Psalms 109 (BOGWICC)

undefined Kwa mtsogoleri wamayimbidwe. Salimo la Davide. 1 Mulungu amene ndimakutamandani,musakhale chete, 2 pakuti anthu oyipa ndi achinyengoatsekula pakamwa pawo kutsutsana nane;iwo ayankhula motsutsana nane ndi malilime abodza. 3 Andizungulira ndi mawu audani,amandinena popanda chifukwa. 4 Mʼmalo mwa chikondi changa amandineneza,koma ine ndine munthu wapemphero. 5 Iwo amandibwezera zoyipa mʼmalo mwa zabwino,ndi udani mʼmalo mwa chikondi changa. 6 Sankhani munthu woyipa kuti amutsutse iye;lolani wotsutsa ayime ku dzanja lake lamanja. 7 Pamene aweruzidwa, apezeke kuti ndi wolakwa,ndipo mapemphero ake amutsutse. 8 Masiku ake akhale owerengeka;munthu wina atenge malo ake a utsogoleri. 9 Ana ake akhale amasiyendipo mkazi wake akhale wopanda mwamuna. 10 Ana ake akhale oyendayenda ndi opemphapempha;apirikitsidwe kuchoka pa mabwinja a nyumba zawo. 11 Wokongoza alande zonse zimene ali nazo;alendo afunkhe ntchito za manja ake. 12 Pasapezeke ndi mmodzi yemwe womukomera mtimakapena kumvera chisoni ana ake amasiye. 13 Zidzukulu zake zithe nʼkufa,mayina awo afafanizidwe mu mʼbado wotsatirawo. 14 Mphulupulu za makolo ake zikumbukiridwe pamaso pa Yehova;tchimo la amayi ake lisadzafafanizidwe. 15 Machimo awo akhale pamaso pa Yehova nthawi zonse,kuti Iye achotse chikumbutso chawo pa dziko lapansi. 16 Pakuti iye sanaganizirepo zochita chifundo,koma anazunza mpaka kuwapha anthu osaukandi osweka mtima. 17 Anakonda kutemberera,matembererowo abwerere kwa iye;sanakondwe nʼkudalitsa anthu ena,choncho madalitso akhale kutali naye. 18 Anavala kutemberera ngati chovala;kutemberera kunalowa mʼthupi lake ngati madzi,kulowa mʼmafupa ake ngati mafuta. 19 Matemberero akhale ngati chofunda chodzikutira nacho,ngati lamba wovala tsiku ndi tsiku. 20 Awa akhale malipiro ochokera kwa Yehova pa onditsutsa anga,kwa iwo amene amayankhula zoyipa za ine. 21 Koma Inu Ambuye Wamphamvuzonse,muchite nane molingana ndi dzina lanu,chifukwa cha ubwino wa chikondi chanu, pulumutseni. 22 Pakuti ndine wosauka ndi wosowa,ndipo mtima wanga ukuwawa mʼkati mwanga. 23 Ndikuzimirira ngati mthunzi wa kumadzulo,ndapirikitsidwa ngati dzombe. 24 Mawondo anga afowoka chifukwa cha kusala zakudya,thupi langa lawonda ndi mutu wanga womwe. 25 Ndine chinthu chotonzedwa kwa otsutsana nane;akandiona, amapukusa mitu yawo. 26 Thandizeni Inu Yehova Mulungu wanga;pulumutseni molingana ndi chikondi chanu. 27 Adaniwo adziwe kuti limeneli ndi dzanja lanu,kuti Inu Yehova mwachita zimenezi. 28 Angathe kutemberera, koma Inu mudzadalitsa;pamene iwo andiputa adzachititsidwa manyazi,koma mtumiki wanu adzasangalala. 29 Onditsutsa adzavekedwa mnyozo,ndipo adzadzifunditsa manyazi ngati chovala. 30 Ndi pakamwa panga ndidzathokoza Yehova kwambiri;ndidzamutamanda mʼgulu lalikulu la anthu. 31 Popeza Iye amayima ku dzanja lamanja la munthu wosowayo,kupulumutsa moyo wake kwa iwo amene agamula molakwa.

