Proverbs 3 (BOGWICC)

1 Mwana wanga, usayiwale malangizo anga,mtima wako usunge malamulo anga. 2 Ukatero zaka za moyo wako zidzachulukandipo udzakhala pa mtendere. 3 Makhalidwe ochitira ena chifundo ndi owonetsa kukhulupirika asakuchokere.Uwamangirire mʼkhosi mwako ngati mkandandi kuwalemba pa mtima pako. 4 Ukatero udzapeza kuyanja ndi mbiri yabwinopamaso pa Mulungu ndi anthu. 5 Uzikhulupirira Yehova ndi mtima wako wonsendipo usadalire nzeru zako za kumvetsa zinthu. 6 Pa zochita zako zonse uvomereze kuti Mulungu alipo,ndipo Iye adzawongola njira zako. 7 Usamadzione ngati wa nzeru.Uziopa Yehova ndi kupewa zoyipa. 8 Ukatero thupi lako lidzakhala la moyo wabwinondi mafupa ako adzakhala olimba. 9 Uzilemekeza Yehova ndi chuma chako chonse;zokolola zonse zoyamba kucha uzilemekeza nazonso Yehova. 10 Ukatero nkhokwe zako zidzadzaza ndi zinthu zambiri,ndiponso mitsuko yako idzadzaza ndi vinyo. 11 Mwana wanga usanyoze malangizo a Yehova,ndipo usayipidwe ndi chidzudzulo chake. 12 Paja Yehova amadzudzula amene amamukonda,monga abambo achitira mwana amene amakondwera naye. 13 Wodala munthu amene wapeza nzeru,munthu amene walandira nzeru zomvetsa zinthu, 14 pakuti phindu la nzeru ndi labwino kuposa la siliva,phindu lakelo ndi labwino kuposanso golide. 15 Nzeru ndi yoposa miyala yamtengowapatali;ndipo zonse zimene umazikhumba sizingafanane ndi nzeru. 16 Mʼdzanja lake lamanja muli moyo wautali;mʼdzanja lake lamanzere muli chuma ndi ulemu. 17 Njira zake ndi njira zosangalatsa,ndipo mu njira zake zonse muli mtendere. 18 Nzeru ili ngati mtengo wopatsa moyo kwa oyigwiritsitsa;wodala munthu amene amayigwiritsa kwambiri. 19 Yehova anakhazikitsa dziko lapansi pogwiritsa ntchito nzeru.Anagwiritsanso ntchito nzeru zakudziwa bwino zinthu pamene ankakhazikitsa zakumwamba. 20 Mwa nzeru zake Yehova anatumphutsa madzi kuchokera mʼnthakandiponso mitambo inagwetsa mvula. 21 Mwana wanga usunge nzeru yeniyeni ndi khalidwe lomalingarira zinthu bwino.Zimenezi zisakuchokere. 22 Zimenezi zidzakupatsa moyo,moyo wake wosangalatsa ndi wabwino ngati mkanda wa mʼkhosi. 23 Choncho udzayenda pa njira yako mosaopa kanthu,ndipo phazi lako silidzapunthwa; 24 pamene ugona pansi, sudzachita mantha;ukadzagona pansi tulo tako tidzakhala tokoma. 25 Usaope tsoka lobwera mwadzidzidzikapena chiwonongeko chimene chidzagwera anthu oyipa, 26 pakuti Yehova adzakulimbitsa mtimandipo adzasunga phazi lako kuti lisakodwe mu msampha. 27 Usaleke kuchitira zabwino amene ayenera kulandira zabwino,pamene uli nazo mphamvu zochitira zimenezi. 28 Usanene kwa mnansi wako kuti,“Pita, uchite kubweranso. Ndidzakupatsa mawa”pamene uli nazo tsopano. 29 Usamukonzere chiwembu mnansi wako,amene anakhala nawe pafupi mokudalira. 30 Usakangane ndi munthu wopanda chifukwapamene iye sanakuchitire zoyipa. 31 Usachite naye nsanje munthu wachiwawakapena kutsanzira khalidwe lake lililonse. 32 Pakuti Yehova amanyansidwa ndi munthu woyipakoma amayanjana nawo anthu olungama. 33 Yehova amatemberera nyumba ya munthu woyipa,koma amadalitsa nyumba ya anthu olungama. 34 Anthu onyoza, Iye amawanyoza,koma amakomera mtima anthu odzichepetsa. 35 Anthu anzeru adzalandira ulemu,koma zitsiru adzazichititsa manyazi.

