2 Thessalonians 1 (BOGWICC)

1 Paulo, Silivano ndi Timoteyo.Kulembera mpingo wa ku Tesalonika, umene uli mwa Mulungu Atate athu ndi Ambuye Yesu Khristu. 2 Chisomo ndi mtendere kwa inu kuchokera kwa Mulungu Atate ndi Ambuye Yesu Khristu. 3 Ife tiyenera kuyamika Mulungu nthawi zonse chifukwa cha inu abale. Ndipo tiyenera kutero chifukwa chikhulupiriro chanu chikukulirakulirabe, ndiponso chikondi chimene aliyense wa inu ali nacho pa mnzake chikuchulukirachulukirabe. 4 Nʼchifukwa chake, timayankhula monyadira mʼmipingo yonse ya Mulungu za kupirira kwanu ndi chikhulupiriro chanu pakati pa masautso onse ndi mayesero amene mukudutsamo. 5 Zonsezi zikutsimikiza kuti Mulungu amaweruza molungama. Zotsatira zake ndi zakuti mudzatengedwa kukhala oyenera kulowa mu ufumu wa Mulungu umene mukuwuvutikira. 6 Mulungu ndi wolungama ndipo adzalanga amene amakusautsaniwo 7 ndikukupatsani mpumulo amene mukusautsidwa, pamodzi ndi ifenso. Izi zidzachitika Ambuye Yesu akadzaoneka mʼmalawi amoto kuchokera kumwamba pamodzi ndi angelo ake amphamvu. 8 Iye adzalanga amene sadziwa Mulungu ndi amene samvera Uthenga Wabwino wa Ambuye athu Yesu. 9 Adzalangidwa ndi chiwonongeko chamuyaya ndipo sadzaonanso nkhope ya Ambuye ndi ulemerero wamphamvu zake 10 pa tsiku limene iye adzabwera kudzalemekezedwa mwa oyera mtima ndi kuyamikidwa ndi onse amene anakhulupirira. Inu mudzakhala nawo mʼgulumo chifukwa munakhulupirira umboni wathu. 11 Nʼchifukwa chake timakupemphererani nthawi zonse, kuti Mulungu wathu akusandutseni oyenera mayitanidwe ake, ndi kuti mwa mphamvu zake akwaniritse cholinga chanu chilichonse chabwino ndi chilichonse chochitika mwachikhulupiriro. 12 Ife timapempherera zimenezi kuti dzina la Ambuye athu Yesu lilemekezedwe mwa inu, ndi inu mulemekezedwe mwa Iyeyo. Zonsezi zidzachitika chifukwa cha chisomo cha Mulungu wathu ndi Ambuye Yesu Khristu.

