Hosea 10 (BOGWICC)
1 Israeli anali mpesa wotambalala;anabereka zipatso zambiri.Pamene zipatso zawo zinanka zichuluka,anawonjezera kumanga maguwa ansembe.Pamene dziko lake linkatukuka,anakongoletsa miyala yake yopatulika. 2 Mtima wawo ndi wonyengandipo tsopano ayenera kulangidwa chifukwa cha kulakwa kwawo.Yehova adzagumula maguwa awo ansembendi kuwononga miyala yawo yopatulika. 3 Pamenepo anthuwo adzanena kuti, “Ife tilibe mfumuchifukwa sitinaope Yehova.Koma ngakhale tikanakhala ndi mfumu,kodi mfumuyo ikanatichitira chiyani?” 4 Mafumu amalonjeza zambiri,amalumbira zabodzapochita mapangano.Kotero maweruzo amaphukangati zitsamba zakupha mʼmunda umene walimidwa. 5 Anthu amene amakhala mu Samariya akuchita manthachifukwa cha fano la mwana wangʼombe ku Beti-Aveni.Anthu ake adzalirira fanolo,chimodzimodzinso ansembe ake adamawo,amene anakondwera ndi kukongola kwake,chifukwa lachotsedwa pakati pawo ndi kupita ku ukapolo. 6 Fanolo lidzatengedwa kupita ku Asiriyangati mphatso kwa mfumu yayikulu.Efereimu adzachititsidwa manyazichifukwa cha mafano ake amitengo. 7 Samariya ndi mfumu yake adzatengedwa kupita kutalingati kanthambi koyenda pa madzi. 8 Malo opembedzerako mafano a ku Aveni adzawonongedwa.Ili ndiye tchimo la Israeli.Minga ndi mitungwi zidzamerandi kuphimba maguwa awo ansembe.Kenaka anthu adzawuza mapiri kuti, “Tiphimbeni!”ndipo adzawuza zitunda kuti, “Tigwereni!” 9 “Iwe Israeli, wachimwa kuyambira mʼmasiku a Gibeya,ndipo wakhala uli pomwepo.Kodi nkhondo sinagonjetse anthuochita zoyipa ku Gibeya? 10 Pamene ndifunire, ndidzalanga anthuwo;mitundu ya anthu idzasonkhanitsidwa kudzalimbana nawo,kuwayika mʼndende chifukwa cha uchimo wawo waukulu. 11 Efereimu ndi mwana wangʼombe wamkazi wophunzitsidwaamene amakonda kupuntha tirigu,choncho Ine ndidzayika golimʼkhosi lake lokongolalo.Ndidzasenzetsa Efereimu goli,Yuda ayenera kulima,ndipo Yakobo ayenera kutipula. 12 Mufese nokha chilungamondipo mudzakolola chipatso cha chikondi changa chosasinthika.Ndipo tipulani munda wanu wosalimidwawo;pakuti ino ndi nthawi yofunafuna Yehova,mpaka Iye atabwerakudzakugwetserani mivumbi ya chilungamo. 13 Koma inu munadzala zolakwa,mwakolola zoyipa;mwadya chipatso cha chinyengo.Chifukwa mumadalira mphamvu zanundiponso ankhondo anu ochulukawo, 14 phokoso lankhondo lidzamveka pakati pa anthu angakotero kuti malinga anu onse adzawonongeka,monga momwe Salimani anawonongera Beti-Aribeli pa nthawi ya nkhondo;pamene anapha amayi pamodzi ndi ana awo omwe. 15 Momwemonso zidzakuchitikira, iwe Betelichifukwa kuyipa kwako ndi kwakukulu.Tsiku limeneli likadzafika,mfumu ya Israeli idzawonongedwa kwathunthu.
