Revelation 8 (BOGWICC)
1 Atatsekula chomatira chachisanu ndi chiwiri, kumwamba kunakhala chete mphindi makumi atatu. 2 Ndipo ndinaona angelo asanu ndi awiri aja amene amayimirira pamaso pa Mulungu, akupatsidwa malipenga asanu ndi awiri. 3 Mngelo wina amene anali ndi chofukizira chagolide anabwera nayimirira pa guwa lansembe. Anapatsidwa lubani wambiri kuti amupereke pamodzi ndi mapemphero a anthu onse oyera mtima pa guwa lansembe lagolide patsogolo pa mpando waufumu. 4 Fungo la lubani pamodzi ndi mapemphero a oyera mtima zinakwera kumwamba kwa Mulungu kuchokera mʼdzanja la mngeloyo. 5 Kenaka mngeloyo anatenga chofukizira nachidzaza ndi moto wochokera pa guwa lansembe ndi kuponya pa dziko lapansi ndipo nthawi yomweyo panachitika mabingu, phokoso, mphenzi ndi chivomerezi. 6 Angelo asanu ndi awiri anakonzekera kuyimba malipenga asanu ndi awiri. 7 Mngelo woyamba anayimba lipenga lake ndipo kunabwera matalala ndi moto wosakanizana ndi magazi ndipo unaponyedwa pa dziko lapansi. Gawo limodzi la magawo atatu a dziko lapansi linapsa, gawo limodzi la magawo atatu a mitengo linapsa ndi gawo limodzi la magawo atatu a udzu wauwisi linapsanso. 8 Mngelo wachiwiri anayimba lipenga lake, ndipo chinthu china chooneka ngati phiri lalikulu loyaka moto, chinaponyedwa mʼnyanja. Gawo limodzi la magawo atatu a nyanja linasanduka magazi. 9 Gawo limodzi mwa magawo atatu a zolengedwa zonse zamoyo za mʼnyanja, linafa, ndipo gawo limodzi la sitima za pamadzi linawonongedwa. 10 Mngelo wachitatu anayimba lipenga lake, ndipo nyenyezi yayikulu, yoyaka ngati muni inachoka kumwamba nigwera pa gawo limodzi la magawo atatu a mitsinje ndi pa akasupe amadzi. 11 Dzina la nyenyeziyo ndi Chowawa. Gawo limodzi la magawo atatu a madzi anasanduka owawa ndipo anthu ambiri anafa chifukwa cha madzi owawawo. 12 Mngelo wachinayi anayimba lipenga lake, ndipo chimodzi cha zigawo zitatu za dzuwa, za mwezi ndi za nyenyezi zinamenyedwa kotero chimodzi mwa zitatu za zonsezi zinada. Panalibenso kuwala pa chimodzi mwa zigawo zitatu za usana, ndi chimodzimodzinso usiku. 13 Ndinayangʼananso ndipo ndinaona ndi kumva chiwombankhanga chimene chinkawuluka mlengalenga kwambiri chikuyankhula mofuwula kuti, “Tsoka, Tsoka! Tsoka lalikulu kwa anthu okhala mʼdziko lapansi, angelo otsala aja akangoyimba malipenga awo!”
