Jeremiah 15 (BOGWICC)

1 Kenaka Yehova anandiwuza kuti, “Ngakhale Mose ndi Samueli akanayima pamaso panga kupempherera anthu awa, Ine sindikanawachitira chisoni. Achotseni ndipo ndisawaonenso! Aleke apite! 2 Ndipo ngati akufunsa iwe kuti, ‘Kodi tipite kuti?’ uwawuze kuti, ‘Yehova akuti,“ ‘Oyenera kufa adzafa;oyenera kufa ndi lupanga adzafa ndi lupanga;oyenera kufa ndi njala adzafa ndi njala;oyenera kupita ku ukapolo adzapita ku ukapolo.’ 3 “Ine ndidzawatumizira mitundu inayi ya zinthu zowononga,” akutero Yehova, “lupanga lowapha, agalu owaluma, mbalame zamumlengalenga ndiponso zirombo zoti ziwadye ndi kuwawononga. 4 Ndidzawasandutsa kukhala chinthu chonyansa kwa anthu a maufumu onse a dziko lapansi chifukwa cha zimene Manase mwana wa Hezekiya mfumu ya Yuda anachita mu Yerusalemu. 5 “Kodi adzakumvera chisoni ndani, Yerusalemu?Kodi adzakulira ndani?Kodi ndani amene adzapatuka kufunsa za moyo wako? 6 Inu mwandikana Ine,” akutero Yehova.“Inu mukubwererabe mʼmbuyo.Choncho Ine ndidzakukanthani.Ndatopa ndi kukuchitirani chifundo. 7 Ine ndidzakubalalitsani kukuchotsani mʼmizinda ya mʼdzikomomonga mmene amachitira ndi mankhusu popeta ndi lichero.Anthu anga ndinawaliritsa ndi kuwawonongachifukwa sanasinthe makhalidwe awo oyipa. 8 Ndinachulukitsa amayi awo amasiyekupambana mchenga wa kunyanja.Amayiwo ndinawawonongera ana awo aamunadzuwa lili pamutu.Mwadzidzidzi ndinawagwetserakuwawa mtima ndi mantha. 9 Mayi wa ana asanu ndi awiri wakomokandipo akupuma wefuwefu.Dzuwa lake lalowa ukanali usana;anamuchititsa manyazi ndipo wathedwa nzeru.Otsala ndidzawapereka mʼmanja mwa adani awokuti awaphe ndi lupanga,”akutero Yehova. 10 Kalanga ine, amayi pakuti munandibereka ine,munthu amene ndikutsutsana ndi kulimbana ndi anthu pa dziko lonse!Ine sindinakongoze kapena kukongola kanthu,komatu aliyense akunditemberera. 11 Yehova anati,“Ndithudi, Ine ndidzakulanditsa kuti upeze bwino.Ndithudi, adani ako adzakupempha pa nthawi ya tsokandi ya mavuto awo. 12 “Palibe munthu amene angathe kudula chitsulo,makamaka chitsulo chochokera kumpoto chosakaniza ndi mkuwa. 13 Anthu ako ndi chuma chakondidzazipereka kwa ofunkha popanda malipiro,chifukwa cha machimo anu onsea mʼdziko lanu lonse. 14 Ndidzakusandutsani akapolo a adani anumʼdziko limene inu simulidziwa,chifukwa mkwiyo wanga wayaka ngati motoumene udzakutenthani.” 15 Ine ndinati, “Inu Yehova, mumadziwa zonse;kumbukireni ndi kundisamalira.Ndilipsireni anthu ondizunza.Ndilezereni mtima musandilande moyo wanga.Onani momwe ndi kuvutikira chifukwa cha Inu. 16 Munandiyankhula ndipo mawu anu ndinawalandira bwino.Mawu anu anandipatsa chimwemwe ndipo mtima wanga unasangalala.Paja ine, Yehova Mulungu Wamphamvuzonse,ndimadziwika ndi dzina lanu. 17 Sindinakhale nawo mʼgulu la anthu amadyera,sindinasangalale nawo anthu amenewo.Ndinakhala ndekha chifukwa choti dzanja lanu linali pa inendipo munadzaza mu mtima mwanga ndi mkwiyo. 18 Nanga nʼchifukwa chiyani mavuto anga sakutha?Bwanji chilonda changa sichikupola?Kodi inu mudzakhala ngati mtsinje wowuma nthawi yachilimwe,kapena ngati kasupe wopanda madzi?” 19 Tsono Yehova anandiyankha kuti,“Ukabwerera kwa Ine, ndidzakulandiransondipo udzakhalanso mtumiki wanga.Ngati udzayankhula mawu oyenera osati achabechabe,udzakhalanso mneneri wanga.Anthu adzabwera kwa iwendipo sipadzafunika kuti iwe upite kwa iwo. 20 Ndidzakusandutsa ngati khoma lolimbangati mkuwa kwa anthu awa.Adzalimbana nawekoma sadzakugonjetsa,pakuti Ine ndili nawekukulanditsa ndi kukupulumutsa,”akutero Yehova. 21 “Ndidzakupulumutsa mʼdzanja la anthu oyipandipo ndidzakuwombola kwa anthu ankhanza.”

