Psalms 89 (BOGWICC)

undefined Ndakatulo ya Etani, wa banja la Ezara. 1 Ndidzayimba za chikondi chachikulu cha Yehova kwamuyaya;ndi pakamwa panga ndidzachititsa kuti kukhulupirika kwanu kudziwike ku mibado yonse. 2 Ndidzalalikira kuti chikondi chanu chidzakhazikika mpaka muyaya,kuti Inu munakhazikitsa kukhulupirika kwanu kumwamba kwenikweniko. 3 Inu munati, “Ndachita pangano ndi wosankhidwa wanga,ndalumbira kwa Davide mtumiki wanga kuti, 4 ‘Ndidzakhazikitsa zidzukulu zako mpaka muyaya.Ndidzachititsa kuti mpando wako waufumu ukhazikike ku mibado yonse,’ ”Sela. 5 Mayiko akumwamba amatamanda zozizwitsa zanu Yehova,kukhulupirika kwanunso, mu msonkhano wa oyera mtima anu. 6 Pakuti ndani mu mlengalenga angalingane ndi Yehova?Ndani wofanana ndi Yehova pakati pa zolengedwa zakumwamba? 7 Mu msonkhano wa oyera mtima Mulungu amaopedwa kwambiri;Iye ndiye wochititsa mantha kupambana onse amene amuzungulira. 8 Inu Yehova Mulungu Wamphamvuzonse, ndani wofanana nanu?Yehova ndinu wamphamvu ndipo kukhulupirika kwanu kwakuzungulirani. 9 Mumalamula nyanja ya mafunde awukali;pamene mafunde ake awundana Inu mumawakhalitsa bata. 10 Munaphwanya Rahabe monga munthu wophedwa;ndi dzanja lanu lamphamvu munabalalitsa adani anu. 11 Mayiko akumwamba ndi anu ndiponso dziko lapansi ndi lanu;munapanga dziko lonse ndi zonse zili mʼmenemo. 12 Munalenga Kumpoto ndi Kummwera;Tabori ndi Herimoni akuyimba ndi chimwemwe pa dzina lanu. 13 Mkono wanu ndi wamphamvu;dzanja lanu ndi lamphamvu, dzanja lanu lamanja ndi lopambana. 14 Chilungamo ndi chiweruzo cholungama ndiye maziko a mpando wanu waufumu;chikondi ndi kukhulupirika zimayenda patsogolo panu. 15 Ndi odala amene aphunzira kuyamika Inu,amene amayenda mʼkuwunika kwa nkhope yanu Yehova. 16 Amakondwera mʼdzina lanu tsiku lonse lathunthu;amasangalala koposa mʼchilungamo chanu. 17 Pakuti Inu ndiye ulemerero wawo ndi mphamvu yawondipo mwa kukoma mtima kwanu Inu mumakweza nyanga yathu. 18 Ndithudi, chishango chathu ndi cha Yehova,Mfumu yathu kwa Woyerayo wa Israeli. 19 Kale munayankhula mʼmasomphenya,kwa anthu anu okhulupirika munati,“Ndapatsa mphamvu wankhondo;ndakweza mnyamata wochokera pakati pa anthu. 20 Ndamupeza mtumiki wanga Davide;ndamudzoza ndi mafuta opatulika. 21 Dzanja langa lidzamuchirikiza;zoonadi, mkono wanga udzamupatsa mphamvu. 22 Adani sadzamulamula kuti apereke msonkho;anthu oyipa sadzamusautsa. 23 Ndidzaphwanya adani ake pamaso pakendi kukantha otsutsana naye. 24 Chikondi changa chokhulupirika chidzakhala naye,ndipo kudzera mʼdzina langa nyanga yake idzakwezedwa. 