In Other Versions
Hosea 10 in the ANGEFD
Hosea 10 in the ANTPNG2D
Hosea 10 in the AS21
Hosea 10 in the BAGH
Hosea 10 in the BBPNG
Hosea 10 in the BBT1E
Hosea 10 in the BDS
Hosea 10 in the BEV
Hosea 10 in the BHAD
Hosea 10 in the BIB
Hosea 10 in the BLPT
Hosea 10 in the BNT
Hosea 10 in the BNTABOOT
Hosea 10 in the BNTLV
Hosea 10 in the BOATCB
Hosea 10 in the BOATCB2
Hosea 10 in the BOBCV
Hosea 10 in the BOCNT
Hosea 10 in the BOECS
Hosea 10 in the BOHCB
Hosea 10 in the BOHCV
Hosea 10 in the BOHLNT
Hosea 10 in the BOHNTLTAL
Hosea 10 in the BOICB
Hosea 10 in the BOILNTAP
Hosea 10 in the BOITCV
Hosea 10 in the BOKCV
Hosea 10 in the BOKCV2
Hosea 10 in the BOKHWOG
Hosea 10 in the BOKSSV
Hosea 10 in the BOLCB
Hosea 10 in the BOLCB2
Hosea 10 in the BOMCV
Hosea 10 in the BONAV
Hosea 10 in the BONCB
Hosea 10 in the BONLT
Hosea 10 in the BONUT2
Hosea 10 in the BOPLNT
Hosea 10 in the BOSCB
Hosea 10 in the BOSNC
Hosea 10 in the BOTLNT
Hosea 10 in the BOVCB
Hosea 10 in the BOYCB
Hosea 10 in the BPBB
Hosea 10 in the BPH
Hosea 10 in the BSB
Hosea 10 in the CCB
Hosea 10 in the CUV
Hosea 10 in the CUVS
Hosea 10 in the DBT
Hosea 10 in the DGDNT
Hosea 10 in the DHNT
Hosea 10 in the DNT
Hosea 10 in the ELBE
Hosea 10 in the EMTV
Hosea 10 in the ESV
Hosea 10 in the FBV
Hosea 10 in the FEB
Hosea 10 in the GGMNT
Hosea 10 in the GNT
Hosea 10 in the HARY
Hosea 10 in the HNT
Hosea 10 in the IRVA
Hosea 10 in the IRVB
Hosea 10 in the IRVG
Hosea 10 in the IRVH
Hosea 10 in the IRVK
Hosea 10 in the IRVM
Hosea 10 in the IRVM2
Hosea 10 in the IRVO
Hosea 10 in the IRVP
Hosea 10 in the IRVT
Hosea 10 in the IRVT2
Hosea 10 in the IRVU
Hosea 10 in the ISVN
Hosea 10 in the JSNT
Hosea 10 in the KAPI
Hosea 10 in the KBT1ETNIK
Hosea 10 in the KBV
Hosea 10 in the KJV
Hosea 10 in the KNFD
Hosea 10 in the LBA
Hosea 10 in the LBLA
Hosea 10 in the LNT
Hosea 10 in the LSV
Hosea 10 in the MAAL
Hosea 10 in the MBV
Hosea 10 in the MBV2
Hosea 10 in the MHNT
Hosea 10 in the MKNFD
Hosea 10 in the MNG
Hosea 10 in the MNT
Hosea 10 in the MNT2
Hosea 10 in the MRS1T
Hosea 10 in the NAA
Hosea 10 in the NASB
Hosea 10 in the NBLA
Hosea 10 in the NBS
Hosea 10 in the NBVTP
Hosea 10 in the NET2
Hosea 10 in the NIV11
Hosea 10 in the NNT
Hosea 10 in the NNT2
Hosea 10 in the NNT3
Hosea 10 in the PDDPT
Hosea 10 in the PFNT
Hosea 10 in the RMNT
Hosea 10 in the SBIAS
Hosea 10 in the SBIBS
Hosea 10 in the SBIBS2
Hosea 10 in the SBICS
Hosea 10 in the SBIDS
Hosea 10 in the SBIGS
Hosea 10 in the SBIHS
Hosea 10 in the SBIIS
Hosea 10 in the SBIIS2
Hosea 10 in the SBIIS3
Hosea 10 in the SBIKS
Hosea 10 in the SBIKS2
Hosea 10 in the SBIMS
Hosea 10 in the SBIOS
Hosea 10 in the SBIPS
Hosea 10 in the SBISS
Hosea 10 in the SBITS
Hosea 10 in the SBITS2
Hosea 10 in the SBITS3
Hosea 10 in the SBITS4
Hosea 10 in the SBIUS
Hosea 10 in the SBIVS
Hosea 10 in the SBT
Hosea 10 in the SBT1E
Hosea 10 in the SCHL
Hosea 10 in the SNT
Hosea 10 in the SUSU
Hosea 10 in the SUSU2
Hosea 10 in the SYNO
Hosea 10 in the TBIAOTANT
Hosea 10 in the TBT1E
Hosea 10 in the TBT1E2
Hosea 10 in the TFTIP
Hosea 10 in the TFTU
Hosea 10 in the TGNTATF3T
Hosea 10 in the THAI
Hosea 10 in the TNFD
Hosea 10 in the TNT
Hosea 10 in the TNTIK
Hosea 10 in the TNTIL
Hosea 10 in the TNTIN
Hosea 10 in the TNTIP
Hosea 10 in the TNTIZ
Hosea 10 in the TOMA
Hosea 10 in the TTENT
Hosea 10 in the UBG
Hosea 10 in the UGV
Hosea 10 in the UGV2
Hosea 10 in the UGV3
Hosea 10 in the VBL
Hosea 10 in the VDCC
Hosea 10 in the YALU
Hosea 10 in the YAPE
Hosea 10 in the YBVTP
Hosea 10 in the ZBP