimathawiramo;musalole nʼkomwe kuti ndichititsidwe manyazi;mundipulumutse chifukwa cha chilungamo chanu. 2 Tcherani khutu lanu kwa ine,bwerani msanga kudzandilanditsa;mukhale thanthwe langa lothawirapo,linga lolimba kundipulumutsa ine. 3 Popeza Inu ndinu thanthwe langa ndi linga langa,chifukwa cha dzina lanu tsogolereni ndi kundiwongolera. 4 Ndimasuleni mu msampha umene anditcherapakuti ndinu pothawirapo panga. 5 Mʼmanja mwanu ndipereka mzimu wanga;womboleni Yehova Mulungu wachoonadi. 6 Koma ine ndimadana nawo amene amamamatira mafano achabechabe;ine ndimadalira Yehova. 7 Ndidzakondwa ndi kusangalala mʼchikondi chanupopeza Inu munaona masautso angandipo mumadziwa kuwawa kwa moyo wanga. 8 Inu simunandipereke kwa mdanikoma mwayika mapazi anga pa malo otakasuka. 9 Mundichitire chifundo Inu Yehova pakuti ndili pa mavuto;maso anga akulefuka ndi chisoni,mʼmoyo mwanga ndi mʼthupi mwanga momwe mukupweteka. 10 Moyo wanga ukunyeka chifukwa cha kuwawidwa mtimandi zaka zanga chifukwa cha kubuwula;mphamvu zanga zatha chifuwa cha masautso,ndipo mafupa anga akulefuka. 11 Chifukwa cha adani anga onse,ndine wonyozeka kwambiri ndi anansi anga;ndine chochititsa manyazi kwa abwenzi anga.Iwo amene amandiona mu msewu amandithawa. 12 Ine ndinayiwalika kwa iwo ngati kuti ndinamwalira;ndakhala ngati mʼphika wosweka. 13 Pakuti ine ndamva zonena zoyipa za anthu ambiri;zoopsa zandizungulira mbali zonse;iwo akukonza chiwembu kuti alimbane nane,kuti atenge moyo wanga. 14 Koma ndikudalira Inu Yehova;ndikunena kuti, “Ndinu Mulungu wanga.” 15 Masiku anga ali mʼmanja mwanu;ndipulumutseni kwa adani angandi kwa iwo amene akundithamangitsa. 16 Walitsani nkhope yanu pa mtumiki wanu;pulumutseni mwa chikondi chanu chosatha. 17 Yehova musalole kuti ndichite manyazi,pakuti ndalirira kwa Inu;koma oyipa achititsidwe manyazindipo agone chete mʼmanda. 18 Milomo yawo yabodzayo ikhale chete,pakuti chifukwa cha kunyadaayankhula modzikuza kutsutsana ndi wolungama. 19 Ndi waukulu ubwino wanuumene mwawasungira amene amakuopani,umene mumapereka anthu akuonakwa iwo amene amathawira kwa Inu. 20 Mu mthunzi wa pamalo popezeka panu muwabisa,kuwateteza ku ziwembu za anthu;mʼmalo anu okhalamo mumawatetezakwa anthu owatsutsa. 21 Matamando akhale kwa Yehova,pakuti anaonetsa chikondi chake chodabwitsa kwa inepamene ndinali mu mzinda wozingidwa. 22 Ndili mʼnkhawa zanga ndinati,“Ine ndachotsedwa pamaso panu!”Komabe Inu munamva kupempha chifundo kwangapamene ndinapempha thandizo kwa Inu. 23 Kondani Yehova oyera mtima ake onse!Yehova amasunga wokhulupirikakoma amalanga kwathunthu anthu odzikuza. 24 Khalani ndi nyonga ndipo limbani mtima,inu nonse amene mumayembekezera Yehova.