In Other Versions

2 Thessalonians 1 in the ANGEFD

2 Thessalonians 1 in the ANTPNG2D

2 Thessalonians 1 in the AS21

2 Thessalonians 1 in the BAGH

2 Thessalonians 1 in the BBPNG

2 Thessalonians 1 in the BBT1E

2 Thessalonians 1 in the BDS

2 Thessalonians 1 in the BEV

2 Thessalonians 1 in the BHAD

2 Thessalonians 1 in the BIB

2 Thessalonians 1 in the BLPT

2 Thessalonians 1 in the BNT

2 Thessalonians 1 in the BNTABOOT

2 Thessalonians 1 in the BNTLV

2 Thessalonians 1 in the BOATCB

2 Thessalonians 1 in the BOATCB2

2 Thessalonians 1 in the BOBCV

2 Thessalonians 1 in the BOCNT

2 Thessalonians 1 in the BOECS

2 Thessalonians 1 in the BOHCB

2 Thessalonians 1 in the BOHCV

2 Thessalonians 1 in the BOHLNT

2 Thessalonians 1 in the BOHNTLTAL

2 Thessalonians 1 in the BOICB

2 Thessalonians 1 in the BOILNTAP

2 Thessalonians 1 in the BOITCV

2 Thessalonians 1 in the BOKCV

2 Thessalonians 1 in the BOKCV2

2 Thessalonians 1 in the BOKHWOG

2 Thessalonians 1 in the BOKSSV

2 Thessalonians 1 in the BOLCB

2 Thessalonians 1 in the BOLCB2

2 Thessalonians 1 in the BOMCV

2 Thessalonians 1 in the BONAV

2 Thessalonians 1 in the BONCB

2 Thessalonians 1 in the BONLT

2 Thessalonians 1 in the BONUT2

2 Thessalonians 1 in the BOPLNT

2 Thessalonians 1 in the BOSCB

2 Thessalonians 1 in the BOSNC

2 Thessalonians 1 in the BOTLNT

2 Thessalonians 1 in the BOVCB

2 Thessalonians 1 in the BOYCB

2 Thessalonians 1 in the BPBB

2 Thessalonians 1 in the BPH

2 Thessalonians 1 in the BSB

2 Thessalonians 1 in the CCB

2 Thessalonians 1 in the CUV

2 Thessalonians 1 in the CUVS

2 Thessalonians 1 in the DBT

2 Thessalonians 1 in the DGDNT

2 Thessalonians 1 in the DHNT

2 Thessalonians 1 in the DNT

2 Thessalonians 1 in the ELBE

2 Thessalonians 1 in the EMTV

2 Thessalonians 1 in the ESV

2 Thessalonians 1 in the FBV

2 Thessalonians 1 in the FEB

2 Thessalonians 1 in the GGMNT

2 Thessalonians 1 in the GNT

2 Thessalonians 1 in the HARY

2 Thessalonians 1 in the HNT

2 Thessalonians 1 in the IRVA

2 Thessalonians 1 in the IRVB

2 Thessalonians 1 in the IRVG

2 Thessalonians 1 in the IRVH

2 Thessalonians 1 in the IRVK

2 Thessalonians 1 in the IRVM

2 Thessalonians 1 in the IRVM2

2 Thessalonians 1 in the IRVO

2 Thessalonians 1 in the IRVP

2 Thessalonians 1 in the IRVT

2 Thessalonians 1 in the IRVT2

2 Thessalonians 1 in the IRVU

2 Thessalonians 1 in the ISVN

2 Thessalonians 1 in the JSNT

2 Thessalonians 1 in the KAPI

2 Thessalonians 1 in the KBT1ETNIK

2 Thessalonians 1 in the KBV

2 Thessalonians 1 in the KJV

2 Thessalonians 1 in the KNFD

2 Thessalonians 1 in the LBA

2 Thessalonians 1 in the LBLA

2 Thessalonians 1 in the LNT

2 Thessalonians 1 in the LSV

2 Thessalonians 1 in the MAAL

2 Thessalonians 1 in the MBV

2 Thessalonians 1 in the MBV2

2 Thessalonians 1 in the MHNT

2 Thessalonians 1 in the MKNFD

2 Thessalonians 1 in the MNG

2 Thessalonians 1 in the MNT

2 Thessalonians 1 in the MNT2

2 Thessalonians 1 in the MRS1T

2 Thessalonians 1 in the NAA

2 Thessalonians 1 in the NASB

2 Thessalonians 1 in the NBLA

2 Thessalonians 1 in the NBS

2 Thessalonians 1 in the NBVTP

2 Thessalonians 1 in the NET2

2 Thessalonians 1 in the NIV11

2 Thessalonians 1 in the NNT

2 Thessalonians 1 in the NNT2

2 Thessalonians 1 in the NNT3

2 Thessalonians 1 in the PDDPT

2 Thessalonians 1 in the PFNT

2 Thessalonians 1 in the RMNT

2 Thessalonians 1 in the SBIAS

2 Thessalonians 1 in the SBIBS

2 Thessalonians 1 in the SBIBS2

2 Thessalonians 1 in the SBICS

2 Thessalonians 1 in the SBIDS

2 Thessalonians 1 in the SBIGS

2 Thessalonians 1 in the SBIHS

2 Thessalonians 1 in the SBIIS

2 Thessalonians 1 in the SBIIS2

2 Thessalonians 1 in the SBIIS3

2 Thessalonians 1 in the SBIKS

2 Thessalonians 1 in the SBIKS2

2 Thessalonians 1 in the SBIMS

2 Thessalonians 1 in the SBIOS

2 Thessalonians 1 in the SBIPS

2 Thessalonians 1 in the SBISS

2 Thessalonians 1 in the SBITS

2 Thessalonians 1 in the SBITS2

2 Thessalonians 1 in the SBITS3

2 Thessalonians 1 in the SBITS4

2 Thessalonians 1 in the SBIUS

2 Thessalonians 1 in the SBIVS

2 Thessalonians 1 in the SBT

2 Thessalonians 1 in the SBT1E

2 Thessalonians 1 in the SCHL

2 Thessalonians 1 in the SNT

2 Thessalonians 1 in the SUSU

2 Thessalonians 1 in the SUSU2

2 Thessalonians 1 in the SYNO

2 Thessalonians 1 in the TBIAOTANT

2 Thessalonians 1 in the TBT1E

2 Thessalonians 1 in the TBT1E2

2 Thessalonians 1 in the TFTIP

2 Thessalonians 1 in the TFTU

2 Thessalonians 1 in the TGNTATF3T

2 Thessalonians 1 in the THAI

2 Thessalonians 1 in the TNFD

2 Thessalonians 1 in the TNT

2 Thessalonians 1 in the TNTIK

2 Thessalonians 1 in the TNTIL

2 Thessalonians 1 in the TNTIN

2 Thessalonians 1 in the TNTIP

2 Thessalonians 1 in the TNTIZ

2 Thessalonians 1 in the TOMA

2 Thessalonians 1 in the TTENT

2 Thessalonians 1 in the UBG

2 Thessalonians 1 in the UGV

2 Thessalonians 1 in the UGV2

2 Thessalonians 1 in the UGV3

2 Thessalonians 1 in the VBL

2 Thessalonians 1 in the VDCC

2 Thessalonians 1 in the YALU

2 Thessalonians 1 in the YAPE

2 Thessalonians 1 in the YBVTP

2 Thessalonians 1 in the ZBP