Job 37 (BOGWICC)
1 “Mtima wanga ukulumphalumpha pa chimenechinsondipo ukuchoka mʼmalo mwake. 2 Tamverani! Tamverani kubangula kwa liwu lake,kugunda kumene kukuchokera mʼkamwa mwake. 3 Iye amaponya chingʼaningʼani chake pansi pa thambo lonsendipo amachitumiza ku dziko lapansi. 4 Pambuyo pake kubangula kwake kumamveka.Iye amabangula ndi liwu lake laulemerero.Pamene wabangula,palibe chimene amalephera kuchita. 5 Liwu la Mulungu limabangula mʼnjira zambiri zodabwitsaIye amachita zinthu zazikulu zimene sitingathe kuzimvetsa. 6 Amalamula chisanu chowundana kuti, ‘Igwa pa dziko lapansi,’ndipo amalamulanso mvula yamawawa kuti, ‘Khala mvula yamphamvu.’ 7 Kuti anthu onse amene anawalenga athe kuzindikira ntchito yake.Iye amalepheretsa anthu kugwira ntchito zawo. 8 Zirombo zimakabisalandipo zimakhala mʼmaenje mwawo. 9 Mphepo yamkuntho imatuluka ku malo ake,kuzizira kumatuluka mʼmphepo yamkunthoyo. 10 Mpweya wa Mulungu umawunditsa madzindipo madzi a mʼnyanja amawuma kuti gwaa. 11 Iye amadzaza mitambo ndi madzi a mvula,amabalalitsa zingʼaningʼani zake kuchokera mʼmitambomo. 12 Mulungu amayendetsa mitamboyomozungulirazungulira dziko lonse lapansikuti ichite zonse zimene Iye akufuna pa dziko lapansi. 13 Iye amagwetsa mvula kuti alange anthu,kapena kubweretsa chinyontho pa dziko lapansi kuti aonetse chikondi chake. 14 “Abambo Yobu, tamvani izi;imani ndipo muganizire ntchito zodabwitsa za Mulungu. 15 Kodi mukudziwa momwe Mulungu amayendetsera mitambondi kuchititsa kuti kukhale zingʼaningʼani? 16 Kodi mukudziwa momwe Mulungu amayalira mitambo,ntchito zodabwitsa za Iye amene ndi wanzeru zangwiro? 17 Inu amene mʼzovala zanu mumatuluka thukutapamene kunja kwatentha chifukwa cha mphepo yakummwera, 18 kodi mungathe kuthandizana naye kutambasula thambolimene ndi lolimba ngati chitsulo? 19 “Tiwuzeni ife zoti tikanene kwa Iye;sitingathe kufotokoza mlandu wathu chifukwa cha mdima umene uli mwa ife. 20 Kodi nʼkofunika kumudziwitsa Mulungu kuti ndili naye mawu?Kodi kutero sikuchita ngati kupempha kuti ndiwonongeke? 21 Tsopano munthu sangathe kuyangʼana dzuwa,ndi kunyezimira mlengalenga,kuwomba kwa mphepo kutachotsa mitambo yonse. 22 Kuwala kwake kumaonekera cha kumpoto;Mulungu amabwera ndi ulemerero woopsa. 23 Wamphamvuzonse sitingathe kumufikira pafupi ndi wa mphamvu zoposa;pa chiweruzo chake cholungama ndi mʼchilungamo chake chachikulu Iye sapondereza anthu ozunzika. 24 Nʼchifukwa chake anthu amamuopa kwambiri,kodi saganizira za onse amene amaganiza kuti ndi anzeru?”
