Job 34 (BOGWICC)

1 Pamenepo Elihu anapitiriza kuyankhula kuti, 2 “Imvani mawu anga, inu anthu anzeru;tcherani khutu inu anthu ophunzira. 3 Pakuti khutu limayesa mawumonga momwe mʼkamwa mumalawira chakudya. 4 Tsono tiyeni tizindikire chomwe chili choyenera;tiphunzire pamodzi chomwe chili chabwino. 5 “Yobu akunena kuti, ‘Ndine wosalakwa,koma Mulungu akukana kundiweruza molungama. 6 Ngakhale ndine wolungama mtima,akundiyesa wabodza;ngakhale ndine wosachimwa,mivi yake ikundichititsa mabala osachiritsidwa.’ 7 Kodi munthu wofanana ndi Yobu ndani,amene amayankhula zamwano ngati akumwa madzi? 8 Iye amayenda ndi anthu ochita zoyipa;amayanjana ndi anthu oyipa mtima. 9 Paja iye amanena kuti, ‘Munthu sapindula kanthupoyesetsa kukondweretsa Mulungu.’ 10 “Tsono mverani ine, inu anthu anzeru zomvetsa zinthu.Mulungu sangachite choyipa ndi pangʼono pomwe,Wamphamvuzonse sangathe kuchita cholakwa. 11 Iye amamubwezera munthu molingana ndi ntchito zake;Mulungu amabweretsa pa munthu molingana ndi zomwe amachita. 12 Nʼchosayembekezeka kuti Mulungu achite cholakwa,kuti Wamphamvuzonse apotoze chilungamo. 13 Kodi anapatsa Mulungu udindo wolamulira dziko lapansi ndani?Ndani anayika Mulungu kuti azilamulira dziko lonse? 14 Mulungu akanakhala ndi maganizooti achotse mzimu wake ndi mpweya wake, 15 zamoyo zonse zikanawonongekeratundipo munthu akanabwerera ku fumbi. 16 “Ngati ndinu omvetsa zinthu, imvani izi;mvetserani zimene ndikunena. 17 Kodi Mulungu wodana ndi chilungamo angathe kukhala wolamulira?Kodi iwe ungathe kuweruza Wolungama ndi Wamphamvuyo? 18 Kodi si Iye amene amanena kwa mafumu kuti, ‘Ndinu opanda pake,’ndipo amawuza anthu otchuka, ‘Ndinu oyipa,’ 19 Iye sakondera akalongandipo salemekeza anthu olemera kupambana osauka,pakuti onsewa ndi ntchito ya manja ake? 20 Iwo amafa mwadzidzidzi, pakati pa usiku;anthu amachita mantha ndipo amamwalira;munthu wamphamvu amachotsedwa popanda dzanja la munthu. 21 “Maso a Mulungu amapenya njira za munthu;amaona mayendedwe ake onse. 22 Palibe malo obisika kapena a mdima wandiweyanikumene anthu ochita zoyipa angabisaleko. 23 Mulungu sasowa kuti apitirizebe kufufuza munthu,kuti abwere pamaso pake kudzaweruzidwa. 24 Popanda kufufuza, Iye amawononga anthu amphamvundipo mʼmalo mwawo amayikamo ena. 25 Pakuti Iyeyo amadziwa bwino ntchito zawoamawagubuduza usiku ndipo amatswanyika. 26 Iye amawalanga chifukwa cha kuyipa kwawo,pamalo pamene aliyense akuwaona; 27 Chifukwa anasiya kumutsatandipo sasamaliranso njira zake zonse. 28 Anachititsa amphawi kuti kulira kwawo kufike pamaso pake,kotero Iyeyo anamva kulira kwa amphawiwo. 29 Koma ngati Mulungu akhala chete, ndani angamunene kuti walakwa?Akabisa nkhope yake, ndani angathe kumupenyabe?Komatu ndiye amene amayangʼana za munthu komanso mtundu wa anthu, 30 kuti asalamuliridwe ndi anthu osapembedza,kuti asatchere anthu misampha. 31 “Mwina munthu atanena kwa Mulungu kuti,‘Ndine wolakwa koma sindidzachimwanso, 32 ndiphunzitseni zimene sindikuzionangati ndachita choyipa, sindidzachitanso.’ 33 Kodi Mulungu akuweruzeni potsata mmene inuyo mukuganizira,pamene inu mukukana kulapa?Chisankho nʼchanu, osati changa;tsono ndiwuzeni zomwe mukudziwa. 34 “Anthu omvetsa zinthu adzakambirana,anthu anzeru amene akundimva adzandiwuza kuti, 35 ‘Yobu akuyankhula mopanda nzeru;mawu ake ndi opanda fundo.’ 36 Aa, kunali bwino Yobu akanayesedwa mpaka kumapetochifukwa choyankha ngati munthu woyipa! 37 Pa tchimo lake amawonjezerapo kuwukira;amawomba mʼmanja mwake monyoza pakati pathu,ndipo amachulukitsa mawu otsutsana ndi Mulungu.”

