Zechariah 9 (BOGWICC)
1 Mawu a Yehova odzudzula dziko la Hadirakindi mzinda wa Damasikopakuti maso a anthu ndiponso mafuko onse a Israeliali pa Yehova— 2 ndiponso mzinda wa Hamati, umene ukuchita malire ndi dzikoli,komanso pa Turo ndi Sidoni, ngakhale kuti iwo ndi anzeru kwambiri. 3 Ndipo Turo anadzimangira linga;wadziwunjikira siliva ngati fumbi,ndi golide ngati zinyalala za mʼmisewu. 4 Taonani Ambuye adzamulanda chuma chakechondi kuwononga mphamvu zake mʼnyanja,ndipo adzapserera ndi moto. 5 Mzinda wa Asikeloni udzaona zimenezi, nʼkuchita mantha;Gaza adzanjenjemera ndi ululu,chimodzimodzinso Ekroni, chifukwa chiyembekezo chake chidzatheratu.Mfumu ya ku Gaza idzaphedwandipo Asikeloni adzakhala opanda anthu. 6 Mu Asidodi mudzakhala mlendo,ndipo ndidzathetsa kunyada kwa Afilisti. 7 Ndidzachotsa nyama ya magazi mʼkamwa mwawo,chakudya choletsedwa mʼmano mwawo.Amene atsala adzakhala anthu a Mulungu wathu,adzasanduka atsogoleri mu Yuda,ndipo Ekroni adzakhala ngati Ayebusi. 8 Koma Ine ndidzalondera Nyumba yangandi kuyiteteza kwa ankhondo osakaza.Palibenso mdani amene adzagonjetse anthu anga,pakuti tsopano ndikuwayangʼanira. 9 Sangalala kwambiri, iwe mwana wamkazi wa Ziyoni!Fuwula, mwana wamkazi wa Yerusalemu!Taona, mfumu yako ikubwera kwa iwe,yolungama ndi yogonjetsa adani,yodzichepetsa ndi yokwera pa bulu,pa mwana wamphongo wa bulu. 10 Ndidzachotsa magaleta ankhondo ku Efereimundi akavalo ankhondo ku Yerusalemu,ndipo uta wankhondo udzathyoka.Mfumuyo idzabweretsa mtendere pakati pa mitundu ya anthu.Ulamuliro wake udzayambira ku nyanja ina mpaka ku nyanja ina,ndipo kuchokera ku Mtsinje (Yufurate) mpaka ku malekezero a dziko lapansi. 11 Tsono kunena za iwe, chifukwa cha magazi a pangano lako ndi Ine,ndidzamasula amʼndende ako, ndidzawatulutsa mʼdzenje lopanda madzi. 12 Bwererani ku malo anu otetezedwa, inu amʼndende achiyembekezo;ngakhale tsopano ndikulengeza kuti ndidzakubwezerani zabwino mowirikiza. 13 Ndidzakoka Yuda monga ndimakokera uta wanga,ndipo Efereimu ndiye muvi wake.Ndidzadzutsa ana ako iwe Ziyoni,kulimbana ndi ana ako iwe Grisi,ndipo ndidzakusandutsa iwe lupanga la munthu wankhondo. 14 Pamenepo Yehova adzaonekera kwa anthu ake;mivi yake idzangʼanima ngati chingʼaningʼani.Ambuye Yehova adzaliza lipenga;ndipo adzayenda mu mkuntho wochokera kummwera, 15 ndipo Yehova Wamphamvuzonse adzawateteza.Iwo adzawonongandipo adzagonjetsa ndi miyala ya legeni.Adzamwa magazi ndi kubangula ngati amwa vinyo;magazi adzayenderera ngati a mʼmbale yowazira magazipa ngodya za guwa lansembe. 16 Tsiku limenelo Yehova Mulungu wawo adzawapulumutsapakuti anthu ake ali ngati nkhosa.Adzanyezimira mʼdziko lakengati miyala yokongola pa chipewa chaufumu. 17 Taonani chikoka ndi kukongola kwawo!Tirigu adzasangalatsa anyamata,ndi vinyo watsopano anamwali.
