Revelation 22 (BOGWICC)

1 Ndipo mngeloyo anandionetsa mtsinje wamadzi amoyo, oyera ngati mwala wa krustalo ukutuluka ku mpando waufumu wa Mulungu ndi wa Mwana Wankhosa, 2 Ukuyenda pakati pa msewu waukulu wa mu mzindawo. Mbali iliyonse ya mtsinjewo kunali mtengo wamoyo, utabala zipatso khumi ndi ziwiri. Kubereka zipatso mwezi uliwonse. Ndipo masamba a mtengowo ndi mankhwala wochiritsa anthu a mitundu ina. 3 Sipadzakhalanso temberero lililonse. Mpando waufumu wa Mulungu ndi wa Mwana Wankhosa udzakhala mu mzindawo, ndipo atumiki ake adzamutumikira. 4 Iwo adzaona nkhope yake ndipo dzina lake lidzalembedwa pa mphumi zawo. 5 Sipadzakhalanso usiku. Sadzafuna kuwala kwa nyale kapena kwa dzuwa pakuti Ambuye Mulungu adzakhala kuwala kwawo. Ndipo adzalamulira kwamuyaya. 6 Mngeloyo anandiwuza kuti, “Mawu awa ndi okhulupirika ndi owona. Ambuye Mulungu wa mizimu ya aneneri anatumiza mngelo wake kudzaonetsa atumiki ake zinthu zimene ziyenera kuchitika posachedwapa.” 7 “Taonani, ndikubwera posachedwa! Wodala ndi amene asunga mawu oneneratu za kutsogolo a mʼbuku ili.” 8 Ine Yohane, ndine amene ndinamva ndi kuona zinthu izi. Ndipo pamene ndinamva ndi kuona izi ndinagwa pansi kuti ndipembedze mngelo amene amandionetsa zimenezi. 9 Koma mngeloyo anandiwuza kuti, “Usatero ayi! Ine ndine wotumikira monga iwe pamodzi ndi abale ako aneneri ndi onse amene amasunga mawu a mʼbuku pembedzani Mulungu.” 10 Kenaka anandiwuza kuti, “Usabise mawu onena zamʼtsogolo a mʼbuku ili chifukwa nthawi yayandikira. 11 Wochita zoyipa apitirire kuchita zoyipazo; wochita zonyansa apitirire kuchita zonyansazo; wochita zabwino apitirire kuchita zabwinozo; ndipo woyera mtima apitirire kukhala woyera mtima.” 12 “Taonani, ndikubwera posachedwa! Ndikubwera ndi mphotho zanga kuti ndidzapereke kwa aliyense malinga ndi zimene anachita. 13 Ine ndine Alefa ndi Omega, Woyamba ndi Wotsiriza, Chiyambi ndi Chimaliziro ndine. 14 “Odala amene achapa mikanjo yawo, kuti akhale ndi ufulu wopita ku mtengo wamoyo ndi kuti akalowe mʼzipata za mu mzindawo. 15 Kunja kuli agalu, amatsenga, achiwerewere, akupha anthu, opembedza mafano ndi aliyense amene amakonda bodza ndi kulichita. 16 “Ine Yesu, ndatuma mngelo wanga kuti achitire umboni uwu ku mipingo. Ine ndine Muzu ndi Chipatso cha Davide ndipo ndine Nthanda Yonyezimira.” 17 Mzimu Woyera ndi mkwatibwi akuti, “Bwerani!” Ndipo amene akumva anena kuti Bwerani! Iye amene ali ndi ludzu abwere, ndipo aliyense amene afuna alandire mphatso yaulere ya madzi amoyo. 18 Ndikuchenjeza aliyense amene akumva mawu onena zamʼtsogolo a mʼbukuli kuti, “Ngati wina awonjezerapo kalikonse, Mulungu adzamuwonjezera miliri imene yalembedwa mʼbuku ili. 19 Ndipo wina akachotsapo mawu onena zamʼtsogolo a mʼbuku ili, Mulungu adzachotsa gawo lake pa mtengo wamoyo ndi la mu mzinda woyera zimene zanenedwa mʼbuku ili.” 20 Iye amene akuchitira umboni pa zinthu izi akuti, “Inde, Ine ndikubwera posachedwa.”Ameni. Bwerani Ambuye Yesu. 21 Chisomo cha Ambuye Yesu chikhale ndi anthu onse. Ameni.

