Hosea 4 (BOGWICC)

1 Inu Aisraeli, imvani mawu a Yehova,chifukwa Yehova ali ndi mlandu ndi inuamene mumakhala mʼdzikoli:“Mʼdziko mwanu mulibe kukhulupirika, mulibe chikondimulibe kulabadira za Mulungu. 2 Muli kutemberera kokha, kunama ndi kupha.Kuba ndi kuchita chigololo;machimo achita kunyanyandipo akungokhalira kuphana. 3 Chifukwa chake dziko likulirandipo onse amene amakhalamo akuvutika;zirombo zakuthengo ndi mbalame zamumlengalengandiponso nsomba zamʼnyanja zikufa. 4 “Koma wina asapeze mnzake chifukwa,wina aliyense asayimbe mlandu mnzake,pakuti anthu ako ali ngati anthuamene amayimba mlandu wansembe. 5 Mumapunthwa usana ndi usikundipo aneneri amapunthwa nanu pamodzi.Choncho ndidzawononga amayi anu. 6 Anthu anga akuwonongeka chifukwa chosadziwa. “Pakuti mwakana kudziwa,Inenso ndidzakukanani monga ansembe anga;chifukwa mwayiwala lamulo la Mulungu wanu,Inenso ndidzayiwala ana anu. 7 Ansembe ankati akachulukaiwo ankandichimwiranso kwambiri;iwo anasinthanitsa ulemerero wawo ndi chinthu china chonyansa. 8 Amalemererapo pa machimo a anthu angandipo amafunitsitsa kuti anthuwo azipitiriza kuchimwa. 9 Ndipo zidzakhala motere: zochitikira anthu ena, zidzachitikiranso ansembe.Ndidzawalanga onsewo chifukwa cha njira zawo,ndidzawabwezera chifukwa cha machitidwe awo. 10 “Iwo azidzadya koma sadzakhuta;azidzachita zachiwerewere koma sadzachulukana,chifukwa anasiya Yehovakuti adzipereke 11 ku zachiwerewere,ku vinyo wakale ndi watsopano,zimene zimachotsa nzeru zomvetsa zinthu 12 za anthu anga.Anthu anga amapempha nzeru ku fano lamtengondipo ndodo yawo yamtengo imawayankha.Mzimu wachiwerewere umawasocheretsa;iwo sakukhulupirika kwa Mulungu wawo. 13 Amapereka nsembe pamwamba pa mapirindi kufukiza lubani pa zitunda,pa tsinde pa mtengo wa thundu, mnjale ndi mkundi,pamene pali mthunzi wabwino.Nʼchifukwa chake ana anu aakazi akuchita zachiwerewerendipo akazi a ana anu akuchita zigololo. 14 “Ine sindidzalanga ana anu aakazipamene iwo adzachita zachiwerewere,kapena akazi a ana anupamene adzachita zigololo.Paja inu nomwe amunanu mumayenda ndi akazi achiwerewere,ndipo mumapereka nsembe pamodzi ndi akazi achiwerewere a ku malo opembedzerako.Anthu amene alibe nzeru adzawonongeka ndithu! 15 “Ngakhale umachita chigololo, iwe Israeli,Yuda asapezeke ndi mlandu wotere. “Usapite ku Giligala.Usapite ku Beti-Aveni.Ndipo usalumbire kuti, ‘Pali Yehova wamoyo!’ 16 Aisraeli ndi nkhutukumve,ngosamva ngati ana angʼombe.Kodi Yehova angathe kuwaweta bwanjingati ana ankhosa pa msipu wabwino? 17 Efereimu waphathana ndi mafano;mulekeni! 18 Ngakhale pamene zakumwa zawo zatha,amapitiriza kuchita zachiwerewere;atsogoleri awo amakonda kwambiri njira zawo zochititsa manyazi. 19 Adzachotsedwa ndi kamvuluvulundipo adzachita manyazi chifukwa cha nsembe zawo.

