Jeremiah 12 (BOGWICC)

1 Yehova, Inu mumakhala wokhoza nthawi zonsendikati nditsutsane nanu.Komabe ndikufuna kuyankhula nanu za mlandu wanga.Chifukwa chiyani anthu oyipa zinthu zimawayendera bwino?Chifukwa chiyani anthu achinyengo amakhala pabwino? 2 Inu munawadzala ndipo anamera mizu;amakula ndi kubereka zipatso.Dzina lanu limakhala pakamwa pawo nthawi zonse,koma mitima yawo imakhala kutali ndi Inu. 3 Koma Inu Yehova, ine mumandidziwa;mumandiona ndipo mumayesa zolingalira zanga.Akokeni anthu oyipawo ngati nkhosa zokaphedwa!Ayikeni padera mpaka tsiku loti akaphedwe! 4 Kodi dziko lidzakhala likulirabe mpaka litindipo udzu mʼmunda uliwonse udzakhalabe ofota mpaka liti?Nyama ndi mbalame kulibiretuchifukwa anthu amene amakhalamo ndi oyipa.Iwo amati:“Yehova sangathe kuona ntchito zathu.” 5 Yehova anayankha kuti, “Ngati kukutopetsa kuthamanga pamodzi ndi anthunanga ungapikisane bwanji ndi akavalo?Ngati ukupunthwa ndi kugwa pa malo abwino,udzatha bwanji kuthamanga mʼnkhalangoza ku Yorodani? 6 Ngakhale abale akondi anansi akuwukira,onsewo amvana zokuyimba mlandu.Usawakhulupirire,ngakhale ayankhule zabwino ndi iwe. 7 “Ine ndawasiya anthu anga;anthu amene ndinawasankha ndawataya.Ndapereka okondedwa angamʼmanja mwa adani awo. 8 Anthu amene ndinawasankhaasanduka ngati mkango wa mʼnkhalango.Akundibangulira mwaukali;nʼchifukwa chake Ine ndikudana nawo. 9 Anthu anga amene ndinawasankhaasanduka ngati mbalame yolusa yamawangamawangaimene akabawi ayizinga.Pitani, kasonkhanitseni nyama zakuthengo.Mubwere nazo kuti zidzadye mbalameyo. 10 Abusa ambiri anawononga munda wanga wa mpesa,anapondereza munda wanga;munda wanga wabwino ujaanawusandutsa chipululu. 11 Unawusandutsadi chipululu.Ukanali wokhawokha chomwecho ukundilirira Ine.Dziko lonse lasanduka chipululuchifukwa palibe wolisamalira. 12 Anthu onse owononga abalalikiraku zitunda zonse za mʼchipululu.Yehova watuma ankhondo akekudzawatha kuyambira kumalire ena a dziko mpaka ku malire enanso a dziko,ndipo palibe amene adzakhale pa mtendere. 13 Anthu anafesa tirigu koma anatuta minga;anadzitopetsa kugwira ntchito koma osapeza phindu lililonse.Choncho mudzachita manyazi ndi zokolola zanuchifukwa cha mkwiyo wa Yehova.” 14 “Anthu oyipa oyandikana ndi anthu anga Aisraeli, akuwalanda Aisraeliwo dziko, cholowa chimene ndinawapatsa. Nʼchifukwa chake ndidzawachotsa mʼdziko limenelo, ndipo ndidzachotsa banja la Yuda pakati pawo. 15 Komabe nditawachotsa, ndidzawachitiranso chifundo, ndipo ndidzabwezera aliyense cholowa chake ndi dziko lake. 16 Ndipo ngati iwo adzaphunzira bwino njira za anthu anga ndi kulumbira mʼdzina langa, namanena kuti, ‘Pali Yehova wamoyo,’ monga iwo anaphunzitsira anthu anga kulumbira mʼdzina la Baala, Ine ndidzawakhazikitsa pakati pa anthu anga. 17 Koma ngati mtundu wina uliwonse sudzamvera, Ine ndidzawuchotsa ndi kuwuwonongeratu,” akutero Yehova.

