Isaiah 10 (BOGWICC)

1 Tsoka kwa anthu amene amapanga malamulo opanda chilungamo,kwa iwo amene amalemba zongovutitsa anzawo, 2 kuwalanda anthu osauka ufulu wawondi kumana chilungamo osautsidwa pakati pa anthu anga,amalanda zinthu za akazi amasiyendi kubera ana amasiye. 3 Kodi mudzatani pa tsiku la chilango,pofika chiwonongeko chochokera kutali?Kodi mudzathawira kwa yani kuti akuthandizeni?Nanga chuma chanu mudzachisiya kuti? 4 Kudzatsala nʼkungozolika mwamanyazi pakati pa anthu ogwidwakapena kufa pamodzi ndi ophedwa.Komabe pa zonsezi mkwiyo wake sunawachokere,mkono wake uli chitambasulire. 5 “Tsoka kwa mfumu ya ku Asiriya, chikwapu cha mkwiyo wanga,iye ndiye ndodo ya mkwiyo wanga! 6 Ndidzamutuma kukalimbana ndi mtundu wosapembedza Mulungu,ndidzamutumiza kukalimbana ndi anthu amene amandikwiyitsa Ine,kukafunkha ndi kulanda chuma,ndi kuwapondereza pansi ngati matope a mʼmisewu. 7 Koma izi si zimene akufuna kukachita,izi si zimene zili mʼmaganizo mwake;cholinga chake ndi kukawononga,kukapulula mitundu yambiri ya anthu. 8 Iye akuti, ‘Kodi atsogoleri anga ankhondo si mafumu okhaokha?’ 9 ‘Kodi Kalino sanagonjetsedwe monga Karikemesi?Kodi Hamati sali ngati Aripadi,nanga Samariya sali ngati Damasiko? 10 Dzanja langa linakantha maufumu a anthu opembedza mafano,mafumu amene mafano awo ndi aakulu kupambana Yerusalemu ndi Samariya; 11 nanga Ine nʼkulephera kodi kuwononga Yerusalemu pamodzi ndi mafano akemonga ndinakanthira Samariya pamodzi ndi mafano ake?’ ” 12 Ambuye akadzamaliza ntchito yonse yolanga phiri la Ziyoni ndi Yerusalemu adzalanganso mfumu ya ku Asiriya chifukwa cha kudzitama ndi kunyada kwake. 13 Pakuti mfumuyo ikuti,“ ‘Ndachita zimenezi ndi dzanja langa,ndiponso ndi nzeru zanga, chifukwa ndine wozindikira zinthu.Ndinachotsa malire a mitundu ya anthu,ndinafunkha chuma chawo;ndinagonjetsa mafumu awo monga munthu wamphamvu. 14 Dzanja langa lagwira chuma cha mitundu ya anthungati momwe munthu amagwirira chisa cha mbalame,ngati momwe anthu amatolera mazira osiyidwa,motero inenso ndinasonkhanitsa mayiko onse;palibe mbalame imene inakupiza mapiko ake,kapena kuyasama kukamwa kuti ilire.’ ” 15 Kodi nkhwangwa ingathe kudzikuza kupambana woyigwiritsa ntchito,kapena macheka angathe kudzikuza kupambana wowagwiritsa ntchito?Ndiye kukhala ngati kuti chikwapu chikuzunguza munthu amene wachinyamula,kapena ngati kuti ndodo ikuopseza amene wayinyamula! 