1 Corinthians 8 (BOGWICC)
1 Tsopano za chakudya choperekedwa nsembe kwa mafano: Ife tidziwa kuti tonse tili ndi chidziwitso. Komatu chidziwitso chokha chimadzitukumula, koma chikondi ndicho chimapindulitsa. 2 Munthu amene amaganiza kuti amadziwa kanthu, ndiye kuti sakudziwa monga mmene amayenera kudziwira. 3 Koma munthu amene amakonda Mulungu amadziwika ndi Mulunguyo. 4 Choncho kunena za chakudya choperekedwa nsembe kwa mafano; ife tikudziwa kuti mafano si kanthu nʼpangʼonongʼono pomwe pa dziko lapansi, ndiponso kuti palibe Mulungu wina koma mmodzi yekha. 5 Popeza kuti ngakhale pali yotchedwa milungu, kaya ndi kumwamba kapena pa dziko lapansi (poti ilipodi milungu yambirimbiri ndi ambuye ambirimbiri), 6 koma kwa ife pali Mulungu mmodzi yekha, Atate, zinthu zonse zinachokera mwa Iye ndipo ndife ake. Komanso pali Ambuye mmodzi Yesu Khristu kumene zinthu zonse zinachokera ndipo mwa Iye ife tili ndi moyo. 7 Koma saliyense amadziwa zimenezi. Alipo ena ozolowera mafano kwambiri mwakuti akadya chakudya chotere amaganiza kuti chakudyacho chinaperekedwa nsembe kwa mafano. Ndiye poti chikumbumtima chawo nʼchofowoka chimadetsedwadi. 8 Koma chakudya sichitisendeza kufupi ndi Mulungu. Tikapanda kudya si vuto, tikadya sitisinthikanso. 9 Komabe samalani kuti ufulu wanu ochita zinthu usafike pokhumudwitsa ofowoka. 10 Pakuti ngati aliyense wachikumbumtima chofowoka akakuonani achidziwitsonu mukudya mʼnyumba yopembedzera mafano, kodi iyeyo sichidzamulimbitsa mtima kuti azidya chakudya choperekedwa nsembe kwa mafano? 11 Kotero kuti chifukwa cha chidziwitso chanu mʼbale wofowokayu amene chifukwa cha iye, Khristu anafa, wawonongeka chifukwa cha chidziwitso chanu. 12 Mukamachimwira abale anu motere ndikuwawonongera chikumbumtima chawo chofowokacho, mukuchimwira Khristu. 13 Nʼchifukwa chake ngati zimene ine ndimadya zichititsa mʼbale wanga kugwa mu tchimo, sindidzadyanso chakudyacho kuti mʼbaleyo ndisamuchimwitse.
In Other Versions
1 Corinthians 8 in the ANGEFD
1 Corinthians 8 in the ANTPNG2D
1 Corinthians 8 in the AS21
1 Corinthians 8 in the BAGH
1 Corinthians 8 in the BBPNG
1 Corinthians 8 in the BBT1E
1 Corinthians 8 in the BDS
1 Corinthians 8 in the BEV
1 Corinthians 8 in the BHAD
1 Corinthians 8 in the BIB
1 Corinthians 8 in the BLPT
1 Corinthians 8 in the BNT
1 Corinthians 8 in the BNTABOOT
1 Corinthians 8 in the BNTLV
1 Corinthians 8 in the BOATCB
1 Corinthians 8 in the BOATCB2
1 Corinthians 8 in the BOBCV
1 Corinthians 8 in the BOCNT
1 Corinthians 8 in the BOECS
1 Corinthians 8 in the BOHCB
1 Corinthians 8 in the BOHCV
1 Corinthians 8 in the BOHLNT
1 Corinthians 8 in the BOHNTLTAL
1 Corinthians 8 in the BOICB
1 Corinthians 8 in the BOILNTAP
1 Corinthians 8 in the BOITCV
1 Corinthians 8 in the BOKCV
1 Corinthians 8 in the BOKCV2
1 Corinthians 8 in the BOKHWOG
1 Corinthians 8 in the BOKSSV
1 Corinthians 8 in the BOLCB
1 Corinthians 8 in the BOLCB2
1 Corinthians 8 in the BOMCV
1 Corinthians 8 in the BONAV
1 Corinthians 8 in the BONCB
1 Corinthians 8 in the BONLT
1 Corinthians 8 in the BONUT2
1 Corinthians 8 in the BOPLNT
1 Corinthians 8 in the BOSCB
1 Corinthians 8 in the BOSNC
1 Corinthians 8 in the BOTLNT
1 Corinthians 8 in the BOVCB
1 Corinthians 8 in the BOYCB
1 Corinthians 8 in the BPBB
1 Corinthians 8 in the BPH
1 Corinthians 8 in the BSB
