Numbers 34 (BOGWICC)

1 Yehova anawuza Mose kuti, 2 “Lamula Aisraeli ndipo uwawuze kuti, ‘Pamene mulowa mʼdziko la Kanaani, dziko lomwe lidzaperekedwa kwa inu ngati cholowa chanu, lidzakhale ndi malire awa: 3 “ ‘Chigawo cha kummwera kwa dziko lanu chidzayambira ku chipululu cha Zini motsatana ndi malire a Edomu. Kummawa malire anu a kummwera adzayambira kummawa, kumathero a Nyanja ya Mchere. 4 Malirewo adzapita kummwera ndipo adzakwera phiri la Akirabimu mpaka ku Zini. Mathero ake adzakhala kummwera kwa Kadesi-Baranea. Ndipo adzapitenso ku Hazari Adari mpaka kukafika ku Azimoni, 5 kumene malirewo adzakhote kuchokera ku Azimoni mpaka ku khwawa la ku Igupto ndi kukathera ku Nyanja Yayikulu. 6 “ ‘Malire anu a ku madzulo adzakhala ku gombe la Nyanja Yayikulu. Amenewo ndiwo adzakhale malire anu a ku madzulo. 7 “ ‘Malire anu a kumpoto, mzere wake uyambire ku Nyanja Yayikulu mpaka ku phiri la Hori 8 ndi kuchokera ku phiri la Hori mpaka ku Lebo Hamati. Malirewa apite ku Zedadi, 9 ndi kupitirira mpaka ku Ziforoni ndi kukathera ku Hazari-Enani. Awa ndiwo adzakhale malire anu a kumpoto. 10 “ ‘Za malire anu a kummawa, mulembe mzere kuchokera ku Hazari-Enani mpaka kukafika ku Sefamu. 11 Malirewo adzatsikire ku Sefamu mpaka ku Ribila cha kummawa kwa Aini ndi kupitirira mpaka ku matsitso a cha kummawa kwa Nyanja ya Kinereti. 12 Tsono malirewo adzatsika motsatana ndi Yorodani ndi kukathera ku Nyanja ya Mchere.“ ‘Limeneli lidzakhala dziko lanu ndi malire ake mbali zonse.’ ” 13 Ndipo Mose analamula Aisraeli kuti, “Limeneli ndi dziko limene mudzalilandira pochita maere kuti likhale cholowa chanu. Yehova analamula kuti liperekedwe ku mafuko asanu ndi anayi ndi theka, 14 chifukwa mabanja a fuko la Rubeni, fuko la Gadi, ndi theka la fuko la Manase analandiriratu cholowa chawo. 15 Mafuko awiriwa pamodzi ndi theka la fuko la Manase analandiriratu cholowa chawo patsidya pa mtsinje wa Yorodani ku Yeriko cha kummawa kotulukira dzuwa.” 16 Yehova anawuza Mose kuti, 17 “Awa ndi mayina a anthu amene adzakugawireni dzikoli kuti likhale cholowa chanu: wansembe Eliezara ndi Yoswa mwana wa Nuni. 18 Musankhe mtsogoleri mmodzi kuchokera ku fuko lililonse kuti athandize kugawa dzikolo. 19 Mayina awo ndi awa: Kalebe mwana wa Yefune,wochokera ku fuko la Yuda, 20 Semueli mwana wa Amihudi,wochokera ku fuko la Simeoni; 21 Elidadi mwana wa Kisiloni,wochokera ku fuko la Benjamini; 22 Buki mwana wa Yogili,mtsogoleri wochokera ku fuko la Dani; 23 Hanieli mwana wa Efodi,mtsogoleri wochokera ku fuko la Manase, mwana wa Yosefe; 24 Kemueli mwana wa Sifitani,mtsogoleri wochokera ku fuko la Efereimu, mwana wa Yosefe. 25 Elizafani mwana wa Parinaki,mtsogoleri wochokera ku fuko la Zebuloni; 26 Palitieli mwana wa Azani,mtsogoleri wochokera ku fuko la Isakara, 27 Ahihudi mwana wa Selomi,mtsogoleri wochokera ku fuko la Aseri; 28 Pedaheli mwana wa Amihudi,mtsogoleri wochokera ku fuko la Nafutali.” 29 Awa ndiwo mayina a anthu amene Yehova analamula kuti agawe cholowa cha Aisraeli mʼdziko la Kanaani.