In Other Versions

Hosea 4 in the ANGEFD

Hosea 4 in the ANTPNG2D

Hosea 4 in the AS21

Hosea 4 in the BAGH

Hosea 4 in the BBPNG

Hosea 4 in the BBT1E

Hosea 4 in the BDS

Hosea 4 in the BEV

Hosea 4 in the BHAD

Hosea 4 in the BIB

Hosea 4 in the BLPT

Hosea 4 in the BNT

Hosea 4 in the BNTABOOT

Hosea 4 in the BNTLV

Hosea 4 in the BOATCB

Hosea 4 in the BOATCB2

Hosea 4 in the BOBCV

Hosea 4 in the BOCNT

Hosea 4 in the BOECS

Hosea 4 in the BOHCB

Hosea 4 in the BOHCV

Hosea 4 in the BOHLNT

Hosea 4 in the BOHNTLTAL

Hosea 4 in the BOICB

Hosea 4 in the BOILNTAP

Hosea 4 in the BOITCV

Hosea 4 in the BOKCV

Hosea 4 in the BOKCV2

Hosea 4 in the BOKHWOG

Hosea 4 in the BOKSSV

Hosea 4 in the BOLCB

Hosea 4 in the BOLCB2

Hosea 4 in the BOMCV

Hosea 4 in the BONAV

Hosea 4 in the BONCB

Hosea 4 in the BONLT

Hosea 4 in the BONUT2

Hosea 4 in the BOPLNT

Hosea 4 in the BOSCB

Hosea 4 in the BOSNC

Hosea 4 in the BOTLNT

Hosea 4 in the BOVCB

Hosea 4 in the BOYCB

Hosea 4 in the BPBB

Hosea 4 in the BPH

Hosea 4 in the BSB

Hosea 4 in the CCB

Hosea 4 in the CUV

Hosea 4 in the CUVS

Hosea 4 in the DBT

Hosea 4 in the DGDNT

Hosea 4 in the DHNT

Hosea 4 in the DNT

Hosea 4 in the ELBE

Hosea 4 in the EMTV

Hosea 4 in the ESV

Hosea 4 in the FBV

Hosea 4 in the FEB

Hosea 4 in the GGMNT

Hosea 4 in the GNT

Hosea 4 in the HARY

Hosea 4 in the HNT

Hosea 4 in the IRVA

Hosea 4 in the IRVB

Hosea 4 in the IRVG

Hosea 4 in the IRVH

Hosea 4 in the IRVK

Hosea 4 in the IRVM

Hosea 4 in the IRVM2

Hosea 4 in the IRVO

Hosea 4 in the IRVP

Hosea 4 in the IRVT

Hosea 4 in the IRVT2

Hosea 4 in the IRVU

Hosea 4 in the ISVN

Hosea 4 in the JSNT

Hosea 4 in the KAPI

Hosea 4 in the KBT1ETNIK

Hosea 4 in the KBV

Hosea 4 in the KJV

Hosea 4 in the KNFD

Hosea 4 in the LBA

Hosea 4 in the LBLA

Hosea 4 in the LNT

Hosea 4 in the LSV

Hosea 4 in the MAAL

Hosea 4 in the MBV

Hosea 4 in the MBV2

Hosea 4 in the MHNT

Hosea 4 in the MKNFD

Hosea 4 in the MNG

Hosea 4 in the MNT

Hosea 4 in the MNT2

Hosea 4 in the MRS1T

Hosea 4 in the NAA

Hosea 4 in the NASB

Hosea 4 in the NBLA

Hosea 4 in the NBS

Hosea 4 in the NBVTP

Hosea 4 in the NET2

Hosea 4 in the NIV11

Hosea 4 in the NNT

Hosea 4 in the NNT2

Hosea 4 in the NNT3

Hosea 4 in the PDDPT

Hosea 4 in the PFNT

Hosea 4 in the RMNT

Hosea 4 in the SBIAS

Hosea 4 in the SBIBS

Hosea 4 in the SBIBS2

Hosea 4 in the SBICS

Hosea 4 in the SBIDS

Hosea 4 in the SBIGS

Hosea 4 in the SBIHS

Hosea 4 in the SBIIS

Hosea 4 in the SBIIS2

Hosea 4 in the SBIIS3

Hosea 4 in the SBIKS

Hosea 4 in the SBIKS2

Hosea 4 in the SBIMS

Hosea 4 in the SBIOS

Hosea 4 in the SBIPS

Hosea 4 in the SBISS

Hosea 4 in the SBITS

Hosea 4 in the SBITS2

Hosea 4 in the SBITS3

Hosea 4 in the SBITS4

Hosea 4 in the SBIUS

Hosea 4 in the SBIVS

Hosea 4 in the SBT

Hosea 4 in the SBT1E

Hosea 4 in the SCHL

Hosea 4 in the SNT

Hosea 4 in the SUSU

Hosea 4 in the SUSU2

Hosea 4 in the SYNO

Hosea 4 in the TBIAOTANT

Hosea 4 in the TBT1E

Hosea 4 in the TBT1E2

Hosea 4 in the TFTIP

Hosea 4 in the TFTU

Hosea 4 in the TGNTATF3T

Hosea 4 in the THAI

Hosea 4 in the TNFD

Hosea 4 in the TNT

Hosea 4 in the TNTIK

Hosea 4 in the TNTIL

Hosea 4 in the TNTIN

Hosea 4 in the TNTIP

Hosea 4 in the TNTIZ

Hosea 4 in the TOMA

Hosea 4 in the TTENT

Hosea 4 in the UBG

Hosea 4 in the UGV

Hosea 4 in the UGV2

Hosea 4 in the UGV3

Hosea 4 in the VBL

Hosea 4 in the VDCC

Hosea 4 in the YALU

Hosea 4 in the YAPE

Hosea 4 in the YBVTP

Hosea 4 in the ZBP