In Other Versions
Zechariah 9 in the ANGEFD
Zechariah 9 in the ANTPNG2D
Zechariah 9 in the AS21
Zechariah 9 in the BAGH
Zechariah 9 in the BBPNG
Zechariah 9 in the BBT1E
Zechariah 9 in the BDS
Zechariah 9 in the BEV
Zechariah 9 in the BHAD
Zechariah 9 in the BIB
Zechariah 9 in the BLPT
Zechariah 9 in the BNT
Zechariah 9 in the BNTABOOT
Zechariah 9 in the BNTLV
Zechariah 9 in the BOATCB
Zechariah 9 in the BOATCB2
Zechariah 9 in the BOBCV
Zechariah 9 in the BOCNT
Zechariah 9 in the BOECS
Zechariah 9 in the BOHCB
Zechariah 9 in the BOHCV
Zechariah 9 in the BOHLNT
Zechariah 9 in the BOHNTLTAL
Zechariah 9 in the BOICB
Zechariah 9 in the BOILNTAP
Zechariah 9 in the BOITCV
Zechariah 9 in the BOKCV
Zechariah 9 in the BOKCV2
Zechariah 9 in the BOKHWOG
Zechariah 9 in the BOKSSV
Zechariah 9 in the BOLCB
Zechariah 9 in the BOLCB2
Zechariah 9 in the BOMCV
Zechariah 9 in the BONAV
Zechariah 9 in the BONCB
Zechariah 9 in the BONLT
Zechariah 9 in the BONUT2
Zechariah 9 in the BOPLNT
Zechariah 9 in the BOSCB
Zechariah 9 in the BOSNC
Zechariah 9 in the BOTLNT
Zechariah 9 in the BOVCB
Zechariah 9 in the BOYCB
Zechariah 9 in the BPBB
Zechariah 9 in the BPH
Zechariah 9 in the BSB
Zechariah 9 in the CCB
Zechariah 9 in the CUV
Zechariah 9 in the CUVS
Zechariah 9 in the DBT
Zechariah 9 in the DGDNT
Zechariah 9 in the DHNT
Zechariah 9 in the DNT
Zechariah 9 in the ELBE
Zechariah 9 in the EMTV
Zechariah 9 in the ESV
Zechariah 9 in the FBV
Zechariah 9 in the FEB
Zechariah 9 in the GGMNT
Zechariah 9 in the GNT
Zechariah 9 in the HARY
Zechariah 9 in the HNT
Zechariah 9 in the IRVA
Zechariah 9 in the IRVB
Zechariah 9 in the IRVG
Zechariah 9 in the IRVH
Zechariah 9 in the IRVK
Zechariah 9 in the IRVM
Zechariah 9 in the IRVM2
Zechariah 9 in the IRVO
Zechariah 9 in the IRVP
Zechariah 9 in the IRVT
Zechariah 9 in the IRVT2
Zechariah 9 in the IRVU
Zechariah 9 in the ISVN
Zechariah 9 in the JSNT
Zechariah 9 in the KAPI
Zechariah 9 in the KBT1ETNIK
Zechariah 9 in the KBV
Zechariah 9 in the KJV
Zechariah 9 in the KNFD
Zechariah 9 in the LBA
Zechariah 9 in the LBLA
Zechariah 9 in the LNT
Zechariah 9 in the LSV
Zechariah 9 in the MAAL
Zechariah 9 in the MBV
Zechariah 9 in the MBV2
Zechariah 9 in the MHNT
Zechariah 9 in the MKNFD
Zechariah 9 in the MNG
Zechariah 9 in the MNT
Zechariah 9 in the MNT2
Zechariah 9 in the MRS1T
Zechariah 9 in the NAA
Zechariah 9 in the NASB
Zechariah 9 in the NBLA
Zechariah 9 in the NBS
Zechariah 9 in the NBVTP
Zechariah 9 in the NET2
Zechariah 9 in the NIV11
Zechariah 9 in the NNT
Zechariah 9 in the NNT2
Zechariah 9 in the NNT3
Zechariah 9 in the PDDPT
Zechariah 9 in the PFNT
Zechariah 9 in the RMNT
Zechariah 9 in the SBIAS
Zechariah 9 in the SBIBS
Zechariah 9 in the SBIBS2
Zechariah 9 in the SBICS
Zechariah 9 in the SBIDS
Zechariah 9 in the SBIGS
Zechariah 9 in the SBIHS
Zechariah 9 in the SBIIS
Zechariah 9 in the SBIIS2
Zechariah 9 in the SBIIS3
Zechariah 9 in the SBIKS
Zechariah 9 in the SBIKS2
Zechariah 9 in the SBIMS
Zechariah 9 in the SBIOS
Zechariah 9 in the SBIPS
Zechariah 9 in the SBISS
Zechariah 9 in the SBITS
Zechariah 9 in the SBITS2
Zechariah 9 in the SBITS3
Zechariah 9 in the SBITS4
Zechariah 9 in the SBIUS
Zechariah 9 in the SBIVS
Zechariah 9 in the SBT
Zechariah 9 in the SBT1E
Zechariah 9 in the SCHL
Zechariah 9 in the SNT
Zechariah 9 in the SUSU
Zechariah 9 in the SUSU2
Zechariah 9 in the SYNO
Zechariah 9 in the TBIAOTANT
Zechariah 9 in the TBT1E
Zechariah 9 in the TBT1E2
Zechariah 9 in the TFTIP
Zechariah 9 in the TFTU
Zechariah 9 in the TGNTATF3T
Zechariah 9 in the THAI
Zechariah 9 in the TNFD
Zechariah 9 in the TNT
Zechariah 9 in the TNTIK
Zechariah 9 in the TNTIL
Zechariah 9 in the TNTIN
Zechariah 9 in the TNTIP
Zechariah 9 in the TNTIZ
Zechariah 9 in the TOMA
Zechariah 9 in the TTENT
Zechariah 9 in the UBG
Zechariah 9 in the UGV
Zechariah 9 in the UGV2
Zechariah 9 in the UGV3
Zechariah 9 in the VBL
Zechariah 9 in the VDCC
Zechariah 9 in the YALU
Zechariah 9 in the YAPE
Zechariah 9 in the YBVTP
Zechariah 9 in the ZBP