Proverbs 10 (BOGWICC)

1 Miyambo ya Solomoni:Mwana wanzeru amakondweretsa abambo ake,koma mwana wopusa amamvetsa amayi ake chisoni. 2 Chuma chochipeza mwachinyengo sichipindulitsa,koma chilungamo chimapulumutsa ku imfa. 3 Yehova salola kuti munthu wolungama azikhala ndi njala;koma amalepheretsa zokhumba za anthu oyipa. 4 Wochita zinthu mwaulesi amasauka,koma wogwira ntchito mwakhama amalemera. 5 Amene amakolola nthawi yachilimwe ndi mwana wanzeru,koma amene amangogona nthawi yokolola ndi mwana wochititsa manyazi. 6 Madalitso amakhala pa mutu wa munthu wolungama,koma pakamwa pa munthu woyipa pamaphimba chiwawa. 7 Munthu wolungama anzake adzamukumbukira ngati mdalitso,koma dzina la munthu woyipa lidzayiwalika. 8 Munthu wa mtima wanzeru amasamala malamulo,koma chitsiru chomangolongolola chidzawonongeka. 9 Munthu woyenda mwangwiro amayenda mosatekeseka;koma amene amayenda njira yokhotakhota adzadziwika. 10 Aliyense wotsinzinira maso mwachinyengo amabweretsa mavuto,koma wodzudzula chitsiru molimba mtima amabweretsa mtendere. 11 Pakamwa pa munthu wolungama ndi kasupe wamoyo,koma pakamwa pa munthu woyipa pamabisa chiwawa. 12 Udani umawutsa mikangano,koma chikondi chimaphimba zolakwa zonse. 13 Nzeru imapezeka pa milomo ya munthu wozindikira zinthu,koma pa msana pa munthu wopanda nzeru sipachoka chikwapu. 14 Anzeru amasunga chidziwitsokoma pakamwa pa chitsiru pamatulutsa zowononga. 15 Chuma cha munthu wolemerandiye chitetezo chake; koma umphawi ndiye chiwonongeko cha osauka. 16 Moyo ndiye malipiro a munthu wolungama,koma phindu la anthu oyipa ndi uchimo ndi imfa. 17 Wosamalira malangizo amayenda mʼnjira ya moyo,koma wonyoza chidzudzulo amasochera. 18 Amene amabisa chidani chake ndi munthu wonama,ndipo amene amafalitsa miseche ndi chitsiru. 19 Mawu akachuluka zolakwa sizisowa,koma amene amasunga pakamwa pake ndi wanzeru. 20 Mawu a munthu wolungama ali ngati siliva wabwino kwambiri,koma mtima wa munthu woyipa ndi wopanda phindu. 21 Milomo ya anthu olungama imalimbikitsa ambiri;koma chitsiru chimafa chifukwa chosowa nzeru. 22 Mdalitso wa Yehova ndiwo umabweretsa chuma,ntchito za munthu siziwonjezerapo kanthu. 23 Kwa chitsiru kuchita zinthu zoyipa ndiye chinthu chomusangalatsa,koma kwa munthu womvetsa bwino zinthu nzeru ndiyo imamusangalatsa. 24 Chimene munthu woyipa amachiopa chidzamuchitikira;chimene munthu wolungama amachilakalaka adzachipeza. 25 Pamene namondwe wawomba, anthu oyipa amachotsedwa,koma anthu olungama amakhazikika mpaka muyaya. 26 Momwe amakhalira vinyo wosasa mʼkamwa ndi momwe umakhalira utsi mʼmaso,ndi momwenso amakhalira munthu waulesi kwa amene amutuma. 27 Kuopa Yehova kumatalikitsa moyo;koma zaka za anthu oyipa zidzafupikitsidwa. 28 Chiyembekezo cha olungama chimapatsa chimwemwe,koma chiyembekezo cha anthu ochimwa chidzafera mʼmazira. 29 Njira za Yehova ndi linga loteteza anthu ochita zabwino,koma wochita zoyipa adzawonongeka. 30 Munthu wolungama sadzachotsedwa, pamalo pakekoma oyipa sadzakhazikika pa dziko. 31 Pakamwa pa munthu wolungama pamatulutsa za nzeru,koma lilime lokhota lidzadulidwa. 32 Milomo ya anthu olungama imadziwa zoyenera kuyankhula,koma pakamwa pa anthu ochimwa pamatulutsa zokhota zokhazokha.