In Other Versions
Psalms 31 in the ANGEFD
Psalms 31 in the ANTPNG2D
Psalms 31 in the AS21
Psalms 31 in the BAGH
Psalms 31 in the BBPNG
Psalms 31 in the BBT1E
Psalms 31 in the BDS
Psalms 31 in the BEV
Psalms 31 in the BHAD
Psalms 31 in the BIB
Psalms 31 in the BLPT
Psalms 31 in the BNT
Psalms 31 in the BNTABOOT
Psalms 31 in the BNTLV
Psalms 31 in the BOATCB
Psalms 31 in the BOATCB2
Psalms 31 in the BOBCV
Psalms 31 in the BOCNT
Psalms 31 in the BOECS
Psalms 31 in the BOHCB
Psalms 31 in the BOHCV
Psalms 31 in the BOHLNT
Psalms 31 in the BOHNTLTAL
Psalms 31 in the BOICB
Psalms 31 in the BOILNTAP
Psalms 31 in the BOITCV
Psalms 31 in the BOKCV
Psalms 31 in the BOKCV2
Psalms 31 in the BOKHWOG
Psalms 31 in the BOKSSV
Psalms 31 in the BOLCB
Psalms 31 in the BOLCB2
Psalms 31 in the BOMCV
Psalms 31 in the BONAV
Psalms 31 in the BONCB
Psalms 31 in the BONLT
Psalms 31 in the BONUT2
Psalms 31 in the BOPLNT
Psalms 31 in the BOSCB
Psalms 31 in the BOSNC
Psalms 31 in the BOTLNT
Psalms 31 in the BOVCB
Psalms 31 in the BOYCB
Psalms 31 in the BPBB
Psalms 31 in the BPH
Psalms 31 in the BSB
Psalms 31 in the CCB
Psalms 31 in the CUV
Psalms 31 in the CUVS
Psalms 31 in the DBT
Psalms 31 in the DGDNT
Psalms 31 in the DHNT
Psalms 31 in the DNT
Psalms 31 in the ELBE
Psalms 31 in the EMTV
Psalms 31 in the ESV
Psalms 31 in the FBV
Psalms 31 in the FEB
Psalms 31 in the GGMNT
Psalms 31 in the GNT
Psalms 31 in the HARY
Psalms 31 in the HNT
Psalms 31 in the IRVA
Psalms 31 in the IRVB
Psalms 31 in the IRVG
Psalms 31 in the IRVH
Psalms 31 in the IRVK
Psalms 31 in the IRVM
Psalms 31 in the IRVM2
Psalms 31 in the IRVO
Psalms 31 in the IRVP
Psalms 31 in the IRVT
Psalms 31 in the IRVT2
Psalms 31 in the IRVU
Psalms 31 in the ISVN
Psalms 31 in the JSNT
Psalms 31 in the KAPI
Psalms 31 in the KBT1ETNIK
Psalms 31 in the KBV
Psalms 31 in the KJV
Psalms 31 in the KNFD
Psalms 31 in the LBA
Psalms 31 in the LBLA
Psalms 31 in the LNT
Psalms 31 in the LSV
Psalms 31 in the MAAL
Psalms 31 in the MBV
Psalms 31 in the MBV2
Psalms 31 in the MHNT
Psalms 31 in the MKNFD
Psalms 31 in the MNG
Psalms 31 in the MNT
Psalms 31 in the MNT2
Psalms 31 in the MRS1T
Psalms 31 in the NAA
Psalms 31 in the NASB
Psalms 31 in the NBLA
Psalms 31 in the NBS
Psalms 31 in the NBVTP
Psalms 31 in the NET2
Psalms 31 in the NIV11
Psalms 31 in the NNT
Psalms 31 in the NNT2
Psalms 31 in the NNT3
Psalms 31 in the PDDPT
Psalms 31 in the PFNT
Psalms 31 in the RMNT
Psalms 31 in the SBIAS
Psalms 31 in the SBIBS
Psalms 31 in the SBIBS2
Psalms 31 in the SBICS
Psalms 31 in the SBIDS
Psalms 31 in the SBIGS
Psalms 31 in the SBIHS
Psalms 31 in the SBIIS
Psalms 31 in the SBIIS2
Psalms 31 in the SBIIS3
Psalms 31 in the SBIKS
Psalms 31 in the SBIKS2
Psalms 31 in the SBIMS
Psalms 31 in the SBIOS
Psalms 31 in the SBIPS
Psalms 31 in the SBISS
Psalms 31 in the SBITS
Psalms 31 in the SBITS2
Psalms 31 in the SBITS3
Psalms 31 in the SBITS4
Psalms 31 in the SBIUS
Psalms 31 in the SBIVS
Psalms 31 in the SBT
Psalms 31 in the SBT1E
Psalms 31 in the SCHL
Psalms 31 in the SNT
Psalms 31 in the SUSU
Psalms 31 in the SUSU2
Psalms 31 in the SYNO
Psalms 31 in the TBIAOTANT
Psalms 31 in the TBT1E
Psalms 31 in the TBT1E2
Psalms 31 in the TFTIP
Psalms 31 in the TFTU
Psalms 31 in the TGNTATF3T
Psalms 31 in the THAI
Psalms 31 in the TNFD
Psalms 31 in the TNT
Psalms 31 in the TNTIK
Psalms 31 in the TNTIL
Psalms 31 in the TNTIN
Psalms 31 in the TNTIP
Psalms 31 in the TNTIZ
Psalms 31 in the TOMA
Psalms 31 in the TTENT
Psalms 31 in the UBG
Psalms 31 in the UGV
Psalms 31 in the UGV2
Psalms 31 in the UGV3
Psalms 31 in the VBL
Psalms 31 in the VDCC
Psalms 31 in the YALU
Psalms 31 in the YAPE
Psalms 31 in the YBVTP
Psalms 31 in the ZBP