2 Samuel 9 (BOGWICC)
1 Davide anafunsa kuti, “Kodi alipo amene watsala mʼbanja la Sauli kuti ndimuchitire chifundo chifukwa cha Yonatani?” 2 Tsono panali mtumiki wina wa banja la Sauli wotchedwa Ziba. Iwo anamuyitana kuti aonekere pamaso pa Davide, ndipo mfumu inamufunsa kuti, “Kodi ndiwe Ziba?”Iyeyo anayankha kuti, “Ine mtumiki wanu.” 3 Mfumu inafunsa kuti, “Kodi palibe amene watsala wa banja la Sauli amene ndingamuchitire chifundo cha Mulungu?”Ziba anayankha mfumu kuti, “Alipo mwana wa Yonatani, koma ndi wolumala mapazi ake onse.” 4 Mfumu inafunsa kuti, “Ali kuti?”Ziba anayankha kuti, “Iye ali ku nyumba ya Makiri mwana wa Amieli ku Lodebara.” 5 Kotero mfumu inamubweretsa kuchokera ku Lodebara, ku nyumba ya Makiri mwana wa Amieli. 6 Mefiboseti mwana wa Yonatani, mwana wa Sauli atafika kwa Davide, anawerama pansi kupereka ulemu kwa iye.Davide anati, “Mefiboseti!”Iye anayankha kuti, “Ine mtumiki wanu.” 7 Davide anati kwa iye, “Usachite mantha, pakuti ndidzakuchitira ndithu chifundo chifukwa cha abambo ako Yonatani. Ine ndidzakubwezera iwe dziko lonse limene linali la agogo ako Sauli, ndipo iweyo udzadya ndi ine nthawi zonse.” 8 Mefiboseti anawerama pansi ndipo anati, “Mtumiki wanu ndine yani kuti musamale galu wakufa ngati ine?” 9 Kenaka Davide anayitanitsa Ziba, mtumiki wa Sauli, ndipo anati, “Ine ndapereka kwa chidzukulu cha mbuye wako chilichonse chimene chinali cha Sauli ndi banja lake. 10 Iwe ndi ana ndi antchito anu muzimulimira mʼdziko lake ndipo muzibweretsa zokololazo kuti chidzukulu cha mbuye wako chikhale ndi chakudya. Ndipo Mefiboseti, chidzukulu cha mbuye wako adzadya ndi ine nthawi zonse.” (Tsono Ziba anali ndi ana aamuna khumi ndi asanu ndi antchito makumi awiri). 11 Ndipo Ziba anati kwa mfumu, “Mtumiki wanu adzachita chilichonse chimene mbuye wanga mfumu mudzalamulire wantchito wanu kuti achite.” Kotero Mefiboseti ankadya ndi Davide monga mmodzi wa ana a mfumu. 12 Mefiboseti anali ndi mwana wamngʼono wamwamuna wotchedwa Mika, ndipo onse a banja la Ziba anali antchito a Mefiboseti. 13 Ndipo Mefiboseti anakhala mu Yerusalemu chifukwa nthawi zonse amadya ndi mfumu. Iye anali wolumala mapazi ake onse.
In Other Versions
2 Samuel 9 in the ANGEFD
2 Samuel 9 in the ANTPNG2D
2 Samuel 9 in the AS21
2 Samuel 9 in the BAGH
2 Samuel 9 in the BBPNG
2 Samuel 9 in the BBT1E
2 Samuel 9 in the BDS
2 Samuel 9 in the BEV
2 Samuel 9 in the BHAD
2 Samuel 9 in the BIB
2 Samuel 9 in the BLPT
2 Samuel 9 in the BNT
2 Samuel 9 in the BNTABOOT
2 Samuel 9 in the BNTLV
2 Samuel 9 in the BOATCB
2 Samuel 9 in the BOATCB2
2 Samuel 9 in the BOBCV
2 Samuel 9 in the BOCNT
2 Samuel 9 in the BOECS
2 Samuel 9 in the BOHCB
2 Samuel 9 in the BOHCV
2 Samuel 9 in the BOHLNT
2 Samuel 9 in the BOHNTLTAL
2 Samuel 9 in the BOICB
2 Samuel 9 in the BOILNTAP
2 Samuel 9 in the BOITCV
2 Samuel 9 in the BOKCV
2 Samuel 9 in the BOKCV2
2 Samuel 9 in the BOKHWOG
2 Samuel 9 in the BOKSSV
2 Samuel 9 in the BOLCB
2 Samuel 9 in the BOLCB2
2 Samuel 9 in the BOMCV
2 Samuel 9 in the BONAV
