Psalms 9 (BOGWICC)
undefined Kwa mtsogoleri wa mayimbidwe. Monga mwa mayimbidwe a nyimbo ya “Imfa ya Mwana.” Salimo la Davide. 1 Ine ndidzakutamandani, Inu Yehova, ndi mtima wanga wonse;ndidzafotokoza za zodabwitsa zanu zonse. 2 Ndidzakondwa ndi kusangalala mwa inu;Ndidzayimba nyimbo zamatamando pa dzina lanu, Inu Wammwambamwamba. 3 Adani anga amathawa,iwo amapunthwa ndi kuwonongedwa pamaso panu. 4 Pakuti Inu mwatsimikiza za kulungama kwanga ndi mlandu wanga;Inu mwakhala pa mpando wanu waufumu, kuweruza mwachilungamo. 5 Mwadzudzula mitundu ya anthu ndipo mwawononga anthu oyipa;Inu mwafafaniza dzina lawo kwamuyaya. 6 Chiwonongeko chosatha chagwera adani,mwafafaniza mizinda yawo;ngakhale chikumbutso chawo chawonongedwa. 7 Yehova akulamulira kwamuyaya;wakhazikitsa mpando wake waufumu woweruzira. 8 Iye adzaweruza dziko mwachilungamo;adzalamulira mitundu ya anthu mosakondera. 9 Yehova ndiye kothawirako kwa opsinjika mtima,linga pa nthawi ya mavuto. 10 Iwo amene amadziwa dzina lanu adzadalira Inu,pakuti Inu Yehova, simunawatayepo amene amafunafuna inu. 11 Imbani nyimbo zamatamando kwa Yehova, ali pa mpando waufumu mu Ziyoni;lengezani pakati pa mitundu ya anthu zimene wachita. 12 Pakuti Iye amene amabwezera chilango akupha anzawo wakumbukira;Iye salekerera kulira kwa ozunzika. 13 Inu Yehova, onani momwe adani anga akundizunzira!Chitireni chifundo ndipo ndichotseni pa zipata za imfa, 14 kuti ndilengeze za matamando anupa zipata za ana aakazi a Ziyoni,kuti pamenepo ndikondwere ndi chipulumutso chanu. 15 Mitundu ya anthu yagwa mʼdzenje limene yakumba;mapazi awo akodwa mu ukonde umene anawubisa. 16 Yehova amadziwika ndi chilungamo chake;oyipa akodwa ndi ntchito za manja awo. Higayoni. Sela 17 Oyipa amabwerera ku manda,mitundu yonse imene imayiwala Mulungu. 18 Koma osowa sadzayiwalika nthawi zonse,kapena chiyembekezo cha ozunzika kutayika nthawi zonse. 19 Dzukani Inu Yehova, musalole munthu kuti apambane;mitundu yonse iweruzidwe pamaso panu. 20 Akantheni ndi mantha aakulu, Inu Yehova;mitundu idziwe kuti iwo ndi anthu wamba. Sela
In Other Versions
Psalms 9 in the ANGEFD
Psalms 9 in the ANTPNG2D
Psalms 9 in the AS21
Psalms 9 in the BAGH
Psalms 9 in the BBPNG
Psalms 9 in the BBT1E
Psalms 9 in the BDS
Psalms 9 in the BEV
Psalms 9 in the BHAD
Psalms 9 in the BIB
Psalms 9 in the BLPT
Psalms 9 in the BNT
Psalms 9 in the BNTABOOT
Psalms 9 in the BNTLV
Psalms 9 in the BOATCB
Psalms 9 in the BOATCB2
Psalms 9 in the BOBCV
Psalms 9 in the BOCNT
Psalms 9 in the BOECS
Psalms 9 in the BOHCB
Psalms 9 in the BOHCV
Psalms 9 in the BOHLNT
Psalms 9 in the BOHNTLTAL
Psalms 9 in the BOICB
Psalms 9 in the BOILNTAP
Psalms 9 in the BOITCV
Psalms 9 in the BOKCV
Psalms 9 in the BOKCV2
Psalms 9 in the BOKHWOG
Psalms 9 in the BOKSSV
Psalms 9 in the BOLCB
Psalms 9 in the BOLCB2
