Micah 7 (BOGWICC)

1 Tsoka ine!Ndili ngati munthu wokunkha zipatso nthawi yachilimwe,pa nthawi yokolola mphesa;palibe phava lamphesa loti nʼkudya,palibe nkhuyu zoyambirira zimene ndimazilakalaka kwambiri. 2 Anthu opembedza atha mʼdziko;palibe wolungama ndi mmodzi yemwe amene watsala.Anthu onse akubisalirana kuti aphane;aliyense akusaka mʼbale wake ndi khoka. 3 Manja awo onse ndi aluso pochita zoyipa;wolamulira amafuna mphatso,woweruza amalandira ziphuphu,anthu amphamvu amalamula kuti zichitike zimene akuzifuna,onse amagwirizana zochita. 4 Munthu wabwino kwambiri pakati pawo ali ngati mtengo waminga,munthu wolungama kwambiri pakati pawo ndi woyipa kuposa mpanda waminga.Tsiku limene alonda ako ananena lafika,tsiku limene Mulungu akukuchezera.Tsopano ndi nthawi ya chisokonezo chawo. 5 Usadalire mnansi;usakhulupirire bwenzi.Usamale zoyankhula zakongakhale kwa mkazi amene wamukumbatira. 6 Pakuti mwana wamwamuna akunyoza abambo ake,mwana wamkazi akuwukira amayi ake,mtengwa akukangana ndi apongozi ake,adani a munthu ndi amene amakhala nawo mʼbanja mwake momwe. 7 Koma ine ndikudikira Yehova mwachiyembekezo,ndikudikira Mulungu Mpulumutsi wanga;Mulungu wanga adzamvetsera. 8 Iwe mdani wanga, usandiseke!Ngakhale ndagwa, ndidzauka.Ngakhale ndikukhala mu mdima,Yehova ndiye kuwunika kwanga. 9 Ndidzapirira mkwiyo wa Yehova,chifukwa ndinamuchimwira,mpaka ataweruza mlandu wangandi kukhazikitsa chilungamo changa.Iye adzanditulutsa ndi kundilowetsa mʼkuwunika;ndidzaona chilungamo chake. 10 Ndipo mdani wanga adzaona zimenezinadzagwidwa ndi manyazi,iye amene anandifunsa kuti,“Ali kuti Yehova Mulungu wako?”Ndidzaona kugonjetsedwa kwake ndi maso anga;ngakhale tsopano adzaponderezedwangati matope mʼmisewu. 11 Idzafika nthawi yomanganso makoma anu,nthawi yokulitsanso malire anu. 12 Nthawi imeneyo anthu adzabwera kwa inukuchokera ku Asiriya ndi mizinda ya ku Igupto,ngakhale kuchokera ku Igupto mpaka ku Yufuratendiponso kuchokera ku nyanja ina mpaka ku nyanja inansokuchokera ku phiri lina mpaka ku phiri linanso. 13 Dziko lapansi lidzasanduka chipululuchifukwa cha anthu okhala mʼdzikomo, potsatira zochita za anthuwo. 14 Wetani anthu anu ndi ndodo yanu yowateteza,nkhosa zimene ndi cholowa chanu,zimene zili zokha mʼnkhalango,mʼdziko la chonde.Muzilole kuti zidye mu Basani ndi mu Giliyadimonga masiku akale. 15 “Ndidzawaonetsa zodabwitsa zanga,ngati masiku amene ndinawatulutsa mʼdziko la Igupto.” 16 Mitundu ya anthu idzaona zimenezi ndipo idzachita manyazi,ngakhale ali ndi mphamvu zotani.Adzagwira pakamwa pawondipo makutu awo adzagontha. 17 Adzabwira fumbi ngati njoka,ngati zolengedwa zomwe zimakwawa pansi.Adzabwera akunjenjemera kuchokera mʼmaenje awo;mwamantha adzatembenukira kwa Yehova Mulungu wathundipo adzachita nanu mantha. 18 Kodi alipo Mulungu wofanana nanu,amene amakhululukira tchimo ndi kuyiwala zolakwaza anthu otsala amene ndi cholowa chake?Inu simusunga mkwiyo mpaka muyayakoma kwanu nʼkuonetsa chikondi chosasinthika. 19 Inu mudzatichitiranso chifundo;mudzapondereza pansi machimo athundi kuponyera zolakwa zathu zonse pansi pa nyanja. 20 Mudzakhala wokhulupirika kwa Yakobo,ndi kuonetsa chifundo chanu kwa Abrahamu,monga munalonjeza molumbira kwa makolo athumasiku amakedzana.