In Other Versions

Proverbs 10 in the ANGEFD

Proverbs 10 in the ANTPNG2D

Proverbs 10 in the AS21

Proverbs 10 in the BAGH

Proverbs 10 in the BBPNG

Proverbs 10 in the BBT1E

Proverbs 10 in the BDS

Proverbs 10 in the BEV

Proverbs 10 in the BHAD

Proverbs 10 in the BIB

Proverbs 10 in the BLPT

Proverbs 10 in the BNT

Proverbs 10 in the BNTABOOT

Proverbs 10 in the BNTLV

Proverbs 10 in the BOATCB

Proverbs 10 in the BOATCB2

Proverbs 10 in the BOBCV

Proverbs 10 in the BOCNT

Proverbs 10 in the BOECS

Proverbs 10 in the BOHCB

Proverbs 10 in the BOHCV

Proverbs 10 in the BOHLNT

Proverbs 10 in the BOHNTLTAL

Proverbs 10 in the BOICB

Proverbs 10 in the BOILNTAP

Proverbs 10 in the BOITCV

Proverbs 10 in the BOKCV

Proverbs 10 in the BOKCV2

Proverbs 10 in the BOKHWOG

Proverbs 10 in the BOKSSV

Proverbs 10 in the BOLCB

Proverbs 10 in the BOLCB2

Proverbs 10 in the BOMCV

Proverbs 10 in the BONAV

Proverbs 10 in the BONCB

Proverbs 10 in the BONLT

Proverbs 10 in the BONUT2

Proverbs 10 in the BOPLNT

Proverbs 10 in the BOSCB

Proverbs 10 in the BOSNC

Proverbs 10 in the BOTLNT

Proverbs 10 in the BOVCB

Proverbs 10 in the BOYCB

Proverbs 10 in the BPBB

Proverbs 10 in the BPH

Proverbs 10 in the BSB

Proverbs 10 in the CCB

Proverbs 10 in the CUV

Proverbs 10 in the CUVS

Proverbs 10 in the DBT

Proverbs 10 in the DGDNT

Proverbs 10 in the DHNT

Proverbs 10 in the DNT

Proverbs 10 in the ELBE

Proverbs 10 in the EMTV

Proverbs 10 in the ESV

Proverbs 10 in the FBV

Proverbs 10 in the FEB

Proverbs 10 in the GGMNT

Proverbs 10 in the GNT

Proverbs 10 in the HARY

Proverbs 10 in the HNT

Proverbs 10 in the IRVA

Proverbs 10 in the IRVB

Proverbs 10 in the IRVG

Proverbs 10 in the IRVH

Proverbs 10 in the IRVK

Proverbs 10 in the IRVM

Proverbs 10 in the IRVM2

Proverbs 10 in the IRVO

Proverbs 10 in the IRVP

Proverbs 10 in the IRVT

Proverbs 10 in the IRVT2

Proverbs 10 in the IRVU

Proverbs 10 in the ISVN

Proverbs 10 in the JSNT

Proverbs 10 in the KAPI

Proverbs 10 in the KBT1ETNIK

Proverbs 10 in the KBV

Proverbs 10 in the KJV

Proverbs 10 in the KNFD

Proverbs 10 in the LBA

Proverbs 10 in the LBLA

Proverbs 10 in the LNT

Proverbs 10 in the LSV

Proverbs 10 in the MAAL

Proverbs 10 in the MBV

Proverbs 10 in the MBV2

Proverbs 10 in the MHNT

Proverbs 10 in the MKNFD

Proverbs 10 in the MNG

Proverbs 10 in the MNT

Proverbs 10 in the MNT2

Proverbs 10 in the MRS1T

Proverbs 10 in the NAA

Proverbs 10 in the NASB

Proverbs 10 in the NBLA

Proverbs 10 in the NBS

Proverbs 10 in the NBVTP

Proverbs 10 in the NET2

Proverbs 10 in the NIV11

Proverbs 10 in the NNT

Proverbs 10 in the NNT2

Proverbs 10 in the NNT3

Proverbs 10 in the PDDPT

Proverbs 10 in the PFNT

Proverbs 10 in the RMNT

Proverbs 10 in the SBIAS

Proverbs 10 in the SBIBS

Proverbs 10 in the SBIBS2

Proverbs 10 in the SBICS

Proverbs 10 in the SBIDS

Proverbs 10 in the SBIGS

Proverbs 10 in the SBIHS

Proverbs 10 in the SBIIS

Proverbs 10 in the SBIIS2

Proverbs 10 in the SBIIS3

Proverbs 10 in the SBIKS

Proverbs 10 in the SBIKS2

Proverbs 10 in the SBIMS

Proverbs 10 in the SBIOS

Proverbs 10 in the SBIPS

Proverbs 10 in the SBISS

Proverbs 10 in the SBITS

Proverbs 10 in the SBITS2

Proverbs 10 in the SBITS3

Proverbs 10 in the SBITS4

Proverbs 10 in the SBIUS

Proverbs 10 in the SBIVS

Proverbs 10 in the SBT

Proverbs 10 in the SBT1E

Proverbs 10 in the SCHL

Proverbs 10 in the SNT

Proverbs 10 in the SUSU

Proverbs 10 in the SUSU2

Proverbs 10 in the SYNO

Proverbs 10 in the TBIAOTANT

Proverbs 10 in the TBT1E

Proverbs 10 in the TBT1E2

Proverbs 10 in the TFTIP

Proverbs 10 in the TFTU

Proverbs 10 in the TGNTATF3T

Proverbs 10 in the THAI

Proverbs 10 in the TNFD

Proverbs 10 in the TNT

Proverbs 10 in the TNTIK

Proverbs 10 in the TNTIL

Proverbs 10 in the TNTIN

Proverbs 10 in the TNTIP

Proverbs 10 in the TNTIZ

Proverbs 10 in the TOMA

Proverbs 10 in the TTENT

Proverbs 10 in the UBG

Proverbs 10 in the UGV

Proverbs 10 in the UGV2

Proverbs 10 in the UGV3

Proverbs 10 in the VBL

Proverbs 10 in the VDCC

Proverbs 10 in the YALU

Proverbs 10 in the YAPE

Proverbs 10 in the YBVTP

Proverbs 10 in the ZBP