2 Samuel 9 in the BONCB
2 Samuel 9 in the BONLT
2 Samuel 9 in the BONUT2
2 Samuel 9 in the BOPLNT
2 Samuel 9 in the BOSCB
2 Samuel 9 in the BOSNC
2 Samuel 9 in the BOTLNT
2 Samuel 9 in the BOVCB
2 Samuel 9 in the BOYCB
2 Samuel 9 in the BPBB
2 Samuel 9 in the BPH
2 Samuel 9 in the BSB
2 Samuel 9 in the CCB
2 Samuel 9 in the CUV
2 Samuel 9 in the CUVS
2 Samuel 9 in the DBT
2 Samuel 9 in the DGDNT
2 Samuel 9 in the DHNT
2 Samuel 9 in the DNT
2 Samuel 9 in the ELBE
2 Samuel 9 in the EMTV
2 Samuel 9 in the ESV
2 Samuel 9 in the FBV
2 Samuel 9 in the FEB
2 Samuel 9 in the GGMNT
2 Samuel 9 in the GNT
2 Samuel 9 in the HARY
2 Samuel 9 in the HNT
2 Samuel 9 in the IRVA
2 Samuel 9 in the IRVB
2 Samuel 9 in the IRVG
2 Samuel 9 in the IRVH
2 Samuel 9 in the IRVK
2 Samuel 9 in the IRVM
2 Samuel 9 in the IRVM2
2 Samuel 9 in the IRVO
2 Samuel 9 in the IRVP
2 Samuel 9 in the IRVT
2 Samuel 9 in the IRVT2
2 Samuel 9 in the IRVU
2 Samuel 9 in the ISVN
2 Samuel 9 in the JSNT
2 Samuel 9 in the KAPI
2 Samuel 9 in the KBT1ETNIK
2 Samuel 9 in the KBV
2 Samuel 9 in the KJV
2 Samuel 9 in the KNFD
2 Samuel 9 in the LBA
2 Samuel 9 in the LBLA
2 Samuel 9 in the LNT
2 Samuel 9 in the LSV
2 Samuel 9 in the MAAL
2 Samuel 9 in the MBV
2 Samuel 9 in the MBV2
2 Samuel 9 in the MHNT
2 Samuel 9 in the MKNFD
2 Samuel 9 in the MNG
2 Samuel 9 in the MNT
2 Samuel 9 in the MNT2
2 Samuel 9 in the MRS1T
2 Samuel 9 in the NAA
2 Samuel 9 in the NASB
2 Samuel 9 in the NBLA
2 Samuel 9 in the NBS
2 Samuel 9 in the NBVTP
2 Samuel 9 in the NET2
2 Samuel 9 in the NIV11
2 Samuel 9 in the NNT
2 Samuel 9 in the NNT2
2 Samuel 9 in the NNT3
2 Samuel 9 in the PDDPT
2 Samuel 9 in the PFNT
2 Samuel 9 in the RMNT
2 Samuel 9 in the SBIAS
2 Samuel 9 in the SBIBS
2 Samuel 9 in the SBIBS2
2 Samuel 9 in the SBICS
2 Samuel 9 in the SBIDS
2 Samuel 9 in the SBIGS
2 Samuel 9 in the SBIHS
2 Samuel 9 in the SBIIS
2 Samuel 9 in the SBIIS2
2 Samuel 9 in the SBIIS3
2 Samuel 9 in the SBIKS
2 Samuel 9 in the SBIKS2
2 Samuel 9 in the SBIMS
2 Samuel 9 in the SBIOS
2 Samuel 9 in the SBIPS
2 Samuel 9 in the SBISS
2 Samuel 9 in the SBITS
2 Samuel 9 in the SBITS2
2 Samuel 9 in the SBITS3
2 Samuel 9 in the SBITS4
2 Samuel 9 in the SBIUS
2 Samuel 9 in the SBIVS
2 Samuel 9 in the SBT
2 Samuel 9 in the SBT1E
2 Samuel 9 in the SCHL
2 Samuel 9 in the SNT
2 Samuel 9 in the SUSU
2 Samuel 9 in the SUSU2
2 Samuel 9 in the SYNO
2 Samuel 9 in the TBIAOTANT
2 Samuel 9 in the TBT1E
2 Samuel 9 in the TBT1E2
2 Samuel 9 in the TFTIP
2 Samuel 9 in the TFTU
2 Samuel 9 in the TGNTATF3T
2 Samuel 9 in the THAI
2 Samuel 9 in the TNFD
2 Samuel 9 in the TNT
2 Samuel 9 in the TNTIK
2 Samuel 9 in the TNTIL
2 Samuel 9 in the TNTIN
2 Samuel 9 in the TNTIP
2 Samuel 9 in the TNTIZ
2 Samuel 9 in the TOMA
2 Samuel 9 in the TTENT
2 Samuel 9 in the UBG
2 Samuel 9 in the UGV
2 Samuel 9 in the UGV2
2 Samuel 9 in the UGV3
2 Samuel 9 in the VBL
2 Samuel 9 in the VDCC
2 Samuel 9 in the YALU
2 Samuel 9 in the YAPE
2 Samuel 9 in the YBVTP
2 Samuel 9 in the ZBP