In Other Versions

Jeremiah 15 in the ANGEFD

Jeremiah 15 in the ANTPNG2D

Jeremiah 15 in the AS21

Jeremiah 15 in the BAGH

Jeremiah 15 in the BBPNG

Jeremiah 15 in the BBT1E

Jeremiah 15 in the BDS

Jeremiah 15 in the BEV

Jeremiah 15 in the BHAD

Jeremiah 15 in the BIB

Jeremiah 15 in the BLPT

Jeremiah 15 in the BNT

Jeremiah 15 in the BNTABOOT

Jeremiah 15 in the BNTLV

Jeremiah 15 in the BOATCB

Jeremiah 15 in the BOATCB2

Jeremiah 15 in the BOBCV

Jeremiah 15 in the BOCNT

Jeremiah 15 in the BOECS

Jeremiah 15 in the BOHCB

Jeremiah 15 in the BOHCV

Jeremiah 15 in the BOHLNT

Jeremiah 15 in the BOHNTLTAL

Jeremiah 15 in the BOICB

Jeremiah 15 in the BOILNTAP

Jeremiah 15 in the BOITCV

Jeremiah 15 in the BOKCV

Jeremiah 15 in the BOKCV2

Jeremiah 15 in the BOKHWOG

Jeremiah 15 in the BOKSSV

Jeremiah 15 in the BOLCB

Jeremiah 15 in the BOLCB2

Jeremiah 15 in the BOMCV

Jeremiah 15 in the BONAV

Jeremiah 15 in the BONCB

Jeremiah 15 in the BONLT

Jeremiah 15 in the BONUT2

Jeremiah 15 in the BOPLNT

Jeremiah 15 in the BOSCB

Jeremiah 15 in the BOSNC

Jeremiah 15 in the BOTLNT

Jeremiah 15 in the BOVCB

Jeremiah 15 in the BOYCB

Jeremiah 15 in the BPBB

Jeremiah 15 in the BPH

Jeremiah 15 in the BSB

Jeremiah 15 in the CCB

Jeremiah 15 in the CUV

Jeremiah 15 in the CUVS

Jeremiah 15 in the DBT

Jeremiah 15 in the DGDNT

Jeremiah 15 in the DHNT

Jeremiah 15 in the DNT

Jeremiah 15 in the ELBE

Jeremiah 15 in the EMTV

Jeremiah 15 in the ESV

Jeremiah 15 in the FBV

Jeremiah 15 in the FEB

Jeremiah 15 in the GGMNT

Jeremiah 15 in the GNT

Jeremiah 15 in the HARY

Jeremiah 15 in the HNT

Jeremiah 15 in the IRVA

Jeremiah 15 in the IRVB

Jeremiah 15 in the IRVG

Jeremiah 15 in the IRVH

Jeremiah 15 in the IRVK

Jeremiah 15 in the IRVM

Jeremiah 15 in the IRVM2

Jeremiah 15 in the IRVO

Jeremiah 15 in the IRVP

Jeremiah 15 in the IRVT

Jeremiah 15 in the IRVT2

Jeremiah 15 in the IRVU

Jeremiah 15 in the ISVN

Jeremiah 15 in the JSNT

Jeremiah 15 in the KAPI

Jeremiah 15 in the KBT1ETNIK

Jeremiah 15 in the KBV

Jeremiah 15 in the KJV