25 Ndidzayika dzanja lake pa nyanja,dzanja lake lamanja pa mitsinje. 26 Iyeyo adzafuwula kwa Ine kuti, ‘Ndinu Atate anga,Mulungu wanga, Thanthwe ndi Chipulumutso changa.’ 27 Ndidzamuyika kuti akhale mwana wanga woyamba kubadwa;wokwezedwa kwambiri pakati pa mafumu a dziko lapansi. 28 Ndidzamusungira chifundo changa kwamuyaya,ndipo pangano langa ndi iye silidzatha. 29 Ine ndidzakhazikitsa zidzukulu zake mpaka muyaya,mpando wake waufumu ngati masiku a miyamba. 30 “Ngati ana ake adzataya lamulo langandi kusatsatira malangizo anga, 31 ngati adzaswa malamulo angandi kulephera kusunga ziphunzitso zanga, 32 Ine ndidzalanga tchimo lawo ndi ndodo,mphulupulu zawo powakwapula. 33 Koma sindidzachotsa chikondi changa pa iye,kapena kukhala wosakhulupirika kwa iyeyo. 34 Sindidzaswa pangano langakapena kusintha zimene milomo yanga yayankhula. 35 Ndinalumbira kamodzi mwa kuyera kwangandipo sindidzanama kwa Davide, 36 kuti zidzukulu zake zidzakhale kwamuyayandipo mpando wake waufumu udzakhazikika pamaso panga ngati dzuwa; 37 udzakhazikika kwamuyaya monga mwezi,mboni yokhulupirika mʼmitambo. Sela 38 “Koma tsopano Inu mwamukana, mwamutaya,mwamukwiyira kwambiri wodzozedwa wanu. 39 Mwakana pangano ndi mtumiki wanundipo mwadetsa mʼfumbi chipewa chake chaufumu. 40 Inu mwagumula makoma ake onsendipo mwasandutsa bwinja malinga ake. 41 Onse amene amadutsa amalanda zinthu zake;iye wakhala chotonzedwa cha anansi ake. 42 Mwakweza dzanja lamanja la adani ake;mwachititsa kuti adani ake akondwere. 43 Mwabunthitsa lupanga lake,simunamuthandize pa nkhondo. 44 Inu mwathetsa kukongola kwa ulemerero wakendipo mwagwetsa pansi mpando wake waufumu. 45 Mwachepetsa masiku a unyamata wake;mwamuphimba ndi chofunda chochititsa manyazi. Sela 46 “Mpaka liti Yehova? Kodi mudzadzibisa mpaka kalekale?Mpaka liti ukali wanu udzayaka ngati moto? 47 Kumbukirani kuti masiku a moyo wanga ndi ochepapakuti munalenga kwachabe anthu onse! 48 Kodi ndi munthu uti angakhale ndi moyo ndi kusaona imfa?Kapena kudzipulumutsa yekha ku mphamvu ya manda?Sela 49 Inu Ambuye kodi chili kuti chikondi chanu chachikulu choyamba chija,chimene mwa kukhulupirika kwanu munalumbira kwa Davide? 50 Kumbukirani, Ambuye momwe mtumiki wanu wanyozedwera,momwe ndakhalira ndi kusunga mu mtima mwanga mawu a pangano a anthu a mitundu yonse, 51 mawu achipongwe amene adani anu akhala akunyoza, Inu Yehova,ndi mawu amene akhala akunyoza mayendedwe onse a wodzozedwa wanu. 52 “Matamando akhale kwa Yehova mpaka muyaya!”Ameni ndi Ameni.

