Revelation 12 (BOGWICC)
1 Chizindikiro chachikulu chinaoneka kuthambo; mayi atavala dzuwa, mapazi ake ataponda mwezi, pamutu pake pali chipewa chaufumu chokhala ndi nyenyezi khumi ndi ziwiri. 2 Mayiyo anali woyembekezera ndipo pa nthawi yake yochira analira mokuwa chifukwa cha ululu wakubala. 3 Kenaka ku thambo kunaonekanso chizindikiro china; chinjoka chachikulu kwambiri, chofiira chomwe chinali ndi mitu isanu ndi iwiri ndi nyanga khumi; pamutu uliwonse chitavala chipewa chaufumu. 4 Mchira wake unakokolola gawo limodzi la magawo atatu a nyenyezi kuzichotsa ku thambo ndi kuziponya pa dziko lapansi. Chinjoka chija chinadzayima patsogolo pa mayi uja amene anali pafupi kuberekayu kuti mwanayo akangobadwa chimudye. 5 Mayiyo anabereka mwana wamwamuna amene adzalamulira anthu a mitundu ina yonse ndi ndodo yachitsulo. Ndipo mwanayo analandidwa ku dzanja la mayiyo ndi kupita naye kwa Mulungu ku mpando wake waufumu. 6 Mayiyo anathawira ku chipululu ku malo kumene Mulungu anamukonzera, kumene akasamalidweko masiku 1,260. 7 Zitatero, kumwamba kunayambika nkhondo. Mikayeli ndi angelo ake kumenyana ndi chinjoka chija. Chinjokacho ndi angelo ake anabwezeranso. 8 Koma analibe mphamvu ndipo anagonjetsedwa nathamangitsidwa kumwambako. 9 Chinjoka chachikulu chija chinagwetsedwa pansi. Ichocho ndiye njoka yakalekale ija yotchedwa Mdierekezi kapena Satana, amene amasocheretsa anthu a pa dziko lonse lapansi. Chinaponyedwa pa dziko la pansi pamodzi ndi angelo ake. 10 Kenaka ndinamva mawu ofuwula kumwamba akunena kuti,“Tsopano chipulumutso, mphamvu,ufumu wa Mulungu wathundi ulamuliro wa Khristu wake zabwera.Pakuti woneneza abale athu uja,amene amangokhalira kuwaneneza pamaso pa Mulungu usana ndi usiku,wagwetsedwa pansi. 11 Abale athuwo anamugonjetsandi magazi a Mwana Wankhosandiponso mawu a umboni wawo.Iwo anadzipereka kwathunthu,moti sanakonde miyoyo yawo. 12 Choncho, kondwerani, inu dziko lakumwambandi onse okhala kumeneko!Koma tsoka dziko lapansi ndi nyanjachifukwa Mdierekezi wagwetsedwa kwa inu!Iye wadzazidwa ndi ukalichifukwa akudziwa kuti nthawi yake ndi yochepa.” 13 Pamene chinjokacho chinaona kuti chagwetsedwa pa dziko lapansi, chinayamba kuthamangitsa mayi uja amene anali atabala mwana wamwamunayu. 14 Mayiyo anapatsidwa mapiko awiri a chiwombankhanga chachikulu kuti athawire ku malo ake aja a ku chipululu. Kumeneko adzasamalidwako zaka zitatu ndi theka kuti chinjoka chija chisamupeze. 15 Kenaka chinjoka chija chinalavulira mayiyo madzi ambiri ngati mtsinje, kuti madziwo amukokolole. 16 Koma dziko lapansi linamuthandiza mayiyo. Nthaka inatsekuka ndi kumeza mtsinje uja unachokera mʼkamwa mwa chinjokacho. 17 Pamenepo chinjokacho chinamupsera mtima mayiyo ndipo chinachoka kupita kukachita nkhondo ndi ana ena onse a mayiyo, ndiye kuti anthu amene anasunga malamulo a Mulungu ndi kuchitira umboni za Yesu. 18 Kenaka ndinaona chinjokacho chitayima mʼmbali mwa nyanja.