Psalms 9 in the BOMCV
Psalms 9 in the BONAV
Psalms 9 in the BONCB
Psalms 9 in the BONLT
Psalms 9 in the BONUT2
Psalms 9 in the BOPLNT
Psalms 9 in the BOSCB
Psalms 9 in the BOSNC
Psalms 9 in the BOTLNT
Psalms 9 in the BOVCB
Psalms 9 in the BOYCB
Psalms 9 in the BPBB
Psalms 9 in the BPH
Psalms 9 in the BSB
Psalms 9 in the CCB
Psalms 9 in the CUV
Psalms 9 in the CUVS
Psalms 9 in the DBT
Psalms 9 in the DGDNT
Psalms 9 in the DHNT
Psalms 9 in the DNT
Psalms 9 in the ELBE
Psalms 9 in the EMTV
Psalms 9 in the ESV
Psalms 9 in the FBV
Psalms 9 in the FEB
Psalms 9 in the GGMNT
Psalms 9 in the GNT
Psalms 9 in the HARY
Psalms 9 in the HNT
Psalms 9 in the IRVA
Psalms 9 in the IRVB
Psalms 9 in the IRVG
Psalms 9 in the IRVH
Psalms 9 in the IRVK
Psalms 9 in the IRVM
Psalms 9 in the IRVM2
Psalms 9 in the IRVO
Psalms 9 in the IRVP
Psalms 9 in the IRVT
Psalms 9 in the IRVT2
Psalms 9 in the IRVU
Psalms 9 in the ISVN
Psalms 9 in the JSNT
Psalms 9 in the KAPI
Psalms 9 in the KBT1ETNIK
Psalms 9 in the KBV
Psalms 9 in the KJV
Psalms 9 in the KNFD
Psalms 9 in the LBA
Psalms 9 in the LBLA
Psalms 9 in the LNT
Psalms 9 in the LSV
Psalms 9 in the MAAL
Psalms 9 in the MBV
Psalms 9 in the MBV2
Psalms 9 in the MHNT
Psalms 9 in the MKNFD
Psalms 9 in the MNG
Psalms 9 in the MNT
Psalms 9 in the MNT2
Psalms 9 in the MRS1T
Psalms 9 in the NAA
Psalms 9 in the NASB
Psalms 9 in the NBLA
Psalms 9 in the NBS
Psalms 9 in the NBVTP
Psalms 9 in the NET2
Psalms 9 in the NIV11
Psalms 9 in the NNT
Psalms 9 in the NNT2
Psalms 9 in the NNT3
Psalms 9 in the PDDPT
Psalms 9 in the PFNT
Psalms 9 in the RMNT
Psalms 9 in the SBIAS
Psalms 9 in the SBIBS
Psalms 9 in the SBIBS2
Psalms 9 in the SBICS
Psalms 9 in the SBIDS
Psalms 9 in the SBIGS
Psalms 9 in the SBIHS
Psalms 9 in the SBIIS
Psalms 9 in the SBIIS2
Psalms 9 in the SBIIS3
Psalms 9 in the SBIKS
Psalms 9 in the SBIKS2
Psalms 9 in the SBIMS
Psalms 9 in the SBIOS
Psalms 9 in the SBIPS
Psalms 9 in the SBISS
Psalms 9 in the SBITS
Psalms 9 in the SBITS2
Psalms 9 in the SBITS3
Psalms 9 in the SBITS4
Psalms 9 in the SBIUS
Psalms 9 in the SBIVS
Psalms 9 in the SBT
Psalms 9 in the SBT1E
Psalms 9 in the SCHL
Psalms 9 in the SNT
Psalms 9 in the SUSU
Psalms 9 in the SUSU2
Psalms 9 in the SYNO
Psalms 9 in the TBIAOTANT
Psalms 9 in the TBT1E
Psalms 9 in the TBT1E2
Psalms 9 in the TFTIP
Psalms 9 in the TFTU
Psalms 9 in the TGNTATF3T
Psalms 9 in the THAI
Psalms 9 in the TNFD
Psalms 9 in the TNT
Psalms 9 in the TNTIK
Psalms 9 in the TNTIL
Psalms 9 in the TNTIN
Psalms 9 in the TNTIP
Psalms 9 in the TNTIZ
Psalms 9 in the TOMA
Psalms 9 in the TTENT
Psalms 9 in the UBG
Psalms 9 in the UGV
Psalms 9 in the UGV2
Psalms 9 in the UGV3
Psalms 9 in the VBL
Psalms 9 in the VDCC
Psalms 9 in the YALU
Psalms 9 in the YAPE
Psalms 9 in the YBVTP
Psalms 9 in the ZBP