In Other Versions

Proverbs 3 in the ANGEFD

Proverbs 3 in the ANTPNG2D

Proverbs 3 in the AS21

Proverbs 3 in the BAGH

Proverbs 3 in the BBPNG

Proverbs 3 in the BBT1E

Proverbs 3 in the BDS

Proverbs 3 in the BEV

Proverbs 3 in the BHAD

Proverbs 3 in the BIB

Proverbs 3 in the BLPT

Proverbs 3 in the BNT

Proverbs 3 in the BNTABOOT

Proverbs 3 in the BNTLV

Proverbs 3 in the BOATCB

Proverbs 3 in the BOATCB2

Proverbs 3 in the BOBCV

Proverbs 3 in the BOCNT

Proverbs 3 in the BOECS

Proverbs 3 in the BOHCB

Proverbs 3 in the BOHCV

Proverbs 3 in the BOHLNT

Proverbs 3 in the BOHNTLTAL

Proverbs 3 in the BOICB

Proverbs 3 in the BOILNTAP

Proverbs 3 in the BOITCV

Proverbs 3 in the BOKCV

Proverbs 3 in the BOKCV2

Proverbs 3 in the BOKHWOG

Proverbs 3 in the BOKSSV

Proverbs 3 in the BOLCB

Proverbs 3 in the BOLCB2

Proverbs 3 in the BOMCV

Proverbs 3 in the BONAV

Proverbs 3 in the BONCB

Proverbs 3 in the BONLT

Proverbs 3 in the BONUT2

Proverbs 3 in the BOPLNT

Proverbs 3 in the BOSCB

Proverbs 3 in the BOSNC

Proverbs 3 in the BOTLNT

Proverbs 3 in the BOVCB

Proverbs 3 in the BOYCB

Proverbs 3 in the BPBB

Proverbs 3 in the BPH

Proverbs 3 in the BSB

Proverbs 3 in the CCB

Proverbs 3 in the CUV

Proverbs 3 in the CUVS

Proverbs 3 in the DBT

Proverbs 3 in the DGDNT

Proverbs 3 in the DHNT

Proverbs 3 in the DNT

Proverbs 3 in the ELBE

Proverbs 3 in the EMTV

Proverbs 3 in the ESV

Proverbs 3 in the FBV

Proverbs 3 in the FEB

Proverbs 3 in the GGMNT

Proverbs 3 in the GNT

Proverbs 3 in the HARY

Proverbs 3 in the HNT

Proverbs 3 in the IRVA

Proverbs 3 in the IRVB

Proverbs 3 in the IRVG

Proverbs 3 in the IRVH

Proverbs 3 in the IRVK

Proverbs 3 in the IRVM

Proverbs 3 in the IRVM2

Proverbs 3 in the IRVO

Proverbs 3 in the IRVP

Proverbs 3 in the IRVT

Proverbs 3 in the IRVT2

Proverbs 3 in the IRVU

Proverbs 3 in the ISVN

Proverbs 3 in the JSNT

Proverbs 3 in the KAPI

Proverbs 3 in the KBT1ETNIK

Proverbs 3 in the KBV

Proverbs 3 in the KJV

Proverbs 3 in the KNFD

Proverbs 3 in the LBA

Proverbs 3 in the LBLA

Proverbs 3 in the LNT

Proverbs 3 in the LSV

Proverbs 3 in the MAAL

Proverbs 3 in the MBV

Proverbs 3 in the MBV2

Proverbs 3 in the MHNT

Proverbs 3 in the MKNFD

Proverbs 3 in the MNG

Proverbs 3 in the MNT

Proverbs 3 in the MNT2

Proverbs 3 in the MRS1T

Proverbs 3 in the NAA

Proverbs 3 in the NASB

Proverbs 3 in the NBLA

Proverbs 3 in the NBS

Proverbs 3 in the NBVTP

Proverbs 3 in the NET2

Proverbs 3 in the NIV11

Proverbs 3 in the NNT

Proverbs 3 in the NNT2

Proverbs 3 in the NNT3

Proverbs 3 in the PDDPT

Proverbs 3 in the PFNT

Proverbs 3 in the RMNT

Proverbs 3 in the SBIAS

Proverbs 3 in the SBIBS

Proverbs 3 in the SBIBS2

Proverbs 3 in the SBICS

Proverbs 3 in the SBIDS

Proverbs 3 in the SBIGS

Proverbs 3 in the SBIHS

Proverbs 3 in the SBIIS

Proverbs 3 in the SBIIS2

Proverbs 3 in the SBIIS3

Proverbs 3 in the SBIKS

Proverbs 3 in the SBIKS2

Proverbs 3 in the SBIMS

Proverbs 3 in the SBIOS

Proverbs 3 in the SBIPS

Proverbs 3 in the SBISS

Proverbs 3 in the SBITS

Proverbs 3 in the SBITS2

Proverbs 3 in the SBITS3

Proverbs 3 in the SBITS4

Proverbs 3 in the SBIUS

Proverbs 3 in the SBIVS

Proverbs 3 in the SBT

Proverbs 3 in the SBT1E

Proverbs 3 in the SCHL

Proverbs 3 in the SNT

Proverbs 3 in the SUSU

Proverbs 3 in the SUSU2

Proverbs 3 in the SYNO

Proverbs 3 in the TBIAOTANT

Proverbs 3 in the TBT1E

Proverbs 3 in the TBT1E2

Proverbs 3 in the TFTIP

Proverbs 3 in the TFTU

Proverbs 3 in the TGNTATF3T

Proverbs 3 in the THAI

Proverbs 3 in the TNFD

Proverbs 3 in the TNT

Proverbs 3 in the TNTIK

Proverbs 3 in the TNTIL

Proverbs 3 in the TNTIN

Proverbs 3 in the TNTIP

Proverbs 3 in the TNTIZ

Proverbs 3 in the TOMA

Proverbs 3 in the TTENT

Proverbs 3 in the UBG

Proverbs 3 in the UGV

Proverbs 3 in the UGV2

Proverbs 3 in the UGV3

Proverbs 3 in the VBL

Proverbs 3 in the VDCC

Proverbs 3 in the YALU

Proverbs 3 in the YAPE

Proverbs 3 in the YBVTP

Proverbs 3 in the ZBP