Isaiah 9 (BOGWICC)
1 Anthu amene anali ndi nkhawa, sadzakhalanso otaya mtima. Masiku amakedzana Mulungu ananyozetsa dziko la Zebuloni ndi dziko la Nafutali, koma kutsogolo kuno dera lonse la Galileya, limene lili dziko la anthu a mitundu ina, kuyambira ku nyanja yayikulu, mʼmbali mwa Yorodani, adzalisandutsa laulemu. 2 Anthu oyenda mu mdimaawona kuwala kwakukulu;kwa iwo okhala mʼdziko la mdima wandiweyanikuwunika kwawafikira. 3 Inu mwauchulukitsa mtundu wanundipo mwawonjezera chimwemwe chawo.Iwo akukondwa pamaso panu,ngati mmene anthu amakondwera nthawi yokolola,ngatinso mmene anthu amakondwerapamene akugawana zolanda ku nkhondo. 4 Monga munachitira pogonjetsa Amidiyani,inu mwathyola golilimene limawalemera,ndodo zimene amamenyera mapewa awo,ndiponso mikwapulo ya anthu owazunza. 5 Nsapato iliyonse ya munthu wankhondo,ndiponso chovala chilichonse chodonthekera magazizidzatenthedwa pa motongati nkhuni. 6 Chifukwa mwana watibadwira,mwana wamwamuna wapatsidwa kwa ife,ndipo ulamuliro udzakhala pa phewa lake.Ndipo adzamutcha dzina lake lakutiPhungu Wodabwitsa, Mulungu Wamphamvu,Atate Amuyaya, ndi Mfumu ya Mtendere. 7 Ulamuliro ndi mtendere wakezidzakhala zopanda malire.Iye adzalamulira ufumu wake ali pampando waufumu wa Davide,ndipo adzawukhazikitsa ndi kuwuchirikizamwa chiweruzo cholungama ndi pochita zachilungamokuyambira nthawi imeneyo mpaka muyaya.Ndi mtima wake wonse, Yehova Wamphamvuzonsewatsimikiza kuchita zimenezi. 8 Ambuye atumiza mawu otsutsa Yakobo;ndipo mawuwo agwera pa Israeli. 9 Anthu onse okhala muEfereimu ndi okhala mu Samariya,adzadziwa zimenezi.Iwo amayankhula modzikuza kuti, 10 “Ngakhale njerwa zagumuka,koma ife tidzamanga ndi miyala yosema.Mitanda ya mkuyu yagwetsedwa,koma ife tidzayika mitanda ya mkungudza mʼmalo mwake.” 11 Koma Yehova wadzutsa adani kuti alimbane nawondipo wawafulumiza adani awo kuti amenyane nawo. 12 Asiriya ochokera kummawa ndi Afilisti ochokera kumadzulo ndipoayasama pakamwa kuti adye a Israeli. Komabe, mkwiyo wake sunawachokere,mkono wake uli chitambasulire. 13 Koma anthu sanabwerere kwa amene anawakantha uja,ngakhale kufunafuna Yehova Wamphamvuzonse. 14 Choncho Yehova adzadula mutu wa Israeli pamodzi ndi mchira womwe,nthambi ya kanjedza ndi bango lomwe tsiku limodzi; 15 mutuwo ndiye akuluakulu ndi olemekezeka,mchira ndiye aneneri ophunzitsa zabodza. 16 Amene amatsogolera anthuwa ndiwo amawasocheretsa,ndipo otsogoleredwa amatayika. 17 Nʼchifukwa chake Ambuye adzakondwera nawo achinyamata,ngakhale kuwachitira chifundo ana amasiye ndi akazi amasiye,pakuti aliyense ndi wosapembedza Mulungu ndiponso ndi wochimwa ndipoaliyense amayankhula zopusa. Komabe, mkwiyo wake sunawachokere,mkono wake uli chitambasulire. 18 Ndithu kuyipa kwa anthuwo kumayaka ngati moto;moto wake umanyeketsa mkandankhuku ndi minga,umayatsa nkhalango yowirira,ndipo utsi wake umachita kuti toloo ngati mtambo. 19 Dziko lidzatenthedwa ndi ukali wa Yehova Wamphamvuzonse,dziko lidzatenthedwandipo anthu adzakhala ngati nkhuni zosonkhera moto;palibe munthu amene adzachitire chifundo mʼbale wake. 20 Kudzanja lamanja adzapeza chakudya nʼkudya,koma adzakhalabe ndi njala;kudzanja lamanzere adzapeza chakudya nʼkudya,koma sadzakhuta.Aliyense azidzadya ana ake omwe. 21 Manase adzadya Efereimu ndipo Efereimu adzadya Manase;onsewa pamodzi adzadya Yuda. Komabe pa zonsezi, mkwiyo wake sunawachokere,mkono wake uli chitambasulire.