In Other Versions
Job 37 in the ANGEFD
Job 37 in the ANTPNG2D
Job 37 in the AS21
Job 37 in the BAGH
Job 37 in the BBPNG
Job 37 in the BBT1E
Job 37 in the BDS
Job 37 in the BEV
Job 37 in the BHAD
Job 37 in the BIB
Job 37 in the BLPT
Job 37 in the BNT
Job 37 in the BNTABOOT
Job 37 in the BNTLV
Job 37 in the BOATCB
Job 37 in the BOATCB2
Job 37 in the BOBCV
Job 37 in the BOCNT
Job 37 in the BOECS
Job 37 in the BOHCB
Job 37 in the BOHCV
Job 37 in the BOHLNT
Job 37 in the BOHNTLTAL
Job 37 in the BOICB
Job 37 in the BOILNTAP
Job 37 in the BOITCV
Job 37 in the BOKCV
Job 37 in the BOKCV2
Job 37 in the BOKHWOG
Job 37 in the BOKSSV
Job 37 in the BOLCB
Job 37 in the BOLCB2
Job 37 in the BOMCV
Job 37 in the BONAV
Job 37 in the BONCB
Job 37 in the BONLT
Job 37 in the BONUT2
Job 37 in the BOPLNT
Job 37 in the BOSCB
Job 37 in the BOSNC
Job 37 in the BOTLNT
Job 37 in the BOVCB
Job 37 in the BOYCB
Job 37 in the BPBB
Job 37 in the BPH
Job 37 in the BSB
Job 37 in the CCB
Job 37 in the CUV
Job 37 in the CUVS
Job 37 in the DBT
Job 37 in the DGDNT
Job 37 in the DHNT
Job 37 in the DNT
Job 37 in the ELBE
Job 37 in the EMTV
Job 37 in the ESV
Job 37 in the FBV
Job 37 in the FEB
Job 37 in the GGMNT
Job 37 in the GNT
Job 37 in the HARY
Job 37 in the HNT
Job 37 in the IRVA
Job 37 in the IRVB
Job 37 in the IRVG
Job 37 in the IRVH
Job 37 in the IRVK
Job 37 in the IRVM
Job 37 in the IRVM2
Job 37 in the IRVO
Job 37 in the IRVP
Job 37 in the IRVT
Job 37 in the IRVT2
Job 37 in the IRVU
Job 37 in the ISVN
Job 37 in the JSNT
Job 37 in the KAPI
Job 37 in the KBT1ETNIK
Job 37 in the KBV
Job 37 in the KJV
Job 37 in the KNFD
Job 37 in the LBA
Job 37 in the LBLA
Job 37 in the LNT
Job 37 in the LSV
Job 37 in the MAAL
Job 37 in the MBV
Job 37 in the MBV2
Job 37 in the MHNT
Job 37 in the MKNFD
Job 37 in the MNG
Job 37 in the MNT
Job 37 in the MNT2
Job 37 in the MRS1T
Job 37 in the NAA
Job 37 in the NASB
Job 37 in the NBLA
Job 37 in the NBS
Job 37 in the NBVTP
Job 37 in the NET2
Job 37 in the NIV11
Job 37 in the NNT
Job 37 in the NNT2
Job 37 in the NNT3
Job 37 in the PDDPT
Job 37 in the PFNT
Job 37 in the RMNT
Job 37 in the SBIAS
Job 37 in the SBIBS
Job 37 in the SBIBS2
Job 37 in the SBICS
Job 37 in the SBIDS
Job 37 in the SBIGS
Job 37 in the SBIHS
Job 37 in the SBIIS
Job 37 in the SBIIS2
Job 37 in the SBIIS3
Job 37 in the SBIKS
Job 37 in the SBIKS2
Job 37 in the SBIMS
Job 37 in the SBIOS
Job 37 in the SBIPS
Job 37 in the SBISS
Job 37 in the SBITS
Job 37 in the SBITS2
Job 37 in the SBITS3
Job 37 in the SBITS4
Job 37 in the SBIUS
Job 37 in the SBIVS
Job 37 in the SBT
Job 37 in the SBT1E
Job 37 in the SCHL
Job 37 in the SNT
Job 37 in the SUSU
Job 37 in the SUSU2
Job 37 in the SYNO
Job 37 in the TBIAOTANT
Job 37 in the TBT1E
Job 37 in the TBT1E2
Job 37 in the TFTIP
Job 37 in the TFTU
Job 37 in the TGNTATF3T
Job 37 in the THAI
Job 37 in the TNFD
Job 37 in the TNT
Job 37 in the TNTIK
Job 37 in the TNTIL
Job 37 in the TNTIN
Job 37 in the TNTIP
Job 37 in the TNTIZ
Job 37 in the TOMA
Job 37 in the TTENT
Job 37 in the UBG
Job 37 in the UGV
Job 37 in the UGV2
Job 37 in the UGV3
Job 37 in the VBL
Job 37 in the VDCC
Job 37 in the YALU
Job 37 in the YAPE
Job 37 in the YBVTP
Job 37 in the ZBP