Deuteronomy 24 (BOGWICC)

1 Ngati mwamuna wakwatira mkazi amene sakukondwera naye chifukwa wapeza vuto pa mkaziyo, namulembera mkaziyo kalata ya chisudzulo, namupatsa ndi kumutulutsa mʼnyumba mwake, 2 mkaziyo ndi kukakwatiwa ndi mwamuna wina, 3 ndipo mwamuna wachiwiriyo nʼkuyipidwa nayenso ndi kumulemberanso kalata ya chisudzulo nʼkumutulutsa mʼnyumba mwake, kapena ngati mwamunayo amwalira, 4 mwamuna wake woyamba uja, amene anamuleka saloledwanso kumukwatira kachiwiri popeza mkaziyo wadetsedwa. Chimenechi ndi chonyansa pamaso pa Yehova. Musalowetse tchimo mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani ngati cholowa chanu. 5 Mwamuna akangokwatira kumene asamatumizidwe ku nkhondo kapena kupatsidwa ntchito ina iliyonse. Kwa chaka chathunthu akhale ndi ufulu wokhala pa khomo pake kumasangalatsa mkazi wakeyo. 6 Munthu akakhala nanu ndi ngongole musamutengere mwala wake wa mphero ngati chikole, chifukwa kutero nʼkumutengera moyo kukhala chikole cha ngongole. 7 Ngati munthu agwidwa akuba mʼbale wake wa Chiisraeli namamuzunza ngati kapolo kapena kumugulitsa, wogulitsa mnzakeyo ayenera kuphedwa. Muyenera kuchotsa choyipa pakati panu. 8 Pakagwa matenda a khate, samalitsani kuchita zonse zimene ansembe, amene ndi Alevi, anakulangizani. Mutsatire mosamalitsa zimene ndinawalamula. 9 Kumbukirani zimene Yehova Mulungu wanu anachita kwa Miriamu muli paulendo mutatuluka mu Igupto. 10 Ukabwereketsa mnzako kanthu kena kalikonse, usalowe mʼnyumba mwake kukatenga chimene wachipereka ngati chikole. 11 Uziyima kunja kwa nyumba kuti munthu amene wamubwereketsa kanthuyo akubweretsere kunja komweko. 12 Ngati munthuyo ndi wosauka, usamutengere chikolecho mpaka kukagona nacho kwanu. 13 Pomalowa dzuwa ukhale utamubwezera mkanjo wakewo kuti akafunde. Pamenepo adzakuthokoza, ndipo amenewa adzawerengedwa ngati machitidwe olungama kwa iweyo pamaso pa Yehova Mulungu wako. 14 Osamapezera mwayi pa anthu aganyu osauka ndi aumphawi, kaya ndi Mwisraeli kapena mlendo wokhala mu umodzi mwa mizinda yanu. 15 Mumulipire malipiro ake a tsiku dzuwa lisanalowe chifukwa ndi wosauka ndipo akudalira malipirowo. Kupanda kutero adzakudandaulirani kwa Yehova ndipo mudzapezeka ochimwa. 16 Makolo asaphedwe chifukwa cha ana awo, ndipo ana asaphedwe chifukwa cha makolo awo, koma aliyense ayenera kufa chifukwa cha zolakwa zake. 17 Musachitire mlendo kapena mwana wamasiye zoyipa, kapena kulanda mkazi wamasiye chovala ngati chikole cha ngongole. 18 Kumbukirani kuti munali akapolo mʼdziko la Igupto ndipo Yehova Mulungu wanu anakuwombolani kumeneko. Nʼchifukwa chake ndikukulamulani kuti muzichita zimenezi. 19 Mukamakolola mʼmunda mwanu ndipo zokolola zina zikasiyidwa, musamabwerere kukazitola. Muzilekere alendo, ana ndi akazi amasiye, kuti Yehova Mulungu wanu akudalitseni pa zochita zanu zonse. 20 Mukathyola zipatso mu mtengo wa olivi, musamabwererenso kachiwiri ku mtengo womwewo. Zotsalazo zilekereni alendo, ana ndi akazi amasiye. 21 Mukakolola mphesa mʼmunda mwanu musamabwereremonso kachiwiri. Zotsalazo muzilekere alendo, ana ndi akazi amasiye. 22 Kumbukirani kuti munali akapolo mʼdziko la Igupto. Nʼchifukwa chake ndikukulamulani kuti muzichita zimenezi.