In Other Versions

Micah 7 in the ANGEFD

Micah 7 in the ANTPNG2D

Micah 7 in the AS21

Micah 7 in the BAGH

Micah 7 in the BBPNG

Micah 7 in the BBT1E

Micah 7 in the BDS

Micah 7 in the BEV

Micah 7 in the BHAD

Micah 7 in the BIB

Micah 7 in the BLPT

Micah 7 in the BNT

Micah 7 in the BNTABOOT

Micah 7 in the BNTLV

Micah 7 in the BOATCB

Micah 7 in the BOATCB2

Micah 7 in the BOBCV

Micah 7 in the BOCNT

Micah 7 in the BOECS

Micah 7 in the BOHCB

Micah 7 in the BOHCV

Micah 7 in the BOHLNT

Micah 7 in the BOHNTLTAL

Micah 7 in the BOICB

Micah 7 in the BOILNTAP

Micah 7 in the BOITCV

Micah 7 in the BOKCV

Micah 7 in the BOKCV2

Micah 7 in the BOKHWOG

Micah 7 in the BOKSSV

Micah 7 in the BOLCB

Micah 7 in the BOLCB2

Micah 7 in the BOMCV

Micah 7 in the BONAV

Micah 7 in the BONCB

Micah 7 in the BONLT

Micah 7 in the BONUT2

Micah 7 in the BOPLNT

Micah 7 in the BOSCB

Micah 7 in the BOSNC

Micah 7 in the BOTLNT

Micah 7 in the BOVCB

Micah 7 in the BOYCB

Micah 7 in the BPBB

Micah 7 in the BPH

Micah 7 in the BSB

Micah 7 in the CCB

Micah 7 in the CUV

Micah 7 in the CUVS

Micah 7 in the DBT

Micah 7 in the DGDNT

Micah 7 in the DHNT

Micah 7 in the DNT

Micah 7 in the ELBE

Micah 7 in the EMTV

Micah 7 in the ESV

Micah 7 in the FBV

Micah 7 in the FEB

Micah 7 in the GGMNT

Micah 7 in the GNT

Micah 7 in the HARY

Micah 7 in the HNT

Micah 7 in the IRVA

Micah 7 in the IRVB

Micah 7 in the IRVG

Micah 7 in the IRVH

Micah 7 in the IRVK

Micah 7 in the IRVM

Micah 7 in the IRVM2

Micah 7 in the IRVO

Micah 7 in the IRVP

Micah 7 in the IRVT

Micah 7 in the IRVT2

Micah 7 in the IRVU

Micah 7 in the ISVN

Micah 7 in the JSNT

Micah 7 in the KAPI

Micah 7 in the KBT1ETNIK

Micah 7 in the KBV

Micah 7 in the KJV

Micah 7 in the KNFD

Micah 7 in the LBA

Micah 7 in the LBLA

Micah 7 in the LNT

Micah 7 in the LSV

Micah 7 in the MAAL

Micah 7 in the MBV

Micah 7 in the MBV2

Micah 7 in the MHNT

Micah 7 in the MKNFD

Micah 7 in the MNG

Micah 7 in the MNT

Micah 7 in the MNT2

Micah 7 in the MRS1T

Micah 7 in the NAA

Micah 7 in the NASB

Micah 7 in the NBLA

Micah 7 in the NBS

Micah 7 in the NBVTP

Micah 7 in the NET2

Micah 7 in the NIV11

Micah 7 in the NNT

Micah 7 in the NNT2

Micah 7 in the NNT3

Micah 7 in the PDDPT

Micah 7 in the PFNT

Micah 7 in the RMNT

Micah 7 in the SBIAS

Micah 7 in the SBIBS

Micah 7 in the SBIBS2

Micah 7 in the SBICS

Micah 7 in the SBIDS

Micah 7 in the SBIGS

Micah 7 in the SBIHS

Micah 7 in the SBIIS

Micah 7 in the SBIIS2

Micah 7 in the SBIIS3

Micah 7 in the SBIKS

Micah 7 in the SBIKS2

Micah 7 in the SBIMS

Micah 7 in the SBIOS

Micah 7 in the SBIPS

Micah 7 in the SBISS

Micah 7 in the SBITS

Micah 7 in the SBITS2

Micah 7 in the SBITS3

Micah 7 in the SBITS4

Micah 7 in the SBIUS

Micah 7 in the SBIVS

Micah 7 in the SBT

Micah 7 in the SBT1E

Micah 7 in the SCHL

Micah 7 in the SNT

Micah 7 in the SUSU

Micah 7 in the SUSU2

Micah 7 in the SYNO

Micah 7 in the TBIAOTANT

Micah 7 in the TBT1E

Micah 7 in the TBT1E2

Micah 7 in the TFTIP

Micah 7 in the TFTU

Micah 7 in the TGNTATF3T

Micah 7 in the THAI

Micah 7 in the TNFD

Micah 7 in the TNT

Micah 7 in the TNTIK

Micah 7 in the TNTIL

Micah 7 in the TNTIN

Micah 7 in the TNTIP

Micah 7 in the TNTIZ

Micah 7 in the TOMA

Micah 7 in the TTENT

Micah 7 in the UBG

Micah 7 in the UGV

Micah 7 in the UGV2

Micah 7 in the UGV3

Micah 7 in the VBL

Micah 7 in the VDCC

Micah 7 in the YALU

Micah 7 in the YAPE

Micah 7 in the YBVTP

Micah 7 in the ZBP