In Other Versions
Isaiah 9 in the ANGEFD
Isaiah 9 in the ANTPNG2D
Isaiah 9 in the AS21
Isaiah 9 in the BAGH
Isaiah 9 in the BBPNG
Isaiah 9 in the BBT1E
Isaiah 9 in the BDS
Isaiah 9 in the BEV
Isaiah 9 in the BHAD
Isaiah 9 in the BIB
Isaiah 9 in the BLPT
Isaiah 9 in the BNT
Isaiah 9 in the BNTABOOT
Isaiah 9 in the BNTLV
Isaiah 9 in the BOATCB
Isaiah 9 in the BOATCB2
Isaiah 9 in the BOBCV
Isaiah 9 in the BOCNT
Isaiah 9 in the BOECS
Isaiah 9 in the BOHCB
Isaiah 9 in the BOHCV
Isaiah 9 in the BOHLNT
Isaiah 9 in the BOHNTLTAL
Isaiah 9 in the BOICB
Isaiah 9 in the BOILNTAP
Isaiah 9 in the BOITCV
Isaiah 9 in the BOKCV
Isaiah 9 in the BOKCV2
Isaiah 9 in the BOKHWOG
Isaiah 9 in the BOKSSV
Isaiah 9 in the BOLCB
Isaiah 9 in the BOLCB2
Isaiah 9 in the BOMCV
Isaiah 9 in the BONAV
Isaiah 9 in the BONCB
Isaiah 9 in the BONLT
Isaiah 9 in the BONUT2
Isaiah 9 in the BOPLNT
Isaiah 9 in the BOSCB
Isaiah 9 in the BOSNC
Isaiah 9 in the BOTLNT
Isaiah 9 in the BOVCB
Isaiah 9 in the BOYCB
Isaiah 9 in the BPBB
Isaiah 9 in the BPH
Isaiah 9 in the BSB
Isaiah 9 in the CCB
Isaiah 9 in the CUV
Isaiah 9 in the CUVS
Isaiah 9 in the DBT
Isaiah 9 in the DGDNT
Isaiah 9 in the DHNT
Isaiah 9 in the DNT
Isaiah 9 in the ELBE
Isaiah 9 in the EMTV
Isaiah 9 in the ESV
Isaiah 9 in the FBV
Isaiah 9 in the FEB
Isaiah 9 in the GGMNT
Isaiah 9 in the GNT
Isaiah 9 in the HARY
Isaiah 9 in the HNT
Isaiah 9 in the IRVA
Isaiah 9 in the IRVB
Isaiah 9 in the IRVG
Isaiah 9 in the IRVH
Isaiah 9 in the IRVK
Isaiah 9 in the IRVM
Isaiah 9 in the IRVM2
Isaiah 9 in the IRVO
Isaiah 9 in the IRVP
Isaiah 9 in the IRVT
Isaiah 9 in the IRVT2
Isaiah 9 in the IRVU
Isaiah 9 in the ISVN
Isaiah 9 in the JSNT
Isaiah 9 in the KAPI
Isaiah 9 in the KBT1ETNIK
Isaiah 9 in the KBV
Isaiah 9 in the KJV
Isaiah 9 in the KNFD
Isaiah 9 in the LBA
Isaiah 9 in the LBLA
Isaiah 9 in the LNT
Isaiah 9 in the LSV
Isaiah 9 in the MAAL
Isaiah 9 in the MBV
Isaiah 9 in the MBV2
Isaiah 9 in the MHNT
Isaiah 9 in the MKNFD
Isaiah 9 in the MNG
Isaiah 9 in the MNT
Isaiah 9 in the MNT2
Isaiah 9 in the MRS1T
Isaiah 9 in the NAA
Isaiah 9 in the NASB
Isaiah 9 in the NBLA
Isaiah 9 in the NBS
Isaiah 9 in the NBVTP
Isaiah 9 in the NET2
Isaiah 9 in the NIV11
Isaiah 9 in the NNT
Isaiah 9 in the NNT2
Isaiah 9 in the NNT3
Isaiah 9 in the PDDPT
Isaiah 9 in the PFNT
Isaiah 9 in the RMNT
Isaiah 9 in the SBIAS
Isaiah 9 in the SBIBS
Isaiah 9 in the SBIBS2
Isaiah 9 in the SBICS
Isaiah 9 in the SBIDS
Isaiah 9 in the SBIGS
Isaiah 9 in the SBIHS
Isaiah 9 in the SBIIS
Isaiah 9 in the SBIIS2
Isaiah 9 in the SBIIS3
Isaiah 9 in the SBIKS
Isaiah 9 in the SBIKS2
Isaiah 9 in the SBIMS
Isaiah 9 in the SBIOS
Isaiah 9 in the SBIPS
Isaiah 9 in the SBISS
Isaiah 9 in the SBITS
Isaiah 9 in the SBITS2
Isaiah 9 in the SBITS3
Isaiah 9 in the SBITS4
Isaiah 9 in the SBIUS
Isaiah 9 in the SBIVS
Isaiah 9 in the SBT
Isaiah 9 in the SBT1E
Isaiah 9 in the SCHL
Isaiah 9 in the SNT
Isaiah 9 in the SUSU
Isaiah 9 in the SUSU2
Isaiah 9 in the SYNO
Isaiah 9 in the TBIAOTANT
Isaiah 9 in the TBT1E
Isaiah 9 in the TBT1E2
Isaiah 9 in the TFTIP
Isaiah 9 in the TFTU
Isaiah 9 in the TGNTATF3T
Isaiah 9 in the THAI
Isaiah 9 in the TNFD
Isaiah 9 in the TNT
Isaiah 9 in the TNTIK
Isaiah 9 in the TNTIL
Isaiah 9 in the TNTIN
Isaiah 9 in the TNTIP
Isaiah 9 in the TNTIZ
Isaiah 9 in the TOMA
Isaiah 9 in the TTENT
Isaiah 9 in the UBG
Isaiah 9 in the UGV
Isaiah 9 in the UGV2
Isaiah 9 in the UGV3
Isaiah 9 in the VBL
Isaiah 9 in the VDCC
Isaiah 9 in the YALU
Isaiah 9 in the YAPE
Isaiah 9 in the YBVTP
Isaiah 9 in the ZBP