1 Corinthians 8 in the CCB
1 Corinthians 8 in the CUV
1 Corinthians 8 in the CUVS
1 Corinthians 8 in the DBT
1 Corinthians 8 in the DGDNT
1 Corinthians 8 in the DHNT
1 Corinthians 8 in the DNT
1 Corinthians 8 in the ELBE
1 Corinthians 8 in the EMTV
1 Corinthians 8 in the ESV
1 Corinthians 8 in the FBV
1 Corinthians 8 in the FEB
1 Corinthians 8 in the GGMNT
1 Corinthians 8 in the GNT
1 Corinthians 8 in the HARY
1 Corinthians 8 in the HNT
1 Corinthians 8 in the IRVA
1 Corinthians 8 in the IRVB
1 Corinthians 8 in the IRVG
1 Corinthians 8 in the IRVH
1 Corinthians 8 in the IRVK
1 Corinthians 8 in the IRVM
1 Corinthians 8 in the IRVM2
1 Corinthians 8 in the IRVO
1 Corinthians 8 in the IRVP
1 Corinthians 8 in the IRVT
1 Corinthians 8 in the IRVT2
1 Corinthians 8 in the IRVU
1 Corinthians 8 in the ISVN
1 Corinthians 8 in the JSNT
1 Corinthians 8 in the KAPI
1 Corinthians 8 in the KBT1ETNIK
1 Corinthians 8 in the KBV
1 Corinthians 8 in the KJV
1 Corinthians 8 in the KNFD
1 Corinthians 8 in the LBA
1 Corinthians 8 in the LBLA
1 Corinthians 8 in the LNT
1 Corinthians 8 in the LSV
1 Corinthians 8 in the MAAL
1 Corinthians 8 in the MBV
1 Corinthians 8 in the MBV2
1 Corinthians 8 in the MHNT
1 Corinthians 8 in the MKNFD
1 Corinthians 8 in the MNG
1 Corinthians 8 in the MNT
1 Corinthians 8 in the MNT2
1 Corinthians 8 in the MRS1T
1 Corinthians 8 in the NAA
1 Corinthians 8 in the NASB
1 Corinthians 8 in the NBLA
1 Corinthians 8 in the NBS
1 Corinthians 8 in the NBVTP
1 Corinthians 8 in the NET2
1 Corinthians 8 in the NIV11
1 Corinthians 8 in the NNT
1 Corinthians 8 in the NNT2
1 Corinthians 8 in the NNT3
1 Corinthians 8 in the PDDPT
1 Corinthians 8 in the PFNT
1 Corinthians 8 in the RMNT
1 Corinthians 8 in the SBIAS
1 Corinthians 8 in the SBIBS
1 Corinthians 8 in the SBIBS2
1 Corinthians 8 in the SBICS
1 Corinthians 8 in the SBIDS
1 Corinthians 8 in the SBIGS
1 Corinthians 8 in the SBIHS
1 Corinthians 8 in the SBIIS
1 Corinthians 8 in the SBIIS2
1 Corinthians 8 in the SBIIS3
1 Corinthians 8 in the SBIKS
1 Corinthians 8 in the SBIKS2
1 Corinthians 8 in the SBIMS
1 Corinthians 8 in the SBIOS
1 Corinthians 8 in the SBIPS
1 Corinthians 8 in the SBISS
1 Corinthians 8 in the SBITS
1 Corinthians 8 in the SBITS2
1 Corinthians 8 in the SBITS3
1 Corinthians 8 in the SBITS4
1 Corinthians 8 in the SBIUS
1 Corinthians 8 in the SBIVS
1 Corinthians 8 in the SBT
1 Corinthians 8 in the SBT1E
1 Corinthians 8 in the SCHL
1 Corinthians 8 in the SNT
1 Corinthians 8 in the SUSU
1 Corinthians 8 in the SUSU2
1 Corinthians 8 in the SYNO
1 Corinthians 8 in the TBIAOTANT
1 Corinthians 8 in the TBT1E
1 Corinthians 8 in the TBT1E2
1 Corinthians 8 in the TFTIP
1 Corinthians 8 in the TFTU
1 Corinthians 8 in the TGNTATF3T
1 Corinthians 8 in the THAI
1 Corinthians 8 in the TNFD
1 Corinthians 8 in the TNT
1 Corinthians 8 in the TNTIK
1 Corinthians 8 in the TNTIL
1 Corinthians 8 in the TNTIN
1 Corinthians 8 in the TNTIP
1 Corinthians 8 in the TNTIZ
1 Corinthians 8 in the TOMA
1 Corinthians 8 in the TTENT
1 Corinthians 8 in the UBG
1 Corinthians 8 in the UGV
1 Corinthians 8 in the UGV2
1 Corinthians 8 in the UGV3
1 Corinthians 8 in the VBL
1 Corinthians 8 in the VDCC
1 Corinthians 8 in the YALU
1 Corinthians 8 in the YAPE
1 Corinthians 8 in the YBVTP
1 Corinthians 8 in the ZBP