Jeremiah 15 in the KNFD

Jeremiah 15 in the LBA

Jeremiah 15 in the LBLA

Jeremiah 15 in the LNT

Jeremiah 15 in the LSV

Jeremiah 15 in the MAAL

Jeremiah 15 in the MBV

Jeremiah 15 in the MBV2

Jeremiah 15 in the MHNT

Jeremiah 15 in the MKNFD

Jeremiah 15 in the MNG

Jeremiah 15 in the MNT

Jeremiah 15 in the MNT2

Jeremiah 15 in the MRS1T

Jeremiah 15 in the NAA

Jeremiah 15 in the NASB

Jeremiah 15 in the NBLA

Jeremiah 15 in the NBS

Jeremiah 15 in the NBVTP

Jeremiah 15 in the NET2

Jeremiah 15 in the NIV11

Jeremiah 15 in the NNT

Jeremiah 15 in the NNT2

Jeremiah 15 in the NNT3

Jeremiah 15 in the PDDPT

Jeremiah 15 in the PFNT

Jeremiah 15 in the RMNT

Jeremiah 15 in the SBIAS

Jeremiah 15 in the SBIBS

Jeremiah 15 in the SBIBS2

Jeremiah 15 in the SBICS

Jeremiah 15 in the SBIDS

Jeremiah 15 in the SBIGS

Jeremiah 15 in the SBIHS

Jeremiah 15 in the SBIIS

Jeremiah 15 in the SBIIS2

Jeremiah 15 in the SBIIS3

Jeremiah 15 in the SBIKS

Jeremiah 15 in the SBIKS2

Jeremiah 15 in the SBIMS

Jeremiah 15 in the SBIOS

Jeremiah 15 in the SBIPS

Jeremiah 15 in the SBISS

Jeremiah 15 in the SBITS

Jeremiah 15 in the SBITS2

Jeremiah 15 in the SBITS3

Jeremiah 15 in the SBITS4

Jeremiah 15 in the SBIUS

Jeremiah 15 in the SBIVS

Jeremiah 15 in the SBT

Jeremiah 15 in the SBT1E

Jeremiah 15 in the SCHL

Jeremiah 15 in the SNT

Jeremiah 15 in the SUSU

Jeremiah 15 in the SUSU2

Jeremiah 15 in the SYNO

Jeremiah 15 in the TBIAOTANT

Jeremiah 15 in the TBT1E

Jeremiah 15 in the TBT1E2

Jeremiah 15 in the TFTIP

Jeremiah 15 in the TFTU

Jeremiah 15 in the TGNTATF3T

Jeremiah 15 in the THAI

Jeremiah 15 in the TNFD

Jeremiah 15 in the TNT

Jeremiah 15 in the TNTIK

Jeremiah 15 in the TNTIL

Jeremiah 15 in the TNTIN

Jeremiah 15 in the TNTIP

Jeremiah 15 in the TNTIZ

Jeremiah 15 in the TOMA

Jeremiah 15 in the TTENT

Jeremiah 15 in the UBG

Jeremiah 15 in the UGV

Jeremiah 15 in the UGV2

Jeremiah 15 in the UGV3

Jeremiah 15 in the VBL

Jeremiah 15 in the VDCC

Jeremiah 15 in the YALU

Jeremiah 15 in the YAPE

Jeremiah 15 in the YBVTP

Jeremiah 15 in the ZBP