In Other Versions

Psalms 89 in the ANGEFD

Psalms 89 in the ANTPNG2D

Psalms 89 in the AS21

Psalms 89 in the BAGH

Psalms 89 in the BBPNG

Psalms 89 in the BBT1E

Psalms 89 in the BDS

Psalms 89 in the BEV

Psalms 89 in the BHAD

Psalms 89 in the BIB

Psalms 89 in the BLPT

Psalms 89 in the BNT

Psalms 89 in the BNTABOOT

Psalms 89 in the BNTLV

Psalms 89 in the BOATCB

Psalms 89 in the BOATCB2

Psalms 89 in the BOBCV

Psalms 89 in the BOCNT

Psalms 89 in the BOECS

Psalms 89 in the BOHCB

Psalms 89 in the BOHCV

Psalms 89 in the BOHLNT

Psalms 89 in the BOHNTLTAL

Psalms 89 in the BOICB

Psalms 89 in the BOILNTAP

Psalms 89 in the BOITCV

Psalms 89 in the BOKCV

Psalms 89 in the BOKCV2

Psalms 89 in the BOKHWOG

Psalms 89 in the BOKSSV

Psalms 89 in the BOLCB

Psalms 89 in the BOLCB2

Psalms 89 in the BOMCV

Psalms 89 in the BONAV

Psalms 89 in the BONCB

Psalms 89 in the BONLT

Psalms 89 in the BONUT2

Psalms 89 in the BOPLNT

Psalms 89 in the BOSCB

Psalms 89 in the BOSNC

Psalms 89 in the BOTLNT

Psalms 89 in the BOVCB

Psalms 89 in the BOYCB

Psalms 89 in the BPBB

Psalms 89 in the BPH

Psalms 89 in the BSB

Psalms 89 in the CCB

Psalms 89 in the CUV

Psalms 89 in the CUVS

Psalms 89 in the DBT

Psalms 89 in the DGDNT

Psalms 89 in the DHNT

Psalms 89 in the DNT

Psalms 89 in the ELBE

Psalms 89 in the EMTV

Psalms 89 in the ESV

Psalms 89 in the FBV

Psalms 89 in the FEB

Psalms 89 in the GGMNT

Psalms 89 in the GNT

Psalms 89 in the HARY

Psalms 89 in the HNT

Psalms 89 in the IRVA

Psalms 89 in the IRVB

Psalms 89 in the IRVG

Psalms 89 in the IRVH

Psalms 89 in the IRVK

Psalms 89 in the IRVM

Psalms 89 in the IRVM2

Psalms 89 in the IRVO

Psalms 89 in the IRVP

Psalms 89 in the IRVT

Psalms 89 in the IRVT2

Psalms 89 in the IRVU

Psalms 89 in the ISVN

Psalms 89 in the JSNT

Psalms 89 in the KAPI

Psalms 89 in the KBT1ETNIK

Psalms 89 in the KBV

Psalms 89 in the KJV

Psalms 89 in the KNFD

Psalms 89 in the LBA

Psalms 89 in the LBLA

Psalms 89 in the LNT

Psalms 89 in the LSV

Psalms 89 in the MAAL

Psalms 89 in the MBV

Psalms 89 in the MBV2

Psalms 89 in the MHNT

Psalms 89 in the MKNFD

Psalms 89 in the MNG

Psalms 89 in the MNT

Psalms 89 in the MNT2

Psalms 89 in the MRS1T

Psalms 89 in the NAA

Psalms 89 in the NASB

Psalms 89 in the NBLA

Psalms 89 in the NBS

Psalms 89 in the NBVTP

Psalms 89 in the NET2

Psalms 89 in the NIV11

Psalms 89 in the NNT

Psalms 89 in the NNT2

Psalms 89 in the NNT3

Psalms 89 in the PDDPT

Psalms 89 in the PFNT

Psalms 89 in the RMNT

Psalms 89 in the SBIAS

Psalms 89 in the SBIBS

Psalms 89 in the SBIBS2

Psalms 89 in the SBICS

Psalms 89 in the SBIDS

Psalms 89 in the SBIGS

Psalms 89 in the SBIHS

Psalms 89 in the SBIIS

Psalms 89 in the SBIIS2

Psalms 89 in the SBIIS3

Psalms 89 in the SBIKS

Psalms 89 in the SBIKS2

Psalms 89 in the SBIMS

Psalms 89 in the SBIOS

Psalms 89 in the SBIPS

Psalms 89 in the SBISS

Psalms 89 in the SBITS

Psalms 89 in the SBITS2

Psalms 89 in the SBITS3

Psalms 89 in the SBITS4

Psalms 89 in the SBIUS

Psalms 89 in the SBIVS

Psalms 89 in the SBT

Psalms 89 in the SBT1E

Psalms 89 in the SCHL

Psalms 89 in the SNT

Psalms 89 in the SUSU

Psalms 89 in the SUSU2

Psalms 89 in the SYNO

Psalms 89 in the TBIAOTANT

Psalms 89 in the TBT1E

Psalms 89 in the TBT1E2

Psalms 89 in the TFTIP

Psalms 89 in the TFTU

Psalms 89 in the TGNTATF3T

Psalms 89 in the THAI

Psalms 89 in the TNFD

Psalms 89 in the TNT

Psalms 89 in the TNTIK

Psalms 89 in the TNTIL

Psalms 89 in the TNTIN

Psalms 89 in the TNTIP

Psalms 89 in the TNTIZ

Psalms 89 in the TOMA

Psalms 89 in the TTENT

Psalms 89 in the UBG

Psalms 89 in the UGV

Psalms 89 in the UGV2

Psalms 89 in the UGV3

Psalms 89 in the VBL

Psalms 89 in the VDCC

Psalms 89 in the YALU

Psalms 89 in the YAPE

Psalms 89 in the YBVTP

Psalms 89 in the ZBP