Job 41 (BOGWICC)
1 “Kodi ungathe kukoka ngʼona ndi mbedza ya nsombakapena kukanikiza lilime lake pansi ndi chingwe? 2 Kodi ungathe kumanga chingwe mʼmphuno mwake,kapena kubowola nsagwada zake ndi mbedza? 3 Kodi ngʼonayo idzakupempha kuti uyichitire chifundo?Kodi idzakuyankhula ndi mawu ofatsa? 4 Kodi idzachita nawe mgwirizanokuti uyisandutse kapolo wako mpaka muyaya? 5 Kodi udzasewera nayo ngati mbalame,kapena kuyimangirira kuti atsikana ako asewere nayo? 6 Kodi anthu adzayitsatsa malonda?Nanga amalondawo nʼkugawanagawana nyama yake kuti akagulitse? 7 Kodi chikopa chake ungathe kuchilasa ndi zisonga,kapena kubowola mutu wake ndi nthungo zophera nsomba? 8 Ukayiputa udziwe kuti pali nkhondo,ndipo iweyo sudzabwereranso. 9 Chiyembekezo choti nʼkuyigonjetsa ndi chabodza;kungoyiona kokha, ndithu iwe kumangodzigwera wekha. 10 Palibe wolimba mtima kuti ndi kuyiputa.Ndani angalimbe mtima kulimbana ndi Ine? 11 Kodi ndani anandipatsa kanthu kuti ndimubwezere?Zonse za pansi pa thambo ndi zanga. 12 “Sindidzaleka kuyankhula za ziwalo zake za chirombocho,za mphamvu zake ndiponso za maonekedwe a thupi lake. 13 Ndani angasende chikopa chake?Ndani angayiyandikire kuti abowole chikopa chake cholimbacho? 14 Ndani angatsekule kukamwa kwake,pakamwa pamene pazunguliridwa ndi mano ochititsa mantha? 15 Kumsana kwake kuli mizere ya mambaonga zishango zolumikizanalumikizana; 16 Mambawo ndi olukanalukanakotero kuti mpweya sungathe kulowa pakati pake. 17 Ndi olumikizanalumikizana;ndi omatirirana kwambiri kotero kuti sangathe kulekana. 18 Kuyetsemula kwake kumatulutsa mbaliwali;maso ake amawala ngati kuwala kwa mʼbandakucha. 19 Mʼkamwa mwake mumatuluka nsakali zamoto ndipomumathetheka mbaliwali zamoto. 20 Mʼmphuno mwake mumatuluka utsingati wa mʼnkhali yowira yomwe ili pa moto wa bango. 21 Mpweya wake umayatsa makala,ndipo malawi amoto amatuluka mʼkamwa mwake. 22 Mphamvu zake zili mʼkhosi mwake;aliyense wokumana nayo amangoti njenjenje ndi mantha. 23 Minyewa ya thupi lake ndi yolumikizana ndipondi yokhwima kwambiri ndi yolimba. 24 Pachifuwa pake ndi powuma ngati mwala,ndi pa gwaa, ngati mwala wamphero. 25 Ngʼonayo ikangovuwuka,ndi anthu amphamvu omwe amaopa; amabwerera mʼmbuyo, kuthawa. 26 Ngakhale ikanthidwe ndi lupanga, lupangalo silichita kanthu,ngakhale mkondo, muvi ndi nthungo, zonse zimalephera. 27 Chitsulo imachiyesa ngati phesi chabendi mkuwa ngati chikuni chowola. 28 Muvi sungathe kuyithawitsa,miyala imene ayilasa nayo imangoyinyenyanyenya. 29 Zibonga zimakhala ngati ziputu;imangoseka pamene akuyibaya ndi nthungo. 30 Mamba a ku mimba kwake ali ngati chopunthira chakunthwa ndipoimasiya mkukuluzi mʼmatope ngati galeta lopunthira tirigu. 31 Imagadutsa madzi ozama ngati madzi a mʼnkhali,imachititsa nyanja kuti iwire ngati mbiya yoyengera mafuta. 32 Kumbuyo kwake imasiya nthubwitubwi zambee,kotero kuti munthu angaganize kuti nyanja yachita imvi. 33 Pa dziko lapansi palibe china chofanana nacho,nʼcholengedwa chopanda mantha. 34 Chimanyoza nyama zina zonse;icho chija ndi mfumu ya nyama zonse.”