In Other Versions

Jeremiah 12 in the ANGEFD

Jeremiah 12 in the ANTPNG2D

Jeremiah 12 in the AS21

Jeremiah 12 in the BAGH

Jeremiah 12 in the BBPNG

Jeremiah 12 in the BBT1E

Jeremiah 12 in the BDS

Jeremiah 12 in the BEV

Jeremiah 12 in the BHAD

Jeremiah 12 in the BIB

Jeremiah 12 in the BLPT

Jeremiah 12 in the BNT

Jeremiah 12 in the BNTABOOT

Jeremiah 12 in the BNTLV

Jeremiah 12 in the BOATCB

Jeremiah 12 in the BOATCB2

Jeremiah 12 in the BOBCV

Jeremiah 12 in the BOCNT

Jeremiah 12 in the BOECS

Jeremiah 12 in the BOHCB

Jeremiah 12 in the BOHCV

Jeremiah 12 in the BOHLNT

Jeremiah 12 in the BOHNTLTAL

Jeremiah 12 in the BOICB

Jeremiah 12 in the BOILNTAP

Jeremiah 12 in the BOITCV

Jeremiah 12 in the BOKCV

Jeremiah 12 in the BOKCV2

Jeremiah 12 in the BOKHWOG

Jeremiah 12 in the BOKSSV

Jeremiah 12 in the BOLCB

Jeremiah 12 in the BOLCB2

Jeremiah 12 in the BOMCV

Jeremiah 12 in the BONAV

Jeremiah 12 in the BONCB

Jeremiah 12 in the BONLT

Jeremiah 12 in the BONUT2

Jeremiah 12 in the BOPLNT

Jeremiah 12 in the BOSCB

Jeremiah 12 in the BOSNC

Jeremiah 12 in the BOTLNT

Jeremiah 12 in the BOVCB

Jeremiah 12 in the BOYCB

Jeremiah 12 in the BPBB

Jeremiah 12 in the BPH

Jeremiah 12 in the BSB

Jeremiah 12 in the CCB

Jeremiah 12 in the CUV

Jeremiah 12 in the CUVS

Jeremiah 12 in the DBT

Jeremiah 12 in the DGDNT

Jeremiah 12 in the DHNT

Jeremiah 12 in the DNT

Jeremiah 12 in the ELBE

Jeremiah 12 in the EMTV

Jeremiah 12 in the ESV

Jeremiah 12 in the FBV

Jeremiah 12 in the FEB

Jeremiah 12 in the GGMNT

Jeremiah 12 in the GNT

Jeremiah 12 in the HARY

Jeremiah 12 in the HNT

Jeremiah 12 in the IRVA

Jeremiah 12 in the IRVB

Jeremiah 12 in the IRVG

Jeremiah 12 in the IRVH

Jeremiah 12 in the IRVK

Jeremiah 12 in the IRVM

Jeremiah 12 in the IRVM2

Jeremiah 12 in the IRVO

Jeremiah 12 in the IRVP

Jeremiah 12 in the IRVT

Jeremiah 12 in the IRVT2

Jeremiah 12 in the IRVU

Jeremiah 12 in the ISVN

Jeremiah 12 in the JSNT

Jeremiah 12 in the KAPI

Jeremiah 12 in the KBT1ETNIK

Jeremiah 12 in the KBV

Jeremiah 12 in the KJV

Jeremiah 12 in the KNFD

Jeremiah 12 in the LBA

Jeremiah 12 in the LBLA

Jeremiah 12 in the LNT

Jeremiah 12 in the LSV

Jeremiah 12 in the MAAL

Jeremiah 12 in the MBV

Jeremiah 12 in the MBV2

Jeremiah 12 in the MHNT

Jeremiah 12 in the MKNFD

Jeremiah 12 in the MNG

Jeremiah 12 in the MNT

Jeremiah 12 in the MNT2

Jeremiah 12 in the MRS1T

Jeremiah 12 in the NAA

Jeremiah 12 in the NASB

Jeremiah 12 in the NBLA

Jeremiah 12 in the NBS

Jeremiah 12 in the NBVTP

Jeremiah 12 in the NET2

Jeremiah 12 in the NIV11

Jeremiah 12 in the NNT

Jeremiah 12 in the NNT2

Jeremiah 12 in the NNT3

Jeremiah 12 in the PDDPT

Jeremiah 12 in the PFNT

Jeremiah 12 in the RMNT

Jeremiah 12 in the SBIAS

Jeremiah 12 in the SBIBS

Jeremiah 12 in the SBIBS2

Jeremiah 12 in the SBICS

Jeremiah 12 in the SBIDS

Jeremiah 12 in the SBIGS

Jeremiah 12 in the SBIHS

Jeremiah 12 in the SBIIS

Jeremiah 12 in the SBIIS2

Jeremiah 12 in the SBIIS3

Jeremiah 12 in the SBIKS

Jeremiah 12 in the SBIKS2

Jeremiah 12 in the SBIMS

Jeremiah 12 in the SBIOS

Jeremiah 12 in the SBIPS

Jeremiah 12 in the SBISS

Jeremiah 12 in the SBITS

Jeremiah 12 in the SBITS2

Jeremiah 12 in the SBITS3

Jeremiah 12 in the SBITS4

Jeremiah 12 in the SBIUS

Jeremiah 12 in the SBIVS

Jeremiah 12 in the SBT

Jeremiah 12 in the SBT1E

Jeremiah 12 in the SCHL

Jeremiah 12 in the SNT

Jeremiah 12 in the SUSU

Jeremiah 12 in the SUSU2

Jeremiah 12 in the SYNO

Jeremiah 12 in the TBIAOTANT

Jeremiah 12 in the TBT1E

Jeremiah 12 in the TBT1E2

Jeremiah 12 in the TFTIP

Jeremiah 12 in the TFTU

Jeremiah 12 in the TGNTATF3T

Jeremiah 12 in the THAI

Jeremiah 12 in the TNFD

Jeremiah 12 in the TNT

Jeremiah 12 in the TNTIK

Jeremiah 12 in the TNTIL

Jeremiah 12 in the TNTIN

Jeremiah 12 in the TNTIP

Jeremiah 12 in the TNTIZ

Jeremiah 12 in the TOMA

Jeremiah 12 in the TTENT

Jeremiah 12 in the UBG

Jeremiah 12 in the UGV

Jeremiah 12 in the UGV2

Jeremiah 12 in the UGV3

Jeremiah 12 in the VBL

Jeremiah 12 in the VDCC

Jeremiah 12 in the YALU

Jeremiah 12 in the YAPE

Jeremiah 12 in the YBVTP

Jeremiah 12 in the ZBP