In Other Versions

Deuteronomy 24 in the ANGEFD

Deuteronomy 24 in the ANTPNG2D

Deuteronomy 24 in the AS21

Deuteronomy 24 in the BAGH

Deuteronomy 24 in the BBPNG

Deuteronomy 24 in the BBT1E

Deuteronomy 24 in the BDS

Deuteronomy 24 in the BEV

Deuteronomy 24 in the BHAD

Deuteronomy 24 in the BIB

Deuteronomy 24 in the BLPT

Deuteronomy 24 in the BNT

Deuteronomy 24 in the BNTABOOT

Deuteronomy 24 in the BNTLV

Deuteronomy 24 in the BOATCB

Deuteronomy 24 in the BOATCB2

Deuteronomy 24 in the BOBCV

Deuteronomy 24 in the BOCNT

Deuteronomy 24 in the BOECS

Deuteronomy 24 in the BOHCB

Deuteronomy 24 in the BOHCV

Deuteronomy 24 in the BOHLNT

Deuteronomy 24 in the BOHNTLTAL

Deuteronomy 24 in the BOICB

Deuteronomy 24 in the BOILNTAP

Deuteronomy 24 in the BOITCV

Deuteronomy 24 in the BOKCV

Deuteronomy 24 in the BOKCV2

Deuteronomy 24 in the BOKHWOG

Deuteronomy 24 in the BOKSSV

Deuteronomy 24 in the BOLCB

Deuteronomy 24 in the BOLCB2

Deuteronomy 24 in the BOMCV

Deuteronomy 24 in the BONAV

Deuteronomy 24 in the BONCB

Deuteronomy 24 in the BONLT

Deuteronomy 24 in the BONUT2

Deuteronomy 24 in the BOPLNT

Deuteronomy 24 in the BOSCB

Deuteronomy 24 in the BOSNC

Deuteronomy 24 in the BOTLNT

Deuteronomy 24 in the BOVCB

Deuteronomy 24 in the BOYCB

Deuteronomy 24 in the BPBB

Deuteronomy 24 in the BPH

Deuteronomy 24 in the BSB

Deuteronomy 24 in the CCB

Deuteronomy 24 in the CUV

Deuteronomy 24 in the CUVS

Deuteronomy 24 in the DBT

Deuteronomy 24 in the DGDNT

Deuteronomy 24 in the DHNT

Deuteronomy 24 in the DNT

Deuteronomy 24 in the ELBE

Deuteronomy 24 in the EMTV

Deuteronomy 24 in the ESV

Deuteronomy 24 in the FBV

Deuteronomy 24 in the FEB

Deuteronomy 24 in the GGMNT

Deuteronomy 24 in the GNT

Deuteronomy 24 in the HARY

Deuteronomy 24 in the HNT

Deuteronomy 24 in the IRVA

Deuteronomy 24 in the IRVB

Deuteronomy 24 in the IRVG

Deuteronomy 24 in the IRVH

Deuteronomy 24 in the IRVK

Deuteronomy 24 in the IRVM

Deuteronomy 24 in the IRVM2

Deuteronomy 24 in the IRVO

Deuteronomy 24 in the IRVP

Deuteronomy 24 in the IRVT

Deuteronomy 24 in the IRVT2

Deuteronomy 24 in the IRVU

Deuteronomy 24 in the ISVN

Deuteronomy 24 in the JSNT

Deuteronomy 24 in the KAPI

Deuteronomy 24 in the KBT1ETNIK

Deuteronomy 24 in the KBV

Deuteronomy 24 in the KJV

Deuteronomy 24 in the KNFD

Deuteronomy 24 in the LBA

Deuteronomy 24 in the LBLA

Deuteronomy 24 in the LNT

Deuteronomy 24 in the LSV

Deuteronomy 24 in the MAAL

Deuteronomy 24 in the MBV

Deuteronomy 24 in the MBV2

Deuteronomy 24 in the MHNT

Deuteronomy 24 in the MKNFD

Deuteronomy 24 in the MNG

Deuteronomy 24 in the MNT

Deuteronomy 24 in the MNT2

Deuteronomy 24 in the MRS1T

Deuteronomy 24 in the NAA

Deuteronomy 24 in the NASB

Deuteronomy 24 in the NBLA

Deuteronomy 24 in the NBS

Deuteronomy 24 in the NBVTP

Deuteronomy 24 in the NET2

Deuteronomy 24 in the NIV11

Deuteronomy 24 in the NNT

Deuteronomy 24 in the NNT2

Deuteronomy 24 in the NNT3

Deuteronomy 24 in the PDDPT

Deuteronomy 24 in the PFNT

Deuteronomy 24 in the RMNT

Deuteronomy 24 in the SBIAS

Deuteronomy 24 in the SBIBS

Deuteronomy 24 in the SBIBS2

Deuteronomy 24 in the SBICS

Deuteronomy 24 in the SBIDS

Deuteronomy 24 in the SBIGS

Deuteronomy 24 in the SBIHS

Deuteronomy 24 in the SBIIS

Deuteronomy 24 in the SBIIS2

Deuteronomy 24 in the SBIIS3

Deuteronomy 24 in the SBIKS

Deuteronomy 24 in the SBIKS2

Deuteronomy 24 in the SBIMS

Deuteronomy 24 in the SBIOS

Deuteronomy 24 in the SBIPS

Deuteronomy 24 in the SBISS

Deuteronomy 24 in the SBITS

Deuteronomy 24 in the SBITS2

Deuteronomy 24 in the SBITS3

Deuteronomy 24 in the SBITS4

Deuteronomy 24 in the SBIUS

Deuteronomy 24 in the SBIVS

Deuteronomy 24 in the SBT

Deuteronomy 24 in the SBT1E

Deuteronomy 24 in the SCHL

Deuteronomy 24 in the SNT

Deuteronomy 24 in the SUSU

Deuteronomy 24 in the SUSU2

Deuteronomy 24 in the SYNO

Deuteronomy 24 in the TBIAOTANT

Deuteronomy 24 in the TBT1E

Deuteronomy 24 in the TBT1E2

Deuteronomy 24 in the TFTIP

Deuteronomy 24 in the TFTU

Deuteronomy 24 in the TGNTATF3T

Deuteronomy 24 in the THAI

Deuteronomy 24 in the TNFD

Deuteronomy 24 in the TNT

Deuteronomy 24 in the TNTIK

Deuteronomy 24 in the TNTIL

Deuteronomy 24 in the TNTIN

Deuteronomy 24 in the TNTIP

Deuteronomy 24 in the TNTIZ

Deuteronomy 24 in the TOMA

Deuteronomy 24 in the TTENT

Deuteronomy 24 in the UBG

Deuteronomy 24 in the UGV

Deuteronomy 24 in the UGV2

Deuteronomy 24 in the UGV3

Deuteronomy 24 in the VBL

Deuteronomy 24 in the VDCC

Deuteronomy 24 in the YALU

Deuteronomy 24 in the YAPE

Deuteronomy 24 in the YBVTP

Deuteronomy 24 in the ZBP