In Other Versions

Job 34 in the ANGEFD

Job 34 in the ANTPNG2D

Job 34 in the AS21

Job 34 in the BAGH

Job 34 in the BBPNG

Job 34 in the BBT1E

Job 34 in the BDS

Job 34 in the BEV

Job 34 in the BHAD

Job 34 in the BIB

Job 34 in the BLPT

Job 34 in the BNT

Job 34 in the BNTABOOT

Job 34 in the BNTLV

Job 34 in the BOATCB

Job 34 in the BOATCB2

Job 34 in the BOBCV

Job 34 in the BOCNT

Job 34 in the BOECS

Job 34 in the BOHCB

Job 34 in the BOHCV

Job 34 in the BOHLNT

Job 34 in the BOHNTLTAL

Job 34 in the BOICB

Job 34 in the BOILNTAP

Job 34 in the BOITCV

Job 34 in the BOKCV

Job 34 in the BOKCV2

Job 34 in the BOKHWOG

Job 34 in the BOKSSV

Job 34 in the BOLCB

Job 34 in the BOLCB2

Job 34 in the BOMCV

Job 34 in the BONAV

Job 34 in the BONCB

Job 34 in the BONLT

Job 34 in the BONUT2

Job 34 in the BOPLNT

Job 34 in the BOSCB

Job 34 in the BOSNC

Job 34 in the BOTLNT

Job 34 in the BOVCB

Job 34 in the BOYCB

Job 34 in the BPBB

Job 34 in the BPH

Job 34 in the BSB

Job 34 in the CCB

Job 34 in the CUV

Job 34 in the CUVS

Job 34 in the DBT

Job 34 in the DGDNT

Job 34 in the DHNT

Job 34 in the DNT

Job 34 in the ELBE

Job 34 in the EMTV

Job 34 in the ESV

Job 34 in the FBV

Job 34 in the FEB

Job 34 in the GGMNT

Job 34 in the GNT

Job 34 in the HARY

Job 34 in the HNT

Job 34 in the IRVA

Job 34 in the IRVB

Job 34 in the IRVG

Job 34 in the IRVH

Job 34 in the IRVK

Job 34 in the IRVM

Job 34 in the IRVM2

Job 34 in the IRVO

Job 34 in the IRVP

Job 34 in the IRVT

Job 34 in the IRVT2

Job 34 in the IRVU

Job 34 in the ISVN

Job 34 in the JSNT

Job 34 in the KAPI

Job 34 in the KBT1ETNIK

Job 34 in the KBV

Job 34 in the KJV

Job 34 in the KNFD

Job 34 in the LBA

Job 34 in the LBLA

Job 34 in the LNT

Job 34 in the LSV

Job 34 in the MAAL

Job 34 in the MBV

Job 34 in the MBV2

Job 34 in the MHNT

Job 34 in the MKNFD

Job 34 in the MNG

Job 34 in the MNT

Job 34 in the MNT2

Job 34 in the MRS1T

Job 34 in the NAA

Job 34 in the NASB

Job 34 in the NBLA

Job 34 in the NBS

Job 34 in the NBVTP

Job 34 in the NET2

Job 34 in the NIV11

Job 34 in the NNT

Job 34 in the NNT2

Job 34 in the NNT3

Job 34 in the PDDPT

Job 34 in the PFNT

Job 34 in the RMNT

Job 34 in the SBIAS

Job 34 in the SBIBS

Job 34 in the SBIBS2

Job 34 in the SBICS

Job 34 in the SBIDS

Job 34 in the SBIGS

Job 34 in the SBIHS

Job 34 in the SBIIS

Job 34 in the SBIIS2

Job 34 in the SBIIS3

Job 34 in the SBIKS

Job 34 in the SBIKS2

Job 34 in the SBIMS

Job 34 in the SBIOS

Job 34 in the SBIPS

Job 34 in the SBISS

Job 34 in the SBITS

Job 34 in the SBITS2

Job 34 in the SBITS3

Job 34 in the SBITS4

Job 34 in the SBIUS

Job 34 in the SBIVS

Job 34 in the SBT

Job 34 in the SBT1E

Job 34 in the SCHL

Job 34 in the SNT

Job 34 in the SUSU

Job 34 in the SUSU2

Job 34 in the SYNO

Job 34 in the TBIAOTANT

Job 34 in the TBT1E

Job 34 in the TBT1E2

Job 34 in the TFTIP

Job 34 in the TFTU

Job 34 in the TGNTATF3T

Job 34 in the THAI

Job 34 in the TNFD

Job 34 in the TNT

Job 34 in the TNTIK

Job 34 in the TNTIL

Job 34 in the TNTIN

Job 34 in the TNTIP

Job 34 in the TNTIZ

Job 34 in the TOMA

Job 34 in the TTENT

Job 34 in the UBG

Job 34 in the UGV

Job 34 in the UGV2

Job 34 in the UGV3

Job 34 in the VBL

Job 34 in the VDCC

Job 34 in the YALU

Job 34 in the YAPE

Job 34 in the YBVTP

Job 34 in the ZBP