16 Nʼchifukwa chake Ambuye Yehova Wamphamvuzonseadzatumiza matenda owondetsa kwa ankhondo amphamvu;kunyada kwa mfumuyo kudzapsandi moto wosazima. 17 Mulungu, Kuwala kwa Israeli, adzakhala ngati moto,Woyera uja wa Israeli adzakhala ngati malawi a moto.Motowo udzawatentha ndi kuwapserezangati minga ndi mkandankhuku pa tsiku limodzi. 18 Ankhondo ake adzawonongedwangati nkhalango yayikulundi ngati nthaka yachonde. 19 Mitengo yotsalira ya mʼnkhalango zake idzakhala yochepa kwambiri,yoti ndi mwana yemwe ndi kuyiwerenga. 20 Tsiku limenelo otsalira a ku Israeli,opulumuka a nyumba ya Yakobo,sadzadaliranso anthuamene anawakantha,koma adzadalira Yehova,Woyerayo wa Israeli. 21 Otsalira adzabwerera, otsalira a Yakoboadzabwerera kwa Mulungu Wamphamvu. 22 Iwe Israeli, ngakhale anthu ako achuluke ngati mchenga wa ku nyanja,otsala okha ndiwo adzabwerere.Chiwonongeko chalamulidwa,chidzaonetsa chilungamo chosefukira. 23 Ambuye Yehova Wamphamvuzonse adzawononga ndithu dziko lonsemonga momwe analamulira. 24 Nʼchifukwa chake, Ambuye Yehova Wamphamvuzonse akunena kuti,“Inu anthu anga okhala mu Ziyoni,musawaope Asiriya,amene amakukanthani ndi ndodonakumenyani ndi zibonga monga mmene Igupto anachitira. 25 Patsala pangʼonongʼono kuti mkwiyo wanga uchoke pa inundipo ndidzaonetsa ukali wanga pa iwo mpaka kuwawononga.” 26 Yehova Wamphamvuzonse adzawakwapula ndi chikwapu,monga momwe anakwapulira Amidiyani ku thanthwe la Orebu;ndipo adzatukula ndodo yake pa madzindikuwalanga monga analangira Igupto pa nyanja. 27 Tsiku limenelo katundu wawo adzachotsedwa pa mapewa anu,goli lawo lidzachoka mʼkhosi mwanu;golilo lidzathyokachifukwa cha kunenepa kwambiri. 28 Adani alowa mu Ayatiapyola ku Migironi;asunga katundu wawo ku Mikimasi. 29 Adutsa pa mpata uja, ndipo akuti,“Tikagona ku Geba”Rama akunjenjemera;Gibeya, mzinda wa Saulo ukuthawa. 30 Lilani mokweza, inu anthu a ku Galimu!Tchera khutu, iwe Laisa!Iwe Anatoti wosauka! 31 Anthu a ku Madimena akuthawa;anthu a ku Gebimu bisalani. 32 Lero lomwe lino adaniwo adzayima ku Nobu;adzagwedeza mikono yawo,kuopseza anthu a ku Ziyoni,pa phiri la Yerusalemu. 33 Taonani, Ambuye Yehova Wamphamvuzonse,adzadula mwamphamvu nthambi za mitengo,mitengo yodzikweza idzadulidwa,mitengo yayitali idzagwetsedwa. 34 Yehova adzadula ndi nkhwangwa mitengo ya mʼnkhalango yowirira;Lebanoni adzagwa pamaso pa Wamphamvu.

