1 Corinthians 5 (BOGWICC)
1 Mbiri yamveka kuti pakati panu pakuchitika chigololo. Ndipo chigololo cha mtunduwu ngakhale pakati pa akunja sichingapezeke; munthu akumagonana ndi mkazi wa abambo ake. 2 Ndipo inu mukudzitukumulabe. Kodi simukanayenera kudzazidwa ndi chisoni ndipo mukanamuchotsa pa chiyanjano chanu munthu wochita zimenezi? 3 Ngakhale sindili nanu mʼthupi, ndili nanu mu mzimu. Ndipo ineyo ndapereka kale chiweruzo pa munthu amene amachita zotere, ngati kuti ndili komweko. 4 Mukasonkhana mu dzina la Ambuye athu Yesu, ine ndili nanu mu mzimu, ndipo mphamvu ya Ambuye athu Yesu ili pomwepo, 5 mumupereke munthuyu kwa Satana, kuti chikhalidwe chake cha uchimo chiwonongedwe ndikuti mzimu wake udzapulumuke pa tsiku la Ambuye. 6 Kudziwa kwanu si kwabwino. Kodi simukudziwa kuti yisiti wochepa amafufumitsa mphumphu yaufa wonse wa tirigu? 7 Chotsani yisiti wakale kuti mukhale ndi mphumphu yopanda yisiti, monga inu muli. Pakuti Khristu, Mwana Wankhosa wa Paska wathu, anaperekedwa nsembe. 8 Choncho, tiyeni tisunge chikondwererochi, osati ndi yisiti wakale, wowononga ndi woyipa, koma ndi buledi wopanda yisiti, buledi woona mtima ndi choonadi. 9 Ndakulemberani mʼkalata yanga kuti musayanjane nawo anthu achigololo. 10 Pamenepatu sindikutanthauzatu anthu a dziko lapansi lino amene ndi achigololo, kapena aumbombo, kapena opeza ndalama mwachinyengo, kapena opembedza mafano. Kukanatero mukanangochoka mʼdziko lapansi lino. 11 Koma tsopano ndikukulemberani kuti musayanjane ndi aliyense amene adzitcha mʼbale koma ndi wachigololo, kapena waumbombo, kapena wopembedza mafano, kapena wonamizira anzake, woledzera kapena wopeza ndalama mwachinyengo. Munthu wotere ngakhale kudya, osadya naye pamodzi. 12 Kodi ndipindulanji kuti ndiweruze anthu amene si a mu mpingo? Kodi simuyenera kuweruza iwo amene ali mu mpingo? 13 Mulungu adzaweruza akunja. “Chotsani woyipayo pakati panu.”
In Other Versions
1 Corinthians 5 in the ANGEFD
1 Corinthians 5 in the ANTPNG2D
1 Corinthians 5 in the AS21
1 Corinthians 5 in the BAGH
1 Corinthians 5 in the BBPNG
1 Corinthians 5 in the BBT1E
1 Corinthians 5 in the BDS
1 Corinthians 5 in the BEV
1 Corinthians 5 in the BHAD
1 Corinthians 5 in the BIB
1 Corinthians 5 in the BLPT
1 Corinthians 5 in the BNT
1 Corinthians 5 in the BNTABOOT
1 Corinthians 5 in the BNTLV
1 Corinthians 5 in the BOATCB
1 Corinthians 5 in the BOATCB2
1 Corinthians 5 in the BOBCV
1 Corinthians 5 in the BOCNT
1 Corinthians 5 in the BOECS
1 Corinthians 5 in the BOHCB
1 Corinthians 5 in the BOHCV
1 Corinthians 5 in the BOHLNT
1 Corinthians 5 in the BOHNTLTAL
1 Corinthians 5 in the BOICB
1 Corinthians 5 in the BOILNTAP
1 Corinthians 5 in the BOITCV
1 Corinthians 5 in the BOKCV
1 Corinthians 5 in the BOKCV2
1 Corinthians 5 in the BOKHWOG
1 Corinthians 5 in the BOKSSV
1 Corinthians 5 in the BOLCB
1 Corinthians 5 in the BOLCB2
1 Corinthians 5 in the BOMCV
1 Corinthians 5 in the BONAV
1 Corinthians 5 in the BONCB
1 Corinthians 5 in the BONLT
1 Corinthians 5 in the BONUT2
1 Corinthians 5 in the BOPLNT
1 Corinthians 5 in the BOSCB
1 Corinthians 5 in the BOSNC
1 Corinthians 5 in the BOTLNT
1 Corinthians 5 in the BOVCB
1 Corinthians 5 in the BOYCB
1 Corinthians 5 in the BPBB
1 Corinthians 5 in the BPH
1 Corinthians 5 in the BSB
1 Corinthians 5 in the CCB