In Other Versions
Revelation 8 in the ANGEFD
Revelation 8 in the ANTPNG2D
Revelation 8 in the AS21
Revelation 8 in the BAGH
Revelation 8 in the BBPNG
Revelation 8 in the BBT1E
Revelation 8 in the BDS
Revelation 8 in the BEV
Revelation 8 in the BHAD
Revelation 8 in the BIB
Revelation 8 in the BLPT
Revelation 8 in the BNT
Revelation 8 in the BNTABOOT
Revelation 8 in the BNTLV
Revelation 8 in the BOATCB
Revelation 8 in the BOATCB2
Revelation 8 in the BOBCV
Revelation 8 in the BOCNT
Revelation 8 in the BOECS
Revelation 8 in the BOHCB
Revelation 8 in the BOHCV
Revelation 8 in the BOHLNT
Revelation 8 in the BOHNTLTAL
Revelation 8 in the BOICB
Revelation 8 in the BOILNTAP
Revelation 8 in the BOITCV
Revelation 8 in the BOKCV
Revelation 8 in the BOKCV2
Revelation 8 in the BOKHWOG
Revelation 8 in the BOKSSV
Revelation 8 in the BOLCB
Revelation 8 in the BOLCB2
Revelation 8 in the BOMCV
Revelation 8 in the BONAV
Revelation 8 in the BONCB
Revelation 8 in the BONLT
Revelation 8 in the BONUT2
Revelation 8 in the BOPLNT
Revelation 8 in the BOSCB
Revelation 8 in the BOSNC
Revelation 8 in the BOTLNT
Revelation 8 in the BOVCB
Revelation 8 in the BOYCB
Revelation 8 in the BPBB
Revelation 8 in the BPH
Revelation 8 in the BSB
Revelation 8 in the CCB
Revelation 8 in the CUV
Revelation 8 in the CUVS
Revelation 8 in the DBT
Revelation 8 in the DGDNT
Revelation 8 in the DHNT
Revelation 8 in the DNT
Revelation 8 in the ELBE
Revelation 8 in the EMTV
Revelation 8 in the ESV
Revelation 8 in the FBV
Revelation 8 in the FEB
Revelation 8 in the GGMNT
Revelation 8 in the GNT
Revelation 8 in the HARY
Revelation 8 in the HNT
Revelation 8 in the IRVA
Revelation 8 in the IRVB
Revelation 8 in the IRVG
Revelation 8 in the IRVH
Revelation 8 in the IRVK
Revelation 8 in the IRVM
Revelation 8 in the IRVM2
Revelation 8 in the IRVO
Revelation 8 in the IRVP
Revelation 8 in the IRVT
Revelation 8 in the IRVT2
Revelation 8 in the IRVU
Revelation 8 in the ISVN
Revelation 8 in the JSNT
Revelation 8 in the KAPI
Revelation 8 in the KBT1ETNIK
Revelation 8 in the KBV
Revelation 8 in the KJV
Revelation 8 in the KNFD
Revelation 8 in the LBA
Revelation 8 in the LBLA
Revelation 8 in the LNT
Revelation 8 in the LSV
Revelation 8 in the MAAL
Revelation 8 in the MBV
Revelation 8 in the MBV2
Revelation 8 in the MHNT
Revelation 8 in the MKNFD
Revelation 8 in the MNG
Revelation 8 in the MNT
Revelation 8 in the MNT2
Revelation 8 in the MRS1T
Revelation 8 in the NAA
Revelation 8 in the NASB
Revelation 8 in the NBLA
Revelation 8 in the NBS
Revelation 8 in the NBVTP
Revelation 8 in the NET2
Revelation 8 in the NIV11
Revelation 8 in the NNT
Revelation 8 in the NNT2
Revelation 8 in the NNT3
Revelation 8 in the PDDPT
Revelation 8 in the PFNT
Revelation 8 in the RMNT
Revelation 8 in the SBIAS
Revelation 8 in the SBIBS
Revelation 8 in the SBIBS2
Revelation 8 in the SBICS
Revelation 8 in the SBIDS
Revelation 8 in the SBIGS
Revelation 8 in the SBIHS
Revelation 8 in the SBIIS
Revelation 8 in the SBIIS2
Revelation 8 in the SBIIS3
Revelation 8 in the SBIKS
Revelation 8 in the SBIKS2
Revelation 8 in the SBIMS
Revelation 8 in the SBIOS
Revelation 8 in the SBIPS
Revelation 8 in the SBISS
Revelation 8 in the SBITS
Revelation 8 in the SBITS2
Revelation 8 in the SBITS3
Revelation 8 in the SBITS4
Revelation 8 in the SBIUS
Revelation 8 in the SBIVS
Revelation 8 in the SBT
Revelation 8 in the SBT1E
Revelation 8 in the SCHL
Revelation 8 in the SNT
Revelation 8 in the SUSU
Revelation 8 in the SUSU2
Revelation 8 in the SYNO
Revelation 8 in the TBIAOTANT
Revelation 8 in the TBT1E
Revelation 8 in the TBT1E2
Revelation 8 in the TFTIP
Revelation 8 in the TFTU
Revelation 8 in the TGNTATF3T
Revelation 8 in the THAI
Revelation 8 in the TNFD
Revelation 8 in the TNT
Revelation 8 in the TNTIK
Revelation 8 in the TNTIL
Revelation 8 in the TNTIN
Revelation 8 in the TNTIP
Revelation 8 in the TNTIZ
Revelation 8 in the TOMA
Revelation 8 in the TTENT
Revelation 8 in the UBG
Revelation 8 in the UGV
Revelation 8 in the UGV2
Revelation 8 in the UGV3
Revelation 8 in the VBL
Revelation 8 in the VDCC
Revelation 8 in the YALU
Revelation 8 in the YAPE
Revelation 8 in the YBVTP
Revelation 8 in the ZBP