In Other Versions

Revelation 22 in the ANGEFD

Revelation 22 in the ANTPNG2D

Revelation 22 in the AS21

Revelation 22 in the BAGH

Revelation 22 in the BBPNG

Revelation 22 in the BBT1E

Revelation 22 in the BDS

Revelation 22 in the BEV

Revelation 22 in the BHAD

Revelation 22 in the BIB

Revelation 22 in the BLPT

Revelation 22 in the BNT

Revelation 22 in the BNTABOOT

Revelation 22 in the BNTLV

Revelation 22 in the BOATCB

Revelation 22 in the BOATCB2

Revelation 22 in the BOBCV

Revelation 22 in the BOCNT

Revelation 22 in the BOECS

Revelation 22 in the BOHCB

Revelation 22 in the BOHCV

Revelation 22 in the BOHLNT

Revelation 22 in the BOHNTLTAL

Revelation 22 in the BOICB

Revelation 22 in the BOILNTAP

Revelation 22 in the BOITCV

Revelation 22 in the BOKCV

Revelation 22 in the BOKCV2

Revelation 22 in the BOKHWOG

Revelation 22 in the BOKSSV

Revelation 22 in the BOLCB

Revelation 22 in the BOLCB2

Revelation 22 in the BOMCV

Revelation 22 in the BONAV

Revelation 22 in the BONCB

Revelation 22 in the BONLT

Revelation 22 in the BONUT2

Revelation 22 in the BOPLNT

Revelation 22 in the BOSCB

Revelation 22 in the BOSNC

Revelation 22 in the BOTLNT

Revelation 22 in the BOVCB

Revelation 22 in the BOYCB

Revelation 22 in the BPBB

Revelation 22 in the BPH

Revelation 22 in the BSB

Revelation 22 in the CCB

Revelation 22 in the CUV

Revelation 22 in the CUVS

Revelation 22 in the DBT

Revelation 22 in the DGDNT

Revelation 22 in the DHNT

Revelation 22 in the DNT

Revelation 22 in the ELBE

Revelation 22 in the EMTV

Revelation 22 in the ESV

Revelation 22 in the FBV

Revelation 22 in the FEB

Revelation 22 in the GGMNT

Revelation 22 in the GNT

Revelation 22 in the HARY

Revelation 22 in the HNT

Revelation 22 in the IRVA

Revelation 22 in the IRVB

Revelation 22 in the IRVG

Revelation 22 in the IRVH

Revelation 22 in the IRVK

Revelation 22 in the IRVM

Revelation 22 in the IRVM2

Revelation 22 in the IRVO

Revelation 22 in the IRVP

Revelation 22 in the IRVT

Revelation 22 in the IRVT2

Revelation 22 in the IRVU

Revelation 22 in the ISVN

Revelation 22 in the JSNT

Revelation 22 in the KAPI

Revelation 22 in the KBT1ETNIK

Revelation 22 in the KBV

Revelation 22 in the KJV

Revelation 22 in the KNFD

Revelation 22 in the LBA

Revelation 22 in the LBLA

Revelation 22 in the LNT

Revelation 22 in the LSV

Revelation 22 in the MAAL

Revelation 22 in the MBV

Revelation 22 in the MBV2

Revelation 22 in the MHNT

Revelation 22 in the MKNFD

Revelation 22 in the MNG

Revelation 22 in the MNT

Revelation 22 in the MNT2

Revelation 22 in the MRS1T

Revelation 22 in the NAA

Revelation 22 in the NASB

Revelation 22 in the NBLA

Revelation 22 in the NBS

Revelation 22 in the NBVTP

Revelation 22 in the NET2

Revelation 22 in the NIV11

Revelation 22 in the NNT

Revelation 22 in the NNT2

Revelation 22 in the NNT3

Revelation 22 in the PDDPT

Revelation 22 in the PFNT

Revelation 22 in the RMNT

Revelation 22 in the SBIAS

Revelation 22 in the SBIBS

Revelation 22 in the SBIBS2

Revelation 22 in the SBICS

Revelation 22 in the SBIDS

Revelation 22 in the SBIGS

Revelation 22 in the SBIHS

Revelation 22 in the SBIIS

Revelation 22 in the SBIIS2

Revelation 22 in the SBIIS3

Revelation 22 in the SBIKS

Revelation 22 in the SBIKS2

Revelation 22 in the SBIMS

Revelation 22 in the SBIOS

Revelation 22 in the SBIPS

Revelation 22 in the SBISS

Revelation 22 in the SBITS

Revelation 22 in the SBITS2

Revelation 22 in the SBITS3

Revelation 22 in the SBITS4

Revelation 22 in the SBIUS

Revelation 22 in the SBIVS

Revelation 22 in the SBT

Revelation 22 in the SBT1E

Revelation 22 in the SCHL

Revelation 22 in the SNT

Revelation 22 in the SUSU

Revelation 22 in the SUSU2

Revelation 22 in the SYNO

Revelation 22 in the TBIAOTANT

Revelation 22 in the TBT1E

Revelation 22 in the TBT1E2

Revelation 22 in the TFTIP

Revelation 22 in the TFTU

Revelation 22 in the TGNTATF3T

Revelation 22 in the THAI

Revelation 22 in the TNFD

Revelation 22 in the TNT

Revelation 22 in the TNTIK

Revelation 22 in the TNTIL

Revelation 22 in the TNTIN

Revelation 22 in the TNTIP

Revelation 22 in the TNTIZ

Revelation 22 in the TOMA

Revelation 22 in the TTENT

Revelation 22 in the UBG

Revelation 22 in the UGV

Revelation 22 in the UGV2

Revelation 22 in the UGV3

Revelation 22 in the VBL

Revelation 22 in the VDCC

Revelation 22 in the YALU

Revelation 22 in the YAPE

Revelation 22 in the YBVTP

Revelation 22 in the ZBP