In Other Versions

Isaiah 10 in the ANGEFD

Isaiah 10 in the ANTPNG2D

Isaiah 10 in the AS21

Isaiah 10 in the BAGH

Isaiah 10 in the BBPNG

Isaiah 10 in the BBT1E

Isaiah 10 in the BDS

Isaiah 10 in the BEV

Isaiah 10 in the BHAD

Isaiah 10 in the BIB

Isaiah 10 in the BLPT

Isaiah 10 in the BNT

Isaiah 10 in the BNTABOOT

Isaiah 10 in the BNTLV

Isaiah 10 in the BOATCB

Isaiah 10 in the BOATCB2

Isaiah 10 in the BOBCV

Isaiah 10 in the BOCNT

Isaiah 10 in the BOECS

Isaiah 10 in the BOHCB

Isaiah 10 in the BOHCV

Isaiah 10 in the BOHLNT

Isaiah 10 in the BOHNTLTAL

Isaiah 10 in the BOICB

Isaiah 10 in the BOILNTAP

Isaiah 10 in the BOITCV

Isaiah 10 in the BOKCV

Isaiah 10 in the BOKCV2

Isaiah 10 in the BOKHWOG

Isaiah 10 in the BOKSSV

Isaiah 10 in the BOLCB

Isaiah 10 in the BOLCB2

Isaiah 10 in the BOMCV

Isaiah 10 in the BONAV

Isaiah 10 in the BONCB

Isaiah 10 in the BONLT

Isaiah 10 in the BONUT2

Isaiah 10 in the BOPLNT

Isaiah 10 in the BOSCB

Isaiah 10 in the BOSNC

Isaiah 10 in the BOTLNT

Isaiah 10 in the BOVCB

Isaiah 10 in the BOYCB

Isaiah 10 in the BPBB

Isaiah 10 in the BPH

Isaiah 10 in the BSB

Isaiah 10 in the CCB

Isaiah 10 in the CUV

Isaiah 10 in the CUVS

Isaiah 10 in the DBT

Isaiah 10 in the DGDNT

Isaiah 10 in the DHNT

Isaiah 10 in the DNT

Isaiah 10 in the ELBE

Isaiah 10 in the EMTV

Isaiah 10 in the ESV

Isaiah 10 in the FBV

Isaiah 10 in the FEB

Isaiah 10 in the GGMNT

Isaiah 10 in the GNT

Isaiah 10 in the HARY

Isaiah 10 in the HNT

Isaiah 10 in the IRVA

Isaiah 10 in the IRVB

Isaiah 10 in the IRVG

Isaiah 10 in the IRVH

Isaiah 10 in the IRVK

Isaiah 10 in the IRVM

Isaiah 10 in the IRVM2

Isaiah 10 in the IRVO

Isaiah 10 in the IRVP

Isaiah 10 in the IRVT

Isaiah 10 in the IRVT2

Isaiah 10 in the IRVU

Isaiah 10 in the ISVN

Isaiah 10 in the JSNT

Isaiah 10 in the KAPI

Isaiah 10 in the KBT1ETNIK

Isaiah 10 in the KBV

Isaiah 10 in the KJV

Isaiah 10 in the KNFD

Isaiah 10 in the LBA

Isaiah 10 in the LBLA

Isaiah 10 in the LNT

Isaiah 10 in the LSV

Isaiah 10 in the MAAL

Isaiah 10 in the MBV

Isaiah 10 in the MBV2

Isaiah 10 in the MHNT

Isaiah 10 in the MKNFD

Isaiah 10 in the MNG

Isaiah 10 in the MNT

Isaiah 10 in the MNT2

Isaiah 10 in the MRS1T

Isaiah 10 in the NAA

Isaiah 10 in the NASB

Isaiah 10 in the NBLA

Isaiah 10 in the NBS

Isaiah 10 in the NBVTP

Isaiah 10 in the NET2

Isaiah 10 in the NIV11

Isaiah 10 in the NNT

Isaiah 10 in the NNT2

Isaiah 10 in the NNT3

Isaiah 10 in the PDDPT

Isaiah 10 in the PFNT

Isaiah 10 in the RMNT

Isaiah 10 in the SBIAS

Isaiah 10 in the SBIBS

Isaiah 10 in the SBIBS2

Isaiah 10 in the SBICS

Isaiah 10 in the SBIDS

Isaiah 10 in the SBIGS

Isaiah 10 in the SBIHS

Isaiah 10 in the SBIIS

Isaiah 10 in the SBIIS2

Isaiah 10 in the SBIIS3

Isaiah 10 in the SBIKS

Isaiah 10 in the SBIKS2

Isaiah 10 in the SBIMS

Isaiah 10 in the SBIOS

Isaiah 10 in the SBIPS

Isaiah 10 in the SBISS

Isaiah 10 in the SBITS

Isaiah 10 in the SBITS2

Isaiah 10 in the SBITS3

Isaiah 10 in the SBITS4

Isaiah 10 in the SBIUS

Isaiah 10 in the SBIVS

Isaiah 10 in the SBT

Isaiah 10 in the SBT1E

Isaiah 10 in the SCHL

Isaiah 10 in the SNT

Isaiah 10 in the SUSU

Isaiah 10 in the SUSU2

Isaiah 10 in the SYNO

Isaiah 10 in the TBIAOTANT

Isaiah 10 in the TBT1E

Isaiah 10 in the TBT1E2

Isaiah 10 in the TFTIP

Isaiah 10 in the TFTU

Isaiah 10 in the TGNTATF3T

Isaiah 10 in the THAI

Isaiah 10 in the TNFD

Isaiah 10 in the TNT

Isaiah 10 in the TNTIK

Isaiah 10 in the TNTIL

Isaiah 10 in the TNTIN

Isaiah 10 in the TNTIP

Isaiah 10 in the TNTIZ

Isaiah 10 in the TOMA

Isaiah 10 in the TTENT

Isaiah 10 in the UBG

Isaiah 10 in the UGV

Isaiah 10 in the UGV2

Isaiah 10 in the UGV3

Isaiah 10 in the VBL

Isaiah 10 in the VDCC

Isaiah 10 in the YALU

Isaiah 10 in the YAPE

Isaiah 10 in the YBVTP

Isaiah 10 in the ZBP