In Other Versions
Job 41 in the ANGEFD
Job 41 in the ANTPNG2D
Job 41 in the AS21
Job 41 in the BAGH
Job 41 in the BBPNG
Job 41 in the BBT1E
Job 41 in the BDS
Job 41 in the BEV
Job 41 in the BHAD
Job 41 in the BIB
Job 41 in the BLPT
Job 41 in the BNT
Job 41 in the BNTABOOT
Job 41 in the BNTLV
Job 41 in the BOATCB
Job 41 in the BOATCB2
Job 41 in the BOBCV
Job 41 in the BOCNT
Job 41 in the BOECS
Job 41 in the BOHCB
Job 41 in the BOHCV
Job 41 in the BOHLNT
Job 41 in the BOHNTLTAL
Job 41 in the BOICB
Job 41 in the BOILNTAP
Job 41 in the BOITCV
Job 41 in the BOKCV
Job 41 in the BOKCV2
Job 41 in the BOKHWOG
Job 41 in the BOKSSV
Job 41 in the BOLCB
Job 41 in the BOLCB2
Job 41 in the BOMCV
Job 41 in the BONAV
Job 41 in the BONCB
Job 41 in the BONLT
Job 41 in the BONUT2
Job 41 in the BOPLNT
Job 41 in the BOSCB
Job 41 in the BOSNC
Job 41 in the BOTLNT
Job 41 in the BOVCB
Job 41 in the BOYCB
Job 41 in the BPBB
Job 41 in the BPH
Job 41 in the BSB
Job 41 in the CCB
Job 41 in the CUV
Job 41 in the CUVS
Job 41 in the DBT
Job 41 in the DGDNT
Job 41 in the DHNT
Job 41 in the DNT
Job 41 in the ELBE
Job 41 in the EMTV
Job 41 in the ESV
Job 41 in the FBV
Job 41 in the FEB
Job 41 in the GGMNT
Job 41 in the GNT
Job 41 in the HARY
Job 41 in the HNT
Job 41 in the IRVA
Job 41 in the IRVB
Job 41 in the IRVG
Job 41 in the IRVH
Job 41 in the IRVK
Job 41 in the IRVM
Job 41 in the IRVM2
Job 41 in the IRVO
Job 41 in the IRVP
Job 41 in the IRVT
Job 41 in the IRVT2
Job 41 in the IRVU
Job 41 in the ISVN
Job 41 in the JSNT
Job 41 in the KAPI
Job 41 in the KBT1ETNIK
Job 41 in the KBV
Job 41 in the KJV
Job 41 in the KNFD
Job 41 in the LBA
Job 41 in the LBLA
Job 41 in the LNT
Job 41 in the LSV
Job 41 in the MAAL
Job 41 in the MBV
Job 41 in the MBV2
Job 41 in the MHNT
Job 41 in the MKNFD
Job 41 in the MNG
Job 41 in the MNT
Job 41 in the MNT2
Job 41 in the MRS1T
Job 41 in the NAA
Job 41 in the NASB
Job 41 in the NBLA
Job 41 in the NBS
Job 41 in the NBVTP
Job 41 in the NET2
Job 41 in the NIV11
Job 41 in the NNT
Job 41 in the NNT2
Job 41 in the NNT3
Job 41 in the PDDPT
Job 41 in the PFNT
Job 41 in the RMNT
Job 41 in the SBIAS
Job 41 in the SBIBS
Job 41 in the SBIBS2
Job 41 in the SBICS
Job 41 in the SBIDS
Job 41 in the SBIGS
Job 41 in the SBIHS
Job 41 in the SBIIS
Job 41 in the SBIIS2
Job 41 in the SBIIS3
Job 41 in the SBIKS
Job 41 in the SBIKS2
Job 41 in the SBIMS
Job 41 in the SBIOS
Job 41 in the SBIPS
Job 41 in the SBISS
Job 41 in the SBITS
Job 41 in the SBITS2
Job 41 in the SBITS3
Job 41 in the SBITS4
Job 41 in the SBIUS
Job 41 in the SBIVS
Job 41 in the SBT
Job 41 in the SBT1E
Job 41 in the SCHL
Job 41 in the SNT
Job 41 in the SUSU
Job 41 in the SUSU2
Job 41 in the SYNO
Job 41 in the TBIAOTANT
Job 41 in the TBT1E
Job 41 in the TBT1E2
Job 41 in the TFTIP
Job 41 in the TFTU
Job 41 in the TGNTATF3T
Job 41 in the THAI
Job 41 in the TNFD
Job 41 in the TNT
Job 41 in the TNTIK
Job 41 in the TNTIL
Job 41 in the TNTIN
Job 41 in the TNTIP
Job 41 in the TNTIZ
Job 41 in the TOMA
Job 41 in the TTENT
Job 41 in the UBG
Job 41 in the UGV
Job 41 in the UGV2
Job 41 in the UGV3
Job 41 in the VBL
Job 41 in the VDCC
Job 41 in the YALU
Job 41 in the YAPE
Job 41 in the YBVTP
Job 41 in the ZBP