In Other Versions
Revelation 12 in the ANGEFD
Revelation 12 in the ANTPNG2D
Revelation 12 in the AS21
Revelation 12 in the BAGH
Revelation 12 in the BBPNG
Revelation 12 in the BBT1E
Revelation 12 in the BDS
Revelation 12 in the BEV
Revelation 12 in the BHAD
Revelation 12 in the BIB
Revelation 12 in the BLPT
Revelation 12 in the BNT
Revelation 12 in the BNTABOOT
Revelation 12 in the BNTLV
Revelation 12 in the BOATCB
Revelation 12 in the BOATCB2
Revelation 12 in the BOBCV
Revelation 12 in the BOCNT
Revelation 12 in the BOECS
Revelation 12 in the BOHCB
Revelation 12 in the BOHCV
Revelation 12 in the BOHLNT
Revelation 12 in the BOHNTLTAL
Revelation 12 in the BOICB
Revelation 12 in the BOILNTAP
Revelation 12 in the BOITCV
Revelation 12 in the BOKCV
Revelation 12 in the BOKCV2
Revelation 12 in the BOKHWOG
Revelation 12 in the BOKSSV
Revelation 12 in the BOLCB
Revelation 12 in the BOLCB2
Revelation 12 in the BOMCV
Revelation 12 in the BONAV
Revelation 12 in the BONCB
Revelation 12 in the BONLT
Revelation 12 in the BONUT2
Revelation 12 in the BOPLNT
Revelation 12 in the BOSCB
Revelation 12 in the BOSNC
Revelation 12 in the BOTLNT
Revelation 12 in the BOVCB
Revelation 12 in the BOYCB
Revelation 12 in the BPBB
Revelation 12 in the BPH
Revelation 12 in the BSB
Revelation 12 in the CCB
Revelation 12 in the CUV
Revelation 12 in the CUVS
Revelation 12 in the DBT
Revelation 12 in the DGDNT
Revelation 12 in the DHNT
Revelation 12 in the DNT
Revelation 12 in the ELBE
Revelation 12 in the EMTV
Revelation 12 in the ESV
Revelation 12 in the FBV
Revelation 12 in the FEB
Revelation 12 in the GGMNT
Revelation 12 in the GNT
Revelation 12 in the HARY
Revelation 12 in the HNT
Revelation 12 in the IRVA
Revelation 12 in the IRVB
Revelation 12 in the IRVG
Revelation 12 in the IRVH
Revelation 12 in the IRVK
Revelation 12 in the IRVM
Revelation 12 in the IRVM2
Revelation 12 in the IRVO
Revelation 12 in the IRVP
Revelation 12 in the IRVT
Revelation 12 in the IRVT2
Revelation 12 in the IRVU
Revelation 12 in the ISVN
Revelation 12 in the JSNT
Revelation 12 in the KAPI
Revelation 12 in the KBT1ETNIK
Revelation 12 in the KBV
Revelation 12 in the KJV
Revelation 12 in the KNFD
Revelation 12 in the LBA
Revelation 12 in the LBLA
Revelation 12 in the LNT
Revelation 12 in the LSV
Revelation 12 in the MAAL
Revelation 12 in the MBV
Revelation 12 in the MBV2
Revelation 12 in the MHNT
Revelation 12 in the MKNFD
Revelation 12 in the MNG
Revelation 12 in the MNT
Revelation 12 in the MNT2
Revelation 12 in the MRS1T
Revelation 12 in the NAA
Revelation 12 in the NASB
Revelation 12 in the NBLA
Revelation 12 in the NBS
Revelation 12 in the NBVTP
Revelation 12 in the NET2
Revelation 12 in the NIV11
Revelation 12 in the NNT
Revelation 12 in the NNT2
Revelation 12 in the NNT3
Revelation 12 in the PDDPT
Revelation 12 in the PFNT
Revelation 12 in the RMNT
Revelation 12 in the SBIAS
Revelation 12 in the SBIBS
Revelation 12 in the SBIBS2
Revelation 12 in the SBICS
Revelation 12 in the SBIDS
Revelation 12 in the SBIGS
Revelation 12 in the SBIHS
Revelation 12 in the SBIIS
Revelation 12 in the SBIIS2
Revelation 12 in the SBIIS3
Revelation 12 in the SBIKS
Revelation 12 in the SBIKS2
Revelation 12 in the SBIMS
Revelation 12 in the SBIOS
Revelation 12 in the SBIPS
Revelation 12 in the SBISS
Revelation 12 in the SBITS
Revelation 12 in the SBITS2
Revelation 12 in the SBITS3
Revelation 12 in the SBITS4
Revelation 12 in the SBIUS
Revelation 12 in the SBIVS
Revelation 12 in the SBT
Revelation 12 in the SBT1E
Revelation 12 in the SCHL
Revelation 12 in the SNT
Revelation 12 in the SUSU
Revelation 12 in the SUSU2
Revelation 12 in the SYNO
Revelation 12 in the TBIAOTANT
Revelation 12 in the TBT1E
Revelation 12 in the TBT1E2
Revelation 12 in the TFTIP
Revelation 12 in the TFTU
Revelation 12 in the TGNTATF3T
Revelation 12 in the THAI
Revelation 12 in the TNFD
Revelation 12 in the TNT
Revelation 12 in the TNTIK
Revelation 12 in the TNTIL
Revelation 12 in the TNTIN
Revelation 12 in the TNTIP
Revelation 12 in the TNTIZ
Revelation 12 in the TOMA
Revelation 12 in the TTENT
Revelation 12 in the UBG
Revelation 12 in the UGV
Revelation 12 in the UGV2
Revelation 12 in the UGV3
Revelation 12 in the VBL
Revelation 12 in the VDCC
Revelation 12 in the YALU
Revelation 12 in the YAPE
Revelation 12 in the YBVTP
Revelation 12 in the ZBP