In Other Versions

Numbers 34 in the ANGEFD

Numbers 34 in the ANTPNG2D

Numbers 34 in the AS21

Numbers 34 in the BAGH

Numbers 34 in the BBPNG

Numbers 34 in the BBT1E

Numbers 34 in the BDS

Numbers 34 in the BEV

Numbers 34 in the BHAD

Numbers 34 in the BIB

Numbers 34 in the BLPT

Numbers 34 in the BNT

Numbers 34 in the BNTABOOT

Numbers 34 in the BNTLV

Numbers 34 in the BOATCB

Numbers 34 in the BOATCB2

Numbers 34 in the BOBCV

Numbers 34 in the BOCNT

Numbers 34 in the BOECS

Numbers 34 in the BOHCB

Numbers 34 in the BOHCV

Numbers 34 in the BOHLNT

Numbers 34 in the BOHNTLTAL

Numbers 34 in the BOICB

Numbers 34 in the BOILNTAP

Numbers 34 in the BOITCV

Numbers 34 in the BOKCV

Numbers 34 in the BOKCV2

Numbers 34 in the BOKHWOG

Numbers 34 in the BOKSSV

Numbers 34 in the BOLCB

Numbers 34 in the BOLCB2

Numbers 34 in the BOMCV

Numbers 34 in the BONAV

Numbers 34 in the BONCB

Numbers 34 in the BONLT

Numbers 34 in the BONUT2

Numbers 34 in the BOPLNT

Numbers 34 in the BOSCB

Numbers 34 in the BOSNC

Numbers 34 in the BOTLNT

Numbers 34 in the BOVCB

Numbers 34 in the BOYCB

Numbers 34 in the BPBB

Numbers 34 in the BPH

Numbers 34 in the BSB

Numbers 34 in the CCB

Numbers 34 in the CUV

Numbers 34 in the CUVS

Numbers 34 in the DBT

Numbers 34 in the DGDNT

Numbers 34 in the DHNT

Numbers 34 in the DNT

Numbers 34 in the ELBE

Numbers 34 in the EMTV

Numbers 34 in the ESV

Numbers 34 in the FBV

Numbers 34 in the FEB

Numbers 34 in the GGMNT

Numbers 34 in the GNT

Numbers 34 in the HARY

Numbers 34 in the HNT

Numbers 34 in the IRVA

Numbers 34 in the IRVB

Numbers 34 in the IRVG

Numbers 34 in the IRVH

Numbers 34 in the IRVK

Numbers 34 in the IRVM

Numbers 34 in the IRVM2

Numbers 34 in the IRVO

Numbers 34 in the IRVP

Numbers 34 in the IRVT

Numbers 34 in the IRVT2

Numbers 34 in the IRVU

Numbers 34 in the ISVN

Numbers 34 in the JSNT

Numbers 34 in the KAPI

Numbers 34 in the KBT1ETNIK

Numbers 34 in the KBV

Numbers 34 in the KJV

Numbers 34 in the KNFD

Numbers 34 in the LBA

Numbers 34 in the LBLA

Numbers 34 in the LNT

Numbers 34 in the LSV

Numbers 34 in the MAAL

Numbers 34 in the MBV

Numbers 34 in the MBV2

Numbers 34 in the MHNT

Numbers 34 in the MKNFD

Numbers 34 in the MNG

Numbers 34 in the MNT

Numbers 34 in the MNT2

Numbers 34 in the MRS1T

Numbers 34 in the NAA

Numbers 34 in the NASB

Numbers 34 in the NBLA

Numbers 34 in the NBS

Numbers 34 in the NBVTP

Numbers 34 in the NET2

Numbers 34 in the NIV11

Numbers 34 in the NNT

Numbers 34 in the NNT2

Numbers 34 in the NNT3

Numbers 34 in the PDDPT

Numbers 34 in the PFNT

Numbers 34 in the RMNT

Numbers 34 in the SBIAS

Numbers 34 in the SBIBS

Numbers 34 in the SBIBS2

Numbers 34 in the SBICS

Numbers 34 in the SBIDS

Numbers 34 in the SBIGS

Numbers 34 in the SBIHS

Numbers 34 in the SBIIS

Numbers 34 in the SBIIS2

Numbers 34 in the SBIIS3

Numbers 34 in the SBIKS

Numbers 34 in the SBIKS2

Numbers 34 in the SBIMS

Numbers 34 in the SBIOS

Numbers 34 in the SBIPS

Numbers 34 in the SBISS

Numbers 34 in the SBITS

Numbers 34 in the SBITS2

Numbers 34 in the SBITS3

Numbers 34 in the SBITS4

Numbers 34 in the SBIUS

Numbers 34 in the SBIVS

Numbers 34 in the SBT

Numbers 34 in the SBT1E

Numbers 34 in the SCHL

Numbers 34 in the SNT

Numbers 34 in the SUSU

Numbers 34 in the SUSU2

Numbers 34 in the SYNO

Numbers 34 in the TBIAOTANT

Numbers 34 in the TBT1E

Numbers 34 in the TBT1E2

Numbers 34 in the TFTIP

Numbers 34 in the TFTU

Numbers 34 in the TGNTATF3T

Numbers 34 in the THAI

Numbers 34 in the TNFD

Numbers 34 in the TNT

Numbers 34 in the TNTIK

Numbers 34 in the TNTIL

Numbers 34 in the TNTIN

Numbers 34 in the TNTIP

Numbers 34 in the TNTIZ

Numbers 34 in the TOMA

Numbers 34 in the TTENT

Numbers 34 in the UBG

Numbers 34 in the UGV

Numbers 34 in the UGV2

Numbers 34 in the UGV3

Numbers 34 in the VBL

Numbers 34 in the VDCC

Numbers 34 in the YALU

Numbers 34 in the YAPE

Numbers 34 in the YBVTP

Numbers 34 in the ZBP