In Other Versions

Psalms 109 in the ANGEFD

Psalms 109 in the ANTPNG2D

Psalms 109 in the AS21

Psalms 109 in the BAGH

Psalms 109 in the BBPNG

Psalms 109 in the BBT1E

Psalms 109 in the BDS

Psalms 109 in the BEV

Psalms 109 in the BHAD

Psalms 109 in the BIB

Psalms 109 in the BLPT

Psalms 109 in the BNT

Psalms 109 in the BNTABOOT

Psalms 109 in the BNTLV

Psalms 109 in the BOATCB

Psalms 109 in the BOATCB2

Psalms 109 in the BOBCV

Psalms 109 in the BOCNT

Psalms 109 in the BOECS

Psalms 109 in the BOHCB

Psalms 109 in the BOHCV

Psalms 109 in the BOHLNT

Psalms 109 in the BOHNTLTAL

Psalms 109 in the BOICB

Psalms 109 in the BOILNTAP

Psalms 109 in the BOITCV

Psalms 109 in the BOKCV

Psalms 109 in the BOKCV2

Psalms 109 in the BOKHWOG

Psalms 109 in the BOKSSV

Psalms 109 in the BOLCB

Psalms 109 in the BOLCB2

Psalms 109 in the BOMCV

Psalms 109 in the BONAV

Psalms 109 in the BONCB

Psalms 109 in the BONLT

Psalms 109 in the BONUT2

Psalms 109 in the BOPLNT

Psalms 109 in the BOSCB

Psalms 109 in the BOSNC

Psalms 109 in the BOTLNT

Psalms 109 in the BOVCB

Psalms 109 in the BOYCB

Psalms 109 in the BPBB

Psalms 109 in the BPH

Psalms 109 in the BSB

Psalms 109 in the CCB

Psalms 109 in the CUV

Psalms 109 in the CUVS

Psalms 109 in the DBT

Psalms 109 in the DGDNT

Psalms 109 in the DHNT

Psalms 109 in the DNT

Psalms 109 in the ELBE

Psalms 109 in the EMTV

Psalms 109 in the ESV

Psalms 109 in the FBV

Psalms 109 in the FEB

Psalms 109 in the GGMNT

Psalms 109 in the GNT

Psalms 109 in the HARY

Psalms 109 in the HNT

Psalms 109 in the IRVA

Psalms 109 in the IRVB

Psalms 109 in the IRVG

Psalms 109 in the IRVH

Psalms 109 in the IRVK

Psalms 109 in the IRVM

Psalms 109 in the IRVM2

Psalms 109 in the IRVO

Psalms 109 in the IRVP

Psalms 109 in the IRVT

Psalms 109 in the IRVT2

Psalms 109 in the IRVU

Psalms 109 in the ISVN

Psalms 109 in the JSNT

Psalms 109 in the KAPI

Psalms 109 in the KBT1ETNIK

Psalms 109 in the KBV

Psalms 109 in the KJV

Psalms 109 in the KNFD

Psalms 109 in the LBA

Psalms 109 in the LBLA

Psalms 109 in the LNT

Psalms 109 in the LSV

Psalms 109 in the MAAL

Psalms 109 in the MBV

Psalms 109 in the MBV2

Psalms 109 in the MHNT

Psalms 109 in the MKNFD

Psalms 109 in the MNG

Psalms 109 in the MNT

Psalms 109 in the MNT2

Psalms 109 in the MRS1T

Psalms 109 in the NAA

Psalms 109 in the NASB

Psalms 109 in the NBLA

Psalms 109 in the NBS

Psalms 109 in the NBVTP

Psalms 109 in the NET2

Psalms 109 in the NIV11

Psalms 109 in the NNT

Psalms 109 in the NNT2

Psalms 109 in the NNT3

Psalms 109 in the PDDPT

Psalms 109 in the PFNT

Psalms 109 in the RMNT

Psalms 109 in the SBIAS

Psalms 109 in the SBIBS

Psalms 109 in the SBIBS2

Psalms 109 in the SBICS

Psalms 109 in the SBIDS

Psalms 109 in the SBIGS

Psalms 109 in the SBIHS

Psalms 109 in the SBIIS

Psalms 109 in the SBIIS2

Psalms 109 in the SBIIS3

Psalms 109 in the SBIKS

Psalms 109 in the SBIKS2

Psalms 109 in the SBIMS

Psalms 109 in the SBIOS

Psalms 109 in the SBIPS

Psalms 109 in the SBISS

Psalms 109 in the SBITS

Psalms 109 in the SBITS2

Psalms 109 in the SBITS3

Psalms 109 in the SBITS4

Psalms 109 in the SBIUS

Psalms 109 in the SBIVS

Psalms 109 in the SBT

Psalms 109 in the SBT1E

Psalms 109 in the SCHL

Psalms 109 in the SNT

Psalms 109 in the SUSU

Psalms 109 in the SUSU2

Psalms 109 in the SYNO

Psalms 109 in the TBIAOTANT

Psalms 109 in the TBT1E

Psalms 109 in the TBT1E2

Psalms 109 in the TFTIP

Psalms 109 in the TFTU

Psalms 109 in the TGNTATF3T

Psalms 109 in the THAI

Psalms 109 in the TNFD

Psalms 109 in the TNT

Psalms 109 in the TNTIK

Psalms 109 in the TNTIL

Psalms 109 in the TNTIN

Psalms 109 in the TNTIP

Psalms 109 in the TNTIZ

Psalms 109 in the TOMA

Psalms 109 in the TTENT

Psalms 109 in the UBG

Psalms 109 in the UGV

Psalms 109 in the UGV2

Psalms 109 in the UGV3

Psalms 109 in the VBL

Psalms 109 in the VDCC

Psalms 109 in the YALU

Psalms 109 in the YAPE

Psalms 109 in the YBVTP

Psalms 109 in the ZBP