1 Corinthians 5 in the CUV
1 Corinthians 5 in the CUVS
1 Corinthians 5 in the DBT
1 Corinthians 5 in the DGDNT
1 Corinthians 5 in the DHNT
1 Corinthians 5 in the DNT
1 Corinthians 5 in the ELBE
1 Corinthians 5 in the EMTV
1 Corinthians 5 in the ESV
1 Corinthians 5 in the FBV
1 Corinthians 5 in the FEB
1 Corinthians 5 in the GGMNT
1 Corinthians 5 in the GNT
1 Corinthians 5 in the HARY
1 Corinthians 5 in the HNT
1 Corinthians 5 in the IRVA
1 Corinthians 5 in the IRVB
1 Corinthians 5 in the IRVG
1 Corinthians 5 in the IRVH
1 Corinthians 5 in the IRVK
1 Corinthians 5 in the IRVM
1 Corinthians 5 in the IRVM2
1 Corinthians 5 in the IRVO
1 Corinthians 5 in the IRVP
1 Corinthians 5 in the IRVT
1 Corinthians 5 in the IRVT2
1 Corinthians 5 in the IRVU
1 Corinthians 5 in the ISVN
1 Corinthians 5 in the JSNT
1 Corinthians 5 in the KAPI
1 Corinthians 5 in the KBT1ETNIK
1 Corinthians 5 in the KBV
1 Corinthians 5 in the KJV
1 Corinthians 5 in the KNFD
1 Corinthians 5 in the LBA
1 Corinthians 5 in the LBLA
1 Corinthians 5 in the LNT
1 Corinthians 5 in the LSV
1 Corinthians 5 in the MAAL
1 Corinthians 5 in the MBV
1 Corinthians 5 in the MBV2
1 Corinthians 5 in the MHNT
1 Corinthians 5 in the MKNFD
1 Corinthians 5 in the MNG
1 Corinthians 5 in the MNT
1 Corinthians 5 in the MNT2
1 Corinthians 5 in the MRS1T
1 Corinthians 5 in the NAA
1 Corinthians 5 in the NASB
1 Corinthians 5 in the NBLA
1 Corinthians 5 in the NBS
1 Corinthians 5 in the NBVTP
1 Corinthians 5 in the NET2
1 Corinthians 5 in the NIV11
1 Corinthians 5 in the NNT
1 Corinthians 5 in the NNT2
1 Corinthians 5 in the NNT3
1 Corinthians 5 in the PDDPT
1 Corinthians 5 in the PFNT
1 Corinthians 5 in the RMNT
1 Corinthians 5 in the SBIAS
1 Corinthians 5 in the SBIBS
1 Corinthians 5 in the SBIBS2
1 Corinthians 5 in the SBICS
1 Corinthians 5 in the SBIDS
1 Corinthians 5 in the SBIGS
1 Corinthians 5 in the SBIHS
1 Corinthians 5 in the SBIIS
1 Corinthians 5 in the SBIIS2
1 Corinthians 5 in the SBIIS3
1 Corinthians 5 in the SBIKS
1 Corinthians 5 in the SBIKS2
1 Corinthians 5 in the SBIMS
1 Corinthians 5 in the SBIOS
1 Corinthians 5 in the SBIPS
1 Corinthians 5 in the SBISS
1 Corinthians 5 in the SBITS
1 Corinthians 5 in the SBITS2
1 Corinthians 5 in the SBITS3
1 Corinthians 5 in the SBITS4
1 Corinthians 5 in the SBIUS
1 Corinthians 5 in the SBIVS
1 Corinthians 5 in the SBT
1 Corinthians 5 in the SBT1E
1 Corinthians 5 in the SCHL
1 Corinthians 5 in the SNT
1 Corinthians 5 in the SUSU
1 Corinthians 5 in the SUSU2
1 Corinthians 5 in the SYNO
1 Corinthians 5 in the TBIAOTANT
1 Corinthians 5 in the TBT1E
1 Corinthians 5 in the TBT1E2
1 Corinthians 5 in the TFTIP
1 Corinthians 5 in the TFTU
1 Corinthians 5 in the TGNTATF3T
1 Corinthians 5 in the THAI
1 Corinthians 5 in the TNFD
1 Corinthians 5 in the TNT
1 Corinthians 5 in the TNTIK
1 Corinthians 5 in the TNTIL
1 Corinthians 5 in the TNTIN
1 Corinthians 5 in the TNTIP
1 Corinthians 5 in the TNTIZ
1 Corinthians 5 in the TOMA
1 Corinthians 5 in the TTENT
1 Corinthians 5 in the UBG
1 Corinthians 5 in the UGV
1 Corinthians 5 in the UGV2
1 Corinthians 5 in the UGV3
1 Corinthians 5 in the VBL
1 Corinthians 5 in the VDCC
1 Corinthians 5 in the YALU
1 Corinthians 5 in the YAPE
1 Corinthians 5 in the YBVTP
1 Corinthians 5 in the ZBP